Ganizo loti a Sidik Mia alowe chipani chotsutsa cha Kongeresi kukhala ngati likuwadwalitsabe mutu akuluakulu a chipani cholamula cha DPP.
Nduna yoona zofalitsa nkhani mu dziko muno amenenso ndi m’dindo mu chipani cholamulachi adatonza a Mia kudzela pa wailesi ya MBC.
Malinga ndi ndunayi a Nicolas Dausi, ati Bambo Mia ndi munthu odalila ndalama basi kuti apeze maudindo pandale.
“Tiwalangize anzathu a Kongeresi, asamangotenga anthu ndi kuwapatsa udindo kamba koti ali ndi ndalama,” anatelo a Dausi amene anakhalapo wamkulu wa Kongeresi asanasinthe thabwa kupita ku DPP.
A Dausi anati a Mia akugwiritsa ntchito ndalama zawo kuti agule udindo wa wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha Kongeresi.
Kuyamba pamene a Mia analengeza kuti alowa Kongeresi, akhala akuthilidwa nkhoko ndi akuluakulu a chipani cha DPP kuphatikizapo mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika.
A Mutharika ananena kuti a Mia anagula MCP pa mtengo wa K200 million.
LETS TRY TOLK ZOTITANDIZA TIZINGONYOZANA MAPETO AKE MKUMANGOSAUKA MKWABWINO TILIKE ZATSOGOLO LATHU ANTHUWA NIANDALAMA KALE TINGOPDNGA NDIFE
DPP yonse yopusa,sitingabwelenso mbuyo mwa DPP chifukwa atibela nthawi yayitali soprano tazindikila
Asadwale amenewo ankayesa anthu one azakhala nawo? Boma lobela ndichoncho spite basis siyikuwafunanso zitsilu ngati zimenezi
Kodi Mia alindin’chiani?.
Amiaaaa MCP yake iti? kapena asithetu dzina la chipani chimene alowacho osatelo akamufuse TEMBO & MULUZI alibenawo DPP kapena MAI wamuthawa MALAWI akukomayu.DPP more fire.
Chorus ya MCP “Abera mavoti” remix will released 2019
Sidik mmene MCP ili mboma mkuti Ali mzaka xohepa
Sleepless why,??
Amalawi tidzasiya liti kunyozana
Mia is a political prostitute. He started with UDF and then DPP later PP and. today he is in MCP such a character cannot be. trusted. He will not not bring any impact to. MCP.
Mbuli ya munthu iyi olo wapita ku mcp dpp 2019 bomaaaa!
Andale musamawakhulupilile zao zinayela kale chuma alinacho iwe ndiine palibe chathu amadya okha ndi ana awo bola za church kusiyana ndi ndale sitimadya ndale timadya nsima amalawi tinachuluka uchitsilu timangotengeka ndi zaziiii kusapota zipani kunyumba kulibe chakudya
Dpp sikugona tulo pano alibizy kupita nsanje
PAKATI PA A ISILAEL NDI AFILISITI GOLIATI ANKATAMA MPHAMVU ,DZIDA ,UKATSWIRI KOMA MODZICHEPETSA DAVID ANADALIRA MULUNGU NDIPO NKHONDO ANAPAMBANA .OTEMBELELEDWA NDI AMENE ATAMA MKONO WA MUNTHU KUSIYA MULUNGU.AMALAWI YAKWANA NTHAWI YOTI TIFUNSIRE KWA MULUNGU POPEMPHERA OSATI PONYOZANA.
PAKATI PA A ISILAEL NDI AFILISITI GOLIATI ANKATAMA MPHAMVU ,DZIDA ,UKATSWIRI KOMA MODZICHEPETSA DAVID ANADALIRA MULUNGU NDIPO NKHONDO ANAPAMBANA .OTEMBELELEDWA NDI AMENE ATAMA MKONO WA MUNTHU KUSIYA MULUNGU.AMALAWI YAKWANA NTHAWI YOTI TIFUNSIRE KWA MULUNGU POPEMPHERA OSATI PONYOZANA.
Amaupola mabi aneyo?
MUNTHU OPANDA NZELU NDIAMENE ANGADZASANKHE DPP KODI AMALAWI SITICHEDWA KUIWALA MBAVA NGATI ZIMENEZI
20 19 kudzavotelaso dpp ndiye uzungulira mutu
Nkhawa Nje Dpp ndi more fire 2019 bomaaa!
kkkkkkk a sidiki angoona kuti gwanda wafa kupita ku mcp akuona ngati akakhala president wa mcp
MCP oooooooyeeeee
Pano nkhani ndi ndalama nafenso tikuzifuna ukwiiiiiiï ali kuti wadholayo tisanangomvera cashgate.
pamalawi pano yakula ndidyela basi mcp sidzalowa boma anthu oipa kwambiri amenewa anyani mikango athakati?
osee andale tikumana 2019
mia sadziwa ndale amagwilitsa ntchito ndalama zake timuona 2019 ngati angawine
Mtengo wolephera nyani…chalaka bakha…Zidamukanika munthu wamkulu Gwanda Chakuamba izi…nzokanika ma member…stingavotere mcp ife…magazi ali chuuuu
Dpp Bomaaaaaaa
There shall be a big fall like a big ax cutting a big tree falling in a big sea what a big fall shall be heard in 2019 Landslide even Lake slide
vote ndimtima makoswe mlongolola for nothing!
MCP NOT MY TYPE
12/08/2017
Geetings friends wherever you are .
we have created this group Malawi Youth Parliament solely for us the Youth so that we can share political, economic, social and technological affairs affecting our nation.
we need members from at least every constituency in Malawi.
I therefore ask you to introduce yourself and the constituency you represent in this august house. by default you are the shadow mp of that constituency
You as well tell us the party you represent. The administration will be very serious to take note of the constituency and the representative plus the party he belongs to.
I therefore advise you honorable members that only issues of national interest will be discussed here.
No politics of castigation and name calling . misbehaving members will face two cautions then a disciplinary hearing later if such a member prove to be of the contrary agenda of the group shall face dismissal from the group.
forward the message to those interested to join so that they submit their details eg full names ,age, constituency and favourite party to any of these contacts: 0882024002
0886826626
0999748763
0992486973
incase the desired seat is occupied the aspirant shall still be added on the group.
We are the Youth
we are the majority
we are the leaders of today
together we can build a better Malawi.
This message is brought to you with the help of GCK CAMERAS the only cameras that have no limit in capturing information .
May God bless Malawi
By the Group administration.
Ntipanga deportee kikikk
Nyansizo ife ai
sanatitu #19—-#kwacha¡¡!!!!¡
Dpp Boma Irooooooo!!!!!!! Mwayamba Kale Kunjenjemera2 Munjenjemerad Musanat Achpani Cha Business Inu Named Mumat Chan Tambala Wa Red Nt Wakuda Shame
ndimaganizo anu amenewo
Mia or patavuta bwanji sangadwalise mutu DPP 2019 tikudusa mosavuta
Malawi 24 you are waisting your time and resources
DPP woyeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee
Palibe mmwachita tikukathaninso
Apite tilibe naye ntchito iyaaa
Unapitako mkuwapeza alimmaso??gossiper of the century you are so fake ishh yosagonetsayo nikhala kwacha l doubt
Let us all wait for the by elections results as that will be our litmus test. Am telling you MCP is sweeping all the seats including Nsanje lalanje constituency. Amene akutsutsa betch K20,000 ndisitika. molimba mtima.Chakwera is a very tactical guy and DPP is very frustrated with how Chakwera has blown off all the sponsored Nkholokolo
Hahaha kd anthu angovotere Mcp cz kuli mia ngt DDP inagwesa chipani cholamura palibe cholepheresa DDP woyeee!
MWASOWA ZOKAMBA INU ANYASA MCP MUKUNAMA MIA TIKUMUDZIWA AKUNGOFUNA UDINDO BASI MUKALUZA MUZIZATI MWABELEDWA MUONA SIMUNATI TINAWINA TISALI MBOMA PANO NDILANTHU MUKUONANGATI TINGALUZE MWALEMBA MADZI CHULE WAWELENGA
Sanati avina mia ndi katundu
Kkkk MCP kumayiopa manyaka achipani ngati awa…….tabayimbani nyimboyo….
Amalawi sangasiye kukamba za ndale chifukwa tsogolo lao limakhala m’manja mwa anthu andale omwe amayendesa boma Amalawi mukhulupirile kuti pattern ya kavotedwe 2019 ikhala yosiyana ndi zisankho zonse za m’buyomu panopa a malawi azuka
Sindisowa kukamba zamia ai akanakhala dolo akanayamba chipani chake osati kunjowina munthu ndiye munthu wake kukhala mcp pano amalawi amaziwa ndale zoti awa ndi andalama zinapita ndi aja lero anthu akufuna mavuto adera lao
Inuyo Ndamene Ikukuwawitsani Mutu DPP , Mia Mkachaniso Via Naeni Ukoo, Mxiiii
Inuyo Ndamene Ikukuwawitsani Mutu DPP , Mia Mkachaniso Via Naeni Ukoo, Mxiiii
Tidzona Nd Mcp Yanuyo
Wakumudzi ndiamene woona ndi maso kuti njala yatha ndi ulamuliro wa professor. whether N, C, S or E ndale zapakamwa anthu anatopanazo ask PP -DPP2019 Bomaaaaaa
Ok
paja mumadya ndale…… onsewo muwauze fotsek zawo!!! instead of concentrating za mavuto kumidzi ndikibwelesa ma opportunities kwa anthu kuti azipeza kenakake!!! busy kuononga ndalama n kumakangana za ziiiii……. achule
Kkkkkkkk kulota saletsa
Inu mwamva kwandani?
Whether Mia is buying his way into MCP is none of dpp’s business. basi munthu nkulukulu kumakhala pa kanema kupanga miseche ati kufuna kusiocheretsa a Malawi.Nkhani yakula apa ndi yakuti Lower Shire tsopano ndi ya MCP whether one likes it or not. Not only lower shire but even some parts of Blantyre, Mwanza, Neno, zomba, machinga, Mangochi and balaka. Wina afa ndi kadyakarista chaka chino.
nthawiyomwe ndimkasapota pp ndinkadana ndianthu omwe amkanena kti pp sidzawina chisankho ndipo idaluzadi.pano anthu omwewo,akuti dpp sidzawina,akumwela komkunosotu.apa ndikuti dpp paulendo
Sanati a DPP nanga achoka ujeni Ku DPP ko ndiye atsekula mmimba
Guyz to say the truth Mia amaziwa ndale even chitukuko nanga peter wapangapo chani anthu akufa ninjala nipomwe akuti ine nilibe problem what kind of a leader is he malo momvera chisoni anthu ake I remember kamuzu anati mukufuna matiparty is a dirty game pano ni izi mukutukwanana cz of ndale kulorela kuphana but 2019 mulungu azatisankhira mtsogoleri
ADausi, adausi ndale ayamba liti. Aaaaaa ndale zaosauka ndiizi akumaba ndalama mbomazitu, president analowa alibe chilisonse pano alindi ndalama azitenga kupi? Adausi analibe ngakhale kozlkakha APA azitenga kuti? Zakuba basi!!!! Amusiye aliyese ali ndi kufuna kwake
Mia,? DPP sleepless? Mia is not a new politician but another political Thief. Which party doesn’t he joined? Si uja anasiya mtembo wa Bingu mnyumba kukalowa Pp chifukwa cha dyera uja?
Am agree with you that is true
Amalaw simukuziw kt miya akukasokonez zithu kt dpp izaduse bwino lomwe?kumbukilan bakili ndi tembo.kaya tikuwonelan
Kodi BP ilekelenji ngati mtsogoleli waDPP wamela tsembwe ndichiganizo chaSidic Mia akanene atonkhwetonkhwe alimmbali mwake zimphwisi zokhazokha, koma 2o19 palikusiyanitsa pakati paNjovu ndimbuzi wamphavu ndindani.
There’s no credible election in Africa. Free & fair on voting with electronic hacked on the process of counting. Yours will not be different.
All pipo u talking about DPP forget ths coming election its for MCP no matter what unles mzabeleso a DPP koma ulendo uno mwachela msapha masana nkhanga zaona MCP boma 2019
DPP go to hell palibe akukufunani mbava inu muli shit kwambiri, forsake!!!!!
Koma yah ma cadet paja ayamba kale kuthulura simunati mutha muona, DPP ya chani? Zazii mwapanga chani zokonza economy ya mw
Malawi sasamva.Inu tayambitsani chipani china inu,komatu nthawi mulinayo,Muzalira mutalephelanso.Ife a malawi tikufuna zipani zatsopano apo bii Uyu ndiye sazatheka kuchosedwa m’boma.INU MUSACHEDWE NDI MCP INU.OOH AYI IFE ATHU NDI MASO.
Km nde wauza tu kkkkk
Zaziii DPP boma
Ife monga amalawi ctngalore MCP muno bcoz w remember what was happened my yrs ago!!!!!
Evey day story about Mia and Dpp mmmmmm news zinazi
never ever will MCP win the government…forget and stop dreaming
mumalo molimbana ndiumphawi wadziko kapena ndiumphawi wa anthu mudziko muno mulibusy kulimbana ndi a Mia asaaaaaaa create job opportunities tikufuna ntchito ife asaaaaa
DPP game yakula
Kodi mia pandale za Malawi adapangapo chani choziwika kuti anthu azimunjejemera? Let them celebrate azalira mia mcp italepheraso pa chisakha azakumbukira agogo ake ku India.
Mukungolankhula ndale simuzidziwa ndale ndi majority, Mia ukumunenayo ndiodziwika bwino kuposa Peter pandale UDF yachitako bwino ku Lowershire kaamba ka Mia Sindikudziwa kuti muziti MCP siingalowe m,boma koma ndinu amoyo kapena mitembo? uziyang’ane wekha ulipo ufuse Dzulo la MCP linalibwanji oneso pa Post iyi ndi angati ali mbali yako? uona wekha kuti anthu sakuikonda DPP ya Petulo
Kkkkkkkk Koma mukulankhulatu Eish! Nkhani yake yazipani? Guyz chomwe tikuenela kudziwa ndichakuti Malawi walero simalawi yamakolo athu. Zinthu zinasintha ndipo tangoyenela kuvomeleza KUTI ifeyo tikumana ndizambiri sitinati, koma ndipemphe nawo KUTI ifeyo ngati Amalawi chonde tisiye kulankhulilana mau achipongwe, ndikunkhulipila kuti tonse timadziwa KUTI anthuwa akamakangana kumakhala kulimbilana ifeyo nde tisamaone ngati akufuna kutithandiza akungofuna kumatingwilisa ntchito koma tisalole kunyozana ndikulankhulilana mau onyoza . aliyense angokhala ndizimene amakhulupilila basi. Ndipo sizingatheke kuti aliyense apange zofanana ndiwina. Tonse nda Malawi dziko ndilathu tiyeni tikondane
Maloto a mphaka munthu wanzeru zake angamaganize zoti mcp ingawineso 2019 dpp koma mosemuja yakhalila ikukukwapulani muja simumamvetsabe?
Amenewatu adwala ndithu asadati
PP 2019 BOMA!!!!!!!!!!
mcp should concetrate in the north & some parts of cetral region where dpp enjoys some support.mia wil contribute nil in the south.muluzi tried to back up mcp it did not materialise.
mcp winning unless if all the votes in thyolo mulanje phalombe chiradzulo zomba blantyre mwanza mneno will be null and void.will ntcheu vote mcp this time massively. will the yao people of balaka machinga and mangochi vote not UDF and dpp second and mcp zero.what about Lilongwe city, ntchisi yoyamika nseu onwe a mcp sanamangile for thirty years.nkhotakota north and sourth.mcp kaya mukwiye cant outsmart Dpp.Dpp will come first and mcp second with a difference of over 400 thousand votes.
a difference of one million…dpp is alone in the south
Ndaknyada MCP yachaniso? munpatuze chani inu ngati ukuyaka wauwisi kulbwanji ouma? Malawi sazatheka usatmate phula kti ndiwe wanzeru Demeti!
Kulra Kwa Mnthu Wamwamuna Bolan Tibwelele Ku Mcp
To be honest am agree with you big boss akunama awa akusowa zonena
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Iwe, this is not 2014. Even myself am based in BT with my family but will vote for MCP. Sitonse Ku south kuno tili opepera enafe tidasukusula kalekale mwene
Dpp motoo kuti buuuuuuuu
Well said brother DPP woyeeeeee
Zanu izoo ife eniake a Congress tili pheee 2019 bomaaaa
Who is mia?
NGATI MIA ANALUZA MA VOTE NGATI MP HOW CAN DPP HV INSOMNIA. NAAA TIONANA PA 2019 POMPO
None of my business
mia si okhazikika thus a problem.
Mukumu tamandira Mia munthu wothawa maliro a malemu Bingu Ali mu nyumba kulephera ndi kukapepesa nkomwe pamene malemu amamutenga ngati mwana wache amamukonda kwambiri pa nduna zonse, Alibe khalidwe ameneyu, JB kumunena kuyenda ngati bakha, shaaaa
Mia or u MP sawina
Kkkkkk Amalawi 24 Tawoneni Anthu Akukanganatu Awa Akamenyana Ine Sindiwalelesatu Owooo! Kkkkkk
Yes that is ma Igwe Martin Chidothie good point
palibe angadwale ndi mia, asakumuziwa mia ndani, d p p singatekeseke olo half, ndi mia ai, ndiponso akabweze ndrama zonse amatenga BINGU asanamwalile amaona ngati sizingakumbukilike, komanso asalowe mu m c p kufuna kukangogawanisa anthu kuwaombanisa mutu ai, palibe d p p singagwedezeke antaaa oolo oloo.
Koma inu amene mukumatibe dpp dpp booma timitu tanuto timagwila tchito kapena timayendela mamina timagwila chito mukamkhala mwadwala chimfin taganizan momwe ife akumidzife momwe tikuzuzikila timadalira ulimi koma taganizan zipangizo zaulimi momwe zikudulila pamene mbeu mitengo mukugula nayo mbeuz ndiye zakufwed
Munyoxananji apa tee va ziiiiiii ndale simungazikwanitse Zonse amadxiwa ndi mulungu
Guys lets keep quite untill date
ONSE AKUONANGATI SIZITHE ULENDO UNO AKHUMUDWA TOSE ACHILUNGAMO TAKUCHOKERANI KWANGOKHALA AKATSIRI AKUBA ADATHAWA KU MCP
Chosagonela tulo nchani pamenepo poti Mia wachoka ku opposition kujoinanso opposition
Ulamuliro uliwonse mmati oipa mukuona ngati yesu angabwere kuzakhala president Ku Malawi,sankhani ndiye emwe mukuona kuti angazakhale 100%,mmalawi zazatheka amwene
Mukazalamuliranso dziko lino a MCP iwalani….ife cheteee pamboyo pa DPP
Idzakhalanso landslide
A Sidik miawo atani kuti mpaka anzawo anjenjemere,zamkutu,tizingochiphunzira Ku school basi ngat history osati kuzachivotera iyaa
Mia yemweyo kuti wa wa wa
daily ndale kuleka kumagwira ntchito kuti mutukule umoyo wanu hahaha amalawi ndichifukwa tikukumana ndiumphawi nthawi zonse kodi ndale zimadibwa? azanu mukulimbana nawowo chuma mkutapa kutaya koma iwe osauka uli ngaaaa!!! pandale hahaha try to improve your daily life not politics.
Ana achepa awa udzingokhalira yotsutsa zaka kumapita uku akuyimba nyimbo yoti tidzatenga boma munalamura mbuyomo panakwana mukufunso chani a MCP???
What Washington can see sitting down cannot be spotted by the Malawi Opposition in a tree… 2019 APM bomaaasss
Kodi Mia ndiye uti?
Kwachaaaaaa wina akomoka
Mwaona inu a MCP mukutokota kwambiri ndie tikadzakunyenyani 2019 ino muzizanamizira kuti takubelani chonsecho inu muli ndi machimo ambiri omwe simunaulapire mtundu Wa amalawi inu amangotsutsa zilizonse osafunako or kuyamikira nkhwidzi basi mudzaziona koma osadzafa ndi ma bp
nde chosagoneraturo ndchan
Eeeh zanu izo odi ndidye nsima ya denje ine!!!
mmmmm! tikuziwa kuti nanu a malawi 24 palibe chomwe mungatiuze chanzeru,koma ndikukuuza kuti muzalira ndipo muzakhumudwa with or without mia dpp ikulowanso ndipo muzabweza ti ndalama tomwe chipani chamagazi chakupasanizo
Ndwe mmlomwe etttiiiiiiiiiii? oky! Tionana 2019 bola musadzabelenso ngat 2014 ija. Komansoooo! Aaaaa! kaya ndit chani kaya? Oky! Takutulukirani tsopano. Mufunaaaa! Aaaaa! Koma Amalawi,inu!!!!!!!
Vuto mwabadwa dzulo mukadzipenta akupasani k50 mwati chipani ndi DPP ndiwe gwirize mkakodze ndiye chifukwa ,koma dziwakuti ,dzulo simawa kunali yani ,anthu amalawa analawa MCP mu chipani chimodzi ,ali tilawe democracy, UDF,DPP1,DPP2 ,aona kuti democracy ndiyabwino koma ,ikugwilitsidwa molakwika, funso mkumati payokha MCP imaopa ndikulemekeza a Malawi kodi mu Democracy ipanga zotani ?
Mia akupereka chiospezo ku DPP thax a fact..!
Amva nyunyunyu
Mia wapelekadi food for thought mchupanichi but politics in multi party era it’s a game of numbers. They have to think how they can get the numbers. The people who are to push it on another levels are leaders themselves. They are the vision of DPP. Is DPP Loved by all, if not why? What is the way forward? PULL SOCKS UP
My vote fo black cock over my dead body
Palibe kanthu apa anali kale uyu
MCP ndi chipani chosusa mpaka kale nkhaza zomwe anapangira Malawi palibe angaiwale ikachoka DPP bola tizabwerere kwa chair osati MCP iyaaaah kutaya nthawi kuganiza zimenezo
Sanati adwala kkkk
mmmmmmmmmmm …… Kodi Mia Mchani….mchakudya?
Nonsense..These were the outcome of past Elections.1999. former Might ALFORD plus MCP=Nil.2009 Achair and UDF plus MCP=Nil. 2004 BJ and NDA plus Tembo and MCP=Nil… How special is Sidik MIA if I may ask? If not careful 2019.MCP seems over confidence may end up loosing also
Abwerera ameneyo dpp ikawina apo ayi akufuna pitchukira then azayambise chipani chake lets wait and see.
Tangosuzumiran mmanifesto anu inu a dpwpwi muone kt zija munayankhla pa ka mpen ndichan chomwe mwakwanisapo, maize gate basi, r.trafficgate, imigration’gate…… Tanenan ., kuno vote ya2 simuzaiona
Kodi a mcp mukuona ngati tingakuvoteleni ku south kuno chifukwa cha mia? Mukunama kwambili inu zoti mudzalamula muiwala
i think the writer is not serious. Mia is not the earth,let people decide
Dpp Yatifinya Mokwanira Ichokee!!
asakugona mtulo ndiiweyo.
Zaziii a Mia abwera lero mu Malawi? Wodwala ndi amene walemba za Mia
Kod mbuyomu Miayu amapanga zichan Zot Ena akazunzike nazo?anayamba walamulirapo dziko?kkkkkkkkkkk olembayud ndiye akudwala
Akusowa zokamba MCP ndiyomwe yayima mitu
Only Dpp the strongest party am say to you foolish guyz no matter where Mia is, Ask your friends Malawian wants a trusted gvt not a party which always negative reports mwava?
kkkk queen’s language
muluzi anakupolamilani a MCP inu simuzawinanso
Mia hoyee 2019 boma
Mia hoyee 2019 boma
Kkkkkkkk mcp anakanika tembo ndiye chakwela angatani
do u knw kt ndale zakumalawi ndzazgawo…MCP can nt & wl never penetrate the southern region… mia has money yes bt nt political power..don’t be foold and gulu LA anthu pamisokhano yandaleyi
Old minds : zigawo zikuyipisa ziko la Malawi. Bingu amayimba NYIMBO kuti: Tiyende pamodzi ndi mtima umodzi. Ngati mukuti DPP ili ku South kokha nanga Mp Ali ukuchitipa, Karonga, Jean Kalilani. Ndiku South. Let us be civilised. MAlawi is one nation.
and based on your explanation your telling me that MCP wl penetrate the southern region?
Mr Vingula frankly speaking,what Mr Liman is saying is true•Malawian politics they are based on Regions•Even a peace MCP can not penetrate Southern region•Am not of any party but its according to my observation
Dpp ilibe nthawi yopanga za mia. Mutulusa mamina mmalo mwa miaonzi ikukhaulisani Dpp . Kodi Dpp inawina Mia ali ku dpp?? Alibe ntchito ameneyo ku dpp
Kwa Ife omwe tikudziwa bwino za ulamuliro wa nkhanza omwe inalipo pa nthawi ya MCP sitingayerekedze kuvotera anthu oipawa…
munawavotera kale coz ena ndiomwe ali ku DPP omwe ankachita khaza pa thawi ya MCP
Fortunately ,nobody exist who did that in M.C.P..tikuti kulibe omwe anapanga zimenezo Ku M.C.P, onse anatha ndipo ena Ali Ku D.P.P monga mtaba ndi dausi..Ku M.C.P kuli mamembala atsopano okhaokha ndipo kulibe ndimodzi yemwe andapanga nao nkhazazo..
Ndipo pafupi fupi 31/4
Alii dyooo chipani cha dpp omwe omwewo mukuti ngakhazawo ndiomwe akutilamulira think mukamakamba zithu osamangotengera poti awa anena zomwezo nanu mbuyomo
enanunso mumangoyankhula ngati ma phone’wo ndiwobwereka mukamati nkhaza za mcp ndye kuti chani,inu anthu amene akutemedwa ndi macadets a dipipi sinkhaza zimenezo nthawi ya democracy ngati ino??? tamakulani kukula ndi azigogo anu kapena bwanji,open your eyes,we’re talking about present coz past cant change anything right!
Chipie wats so called yal foolish damb suckers wt yal dpp
Anthu onse omwe ankachita nkhaza nthawi ya MCP pano akutsogolera a young cadets & ndwomweonso akuchitra nkhaza anthu masiku ano. Kaya. Andalenu zanu zimenezooooo!
Iwe sudziwa kuti nkhaza amapanga ndiachina Dausi zoti adaliwamkulu wa young payania sudziwa?
Av talked of my experience…. talk yours then..
Mmmmmmmmh kutsalira nkhaza zipose zogwetsa economy nkubazi kodi bwanji amalawi kupusa!!!!
you hav not talked of experience, u hv tokd out of kusazindikira, umbuli ndikusazitsata zinthu.
Kodi Goerge Chaponda Nkhaza Zoba Chimanga Cha Amalawife Paja Ndi Wa Mcp Eti?
MCP nyasi ya chipani,sidzawinaso
Noma 5-1 Moyare
Chipani cha anthu amvura zakale
I will never forget what happened when I was in Std 2. Kamuzu amabwela ku Namadzi Zomba ine ndikukhala ku Nasawa Zomba. Kunabwela wa Youth League dzina lake kapyola ndipo analengeza pa nzere ku primary school mamawa kuti aliyense akawone kamuzu. Ndinayenda ntunda wautali mpaka my late sister Kundibeleka miyendo ikupweteka. Lucky enough my Dad come pa njinga yamoto kuzatitenga. MCP sindizaiiwala.
Kkkk I don’t think so. Mwina mm waiwala kt DPP inawina election ili Ku opposition mia mukumunenayo Ali m’boma ndi a jb
MCP 2019 Boma
My foot
Yours yes
Kkkkkkkk Amiaa
Kkkkkkk
I hate what DPP is doin now Koma sindingasekerere a MCP kulamulira Malawi, Never ,sizizatheka ndithu!
Akuziwa Kuti iwina
am nt a dpp fan bt trust mi Mcp cgazalamulileso this country…. tak t o leav t
#Rich..ndiye ndiwe mulungu2,Mbuzi yamano kusi
Iweyo ndiwe ndani? Ati sindingasekerere kuti M.C.P kuti idzalamule kkkkkk dziko ndilagogo ako okha? Zoti tilimo anthu amitundu yosiyanasiyana sumadziwa? Idiot you talk like as if you own Malawi chosencho mulimbuuu…
Mpaka mbuzi ya mano kusi khalani serious ndale zisatiphudzitse kunyodzana munganve bwanji munthu mukumunena mbuzi mawa akukwatira mlongo wanu ?lets respect each ndife amodzi ngakhale tikusiyana ndale kapena zikhulupiliro
nde ngat muli madolo beat mutharika and win, chipani chotembereredwacho, inu mutawina nde mukuona ngat azakhale atsogoleri otsutsa ndinda?
a chikondano Khwadzu, ine ndi mphwake wamulungu Kumene, MCP izakhala ikutsogolera otsutsa forever
Zonse akudziwa ndi namalenga titha kunyozana no profit ainiwake akumwelana tea kudyerana nsima kuendetana koma ife amphawife kunyozana basi tien tipasanen ulem monga fuko limodzi mmalawi wamtendere osauka wa cash gate mbiteeeeeeee
Haibo mpaka mulungu kukhala ndi phwake?khalani serious comrade
mcp supporters kukonda kutukwana chocho mkumat mukufuna kuzalamulila malawi…politics has changed over the years ndale zotukwanzana znapita dis days pple can debate peacefully
I can’t waste my time arguing with dickheard just like you… Mulimbuuu kuona timafoto tanu tonunkha kkkkkk koma adha .
@ Bwanali ifetu tangovomereza kuti ndife aphwao a Mulungu poona mmene akutinyozera, a Luciano kunyoza anzao as if tinadyapo kwao, ngat akudziwanso status yathu, shame
zaife zsakukhudzeni, takula kwathu timadya zathu siinu abale athu, ma choices athu sianu, pangani zanu, kondani chipani chanu i was a DPP fan komano they r doin rubish but still i hate DPP Koma MCP nde NDI worse !!!! akakhala ma pic omwe mmaonawo thus true me,
J Kay Luciano Ma pic awo akuwayamikira kuti zawo zilipabwino omwewo a woimba aku America WO, hahahahaha akukanika kuika zithunzi zake mwina alibe nkhope shame.
Koma ndiwedi Chitsilu mbuli wekhaso ukunena kuti Choice yako siyawina ukhalilanji bize kutunyoza choice yaazako ? kudzitemberera ukuchitaku Mulungu si Peter kuti uzimufanizila ndiiwe galu wachabechabe ,Tabadwa takulila m Malawi zofooka za MCP tikuzidziwa koma Pano zanyanya bola kale
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk akuchoka pa ndeu angaike pa profile pic?
sindikunyoza koma kunena reality sinnanyoze munthu koma ndanena za chipani
Agalu a #MCP… Do u thnk mungazalamulirenso dziko lino??
Kkkkkk koma adha, #RichArmsonEGgomani ndiwe rapper eti ,udzandipeze Ku area 18 Ku Lilongwe tidzamenye ka collaboration.. I don’t hate anybody bro, koma osamakamba ngati Malawi ndiyanu yokha …
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk umatha #J_kay
kma kosowa zochta et
tpezetseni chochita @ #Eliza
Panyo pamanu macadat aDPP mphoto yomwe mumapeza ndiyomweyo yapent? tikuvutikila limodzi kumangofela kuti ndiwakwathu?panyini pamanu!
mcp kutukwana bas, inu nde munatembereredwadi, muzakhala otssutsa mpaka kalekale
Thanx for your opinion. There is sense in that nonsense.MCP is the public party DPP is the regional party. Nde ukuyankhula zanziiiiiii.
ife tonse bomaaaaa ..mcp yagwila nsewo
Ndiwe wabodza mcp sizawina olo itatan
Ife ndetipanga zoti mcp nayo ilowe bwalo basi
Blindness, deaf,mute is with most Malawians.
..its difficult to convince them how the current govt has failed.
yesesani
MCP can make it chifukwa fundo zawo panopa zilibwino tisamalankhule ngait ndife mulungu zonse zili muzanja pa mulungu zitha kutheka DPP kuwina olo kuluza that iz god’s plan
You will rule yourself and people will vote for you and your friends
Mcp the only party!!!!!!!!$
Guys I know #Rich now Ali kujoni so mukudziwa anthu omwe amathawa Ku Malawi kuno kupita Ku jon zmakhala kuti kwathu kuno zavuta awa ndi anthu omwe safunila Malawi zabwino amafuna kuwononga Malawi ndipo akuti sangalole mcp kulamula dziko lino pliz guys Mulungu so #Rich ndipo sadzakhala #Rich for ever and tikamatengela kuti timachokumwela tikhale a UDF or DPP izi sitingatukule Malawi kapena ndife amakati tikhale a MCP izi sitingatukule Malawi pakufunika tonse kusakha muthu amene angati thandize bcoz dzikoli tisaname apresedent anthu alephela koma tikuvutika tonse amene anavotela DPP ndi mcp onse akuvutika muthu kuthawa dziko lako mmmmm zimakhala kuti zavuta iwe #Rich sukudziwa kuti Malawi wafika pati #mia osalimbana naye Ali ndindalama zodya zaka 200 osasawuka kulimbana ndi mia mmmm kutaya thawi man tiye iwe ndi ine tikokele zanthu tisachedwe ndi mia
Tionana 2019 Mulira muona MCP????? Tambala wakudanso?? Alirenso kuno ku Malawi tizamudula khosi
Dpp woyeee 2019 bomaaa
Ndanva
Iweyo ndi amene sukugona tulo ndi DPP
shatapu, mia nde ndaninso,? mwayambira Mia Mia ngat tinadyapo kwacha yake bwanji?
Akhala anadwala Mutu waukulu, koma uwuwu ukuwachekela mmbalimmbalimu chifukwa tinyonga tolankhulila akumakhala natobe, ukadawapeza waching’alang’ala koma kuti adzinge zanzene,,,, Mxiewwww nanga mkulu wa zachisankho uja, ankalilanji ko?
2019 around the corner. MCP boma ilo. Like it or not unless rigging but fair game ena BP yakula
Namwe bodza MCP yake yiti! Yakoma lero? iyo imwe mukaukulirapo who can trust and believe in you? You misled the Nation with your multiparty trials who said maliro amalowaso mnyumba?
MCP ngati mukufuna kuzawina muthese mapokoso Ali muchipani chanu. Ndikumva zaalliance muyipange table bwinobwino. Mukamapeleka unthenga mukhale ndi fundo imodzi osati awa anena izi awo akuti izi.
My sister let’s be honesty. We only experienced MCP only in one party system. Not in multi party. That time it was Kamuzu administration not Chakwera administration. Multi party is a competition of party that put people’s first not party first. Honestly we have experienced MCP, UDF, DPP. Its only AFORD that we have not tested. So with Democracy I am convinced that the only party that can bring people together is MCP. UDF is confused. DPP is tribalism and regional. They only care other regions not Northern. They don’t listen to the people who voted them. If MCP do the same they will be voted out that is multi party. So my sister do research and tell me why would you vote DPP. It came thru back door by Bingo. If it was not like that they didn’t have majority.
My sister pali mau oti chitsime chimadziwika kuya chitauma. Now we can see how deep MCP was and the nice thing its democracy
#MichaelMkandawire well said bro, M.C.P did a lot that today’s D.P.P thugs.. Most of infrastructures which currently exist in Malawi done by M.C.P.tisangoona zoipa zokhazokha ,M.C.P inamanga zinthu zambiri M’malawi kusiyani ndi mbavazi…kkkkkk sister #JulietNYamkandawire ndi aD.P.P asakupusitseni ndimaona ma comment ambiri Aku defender D.P.P .
I agree J Kay Luciano. MCP when it was in power our money value was good. They was food for every citizens. The roads were well maintained. The security was tight. But now its just disorder. The democracy is being dragged back wards. I honestly that what was lacking is democracy. So the manifesto and ideology of MCP will be good with democracy. MCP is the only hope to change things back to better
#MichaelMkandawire exactly.
Talking truth Mr Michael Mkandawire
Go and vote according to your choice which is your freedom- the same with others you do not force a horse to drink water.No one is perfect we are not looking for an Angel better the devil that you know than the unknown.
Kkkk my sister no one is forcing anyone. According to our laws you have a right to vote anyone without force or fear. I have just put my facts about current leadership. Its your choice to take it or leave it. That’s why if you vote you are alone in that box. I will advice you that when you engage in a debate don’t be emotional. Debate with your opinion not anger. That is democracy. U have a right of expression but must be valid. Yes no one is perfect but we go for better one. No one here said we want angel. Now you label other people devil. I think you also need civic education. No one is fighting here. We are just debating. If I ask you that who is evil. The one who is manufacturing allegations to every potential candidate so that he compete with weak opponents, with the one asking for a fair election. DPP cadets assaulting people and call it democracy is that not evil.
Mudwaladi simunati kkkkk