Pamene oyankhula pa fesibuku Joshua Chisa Mbele yemweso ndi mmodzi mwa akuluakulu abungwe la Citizens Against Impunity and Corruption waitanitsa zionetsero sabata yamawa, Bon Kalindo yemwe mmbuyomu analankhula kuti 'a Malawi siowafela' wati akachita nawo… ...