MDF plans to recruit soldiers

Advertisement
MDF Soldiers

After spending a  number of years without recruiting soldiers, the Malawi Defence Force (MDF) has disclosed that it will soon conduct a recruitment exercise for new soldiers in the country.

Speaking in Lilongwe at Kamuzu Barracks, MDF Commander Griffin Supuni Phiri disclosed that all resources are ready for the recruitment of new Malawi Defence Force officers.

“As you know that it took years without recruiting soldiers, MDF will soon do the exercise,” Phiri said.

However, Phiri did not disclose the exact dates when the recruitment exercise will be conducted.

Last year social media was rocked by speculations claiming that Malawi Defence Force was inviting people to join the military.

Malawi Defence Force refuted the claims saying that it did not have plans of conducting the recruitment exercise that time.

Advertisement

185 Comments

  1. guyz osazivuta kudalira kuti this year mugwira mfuti palibe mapeto ake uzipeperesa wekha bcoz owatenga awatenga kale.pamene zikufika pa public-pa ndiye kuti ana a asilikali akwana kale

  2. Zongotha ndalama zaboma basi, msilikali kuyamba ntchito mpakana kudzalandira pension opanda kulidzapo mfuti ngakhale tsiku limodzi daily kumangopolisha jombo basi akati agwira ntchito ndiye kuti apita kokayan’ganira mitengo ku Chikangawa.

  3. Zachibwana zenizen pa Malawi, bola otsatulutsa ma vacancy WO, mungotenga abale anuwo kusiyana ndi kubitsala kumbuyo kwa ife aphevu dyera Ku mthiko opanda abale kumeneko.

  4. opanga training ndi ena ,okagwila ntchto ananu & abale anu.ndy chonzuzla anthu kutrainer ndkumawacosa b4 one month to finish thea carear ndchani .

  5. uthengau chonde admn anthu amene amalemca ntchito zimenezi aumve,chinyengo chachuluka ngati akufuna azingolembana okhaokha osati azitisokosera apa akuwona ngat asafuna ntchito pamalawi pano ndani nde sibwino kumayesana.

  6. Wat aa fuck’n’ story is……………….
    ..

    .,………………………….. ……
    ……………,..m…….m………

  7. soldiers on this pic are looking very sad what happen ? they meant to look happy ,after all they are well payed than teachers they receive they salary on time

  8. I remember in 2002 the army recruitment exercise got me in after passing presentation,dictation and medical tests at Cobe barracks in Zomba. Recruits were immediately transported to MAFCO in Salima,after a week we were introduced an introductory military ground parading. I liked it because at school history subject was my cup of cool ground water,week two there were faces that “completely failed recruitment tests” arriving at the college then it was when I personally realized that Nepotism is here to stay with its cousin Corruption bobbing up and down in Officers’ mess. There was No ways I could be a regular soldier because I didn’t have military authoritative “backing” via nepotism or corruption. My friend who I passed with had his soldier brother-in-law frequently visiting him. Recruits! “Another medical test on the way soon at Salima hospital” In my heart I named that Salima hospital test [for rib cage] a “filtration gauze” where recruits with military brothers,sisters,fathers,cousins,in-laws,sons,daughters and relatives or via “palming” had exclusive “live wire” advantage. Finally from Zomba District recruits 87 including those who failed Test at Cobe barraks. 32 from 87 were immediately weeded so it was like the 32 were temporarily holding positions for those who came afterwards. It was fucking painful.

  9. Obvious family first, or ntakhala ine i can’t employ some1 else while my brother akugudubuzika ndi ulova, n its not only ku mdf kokha akuchita izi its ol over Malawi nation, WAKWITHU

  10. Asilikali palibe chomwe amachita agalu amenewa ntchito kulanda makala amphawi kapena kukwata azimai by force. Bola apolisi ngakhale naoso ndiagalu alibe khalidwe kupempha too much…………

    1. unyatu agalu omwewo by the end of the month akulandila salary.ukhala choncho ndi umbuli wakowo unkathawila dala xcul n’gooo uliladi siunati

  11. musavutike ndi kulengeza pa media pa nkhani ya recruitment chonsecho mukudziwa kuti mumatenga ananu ndi abale anu,zausiru eti

  12. U don’t hav to tell us that. Jst tell soldiers to bring their Relatives. That’s wat happens wen it comes to the recrutment of soldiers. Do u call that recrutment or Chieftancy.

  13. Ntchito yausilikali kaya kupolisi amalemberana chibale kodi zimenezi zizatha liti? Zimatiwawa kwambiri anthu okonda chinyengo inu musamatiuze zimenezo zingolembanani basi

  14. Ngati pali recruitment ya chinyango pantchito zonse ku Malawi iyiyi ndi number one. Otengedwa amakhala ana a Silikali. Akati lero tilemba aku Chitipa siumupezapo or mmodzi. Munthu kudabwa kupeza otengedwa nkukhala aku Mchinji, Zomba. kumamva ndithu chiyawo chikulankhulidwa pa recruitment yaku Chitipa.

  15. Ngati pali recruitment ya chinyango pantchito zonse ku Malawi iyiyi ndi number one. Otengedwa amakhala ana a Silikali. Akati lero tilemba aku Chitipa siumupezapo or mmodzi. Munthu kudabwa kupeza otengedwa nkukhala aku Mchinji, Zomba. kumamva ndithu chiyawo chikulankhulidwa pa recruitment yaku Chitipa.

    1. Ayise Jukad Kantengule Ndikunena moopa Mulungu. Tinkachita kuwaona akutsika ma TATA kufikira kuma Stand ku Mzuzu Stadium ena akuvutika ndi interview. Kenako poitana maina, munthu kumayankhira ku Stand freezes ali kukamwa. Kkkkkk

  16. Yes !! We need it ndkale lija please we are stil waiting!!

  17. asilikali achepad ofunika kuwonjezela kut akateteze nyanja uko.koma chaka chino munditengeko ndinayamba lija ndikale.

  18. AMALAWI!! TATANI KODI? NDANI ANGASANGALATSIDWE NDI KUPHA KAPENA KUPHEDWA? ZOONA M’MALAWI OLIKONDA DZIKO LAKE MPAKA KUCHEMELERA LIU LA NKHONDO?? NDI BWINO NDITHU AMALAWI TITACHEMELERA KWA YEHOVA KUTI AWALETSE AMALIWONGO KUTI ZOLINGA ZAO ZILEPHELEKE!! MALIRO SAOMBELA M’MANJA KOMA UFULU-MTENDERE!!!!

  19. AMALAWI!! TATANI KODI? NDANI ANGASANGALATSIDWE NDI KUPHA KAPENA KUPHEDWA? ZOONA M’MALAWI OLIKONDA DZIKO LAKE MPAKA KUCHEMELERA LIU LA NKHONDO?? NDI BWINO NDITHU AMALAWI TITACHEMELERA KWA YEHOVA KUTI AWALETSE AMALIWONGO KUTI ZOLINGA ZAO ZILEPHELEKE!! MALIRO SAOMBELA M’MANJA KOMA UFULU-MTENDERE!!!!

    1. Tikapita kukamenya nkhondo.. Mulungu azatithandiza ngati nyanjayo ili mbali yathu. Kodi mi bible mesano opembeza amamenyaso nkhondo kodi? Chi Christu chamasiku ano ndi chamantha. Mumangobisarira mudzina lakuti Mulungu atimenyera nkhondo. Tipempheredi kuti asirikali athu ndi dziko lathuli liteteze chuma chake. Zikafika komenyanako, timenyana basi.. Mulungu atithangata.

    2. ABALE ANGA NONSE AWIRI POTI MAINA ANU NGOFANA A DENIS!! EEE! Ndizoonadi mu BIBLE nkhondo zinalembedwa komatu mutawelenga bwino-bwino muona kuti nkhondozo zinali nkuchitika pokweza dzina la YEHOVA NDI MTUNDU WOMUDZIWA YEHOVA! Potero a DENISI dzina la YEHOVA LIMATANDIDWA! Kachiwiri-mwina mwangothamanga a bale anga kuti muchite m’tsutso-pepani! wina wanena ndithu kuti alembedwe poti apita kukapululuka pa nkhani ya nyanja ndi TZ. Mukatero a DENIS chimenecho ndiye CHITUKUKO? Kachitatu- Ambuye Yesu adati masiku otsiriza mudzamva mbiri za nkhondo komanso kuukilana pachibale mpaka kuphana! okondedwa abale anga mwaima pati? INE NDI PEMPHERO LANGA MULUNGU ATICHITIRE CHIFUNDO NKHONDO TOTO!!!

    3. ABALE ANGA NONSE AWIRI POTI MAINA ANU NGOFANA A DENIS!! EEE! Ndizoonadi mu BIBLE nkhondo zinalembedwa komatu mutawelenga bwino-bwino muona kuti nkhondozo zinali nkuchitika pokweza dzina la YEHOVA NDI MTUNDU WOMUDZIWA YEHOVA! Potero a DENISI dzina la YEHOVA LIMATANDIDWA! Kachiwiri-mwina mwangothamanga a bale anga kuti muchite m’tsutso-pepani! wina wanena ndithu kuti alembedwe poti apita kukapululuka pa nkhani ya nyanja ndi TZ. Mukatero a DENIS chimenecho ndiye CHITUKUKO? Kachitatu- Ambuye Yesu adati masiku otsiriza mudzamva mbiri za nkhondo komanso kuukilana pachibale mpaka kuphana! okondedwa abale anga mwaima pati? INE NDI PEMPHERO LANGA MULUNGU ATICHITIRE CHIFUNDO NKHONDO TOTO!!!

    4. Ndiye kuti mukufuna kutsutsana ndi bible abusa? Mwati bible lidati masiku otsiriza mitundu idzaukirana. Nanga patapezeka kuti palibe mtundu womwe waukiranapo muzatinji? Alekeni malemba akwaniritsidwe. Kukafa ndikumenyera nkhondo dziko langa sindikuwona cholakwika, kusiyana ndikungokhala nkumati Mulungu andimenyera nkhondo mtundu wanga onse nkutha.. Mulungu azandifusa kuti ” inu mudapabgapo chani pamene mtundu wanu umapululuka?” Abusa, dziko lililose anthu ake amapemphera, muyesere lero, mungokhala kwanuko osakagwira ntchito, muzingopemphera kuti Mulungu akupatseni chakudya chanu chalero. Ndithudi ndikukuuzani, inu mutsutsana ndi lemba lakuti ”uzadya thukuta lako” Ambuye Mulungu, amathandiza yemwe wapemphera nkunyamuka kukagwira ntchito yomwe amapemphererayo. Kodi mukundiuza kuti Asilikali a Tanzania atayamba kumenya a Malawi omwe azungulira nyanja ya Malawi, nkumawathamangutsira kumtunda. Mungasangalale asilikali a Malawi atangokhala osapangapo kanthu? YANKHO LANU LIKHALE LOWONA.. Ndiposo Mulungu angathe kuwalanga asirikali a Malawi atapanda kuchitapo kanthu. Kapena mukufuna asirikali m’malo mokamenya nkhondo apite ku phiri kukapemphera? ”UZADYA THUKUTA LAKO” mawu amenewa osamawachepesa. Kumbukirani kuti Malawi siikuyambisa nkhondo ayi, koma ukuteteza dziko lake. SINDIKUWONAPO CHOLAKWA KUTETEZA DZIKO LAKO.. GANIZILANI ZA M’BUSA JOHN CHILEMBWE, tiziti iye samawaziwa mau akuti Mulungu Wanu Azakumenyerani Nkhondo? Iye ankadziwa bwino lomwe tanthauzo lake, ndipi Mulungu anamumenyera nkhondo pomupasa mzeru ndi mphanvu zokalowera kwa adaniwo mpaka kukwanilitsa zifuna zake.. MULUNGU AKUDALITSENI ABUSA, KOMA MUSALOLE DZIKO LANU LIWONONGEKE MOPHWEKA. MPEMPHENI MULUNGU AWADALITSE ASILIKALI ANU NDI MZERU KOMASO MPHAMVU ZOMENYERA NKHONDO KUTETEZA DZIKO NDI ANTHU AKE.. BE BLESSED.

  20. Aaah antchito yanji asilikali wo?
    .
    Ndalama zolembera a silikalizo tapititsani ku Education ana a eni wake alembedwe ntchito lika ndi kale

  21. Chinyengo chimakula ife anatisisa mutata okhoza khoza anangobwela wina amvekele ant 8 atsike iwe,iwe ,iwe tatsikani mpakana pa no ndie muziti kulibe chinyengo?

    1. iweyo tebulo ndiwe savage tandiwuza pano amene akulembedwa ntchito panopa ambiri akuchokela kuti? Agalu. Iweso kachulu wawonetselatu kuti ndiwembulithelu chidzete chigendere ukutchula chinthu choti ulinacho mayi ako ulinawo palizazelu apa koma alomwa mundisamale fwetseke.

    2. iwe Gwiremaso ukanakhala siiwe savage sukanayamba kulemba dzina langa with small letter. Kodi kwanu nkuti? Ndiwe mtundu wanji wamunthu, opanda khalidwe iwe kma unabadwa mwa munthudi iwe? Kapena mwa nyama? Muoneni akati vimaso mxieeew galu

  22. kkk ndiimeneyo ikufuna kupezeka ntchito ija waku TZ mukalakatike ngati maverteynum kumeneko muzikakhala pasogolo madoloo pambuyo kkkkk

  23. more Sojah akufunikadi…..chifukwa nde dziko lathuli limenya nkhondo pompano….

  24. Yes we need enough young active soldiers to defend our borders. We don’t know when Tanzania will slaughter us. We need enough our sons and daughters to defend us. We need enough recruitment not just 2000. We have enough money politicians are just stealing it because we don’t know how to use it

Comments are closed.