Champweteka chimanga Chaponda: Amuchotsa pa unduna paja

207

Atapulumuka kwa kanthawi, tsopano wagwa chagada George Chaponda.

George Chaponda.

Chaponda champweteka chimanga

Chikalata chochoka ku nyumba ya boma chimene wasayinila mneneri wa a President chalengeza kuti a President a Peter Mutharika amuchotsa Chaponda pa unduna.

Malinga ndi chikalatachi chimene a Malawi24 tachiona, a President ati atenga mphamvu zonse ndi ma udindo a unduna wa zamalimidwe.

Kunalowa chipolowe ku unduna wa zamalimidwe pamene nduna yake inapezeka kuti inachita utambwali.

Share.

207 Comments

 1. Kodi iwe chaponda mutu wakoo anakupondani amai ako uli mwana .??? Nakupangani amai ako pokumbeka chonchi chimutu chonyasa dengu latomato ku Ncheu. Amathamangira kuti bambo ndi amai ako. I mean time for sex masimmba amuthu

 2. Joseph. Mkasa ndi muthu chinzeleze ophunsa iye amafuna. Kungelera ndalama kapena kuti papsa tonola .mutu uja sugwirchito anawagwensa amai ake Ali mwana.wang’no Ali kumbuyo kwa amai kumunda

 3. Point! Play a song to this man called chaponda done by Joseph mkasa dedicated to him….
  Mr Mkasa backed up him with total mind but he forgotten that “chomwe wamkulu sakuchiina atakhala pansi…ngakhale ana ngati che mkasa ndi ineyo pandale or titakwera mumtengo…sitingachionenso.

  Mr mkasa can u just interprete that song as quick as u can paja simumachedwa kutembenudza.

  Shame! Malawi! Above all…the heavenly judgement is heading you…if u don’t repent!

 4. “This inquiry is a waste of time and resources,you will not find anything,its just jelousy of Malawians-kaduka.Am innocent and i cant resign”.

 5. Dr Chaponda musadandaule chifukwa mwayesedwa kawili kasala kamodzi kowawa kwambili for you to break through in the mighty name of Jesus. Simungakhale pamwamba musanayesedwe katatu never, even professor A Mutharika tempted for three times ;(1) when he was the minster of education (2)green card and (3)treason case then he broke through -amen

 6. Dr Chaponda musadandaule chifukwa mwayesedwa kawili kasala kamodzi kowawa kwambili for you to break through in the mighty name of Jesus. Simungakhale pamwamba musanayesedwe katatu never, even professor A Mutharika tempted for three times ;(1) when he was the minster of education (2)green card and (3)treason case then he broke through -amen

 7. Inuyonso ndi mbava panokha Ndalama zabungwe mwaba zja?Nanga zakumpingo zja?Kuofesi Kwanu Mwabakonso,nanga ndalama Mwagulitsa Katundu Wa Akazi Anu Zja Mwapita Nazo Kt? INUYONSO MBAVA KOMA SIMUNAGWIDWE

 8. Ife Tikuvutika Kufuna Ntchito, Inu Ndikumangogona Mpaliamenti,mwezi Ukatha Mukulandir Ndalama Za Nkhan-nkhani, Yendetsani Ntchito Iyi Amalawi Akufa Ndi Njala, Mukupezapo Mwayi Woberapo Ndalama, Ndi Zimenezotu Mwadzimenya Double Kick!!i

 9. Kungochotsa akagone pa shamba pa maximum person, he think’s is aboves every one chifukwa cha zindalama zakubazo?nkumayakhulanso motumbwa kuti ali clean mbone ndi mlungo,haha atsanso azinzako!

 10. Acitabwino Kumlanda Udindo Tsopano Mwina Dzithu Zingayende Bo,o Ndik Ziwa Kut Athu Amzuko La Malawi Asangalara Makamaka Ineyo

 11. Christ mollywood malawi
  A drama group that aims at preaching christ through drama and movies is looking for actors and actresses to be part of their upcoming drama plays.

  Qualification
  1.should be bornagain christian
  2.fluent in english and chichewa
  3.should be based in lilongwe

  Person specification
  1.willing to travel and take part in both movie or drama plays
  2.good communication skills and good understanding of the bible and pentecost deeds
  3.understanding and godly
  4.bornagain christ like christian

  Salary :N/A
  Employment type: part time
  Location:lilongwe
  For more info on how to apply follow and inbox christ mollywood malawi page by using this link
  http://www.facebook.com/Christ-Mollywood-m...

 12. The ruler of the world is devil. So you want good things from devil. Jesus refuse to pay tax, ma fello forks love money love evil.

 13. musangonena kuti mwamuchotsa mpamene kuseri muli limodzi.
  muzimva chisoni ndi momwe anthu akuvutikira m’midzimu. mwina poti simumayenda.
  amangidwe ailawe jail.

 14. Osangonena kuti mwamuchotsa mpamene kuseri muli limodzi.
  muzimva chisoni ndi momwe makolo ndi ena akuvutikira m’midzimu.
  amangidwe ailawe ndende Galu ameneyu!

 15. am following malawi 24 from zambia, u guys in malawi u are even luck that that chaponda has has been fired, though too late, us here in zambia the agriculture minister was even promoted from the ministry of agric to the ministry of justice, despite having overwhilming evedence about the maizegate, but the presidend is busy merrying with the corrupt minister, as we are talking there is no comment from the president. the anti corruption commission has been a toothless shit, there is nothing to do. so well done malawi for pressuring mr muthalika to do the right thing. let not politicians tbke advantage of us.

 16. Amati atani ndi Peter wakeyo? Agonjera zofuna za anthu. Ndani angalore kuti anthu omwe akuganidzilidwa kuba adzikakamirabe pa mipando? Nawonso a peter kuganidza mochedwa ndi bwenzi atamuchotsa kalekale.

 17. Nde muchiyitane chinja chinadzipatsa chokha uphungu chija chitiyimbile nyimbo yake ija kkk koma dyera lako likupweteketsa ndithu kaya unazimvela fungo ndalamazo nde wawuponda chifukwa nde zatutidwako

 18. Remember that these people are on the same. Pipeline including the president himself, he want to blind Malawians, onse ndianthu akuba okhaokha musatipusisepo apa,

 19. To late to save Jerusalem mr president,while the cty has already flooded,people were talking about it bt you were giving them death ear and now its wen you have realised that its true”timadziwa kt mwana wako umamukhalira khonde akalakwa,kmabe ukapita kobisika umamukwapulamo ndthu nanga.

 20. The problem we decided to elect presidents frnd one family as if all Malawianz r dull. Wats so special wth Munthalika family …????? They steal bt we still trust them. After th death of Bingu ACB found bags of cash in his house ..bt stupid ppl still chose his brother. Wat r we looking for Malawi? ??/. Peter wants to make us dumb n trust that he’s nt behind scenes …bt surely he’s there
  Nonsense! !!!!! We r suffering coz of few stupid so called “educated ppl “. Do u think its only 1 educated family in here? ? Pls Malawianz …lets consider this as a grt lesson so that we vote for a change this 2019. Otherwise we wil still sing this same chorus til our innocent kids suffer mo thn us now

  • so who in this failed state do you think can do better? don’t tell me about chakwera or Chilima. Jesus come back and save your people

  • Th problem wth us we want to chose someone wth a political history …..not someone hu wil rescue us. Bt I really hate this family mostly this idiot so called APM .. maybe his brother dd something nt this duck.

  • oky fine we head everything mwanena so we asking u to choose aright leader especialy ur uncle pa udindo wa uplezdnt my be banja lakwanuli lizakhala la chilungamo tikazakuvoterani. koma chomwe ndiziwa ine mw palibe wabwino timangosiyana ma %pa nkhani yakatangaleyi.

  • Whatever u can say bt its being stupid to b ruled by 1 family in this whole nation. I dnt mean must b my uncle as some of u take it bt we hv to try someone else for a change …we never knw maybe we can c a hand of God thru him coz wat we nid as a nation z someone hu can rescue Malawi frm this situation … I knw he wil still have to steal frm us again bt maybe he won’t reach this point. Remember the 1st term for Bingu ….. he really dd t well. So maybe someone can do that again for th better of our kids.

  • They can’t agree with u #mathewsEkasamba coz they are members of D.P.P.why you always talk about Jesus? What about those countries who don’t know Jesus yet they are rich more than us? for example China ,Japan ,Korea, Arab countries and many more.

  • AMalawi tili maso n we r watching wateva nonsense z happening in this government. We knw wat we want. Remember wen u talk ur nonsense to say DPP woyeee… its only u on fb…bt hav a look @ millions of ppl in th village hu r sleeping wth empty stomach yet their food z being consumed by Zambians thru ur selfish Chaponda. How do u feel to c them crying? ???? Dnt just talk coz u hv ur data then u can write ur rubbish. I feel sorry for our nation mostly those in rural areas as I hv been raised there n I knw wat it means to sleep wth an empty stomach.

  • Chinanso chisilu ndinu uncle Mkasa. Umbuli uzakuchokani liti monse munayambira kuinbira mfiti mmanja? ? Mwaimbira Bingu .. wen he died munali ndi Amayi …pano mwakweranso izi. R u happy to hear us crying? ? Yamba kuimba gospel coz nthawi yako yatha … bt usanatero, tulusa kay ina yopepesa amalawi kuti watinamiza popanga encourage umbanda thru ur music. Suka ……

 21. I am Mozambican and I know very well the history of Malawi… Malaweans are easy to be feaked. Bingo Want hark a did shit and you elected his Peter Mutharika, which future are you waiting that Peter can give you?Malawi it’s not under Kingdom rule, so why you still believe thieves. Be wise….

 22. Sitikuwopa ife a Dpp war on 2019.Tilipo ife ndi boma.Olo mufuni !!!! peter!!!!! no fear kamlepo,or ulandi mussa and chakwera now!!!! ?

 23. Handsome Man Mr Chaponda, adakakhala munthu wamba bwezi ali manja mwa apolice mkumati tamanga chifukwa tikuganizira kt adapezeka ndi ndalalama zochuluka mnyumba

  • Zoona ndipo olo amwenye onse akhala akugwidwa ndi cash aja, palibe ali ku ndende andyet they call themselves malawians.

 24. kuba kutchuka mpaka kufikanapo pauchitsiru, munthu amalemekezeka uyu koma lelo aaah!!! mbola timayembekeza 2024 kuti tizamuvotele koma wandipasa chikayiko

 25. Chaponda thawaaaaaaaaaaa apolisi akubwera.malingaliro odzakhala president apa ndie asokonekera.mwakhala mukumukumbira dzenje chilima lero mwayaluka

 26. Kikkkkkk champweteka nchimanga patse nyama nkaotche, champweteka nchimanga patse nyama nkaotche singing,,, kikkkk Njoka sitiweta ayi, mmaseela zedi ame aja, asadzachitaso bwana president

 27. mmalo moti muziti chaponda wamangidwa ndiye mukuti amuchosa pa unduna ndiye ife titani bola akanamangidwa bwezi zili bwino

%d bloggers like this: