After spending a number of years without recruiting soldiers, the Malawi Defence Force (MDF) has disclosed that it will soon conduct a recruitment exercise for new soldiers in the country.
Speaking in Lilongwe at Kamuzu Barracks, MDF Commander Griffin Supuni Phiri disclosed that all resources are ready for the recruitment of new Malawi Defence Force officers.
“As you know that it took years without recruiting soldiers, MDF will soon do the exercise,” Phiri said.
However, Phiri did not disclose the exact dates when the recruitment exercise will be conducted.
Last year social media was rocked by speculations claiming that Malawi Defence Force was inviting people to join the military.
Malawi Defence Force refuted the claims saying that it did not have plans of conducting the recruitment exercise that time.
Atengeni ana anu, bwanji mumabisala pa chipande?
ZOONA
But it needs corruption and relatives to be qaulify as a soldier
This yr ndi waku Tz kukaliza futibasi, tchito zathu amuna izi enieni olimba mtima osati azimayinu!
guyz osazivuta kudalira kuti this year mugwira mfuti palibe mapeto ake uzipeperesa wekha bcoz owatenga awatenga kale.pamene zikufika pa public-pa ndiye kuti ana a asilikali akwana kale
Where were the ppo trained to be soldiers waiting ‘recrutment?’
Tiyese zimenezi
Zilembanani muzikaphedwa uko if zapamalawi tinazisiya tikusaka saka kuno jon
09 June,2017.
Zathu zomwe izi….tikathamange pa mafco bas,like father like daugh
hahaha unganthamange iwe???
thocco mweneungu…..weee ulipo…
hehehhehe MDF is a nightmare for us. having the smallest army army in the entire region
Ife tikathamanga ndithu chaka chino,ndizomwe timafuna zimenezi.big up MDF !!!!.
Awa ndie amandimvesa kuwawa nthawi zonse amangonsisiya
Kungofuna kukwanirisa lamulo loti mwatulusa vacancy ogwirawo mutawalemba kale shame on u.
Let’s see
ready to protect my nation
Kale ntchito ya usilikali anthu amayiwopa koma lero ndiyimene akulimbilana.ulova wavutadi panyasa
Achani
Yes amalawi timadalira inuyo
Thats welcoming idea my be chaka chino tibvare jombo basi.
zaulendo munditenge.
Zongotha ndalama zaboma basi, msilikali kuyamba ntchito mpakana kudzalandira pension opanda kulidzapo mfuti ngakhale tsiku limodzi daily kumangopolisha jombo basi akati agwira ntchito ndiye kuti apita kokayan’ganira mitengo ku Chikangawa.
msamatiphimbe kumaso chosecho mnawatenga kale azibale anu iyaaaa
Zachibwana zenizen pa Malawi, bola otsatulutsa ma vacancy WO, mungotenga abale anuwo kusiyana ndi kubitsala kumbuyo kwa ife aphevu dyera Ku mthiko opanda abale kumeneko.
bola pasachike chinyengo
Kkkk whats the qualification????
18+
opanga training ndi ena ,okagwila ntchto ananu & abale anu.ndy chonzuzla anthu kutrainer ndkumawacosa b4 one month to finish thea carear ndchani .
Mmene mwateromo alemba kale achibale awo kwa amene ali kale konko,ife omwe tilibe abale athu kumeneko chafa kwa dolo
They ar so corrupt and favourtism ine bola ndipange pasport wautali nkaoloke zambezi mwina nkaonako zina
Msitikali wanji.opezeka mwakachasu
Mbuzi inu osataya nthawi ndikutiuza ife zopusa zanuzo ndintchitoso imeneyo beta G4s
uthengau chonde admn anthu amene amalemca ntchito zimenezi aumve,chinyengo chachuluka ngati akufuna azingolembana okhaokha osati azitisokosera apa akuwona ngat asafuna ntchito pamalawi pano ndani nde sibwino kumayesana.
Kumalandila marands wosati makwacha
Amry yakumalawi ndiyauchitsilu amalembana ntchito pachibale chinyengo chinakula bolo kumagwila yaugarden pajoni
JST WETNG TO GOD BE THE GROLY
Wat aa fuck’n’ story is……………….
..
.,………………………….. ……
……………,..m…….m………
ntchitoyo nafe tikuyifuna nafe tigwirepo mfuti,nchifukwa chake timagula magogodela kuopa kufa opanda kugwirapo mfuti
home of corruption but when war reap Malawi soldiers hahahahaha they will recruit even nganga zowotcha makala
Zausilu
hahahaha koma zimenezi zomatengana pa chibale muzatha nonse pakamodzi
soldiers on this pic are looking very sad what happen ? they meant to look happy ,after all they are well payed than teachers they receive they salary on time
I remember in 2002 the army recruitment exercise got me in after passing presentation,dictation and medical tests at Cobe barracks in Zomba. Recruits were immediately transported to MAFCO in Salima,after a week we were introduced an introductory military ground parading. I liked it because at school history subject was my cup of cool ground water,week two there were faces that “completely failed recruitment tests” arriving at the college then it was when I personally realized that Nepotism is here to stay with its cousin Corruption bobbing up and down in Officers’ mess. There was No ways I could be a regular soldier because I didn’t have military authoritative “backing” via nepotism or corruption. My friend who I passed with had his soldier brother-in-law frequently visiting him. Recruits! “Another medical test on the way soon at Salima hospital” In my heart I named that Salima hospital test [for rib cage] a “filtration gauze” where recruits with military brothers,sisters,fathers,cousins,in-laws,sons,daughters and relatives or via “palming” had exclusive “live wire” advantage. Finally from Zomba District recruits 87 including those who failed Test at Cobe barraks. 32 from 87 were immediately weeded so it was like the 32 were temporarily holding positions for those who came afterwards. It was fucking painful.
kafiken
Denis Kisa Bulenge yambaibulo ndiyamake zana pano nkhondo ndi ya Ambuye
do it ngati intenal vacancy mukamapanga select achabale anuwo palibe zizamupange affect osavutisa ana anthu is not fair at all
Goodnews
I hope now atengana kale anthu amenewa pantundu,enawa akangopalidwa pakamwa osatengedwanso ayi.eeeeeish guys Malawi
Kungoti sindimaisilila ai koma ndipange zanga tithamangisane
Kkkkk agalu inu katengeni akazanu ndi ana anu mukawarembe osasokosa anthu zopusa
Obvious family first, or ntakhala ine i can’t employ some1 else while my brother akugudubuzika ndi ulova, n its not only ku mdf kokha akuchita izi its ol over Malawi nation, WAKWITHU
Zoona lembani anthu opanda chinyengo posaona kuti akuchokera kuti ndipo ndi mtundu wanji wa anthu
Tanzania yaopsadi eti….kkkkk anzanuwo nde aku trainer ndi North Korea inu muli ndwii…kkkkk
Asilikali palibe chomwe amachita agalu amenewa ntchito kulanda makala amphawi kapena kukwata azimai by force. Bola apolisi ngakhale naoso ndiagalu alibe khalidwe kupempha too much…………
Agalu omwewo anakwatira achemwali ako
unyatu agalu omwewo by the end of the month akulandila salary.ukhala choncho ndi umbuli wakowo unkathawila dala xcul n’gooo uliladi siunati
Chilungamo ndichikondi chinatha akatero analembana kale anao ndi achibaleo opanda abale kunkhondokofe olo titani sangalembe ananthu
Dzakuti dzamawo lembana ana anuwo bax
Hokheee…tiyeni nazo
Ndipo mlembe ambiri, kuti tikonzekere bwino zososolana ndimaswahiriwa akuderera kwabasi!
#jombo
Musiye chinyengo anthunu m’mangotena paubale wanu aaah! tatopananu pano! nafe tchito imeneyo timayifunatu
akapolo athu zilowani
ndimayifuna koma nkhani ndiya atoti manje”kulibeko m’balewanga ku barracks”
kkkkkkkk pamalawi ndepamenepo atengakale anthu 1000 achibale
Chinyengo ndeeee disease Yopanda mankhwala pa Malawi piano, komabe ngat ndili and mwayi ndigwira mfut chaka chino.
musavutike ndi kulengeza pa media pa nkhani ya recruitment chonsecho mukudziwa kuti mumatenga ananu ndi abale anu,zausiru eti
world war warm ups
Tangonenani kuti abale ao asilikali abwele talembe zopusisana. Zatikwana
Zaboza
Left! Right!
Zapansi pompano izi kumwamba kulibe evn mpang’ono pomwe.
Ngati nkhani ili ya nyanja nde kuti akufuna anthu a pa battlefront….. hahahahaha
U don’t hav to tell us that. Jst tell soldiers to bring their Relatives. That’s wat happens wen it comes to the recrutment of soldiers. Do u call that recrutment or Chieftancy.
Yeah
Kumatenga azibali awo ndichifukwa chake masiku ano Asirikali ambiri ali opepera. mphamvu alibe amangokhalira kumwa kachasu basi.
Tell them to bring their brothers to be soldiers as usually,osati zomapusitsa anthu apa!!!
People are using old maps teach them proper map reading. Man the posts beef up
Mwina tipange defend nyanja yathu
am ready to be recruited as a melitia soldier I want to defend my country from being robbed of our lake by the taifas!
Ntchito yausilikali kaya kupolisi amalemberana chibale kodi zimenezi zizatha liti? Zimatiwawa kwambiri anthu okonda chinyengo inu musamatiuze zimenezo zingolembanani basi
Nkhondo ndi iyi ikubwerayi yatanzania,ndiye mumalembana pachibale mutha ntunduwonse
Anatenga kale anthu ali pa list, onyema, achibale, azinzawo ndi ana awo… Akanapanda olo kunena, azimgosankhana okha
Luke Chinoko.what you wanted right?
Just indicate here how much money should we keep …am a secret person .kkkk i can only tell five people sir
Zazii mipala yanu nonse asilikali bola ndizingosambitsa nkhalamba ku jon konkuno
Ngati pali recruitment ya chinyango pantchito zonse ku Malawi iyiyi ndi number one. Otengedwa amakhala ana a Silikali. Akati lero tilemba aku Chitipa siumupezapo or mmodzi. Munthu kudabwa kupeza otengedwa nkukhala aku Mchinji, Zomba. kumamva ndithu chiyawo chikulankhulidwa pa recruitment yaku Chitipa.
Ngati pali recruitment ya chinyango pantchito zonse ku Malawi iyiyi ndi number one. Otengedwa amakhala ana a Silikali. Akati lero tilemba aku Chitipa siumupezapo or mmodzi. Munthu kudabwa kupeza otengedwa nkukhala aku Mchinji, Zomba. kumamva ndithu chiyawo chikulankhulidwa pa recruitment yaku Chitipa.
Kkkkkkk koma iwe undipha ndi mphwete
Ayise Jukad Kantengule Ndikunena moopa Mulungu. Tinkachita kuwaona akutsika ma TATA kufikira kuma Stand ku Mzuzu Stadium ena akuvutika ndi interview. Kenako poitana maina, munthu kumayankhira ku Stand freezes ali kukamwa. Kkkkkk
pure true mbuzi za anthu
Wandinenela ndi kwanga komwe.
Timva kuti wina wanhatidwa atalandira ndalama kumunamiza wina ati akamulowetsa usilikali
Kutigwira m’maso ife uku..tilibe ma 50 thousand aja munksti tipereke aja atengeni ana amabwana omweo
Tilembeni tikalande nyanja
Yes !! We need it ndkale lija please we are stil waiting!!
kodi amati udf kapena mdf zandale izi!!!
asilikali achepad ofunika kuwonjezela kut akateteze nyanja uko.koma chaka chino munditengeko ndinayamba lija ndikale.
Mukulengeza apa ngati zenizeni pomwe mwalembana kale pachibale ntchito imeneyi
AMALAWI!! TATANI KODI? NDANI ANGASANGALATSIDWE NDI KUPHA KAPENA KUPHEDWA? ZOONA M’MALAWI OLIKONDA DZIKO LAKE MPAKA KUCHEMELERA LIU LA NKHONDO?? NDI BWINO NDITHU AMALAWI TITACHEMELERA KWA YEHOVA KUTI AWALETSE AMALIWONGO KUTI ZOLINGA ZAO ZILEPHELEKE!! MALIRO SAOMBELA M’MANJA KOMA UFULU-MTENDERE!!!!
AMALAWI!! TATANI KODI? NDANI ANGASANGALATSIDWE NDI KUPHA KAPENA KUPHEDWA? ZOONA M’MALAWI OLIKONDA DZIKO LAKE MPAKA KUCHEMELERA LIU LA NKHONDO?? NDI BWINO NDITHU AMALAWI TITACHEMELERA KWA YEHOVA KUTI AWALETSE AMALIWONGO KUTI ZOLINGA ZAO ZILEPHELEKE!! MALIRO SAOMBELA M’MANJA KOMA UFULU-MTENDERE!!!!
Tikapita kukamenya nkhondo.. Mulungu azatithandiza ngati nyanjayo ili mbali yathu. Kodi mi bible mesano opembeza amamenyaso nkhondo kodi? Chi Christu chamasiku ano ndi chamantha. Mumangobisarira mudzina lakuti Mulungu atimenyera nkhondo. Tipempheredi kuti asirikali athu ndi dziko lathuli liteteze chuma chake. Zikafika komenyanako, timenyana basi.. Mulungu atithangata.
Kodi pa mutu wa nkhani anena kuti kuli nkhondo? akungowonjezera asirikaliwo basi si za nkhondo komanso kufuna kuchepesa umphawi
ABALE ANGA NONSE AWIRI POTI MAINA ANU NGOFANA A DENIS!! EEE! Ndizoonadi mu BIBLE nkhondo zinalembedwa komatu mutawelenga bwino-bwino muona kuti nkhondozo zinali nkuchitika pokweza dzina la YEHOVA NDI MTUNDU WOMUDZIWA YEHOVA! Potero a DENISI dzina la YEHOVA LIMATANDIDWA! Kachiwiri-mwina mwangothamanga a bale anga kuti muchite m’tsutso-pepani! wina wanena ndithu kuti alembedwe poti apita kukapululuka pa nkhani ya nyanja ndi TZ. Mukatero a DENIS chimenecho ndiye CHITUKUKO? Kachitatu- Ambuye Yesu adati masiku otsiriza mudzamva mbiri za nkhondo komanso kuukilana pachibale mpaka kuphana! okondedwa abale anga mwaima pati? INE NDI PEMPHERO LANGA MULUNGU ATICHITIRE CHIFUNDO NKHONDO TOTO!!!
ABALE ANGA NONSE AWIRI POTI MAINA ANU NGOFANA A DENIS!! EEE! Ndizoonadi mu BIBLE nkhondo zinalembedwa komatu mutawelenga bwino-bwino muona kuti nkhondozo zinali nkuchitika pokweza dzina la YEHOVA NDI MTUNDU WOMUDZIWA YEHOVA! Potero a DENISI dzina la YEHOVA LIMATANDIDWA! Kachiwiri-mwina mwangothamanga a bale anga kuti muchite m’tsutso-pepani! wina wanena ndithu kuti alembedwe poti apita kukapululuka pa nkhani ya nyanja ndi TZ. Mukatero a DENIS chimenecho ndiye CHITUKUKO? Kachitatu- Ambuye Yesu adati masiku otsiriza mudzamva mbiri za nkhondo komanso kuukilana pachibale mpaka kuphana! okondedwa abale anga mwaima pati? INE NDI PEMPHERO LANGA MULUNGU ATICHITIRE CHIFUNDO NKHONDO TOTO!!!
Nchito ya soldier ndi nkhondo nchito ya mbusa ndi kulalikira, malemba omweo amati oyenda ndi lupanga azafa ndilupanga
Ndiye kuti mukufuna kutsutsana ndi bible abusa? Mwati bible lidati masiku otsiriza mitundu idzaukirana. Nanga patapezeka kuti palibe mtundu womwe waukiranapo muzatinji? Alekeni malemba akwaniritsidwe. Kukafa ndikumenyera nkhondo dziko langa sindikuwona cholakwika, kusiyana ndikungokhala nkumati Mulungu andimenyera nkhondo mtundu wanga onse nkutha.. Mulungu azandifusa kuti ” inu mudapabgapo chani pamene mtundu wanu umapululuka?” Abusa, dziko lililose anthu ake amapemphera, muyesere lero, mungokhala kwanuko osakagwira ntchito, muzingopemphera kuti Mulungu akupatseni chakudya chanu chalero. Ndithudi ndikukuuzani, inu mutsutsana ndi lemba lakuti ”uzadya thukuta lako” Ambuye Mulungu, amathandiza yemwe wapemphera nkunyamuka kukagwira ntchito yomwe amapemphererayo. Kodi mukundiuza kuti Asilikali a Tanzania atayamba kumenya a Malawi omwe azungulira nyanja ya Malawi, nkumawathamangutsira kumtunda. Mungasangalale asilikali a Malawi atangokhala osapangapo kanthu? YANKHO LANU LIKHALE LOWONA.. Ndiposo Mulungu angathe kuwalanga asirikali a Malawi atapanda kuchitapo kanthu. Kapena mukufuna asirikali m’malo mokamenya nkhondo apite ku phiri kukapemphera? ”UZADYA THUKUTA LAKO” mawu amenewa osamawachepesa. Kumbukirani kuti Malawi siikuyambisa nkhondo ayi, koma ukuteteza dziko lake. SINDIKUWONAPO CHOLAKWA KUTETEZA DZIKO LAKO.. GANIZILANI ZA M’BUSA JOHN CHILEMBWE, tiziti iye samawaziwa mau akuti Mulungu Wanu Azakumenyerani Nkhondo? Iye ankadziwa bwino lomwe tanthauzo lake, ndipi Mulungu anamumenyera nkhondo pomupasa mzeru ndi mphanvu zokalowera kwa adaniwo mpaka kukwanilitsa zifuna zake.. MULUNGU AKUDALITSENI ABUSA, KOMA MUSALOLE DZIKO LANU LIWONONGEKE MOPHWEKA. MPEMPHENI MULUNGU AWADALITSE ASILIKALI ANU NDI MZERU KOMASO MPHAMVU ZOMENYERA NKHONDO KUTETEZA DZIKO NDI ANTHU AKE.. BE BLESSED.
Aboooout turn!!!!
shaaaa anthu oti list yopita alembana kale !stop corruption abale
Aaah antchito yanji asilikali wo?
.
Ndalama zolembera a silikalizo tapititsani ku Education ana a eni wake alembedwe ntchito lika ndi kale
Analembedwa kale.
kkkk azilipidwachan
Munangoti talembana kale poti ngati Suli osewera mpira kapena wa nkhonya ntchito sungaipeze Ku MDF tikudziwa kale
kkkkkk musatayiletu ntima
Ndezachan poti nyanja anatenga a Tanzania
I can’t wait to be one of them?
takonzeka yambani tikathamange basi
Only Kaliati, Nankhumwas,Chapondas,Mwanamvekas allied will be entertained, Nkando Battalion
lekelatu m’bale kaliati-nkando battalion
Chabwino koma zikakhale zakamuzu zolembala pa Cominity centre Ground sizolemba ana azibale anuzo ayi
Chabwino koma zikakhale zakamuzu zolembala pa Cominity centre Ground sizolemba ana azibale anuzo ayi
ndikudikira coz panopa ulova washupha heve.
Lembani koma aloleni anthu opanda dzina alembedwenso
Tikathamange bas
Mukakula mtima mufa ndi u graduate wanu,anzanu akupata sure mochepa momwemo
2times Kulembela Osanditenga Ulendo Uno Ndizikadikilira Pa Gate Ansaaaaaa
They won’t still win a war against Tanzania
Zapachibale izi timadziwa kale ndiye zilembanani ngatinso ndintchito zonyadisa ….
Pamenepa Kumauzanatu Apa Guyz Tikaferekomweko Ulova Watikwana Ife.
Pamenepa Kumauzanatu Apa Guyz Tikaferekomweko Ulova Watikwana Ife.
I really need this job but too much corruption
Mac David Kamanga… Izitu izi… Be on the look out
Seen
Agalu achinyengo inu munandisiya zaka zapitazo chifukwa ndinalibe money pitani uko ndiziphuphu zanuzo
mudzangotenga adzibale awo
I will be there
lole! aya!ya!
We need more soldiers indeed. We need fresh blood.
Kkkkkkk adalemba kale abale awo ali kujoni uko akangofikira kukwera Tata
Kkkkkkkkkkk
Chinyengo chimakula ife anatisisa mutata okhoza khoza anangobwela wina amvekele ant 8 atsike iwe,iwe ,iwe tatsikani mpakana pa no ndie muziti kulibe chinyengo?
Eish!! That really bad.
Mmmm pepa Bro zibale ndi ndalama zatseka khomo olo zokuyenereza zitakhalapo
Mmmm pepa Bro zibale ndi ndalama zatseka khomo olo zokuyenereza zitakhalapo
inenso mnaziona pa chichiri
Waiting
zolowachinyengozi maka alomwe mungolowetsedwa chosecho ndinu mbuli dpp mundisamale
Machende ako mbuli ndi amako usayankhule ngati ulibe chonena.
Upezeni Rasta Malaya okongola mwavala ndi achifumu,,,ndikutukwana sizikugwirizana kkkkkkkk
Upezeni Rasta Malaya okongola mwavala ndi achifumu,,,ndikutukwana sizikugwirizana kkkkkkkk
Kodi Alhomwe ndi M D F recrutment zikugwirizana bwanji nangano umbuli wa Dpp govment zikugwirizana motani?? Mwadumpha maliretu!
Apo pokha mbuli ndiweyo sure coz ukanakhala wamzeru ndiozindikila sukanayankhula zopusa zakozo infact u r a savage mxiewww!!!
iweyo tebulo ndiwe savage tandiwuza pano amene akulembedwa ntchito panopa ambiri akuchokela kuti? Agalu. Iweso kachulu wawonetselatu kuti ndiwembulithelu chidzete chigendere ukutchula chinthu choti ulinacho mayi ako ulinawo palizazelu apa koma alomwa mundisamale fwetseke.
respect the peace colour mr kachulu
Anthu inu mumatikwiitsa zonyozana mitundu sizabwino
iwe Gwiremaso ukanakhala siiwe savage sukanayamba kulemba dzina langa with small letter. Kodi kwanu nkuti? Ndiwe mtundu wanji wamunthu, opanda khalidwe iwe kma unabadwa mwa munthudi iwe? Kapena mwa nyama? Muoneni akati vimaso mxieeew galu
kkk ndiimeneyo ikufuna kupezeka ntchito ija waku TZ mukalakatike ngati maverteynum kumeneko muzikakhala pasogolo madoloo pambuyo kkkkk
Paja wina walemba kale ku Karonga.
#GiftThindwa…
Chinyengo komaa
Zomwe Timafuna Zmenezo
Ndimadikira zimenezo, komano osati mukhale mwalembana kale3
They already know who they Wil take, very disappointing department
anthu oti adzatengedwe amakhara akuyenda nawo ,zachinyengo zokhazokha,
tikudikilira ndiwakonko uwu
Alembana kale musavutike
If Ts True,then A Sigh Of Relief.Am Desperately Looking 4 A Job.
iiiiiiiii kkkkkkkkk
Koma Chinyengo Chimachukuka
mwasiya,,,,chinyengo,,,,,
anzako alowa omwe ali ndi hope,
Saonanso zaka or msinkhu ayi, chifukwa gulu limeneli ndi straight wa ku nyanja…
Are they serious or they r just trying to impress the youth? These readers r full of lies,they only care about themselves
Recruiting soldiers ready for Tanzania over lake malawi dispute.
Im the one in need of this job!!!!
It’s my time to Come back second chance
tikudkrabe
nice
nde yake
more Sojah akufunikadi…..chifukwa nde dziko lathuli limenya nkhondo pompano….
Yes we need enough young active soldiers to defend our borders. We don’t know when Tanzania will slaughter us. We need enough our sons and daughters to defend us. We need enough recruitment not just 2000. We have enough money politicians are just stealing it because we don’t know how to use it
Tanzania man…kkk