Police Commissioner for Central region Mr. John Nyondo has advised his officers in Dowa to dedicate themselves to duty.
The commissioner made the remarks in Dowa where he was the guest of honour in a Station Executive Committee Meeting (SEC) on Friday.
Addressing the officers before the (SEC) Meeting, the central region police Boss said the police have the noble job of creating a safe and secure Malawi.
“For us to achieve this we should follow Police Procedures and discipline, and put God first, as Police is a God given Job,” said the Commissioner.
He highlighted that the police need to be alert while on duty.
He further thanked the police officers for reducing the crime in the second quarter to 30.4% and asked them to put extra gear to reduce road accidents in the District as they were high with 8.1% Compared to the first quarter.
Tulo ndi nkhondo
Palimbe muthu yemwe sagona iwonso ndi athu sangalephere kugona
Kumpeza akugona kumuombera basi
Expected results from sleepless off hours, use of drugs & alcohol whilst on duty,
Tel them
Slap him first
Azigona akawalala akazawabela mfuti ntchito izathele pompo!
Kkkkkkkk timagona bwanji
Ndekuti amagona??? Chipongwetu ichi….
Bwanjinso apa, ndiye kt katangare wavuta kumeneku eti, tiuzeni zoona
Sindumuziwa Wa Police Amakhala Kut Amagwira Tchito Yanyi Nanga K Malawi Aliko
why advising them,what does the rule say when someone sleeping on duty
No simbunzi kkkk koma angowasova ndima fine
kumangowapatsa ma fine k20000 kuti asamagone osachotsa tchito
Kungowachotsa amene akumagonawo, sakufuna kugwira ntchito salary yawo ndikuwaonjezera anzawo akulimbikira ntchito basi.
umbuli ndi matenda eti? paja police mumayifuna mukavutika, siku lina udzaona ubwino wa police…
Kodi Ku Malawi kuli polisi?bolaso G4 security. Mbuzi za apolisi.