Atapulumuka kwa kanthawi, tsopano wagwa chagada George Chaponda.
Chikalata chochoka ku nyumba ya boma chimene wasayinila mneneri wa a President chalengeza kuti a President a Peter Mutharika amuchotsa Chaponda pa unduna.
Malinga ndi chikalatachi chimene a Malawi24 tachiona, a President ati atenga mphamvu zonse ndi ma udindo a unduna wa zamalimidwe.
Kunalowa chipolowe ku unduna wa zamalimidwe pamene nduna yake inapezeka kuti inachita utambwali.
I will be glad if Chaponda is going to mention others in order to fire them all
We are not vote Peter muthalika but he was stealing vote Malawi news.
Mkasa nayenso achotsedwe pa gulu la oimba
Kkkkkkkkkk
You can do what ever you want coz its your time, but dont 4get that it will become the time of others. Then you will feel pain when they will do things according to their time, time tell you’ll blve this
Kodi iwe chaponda mutu wakoo anakupondani amai ako uli mwana .??? Nakupangani amai ako pokumbeka chonchi chimutu chonyasa dengu latomato ku Ncheu. Amathamangira kuti bambo ndi amai ako. I mean time for sex masimmba amuthu
Joseph. Mkasa ndi muthu chinzeleze ophunsa iye amafuna. Kungelera ndalama kapena kuti papsa tonola .mutu uja sugwirchito anawagwensa amai ake Ali mwana.wang’no Ali kumbuyo kwa amai kumunda
Nkhope ya chapondayo ikuyenera kukhala nyapala osati nduna ya boma
Ammange ndikumulanda ma billion WO. Mkutigaila aliyense ma 5 handz tidye nao
Musiyeni adyeko ndalama za boma
La 40 lakukwanirani mdara. Tachiwoneni ngati achidyetsa manyii. Utimva kuwawa iweee
Point! Play a song to this man called chaponda done by Joseph mkasa dedicated to him….
Mr Mkasa backed up him with total mind but he forgotten that “chomwe wamkulu sakuchiina atakhala pansi…ngakhale ana ngati che mkasa ndi ineyo pandale or titakwera mumtengo…sitingachionenso.
Mr mkasa can u just interprete that song as quick as u can paja simumachedwa kutembenudza.
Shame! Malawi! Above all…the heavenly judgement is heading you…if u don’t repent!
Achoke
Lafika la 40 achimwene anga achaponda muziona mumaba nokha kkkkkkkj
Peter and Chaponda are congruent. Look at them. They seem to be brothers from same parents
Nthawi ikakwana yakwana basi
Inu mumachedwa kut?muzpanga zoti anthu azkukhulupililan chidodo bas
Nkasa ngati mutumo nyimbo zathamo pita uzikalima usamadye ndalama za magazi
Atsogoleri athu.Kodi mukutilondolera kuti ?
Enafenso nd akuba koma kusagwidwa
Kkkkkkkkk kma yaaah
chaponda bwanji manyazi nanu ankasa znazi mmnmmmm kaya ndichimutucho kukulako galu iwe
“This inquiry is a waste of time and resources,you will not find anything,its just jelousy of Malawians-kaduka.Am innocent and i cant resign”.
Dr Chaponda musadandaule chifukwa mwayesedwa kawili kasala kamodzi kowawa kwambili for you to break through in the mighty name of Jesus. Simungakhale pamwamba musanayesedwe katatu never, even professor A Mutharika tempted for three times ;(1) when he was the minster of education (2)green card and (3)treason case then he broke through -amen
Dr Chaponda musadandaule chifukwa mwayesedwa kawili kasala kamodzi kowawa kwambili for you to break through in the mighty name of Jesus. Simungakhale pamwamba musanayesedwe katatu never, even professor A Mutharika tempted for three times ;(1) when he was the minster of education (2)green card and (3)treason case then he broke through -amen
Dr Chaponda musadandaule chifukwa mwayesedwa kawili kasala kamodzi kowawa kwambili for you to break through in the mighty name of
Alandilaso zindalama zambirimbiribe,
Masaya otupao chisiru nkasa uzafa osauka nfi dyera galu
Yayah Jammeh wathu uyu.
Zdina lake likusatadi zitchito zake. “Chaponda”,wapondadi.kkkk. Malawi,eti ndi dziko lamutende,,ndakaika.
Kkkkkk
Ugona moti udzimva shupit zako
Good move.
Kodi chithuzichi ni cha munthu kapena nkhwere?
Kkkkkkkkkkkkk
Chinkhope ngati nyani wamasiye
Inuyonso ndi mbava panokha Ndalama zabungwe mwaba zja?Nanga zakumpingo zja?Kuofesi Kwanu Mwabakonso,nanga ndalama Mwagulitsa Katundu Wa Akazi Anu Zja Mwapita Nazo Kt? INUYONSO MBAVA KOMA SIMUNAGWIDWE
Ife Tikuvutika Kufuna Ntchito, Inu Ndikumangogona Mpaliamenti,mwezi Ukatha Mukulandir Ndalama Za Nkhan-nkhani, Yendetsani Ntchito Iyi Amalawi Akufa Ndi Njala, Mukupezapo Mwayi Woberapo Ndalama, Ndi Zimenezotu Mwadzimenya Double Kick!!i
Mwabaya penipeni kkkkkkkkk
Palibe boma limene lizabwela lopanda mbava (MCP,UDF,PP,DPP)Palibepo Boma labwino Amalawi Muzingovutika.
Alipo ambiri
Kungochotsa akagone pa shamba pa maximum person, he think’s is aboves every one chifukwa cha zindalama zakubazo?nkumayakhulanso motumbwa kuti ali clean mbone ndi mlungo,haha atsanso azinzako!
KUbanda Onse awiri
Acitabwino Kumlanda Udindo Tsopano Mwina Dzithu Zingayende Bo,o Ndik Ziwa Kut Athu Amzuko La Malawi Asangalara Makamaka Ineyo
They just want to hide behind the scene akudziwana amaba limodzi awa!!!!!!
Mesa munkat alomwe ndi oyera?? Nanga chapondayu kkkkkk
Tym basi
Malawi fo sho!!
I thought he is the untouchable
A bad did has o redie done .Mmadikira aotche kaye ofesi
A Peter Sanalakwise Kumuchosa Panopa Chilungamo Chaziwika
q
Christ mollywood malawi
A drama group that aims at preaching christ through drama and movies is looking for actors and actresses to be part of their upcoming drama plays.
Qualification
1.should be bornagain christian
2.fluent in english and chichewa
3.should be based in lilongwe
Person specification
1.willing to travel and take part in both movie or drama plays
2.good communication skills and good understanding of the bible and pentecost deeds
3.understanding and godly
4.bornagain christ like christian
Salary :N/A
Employment type: part time
Location:lilongwe
For more info on how to apply follow and inbox christ mollywood malawi page by using this link
http://www.facebook.com/Christ-Mollywood-m...
Ngati akunama zawo komaso court likamupeza olakwa azazalangidwe ngati momwe ena aja adachitila posatengela kuti ndi wa kuchipani kwawo
The ruler of the world is devil. So you want good things from devil. Jesus refuse to pay tax, ma fello forks love money love evil.
Wavina manganje kkkkkkkkk
apo zakhala bwino watenga yekha unduna
Kumuchosa mumangeni nanga abweze ndalama
Dukhwi 😎
Ndichifukwa chiyani a dpp mumatsunga mbava?
musangonena kuti mwamuchotsa mpamene kuseri muli limodzi.
muzimva chisoni ndi momwe anthu akuvutikira m’midzimu. mwina poti simumayenda.
amangidwe ailawe jail.
Wakuba uyo, wakuba uyo×5
Osangonena kuti mwamuchotsa mpamene kuseri muli limodzi.
muzimva chisoni ndi momwe makolo ndi ena akuvutikira m’midzimu.
amangidwe ailawe ndende Galu ameneyu!
Chaponda analemera kale ameneyo,Panga zako.
Amadya ndi mkasa
Mmmmm mwatelo
Eeeesh but who is goin to fire you now coz we use votes to fire you kkkkk
Mr peter munthalika …..you are my first suspect
Senseless equation, in this, full of idioms and funnies.
Zaka zitatu kundendeeeeeee
Kkkk apa ndiye mwalemba mchichewa kut timve mvemvemve.aisova amayesa ngat sagwidwa
am following malawi 24 from zambia, u guys in malawi u are even luck that that chaponda has has been fired, though too late, us here in zambia the agriculture minister was even promoted from the ministry of agric to the ministry of justice, despite having overwhilming evedence about the maizegate, but the presidend is busy merrying with the corrupt minister, as we are talking there is no comment from the president. the anti corruption commission has been a toothless shit, there is nothing to do. so well done malawi for pressuring mr muthalika to do the right thing. let not politicians tbke advantage of us.
Koma ka Malawi
Amati atani ndi Peter wakeyo? Agonjera zofuna za anthu. Ndani angalore kuti anthu omwe akuganidzilidwa kuba adzikakamirabe pa mipando? Nawonso a peter kuganidza mochedwa ndi bwenzi atamuchotsa kalekale.
Nde muchiyitane chinja chinadzipatsa chokha uphungu chija chitiyimbile nyimbo yake ija kkk koma dyera lako likupweteketsa ndithu kaya unazimvela fungo ndalamazo nde wawuponda chifukwa nde zatutidwako
Munthu oipa mtima Chaponda,,kusokoneza chimanga,kuotcha office,,ndani makamaka iyeyu??
La 4o Lamukwanira
La 4o Lamukwanira
Remember that these people are on the same. Pipeline including the president himself, he want to blind Malawians, onse ndianthu akuba okhaokha musatipusisepo apa,
VERY 2RU.
galu ameneyu or ntakumana naye pa njila nditha kumu ombela galu ameneyu
Tiwotche mbala zonse
To late to save Jerusalem mr president,while the cty has already flooded,people were talking about it bt you were giving them death ear and now its wen you have realised that its true”timadziwa kt mwana wako umamukhalira khonde akalakwa,kmabe ukapita kobisika umamukwapulamo ndthu nanga.
Kkkk uziona
kkkkkkkkkkk sonooo mwatii wapwetekekaa na nkhowee etiii kkkkkkk iiiiih
R l P
The problem we decided to elect presidents frnd one family as if all Malawianz r dull. Wats so special wth Munthalika family …????? They steal bt we still trust them. After th death of Bingu ACB found bags of cash in his house ..bt stupid ppl still chose his brother. Wat r we looking for Malawi? ??/. Peter wants to make us dumb n trust that he’s nt behind scenes …bt surely he’s there
Nonsense! !!!!! We r suffering coz of few stupid so called “educated ppl “. Do u think its only 1 educated family in here? ? Pls Malawianz …lets consider this as a grt lesson so that we vote for a change this 2019. Otherwise we wil still sing this same chorus til our innocent kids suffer mo thn us now
…
so who in this failed state do you think can do better? don’t tell me about chakwera or Chilima. Jesus come back and save your people
Th problem wth us we want to chose someone wth a political history …..not someone hu wil rescue us. Bt I really hate this family mostly this idiot so called APM .. maybe his brother dd something nt this duck.
oky fine we head everything mwanena so we asking u to choose aright leader especialy ur uncle pa udindo wa uplezdnt my be banja lakwanuli lizakhala la chilungamo tikazakuvoterani. koma chomwe ndiziwa ine mw palibe wabwino timangosiyana ma %pa nkhani yakatangaleyi.
i am hundred % sho dat dat president si Mmalawi
Whatever u can say bt its being stupid to b ruled by 1 family in this whole nation. I dnt mean must b my uncle as some of u take it bt we hv to try someone else for a change …we never knw maybe we can c a hand of God thru him coz wat we nid as a nation z someone hu can rescue Malawi frm this situation … I knw he wil still have to steal frm us again bt maybe he won’t reach this point. Remember the 1st term for Bingu ….. he really dd t well. So maybe someone can do that again for th better of our kids.
They can’t agree with u #mathewsEkasamba coz they are members of D.P.P.why you always talk about Jesus? What about those countries who don’t know Jesus yet they are rich more than us? for example China ,Japan ,Korea, Arab countries and many more.
DPP 2019 Bomaaaaaaa……
AMalawi tili maso n we r watching wateva nonsense z happening in this government. We knw wat we want. Remember wen u talk ur nonsense to say DPP woyeee… its only u on fb…bt hav a look @ millions of ppl in th village hu r sleeping wth empty stomach yet their food z being consumed by Zambians thru ur selfish Chaponda. How do u feel to c them crying? ???? Dnt just talk coz u hv ur data then u can write ur rubbish. I feel sorry for our nation mostly those in rural areas as I hv been raised there n I knw wat it means to sleep wth an empty stomach.
Chinanso chisilu ndinu uncle Mkasa. Umbuli uzakuchokani liti monse munayambira kuinbira mfiti mmanja? ? Mwaimbira Bingu .. wen he died munali ndi Amayi …pano mwakweranso izi. R u happy to hear us crying? ? Yamba kuimba gospel coz nthawi yako yatha … bt usanatero, tulusa kay ina yopepesa amalawi kuti watinamiza popanga encourage umbanda thru ur music. Suka ……
Nkasa masaya otupao chisiru
https://www.facebook.com/drchaponda/
Siwagona amene tamudzutsani!!!.
Mkasa ayimbenso zoti chaponda wapezeka ndi ndalama zambirimbiri Ku nyumba what a stupid musicians appreciating every thing
Poyamba inu nomwe a 24 kaya chani uko mumati he’s resigned, manyazi mulibe reporting conflicting stories!
A EVERY BIGHAND TO MR PRESIDENT FOR THE JOB WELL DONE PATSALANSO ENA AWO NA UYONSO BWANJI VIKUWONONGA DZIKO VIMENEVI.
Chaponda ndi mbuzi enieni
chaponda ngati sanakunge ibani kachiwili ndalama ilipobe m bomamo m kulu wanuyu sadakumangise
I am Mozambican and I know very well the history of Malawi… Malaweans are easy to be feaked. Bingo Want hark a did shit and you elected his Peter Mutharika, which future are you waiting that Peter can give you?Malawi it’s not under Kingdom rule, so why you still believe thieves. Be wise….
Bligado patarau voce fara true
ur from Mozambique so Wat is affect u in our country??
Nothing wrong Carlos.Continue to comment please. We are in a global village
Carlos if you are wise enough end the fighting in your country.
Pointless
#Carlos you are talking true bro, don’t worry who disagreed with u.they are brainwashed by D.P.P thieves. U r right D.P.P is full of thieves.
but CARLOS is only try to open ur eyes Guys…kkk what is wrong about that?? Eiish amalawi enawa??? mr Carlos u can speak ur mind n u r most welcome.
Sounds good mr Carlos but next tym, remember to shut your mouth its none of yo fucking bussiness” but yeah… I like your great comment
Kkkkkkkk… but u guyz whats wrong with Mr Carlos there? I guss he is chewing the cud nothing wrong with him,…
U r true most malawian people r blind people they dont see,the driver is the drunker
I thought of the same thing when Peter won, why would a country elect the brother of someone who had messed up the country? But I came to realise that we play politics of tribalism, and this is common in Africa, we don’t listen to the issues the candidate is promising instead we follow regionalism and tribalism.
To be a leader is a gift from God not the power of the people, the people are there just to finish the bussiness. Malawians are not stupid bro
@ Chiku, r u sure u’r not mentally distabed? Read dat carlos comment again pls, u wanna tell me dat there’s nothng wrong de? Ok” hw come a Mocambiqan ass-holle knw malawian history vry well? School me on dat one, he may know anythng in Malawi but not EVERYTHING
hay guys I love Bingu but not his brother.. if you call Bingu being whatever you say, then wabwino ndani?? remember how he has developed Malawi, there is no need to remind you,maybe iweo ndiye wabwino eti?? to what Mozambique guy and unthinkable malawian chiku
Why you still keeping Mugabe brother,is he a life president?
Rashid” it is impossible for yew to learn what u thinks u already knows
Ummmmm kuchita kugona chifukwa cha kukhuta Vingoma. kkkkkkkkk. Yamupweteka mnthumbo makande kkkkkkkk
NDIMUNTHU WAKUBA AMENEYU
THEIF WAS IN THE BUSH BUT KNOW HE IS ON THE HAND OF JUDJEMENT
Kkk
Eya koma chimangacho ife tuchifuna zachabechabe ife ayi,
Koma ndiye mochedwa zinthu zitayipa kale
mulungu alemekezeke pothana ndizimenezi komazisathele apa iyayi ofunika àkalowe bac
Ali limodzi ndi bwana mkubwayo nayeso asechedwe they are just the bunch of robers in blues fuck men!
Kkkkkk nde mwati Champweteka nchimanga etiii oky!!
Hon. DAUSI NDI YUSUFU NKASA ALI KUT PA NKHAN YII??
Mr. DAUSSI come and tell us now about money laundering (sp).coz malamulo mukuwadziwa .
Alibe chonena pano, vocabulary yonse vruuuu pha kkkk
nkasa tikudikira ma lyrics ena
when chakwera comes to power,all rotten thieves will be booked
maybe 2039
Chakwera is too dictatorial(arogant) titha kuzalira naye. Amene azawineyo ndi yemweyo koma kwaine, am fed up!
Billy C Jali and its just too short…waya say ?
Don’t dream during day time ,CHAKWERA will not server mcp as TEMBO did and cannot rule MALAWI
May be 2080
May be 2080
Weather u like or not we will vote for him, chakwera is not worse than Peter muntharika.
You always vote for him but he doesn’t win ?????, do you like losers?
Even if it can be 2059, mbala zonse where they belong basi
DPP 2019 boma……..APM 2019 bomaaaa
Zakhala bwino kumukhiya chaponda
Following
President sangachotse munthu asafufuze tithokoze kuti amuntharika asiyana ndi chair,Achair anathawitsa aMlamba
Abweze zomwe anabazo ngati ndi chimanga abwezeso galu ameneyo
Chaponda Ndi Ofoira Chikhalirenicho Akumakufufudza Iweyo Ndalama Kumazisiya Patete,anzako Adayesetsa Kumakuikira Ku Mbuyo Kma Zakukanika Wekha
Vuto Mukuba Mutakalamba Zoona Mamillioo Onsewa Kumasunga Mnyumba
Chibadwileni Peter Muthalika cha mzelu wachita ndichimenechi,chatsala chilango tsopano.
Ayi ndithu sanachite za nzeru olo pangono
He has done it coz of the peer pressure, otherwise he wouldn’t have fired him
kumene samafuna ku fire km achita manyazi kamba kamamil……n apezekawa.
kulinjala chifukwa cha ameyo
LEt this idiot go with his sekfishiness after all
kkkkkkkkkk chapweteka chimanga, chapweteka chaponda, Hopeful wa DPP 2019 Bomaaaaaaa, ng’oooo…
Komaso aulule amaba nawo usapite wekha n”samilo tengopo pls
Work done!
President ndiwakubanso asatipusitse apa, bwanji amasiya nthawi yonseyi osamuchotsa? mbava yaikulu ndi president.
Nkasa And Kapito Where Are You?
Musamalimbane Ndi Mabilionare.Ma Mp Osusa Onse Can Be Paid By Chaponda For Ten Years.
Don’t stop there those who robbed Malawians funds for the last 20 years must be investigated and should brought to book
Zavuta
Sitikuwopa ife a Dpp war on 2019.Tilipo ife ndi boma.Olo mufuni !!!! peter!!!!! no fear kamlepo,or ulandi mussa and chakwera now!!!! ?
Ukufunika chipatala chachikulu iwe
alinane civic education yamphamvu Pepani mulungu akupatseni madalitso.
Za ziii
pa zako iwe
He will be nexst president
Chisiru sopano ndi Joseph mkasa hhhhhhh kuimbila mfiti manja. Koma umburi zedi siwabwino
Ndiye mwati champweteka nchani? Admin ndipatse ng’oma ndiimbe champweteka nchimanga
ndigaire meter chaponda tiulure gulu
Following…..Sikut Zithere Pompatu Tudikra Kuona Zilango Zomwe Alandire Mdallayu…..
Bank Nkhonde Chaponda
Handsome Man Mr Chaponda, adakakhala munthu wamba bwezi ali manja mwa apolice mkumati tamanga chifukwa tikuganizira kt adapezeka ndi ndalalama zochuluka mnyumba
Zoona ndipo olo amwenye onse akhala akugwidwa ndi cash aja, palibe ali ku ndende andyet they call themselves malawians.
Amangidwa liti? Akuchedwa
Musanģomuçhosa kokha komanso akaleweko maula galu ameneyi
Boma lilibe ndalama koma mukutsamira ma Dollar ngati pilo? BP will strike you.
zaboza zmenezo amangidwe ameneyo
muyende bwino a chaponda
Uziona wakalamba watha Iweyo
ok
Kkkkkklkk Asova Nd Umbava Wake
kuba kutchuka mpaka kufikanapo pauchitsiru, munthu amalemekezeka uyu koma lelo aaah!!! mbola timayembekeza 2024 kuti tizamuvotele koma wandipasa chikayiko
koma ndi billioner or wasauuka ?
Chaponda thawaaaaaaaaaaa apolisi akubwera.malingaliro odzakhala president apa ndie asokonekera.mwakhala mukumukumbira dzenje chilima lero mwayaluka
Khope ya munthu okuba ndi mmene ndimaiziwila ine imakhala chomchi!
Praise the lord
Komaso ameneyu mukanangopita naye kumaula akafele konko.
Friends become enemies! Soory mzimu wanu uwuse mumtendere munatinyasa daily kumamva zochita ZANU asaah
Kikkkkkk champweteka nchimanga patse nyama nkaotche, champweteka nchimanga patse nyama nkaotche singing,,, kikkkk Njoka sitiweta ayi, mmaseela zedi ame aja, asadzachitaso bwana president
Wandikumbusa chenjenzo lochokela kwa a V.P,njoka saweta, km wamva ili mmutu
Kikkkk kumaweta msalulu wati? eti umatelo kuti umalumila tsoka
Akuti umalumira ku mchira
Kikkkkk ndiye lero walumatu
Uyende bwino chaponda,
aichita bwno mbava imeneyi
Eya Amububuda
997
mmalo moti muziti chaponda wamangidwa ndiye mukuti amuchosa pa unduna ndiye ife titani bola akanamangidwa bwezi zili bwino
Thanks! ngati zampweteka awulure anzake
Kamlepo kalua siwopenga koma openga a DPP.tsek
Zikomo kwambiri mulungu osati peter
Tikufuna kuti amangidwe chimanga chimenecho akadyere ku maula
Too Gd!!