Bungwe loyendetsa zisankho m'dziko muno la MEC lapempha anthu omwe analembetsa pa mavoti kuti akatsimikize ngati maina awo ali mu nkaundula ndipo izi zichitika lachitatu ndi lachinayi sabata ino. Watsimikiza zankhaniyi ndi mneneri wa bungwe… ...