Ku DPP sakugona tulo chifukwa cha a Mia

Advertisement
Sidik Mia

Ganizo loti a Sidik Mia alowe chipani chotsutsa cha Kongeresi kukhala ngati likuwadwalitsabe mutu akuluakulu a chipani cholamula cha DPP.

Nduna yoona zofalitsa nkhani mu dziko muno amenenso ndi m’dindo mu chipani cholamulachi adatonza a Mia kudzela pa wailesi ya MBC.

Sidik Mia
Dausi: A MiA akutenga udindo poti ali ndi ndalama

Malinga ndi ndunayi a Nicolas Dausi, ati Bambo Mia ndi munthu odalila ndalama basi kuti apeze maudindo pandale.

“Tiwalangize anzathu a Kongeresi, asamangotenga anthu ndi kuwapatsa udindo kamba koti ali ndi ndalama,” anatelo a Dausi amene anakhalapo wamkulu wa Kongeresi asanasinthe thabwa kupita ku DPP.

A Dausi anati a Mia akugwiritsa ntchito ndalama zawo kuti agule udindo wa wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha Kongeresi.

Kuyamba pamene a Mia analengeza kuti alowa Kongeresi, akhala akuthilidwa nkhoko ndi akuluakulu a chipani cha DPP kuphatikizapo mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika.

A Mutharika ananena kuti a Mia anagula MCP pa mtengo wa K200 million.

Advertisement

230 Comments

 1. Amiaaaa MCP yake iti? kapena asithetu dzina la chipani chimene alowacho osatelo akamufuse TEMBO & MULUZI alibenawo DPP kapena MAI wamuthawa MALAWI akukomayu.DPP more fire.

 2. Mia is a political prostitute. He started with UDF and then DPP later PP and. today he is in MCP such a character cannot be. trusted. He will not not bring any impact to. MCP.

 3. Andale musamawakhulupilile zao zinayela kale chuma alinacho iwe ndiine palibe chathu amadya okha ndi ana awo bola za church kusiyana ndi ndale sitimadya ndale timadya nsima amalawi tinachuluka uchitsilu timangotengeka ndi zaziiii kusapota zipani kunyumba kulibe chakudya

 4. PAKATI PA A ISILAEL NDI AFILISITI GOLIATI ANKATAMA MPHAMVU ,DZIDA ,UKATSWIRI KOMA MODZICHEPETSA DAVID ANADALIRA MULUNGU NDIPO NKHONDO ANAPAMBANA .OTEMBELELEDWA NDI AMENE ATAMA MKONO WA MUNTHU KUSIYA MULUNGU.AMALAWI YAKWANA NTHAWI YOTI TIFUNSIRE KWA MULUNGU POPEMPHERA OSATI PONYOZANA.

 5. PAKATI PA A ISILAEL NDI AFILISITI GOLIATI ANKATAMA MPHAMVU ,DZIDA ,UKATSWIRI KOMA MODZICHEPETSA DAVID ANADALIRA MULUNGU NDIPO NKHONDO ANAPAMBANA .OTEMBELELEDWA NDI AMENE ATAMA MKONO WA MUNTHU KUSIYA MULUNGU.AMALAWI YAKWANA NTHAWI YOTI TIFUNSIRE KWA MULUNGU POPEMPHERA OSATI PONYOZANA.

 6. Mtengo wolephera nyani…chalaka bakha…Zidamukanika munthu wamkulu Gwanda Chakuamba izi…nzokanika ma member…stingavotere mcp ife…magazi ali chuuuu

 7. 12/08/2017

  Geetings friends wherever you are .
  we have created this group Malawi Youth Parliament solely for us the Youth so that we can share political, economic, social and technological affairs affecting our nation.
  we need members from at least every constituency in Malawi.
  I therefore ask you to introduce yourself and the constituency you represent in this august house. by default you are the shadow mp of that constituency
  You as well tell us the party you represent. The administration will be very serious to take note of the constituency and the representative plus the party he belongs to.

  I therefore advise you honorable members that only issues of national interest will be discussed here.

  No politics of castigation and name calling . misbehaving members will face two cautions then a disciplinary hearing later if such a member prove to be of the contrary agenda of the group shall face dismissal from the group.

  forward the message to those interested to join so that they submit their details eg full names ,age, constituency and favourite party to any of these contacts: 0882024002
  0886826626
  0999748763
  0992486973
  incase the desired seat is occupied the aspirant shall still be added on the group.
  We are the Youth
  we are the majority
  we are the leaders of today
  together we can build a better Malawi.

  This message is brought to you with the help of GCK CAMERAS the only cameras that have no limit in capturing information .

  May God bless Malawi

  By the Group administration.

 8. Dpp Boma Irooooooo!!!!!!! Mwayamba Kale Kunjenjemera2 Munjenjemerad Musanat Achpani Cha Business Inu Named Mumat Chan Tambala Wa Red Nt Wakuda Shame

 9. Unapitako mkuwapeza alimmaso??gossiper of the century you are so fake ishh yosagonetsayo nikhala kwacha l doubt

 10. Let us all wait for the by elections results as that will be our litmus test. Am telling you MCP is sweeping all the seats including Nsanje lalanje constituency. Amene akutsutsa betch K20,000 ndisitika. molimba mtima.Chakwera is a very tactical guy and DPP is very frustrated with how Chakwera has blown off all the sponsored Nkholokolo

 11. MWASOWA ZOKAMBA INU ANYASA MCP MUKUNAMA MIA TIKUMUDZIWA AKUNGOFUNA UDINDO BASI MUKALUZA MUZIZATI MWABELEDWA MUONA SIMUNATI TINAWINA TISALI MBOMA PANO NDILANTHU MUKUONANGATI TINGALUZE MWALEMBA MADZI CHULE WAWELENGA

 12. Amalawi sangasiye kukamba za ndale chifukwa tsogolo lao limakhala m’manja mwa anthu andale omwe amayendesa boma Amalawi mukhulupirile kuti pattern ya kavotedwe 2019 ikhala yosiyana ndi zisankho zonse za m’buyomu panopa a malawi azuka

 13. Sindisowa kukamba zamia ai akanakhala dolo akanayamba chipani chake osati kunjowina munthu ndiye munthu wake kukhala mcp pano amalawi amaziwa ndale zoti awa ndi andalama zinapita ndi aja lero anthu akufuna mavuto adera lao

 14. Wakumudzi ndiamene woona ndi maso kuti njala yatha ndi ulamuliro wa professor. whether N, C, S or E ndale zapakamwa anthu anatopanazo ask PP -DPP2019 Bomaaaaaa

 15. paja mumadya ndale…… onsewo muwauze fotsek zawo!!! instead of concentrating za mavuto kumidzi ndikibwelesa ma opportunities kwa anthu kuti azipeza kenakake!!! busy kuononga ndalama n kumakangana za ziiiii……. achule

 16. Whether Mia is buying his way into MCP is none of dpp’s business. basi munthu nkulukulu kumakhala pa kanema kupanga miseche ati kufuna kusiocheretsa a Malawi.Nkhani yakula apa ndi yakuti Lower Shire tsopano ndi ya MCP whether one likes it or not. Not only lower shire but even some parts of Blantyre, Mwanza, Neno, zomba, machinga, Mangochi and balaka. Wina afa ndi kadyakarista chaka chino.

 17. nthawiyomwe ndimkasapota pp ndinkadana ndianthu omwe amkanena kti pp sidzawina chisankho ndipo idaluzadi.pano anthu omwewo,akuti dpp sidzawina,akumwela komkunosotu.apa ndikuti dpp paulendo

 18. Guyz to say the truth Mia amaziwa ndale even chitukuko nanga peter wapangapo chani anthu akufa ninjala nipomwe akuti ine nilibe problem what kind of a leader is he malo momvera chisoni anthu ake I remember kamuzu anati mukufuna matiparty is a dirty game pano ni izi mukutukwanana cz of ndale kulorela kuphana but 2019 mulungu azatisankhira mtsogoleri

 19. ADausi, adausi ndale ayamba liti. Aaaaaa ndale zaosauka ndiizi akumaba ndalama mbomazitu, president analowa alibe chilisonse pano alindi ndalama azitenga kupi? Adausi analibe ngakhale kozlkakha APA azitenga kuti? Zakuba basi!!!! Amusiye aliyese ali ndi kufuna kwake

 20. Mia,? DPP sleepless? Mia is not a new politician but another political Thief. Which party doesn’t he joined? Si uja anasiya mtembo wa Bingu mnyumba kukalowa Pp chifukwa cha dyera uja?

 21. Kodi BP ilekelenji ngati mtsogoleli waDPP wamela tsembwe ndichiganizo chaSidic Mia akanene atonkhwetonkhwe alimmbali mwake zimphwisi zokhazokha, koma 2o19 palikusiyanitsa pakati paNjovu ndimbuzi wamphavu ndindani.

 22. There’s no credible election in Africa. Free & fair on voting with electronic hacked on the process of counting. Yours will not be different.

 23. All pipo u talking about DPP forget ths coming election its for MCP no matter what unles mzabeleso a DPP koma ulendo uno mwachela msapha masana nkhanga zaona MCP boma 2019

 24. Malawi sasamva.Inu tayambitsani chipani china inu,komatu nthawi mulinayo,Muzalira mutalephelanso.Ife a malawi tikufuna zipani zatsopano apo bii Uyu ndiye sazatheka kuchosedwa m’boma.INU MUSACHEDWE NDI MCP INU.OOH AYI IFE ATHU NDI MASO.

 25. mumalo molimbana ndiumphawi wadziko kapena ndiumphawi wa anthu mudziko muno mulibusy kulimbana ndi a Mia asaaaaaaa create job opportunities tikufuna ntchito ife asaaaaa

 26. Kodi mia pandale za Malawi adapangapo chani choziwika kuti anthu azimunjejemera? Let them celebrate azalira mia mcp italepheraso pa chisakha azakumbukira agogo ake ku India.

  1. Mukungolankhula ndale simuzidziwa ndale ndi majority, Mia ukumunenayo ndiodziwika bwino kuposa Peter pandale UDF yachitako bwino ku Lowershire kaamba ka Mia Sindikudziwa kuti muziti MCP siingalowe m,boma koma ndinu amoyo kapena mitembo? uziyang’ane wekha ulipo ufuse Dzulo la MCP linalibwanji oneso pa Post iyi ndi angati ali mbali yako? uona wekha kuti anthu sakuikonda DPP ya Petulo

 27. Kkkkkkkk Koma mukulankhulatu Eish! Nkhani yake yazipani? Guyz chomwe tikuenela kudziwa ndichakuti Malawi walero simalawi yamakolo athu. Zinthu zinasintha ndipo tangoyenela kuvomeleza KUTI ifeyo tikumana ndizambiri sitinati, koma ndipemphe nawo KUTI ifeyo ngati Amalawi chonde tisiye kulankhulilana mau achipongwe, ndikunkhulipila kuti tonse timadziwa KUTI anthuwa akamakangana kumakhala kulimbilana ifeyo nde tisamaone ngati akufuna kutithandiza akungofuna kumatingwilisa ntchito koma tisalole kunyozana ndikulankhulilana mau onyoza . aliyense angokhala ndizimene amakhulupilila basi. Ndipo sizingatheke kuti aliyense apange zofanana ndiwina. Tonse nda Malawi dziko ndilathu tiyeni tikondane

 28. Maloto a mphaka munthu wanzeru zake angamaganize zoti mcp ingawineso 2019 dpp koma mosemuja yakhalila ikukukwapulani muja simumamvetsabe?

 29. mcp should concetrate in the north & some parts of cetral region where dpp enjoys some support.mia wil contribute nil in the south.muluzi tried to back up mcp it did not materialise.

 30. mcp winning unless if all the votes in thyolo mulanje phalombe chiradzulo zomba blantyre mwanza mneno will be null and void.will ntcheu vote mcp this time massively. will the yao people of balaka machinga and mangochi vote not UDF and dpp second and mcp zero.what about Lilongwe city, ntchisi yoyamika nseu onwe a mcp sanamangile for thirty years.nkhotakota north and sourth.mcp kaya mukwiye cant outsmart Dpp.Dpp will come first and mcp second with a difference of over 400 thousand votes.

  1. Ndaknyada MCP yachaniso? munpatuze chani inu ngati ukuyaka wauwisi kulbwanji ouma? Malawi sazatheka usatmate phula kti ndiwe wanzeru Demeti!

  2. Iwe, this is not 2014. Even myself am based in BT with my family but will vote for MCP. Sitonse Ku south kuno tili opepera enafe tidasukusula kalekale mwene

 31. Mukumu tamandira Mia munthu wothawa maliro a malemu Bingu Ali mu nyumba kulephera ndi kukapepesa nkomwe pamene malemu amamutenga ngati mwana wache amamukonda kwambiri pa nduna zonse, Alibe khalidwe ameneyu, JB kumunena kuyenda ngati bakha, shaaaa

 32. palibe angadwale ndi mia, asakumuziwa mia ndani, d p p singatekeseke olo half, ndi mia ai, ndiponso akabweze ndrama zonse amatenga BINGU asanamwalile amaona ngati sizingakumbukilike, komanso asalowe mu m c p kufuna kukangogawanisa anthu kuwaombanisa mutu ai, palibe d p p singagwedezeke antaaa oolo oloo.

 33. Koma inu amene mukumatibe dpp dpp booma timitu tanuto timagwila tchito kapena timayendela mamina timagwila chito mukamkhala mwadwala chimfin taganizan momwe ife akumidzife momwe tikuzuzikila timadalira ulimi koma taganizan zipangizo zaulimi momwe zikudulila pamene mbeu mitengo mukugula nayo mbeuz ndiye zakufwed

 34. Ulamuliro uliwonse mmati oipa mukuona ngati yesu angabwere kuzakhala president Ku Malawi,sankhani ndiye emwe mukuona kuti angazakhale 100%,mmalawi zazatheka amwene

 35. daily ndale kuleka kumagwira ntchito kuti mutukule umoyo wanu hahaha amalawi ndichifukwa tikukumana ndiumphawi nthawi zonse kodi ndale zimadibwa? azanu mukulimbana nawowo chuma mkutapa kutaya koma iwe osauka uli ngaaaa!!! pandale hahaha try to improve your daily life not politics.

 36. Mwaona inu a MCP mukutokota kwambiri ndie tikadzakunyenyani 2019 ino muzizanamizira kuti takubelani chonsecho inu muli ndi machimo ambiri omwe simunaulapire mtundu Wa amalawi inu amangotsutsa zilizonse osafunako or kuyamikira nkhwidzi basi mudzaziona koma osadzafa ndi ma bp

 37. mmmmm! tikuziwa kuti nanu a malawi 24 palibe chomwe mungatiuze chanzeru,koma ndikukuuza kuti muzalira ndipo muzakhumudwa with or without mia dpp ikulowanso ndipo muzabweza ti ndalama tomwe chipani chamagazi chakupasanizo

  1. Ndwe mmlomwe etttiiiiiiiiiii? oky! Tionana 2019 bola musadzabelenso ngat 2014 ija. Komansoooo! Aaaaa! kaya ndit chani kaya? Oky! Takutulukirani tsopano. Mufunaaaa! Aaaaa! Koma Amalawi,inu!!!!!!!

  2. Vuto mwabadwa dzulo mukadzipenta akupasani k50 mwati chipani ndi DPP ndiwe gwirize mkakodze ndiye chifukwa ,koma dziwakuti ,dzulo simawa kunali yani ,anthu amalawa analawa MCP mu chipani chimodzi ,ali tilawe democracy, UDF,DPP1,DPP2 ,aona kuti democracy ndiyabwino koma ,ikugwilitsidwa molakwika, funso mkumati payokha MCP imaopa ndikulemekeza a Malawi kodi mu Democracy ipanga zotani ?

 38. Mia wapelekadi food for thought mchupanichi but politics in multi party era it’s a game of numbers. They have to think how they can get the numbers. The people who are to push it on another levels are leaders themselves. They are the vision of DPP. Is DPP Loved by all, if not why? What is the way forward? PULL SOCKS UP

 39. MCP ndi chipani chosusa mpaka kale nkhaza zomwe anapangira Malawi palibe angaiwale ikachoka DPP bola tizabwerere kwa chair osati MCP iyaaaah kutaya nthawi kuganiza zimenezo

 40. Nonsense..These were the outcome of past Elections.1999. former Might ALFORD plus MCP=Nil.2009 Achair and UDF plus MCP=Nil. 2004 BJ and NDA plus Tembo and MCP=Nil… How special is Sidik MIA if I may ask? If not careful 2019.MCP seems over confidence may end up loosing also

 41. Tangosuzumiran mmanifesto anu inu a dpwpwi muone kt zija munayankhla pa ka mpen ndichan chomwe mwakwanisapo, maize gate basi, r.trafficgate, imigration’gate…… Tanenan ., kuno vote ya2 simuzaiona

 42. Only Dpp the strongest party am say to you foolish guyz no matter where Mia is, Ask your friends Malawian wants a trusted gvt not a party which always negative reports mwava?

 43. do u knw kt ndale zakumalawi ndzazgawo…MCP can nt & wl never penetrate the southern region… mia has money yes bt nt political power..don’t be foold and gulu LA anthu pamisokhano yandaleyi

  1. Old minds : zigawo zikuyipisa ziko la Malawi. Bingu amayimba NYIMBO kuti: Tiyende pamodzi ndi mtima umodzi. Ngati mukuti DPP ili ku South kokha nanga Mp Ali ukuchitipa, Karonga, Jean Kalilani. Ndiku South. Let us be civilised. MAlawi is one nation.

  2. Mr Vingula frankly speaking,what Mr Liman is saying is true•Malawian politics they are based on Regions•Even a peace MCP can not penetrate Southern region•Am not of any party but its according to my observation

 44. Dpp ilibe nthawi yopanga za mia. Mutulusa mamina mmalo mwa miaonzi ikukhaulisani Dpp . Kodi Dpp inawina Mia ali ku dpp?? Alibe ntchito ameneyo ku dpp

 45. Kwa Ife omwe tikudziwa bwino za ulamuliro wa nkhanza omwe inalipo pa nthawi ya MCP sitingayerekedze kuvotera anthu oipawa…

  1. Fortunately ,nobody exist who did that in M.C.P..tikuti kulibe omwe anapanga zimenezo Ku M.C.P, onse anatha ndipo ena Ali Ku D.P.P monga mtaba ndi dausi..Ku M.C.P kuli mamembala atsopano okhaokha ndipo kulibe ndimodzi yemwe andapanga nao nkhazazo..

  2. Alii dyooo chipani cha dpp omwe omwewo mukuti ngakhazawo ndiomwe akutilamulira think mukamakamba zithu osamangotengera poti awa anena zomwezo nanu mbuyomo

  3. enanunso mumangoyankhula ngati ma phone’wo ndiwobwereka mukamati nkhaza za mcp ndye kuti chani,inu anthu amene akutemedwa ndi macadets a dipipi sinkhaza zimenezo nthawi ya democracy ngati ino??? tamakulani kukula ndi azigogo anu kapena bwanji,open your eyes,we’re talking about present coz past cant change anything right!

  4. Anthu onse omwe ankachita nkhaza nthawi ya MCP pano akutsogolera a young cadets & ndwomweonso akuchitra nkhaza anthu masiku ano. Kaya. Andalenu zanu zimenezooooo!

  5. I will never forget what happened when I was in Std 2. Kamuzu amabwela ku Namadzi Zomba ine ndikukhala ku Nasawa Zomba. Kunabwela wa Youth League dzina lake kapyola ndipo analengeza pa nzere ku primary school mamawa kuti aliyense akawone kamuzu. Ndinayenda ntunda wautali mpaka my late sister Kundibeleka miyendo ikupweteka. Lucky enough my Dad come pa njinga yamoto kuzatitenga. MCP sindizaiiwala.

  1. Iweyo ndiwe ndani? Ati sindingasekerere kuti M.C.P kuti idzalamule kkkkkk dziko ndilagogo ako okha? Zoti tilimo anthu amitundu yosiyanasiyana sumadziwa? Idiot you talk like as if you own Malawi chosencho mulimbuuu…

  2. Mpaka mbuzi ya mano kusi khalani serious ndale zisatiphudzitse kunyodzana munganve bwanji munthu mukumunena mbuzi mawa akukwatira mlongo wanu ?lets respect each ndife amodzi ngakhale tikusiyana ndale kapena zikhulupiliro

  3. Zonse akudziwa ndi namalenga titha kunyozana no profit ainiwake akumwelana tea kudyerana nsima kuendetana koma ife amphawife kunyozana basi tien tipasanen ulem monga fuko limodzi mmalawi wamtendere osauka wa cash gate mbiteeeeeeee

  4. mcp supporters kukonda kutukwana chocho mkumat mukufuna kuzalamulila malawi…politics has changed over the years ndale zotukwanzana znapita dis days pple can debate peacefully

  5. I can’t waste my time arguing with dickheard just like you… Mulimbuuu kuona timafoto tanu tonunkha kkkkkk koma adha .

  6. @ Bwanali ifetu tangovomereza kuti ndife aphwao a Mulungu poona mmene akutinyozera, a Luciano kunyoza anzao as if tinadyapo kwao, ngat akudziwanso status yathu, shame

  7. zaife zsakukhudzeni, takula kwathu timadya zathu siinu abale athu, ma choices athu sianu, pangani zanu, kondani chipani chanu i was a DPP fan komano they r doin rubish but still i hate DPP Koma MCP nde NDI worse !!!! akakhala ma pic omwe mmaonawo thus true me,

  8. J Kay Luciano Ma pic awo akuwayamikira kuti zawo zilipabwino omwewo a woimba aku America WO, hahahahaha akukanika kuika zithunzi zake mwina alibe nkhope shame.

  9. Koma ndiwedi Chitsilu mbuli wekhaso ukunena kuti Choice yako siyawina ukhalilanji bize kutunyoza choice yaazako ? kudzitemberera ukuchitaku Mulungu si Peter kuti uzimufanizila ndiiwe galu wachabechabe ,Tabadwa takulila m Malawi zofooka za MCP tikuzidziwa koma Pano zanyanya bola kale

  10. Kkkkkk koma adha, #RichArmsonEGgomani ndiwe rapper eti ,udzandipeze Ku area 18 Ku Lilongwe tidzamenye ka collaboration.. I don’t hate anybody bro, koma osamakamba ngati Malawi ndiyanu yokha …

  11. Thanx for your opinion. There is sense in that nonsense. MCP is the public party DPP is the regional party. Nde ukuyankhula zanziiiiiii.

  12. Blindness, deaf,mute is with most Malawians.
   ..its difficult to convince them how the current govt has failed.

  13. MCP can make it chifukwa fundo zawo panopa zilibwino tisamalankhule ngait ndife mulungu zonse zili muzanja pa mulungu zitha kutheka DPP kuwina olo kuluza that iz god’s plan

  14. Guys I know #Rich now Ali kujoni so mukudziwa anthu omwe amathawa Ku Malawi kuno kupita Ku jon zmakhala kuti kwathu kuno zavuta awa ndi anthu omwe safunila Malawi zabwino amafuna kuwononga Malawi ndipo akuti sangalole mcp kulamula dziko lino pliz guys Mulungu so #Rich ndipo sadzakhala #Rich for ever and tikamatengela kuti timachokumwela tikhale a UDF or DPP izi sitingatukule Malawi kapena ndife amakati tikhale a MCP izi sitingatukule Malawi pakufunika tonse kusakha muthu amene angati thandize bcoz dzikoli tisaname apresedent anthu alephela koma tikuvutika tonse amene anavotela DPP ndi mcp onse akuvutika muthu kuthawa dziko lako mmmmm zimakhala kuti zavuta iwe #Rich sukudziwa kuti Malawi wafika pati #mia osalimbana naye Ali ndindalama zodya zaka 200 osasawuka kulimbana ndi mia mmmm kutaya thawi man tiye iwe ndi ine tikokele zanthu tisachedwe ndi mia

 46. Akhala anadwala Mutu waukulu, koma uwuwu ukuwachekela mmbalimmbalimu chifukwa tinyonga tolankhulila akumakhala natobe, ukadawapeza waching’alang’ala koma kuti adzinge zanzene,,,, Mxiewwww nanga mkulu wa zachisankho uja, ankalilanji ko?

  1. Namwe bodza MCP yake yiti! Yakoma lero? iyo imwe mukaukulirapo who can trust and believe in you? You misled the Nation with your multiparty trials who said maliro amalowaso mnyumba?

  2. MCP ngati mukufuna kuzawina muthese mapokoso Ali muchipani chanu. Ndikumva zaalliance muyipange table bwinobwino. Mukamapeleka unthenga mukhale ndi fundo imodzi osati awa anena izi awo akuti izi.

  3. My sister let’s be honesty. We only experienced MCP only in one party system. Not in multi party. That time it was Kamuzu administration not Chakwera administration. Multi party is a competition of party that put people’s first not party first. Honestly we have experienced MCP, UDF, DPP. Its only AFORD that we have not tested. So with Democracy I am convinced that the only party that can bring people together is MCP. UDF is confused. DPP is tribalism and regional. They only care other regions not Northern. They don’t listen to the people who voted them. If MCP do the same they will be voted out that is multi party. So my sister do research and tell me why would you vote DPP. It came thru back door by Bingo. If it was not like that they didn’t have majority.

  4. #MichaelMkandawire well said bro, M.C.P did a lot that today’s D.P.P thugs.. Most of infrastructures which currently exist in Malawi done by M.C.P.tisangoona zoipa zokhazokha ,M.C.P inamanga zinthu zambiri M’malawi kusiyani ndi mbavazi…kkkkkk sister #JulietNYamkandawire ndi aD.P.P asakupusitseni ndimaona ma comment ambiri Aku defender D.P.P .

  5. I agree J Kay Luciano. MCP when it was in power our money value was good. They was food for every citizens. The roads were well maintained. The security was tight. But now its just disorder. The democracy is being dragged back wards. I honestly that what was lacking is democracy. So the manifesto and ideology of MCP will be good with democracy. MCP is the only hope to change things back to better

  6. Go and vote according to your choice which is your freedom- the same with others you do not force a horse to drink water.No one is perfect we are not looking for an Angel better the devil that you know than the unknown.

  7. Kkkk my sister no one is forcing anyone. According to our laws you have a right to vote anyone without force or fear. I have just put my facts about current leadership. Its your choice to take it or leave it. That’s why if you vote you are alone in that box. I will advice you that when you engage in a debate don’t be emotional. Debate with your opinion not anger. That is democracy. U have a right of expression but must be valid. Yes no one is perfect but we go for better one. No one here said we want angel. Now you label other people devil. I think you also need civic education. No one is fighting here. We are just debating. If I ask you that who is evil. The one who is manufacturing allegations to every potential candidate so that he compete with weak opponents, with the one asking for a fair election. DPP cadets assaulting people and call it democracy is that not evil.

Comments are closed.