Be Forward Wanderers have completed the signing of veteran goalkeeper Vales Kamzere on a 2 year long term contract, Malawi24 understands.
The Nomads have confirmed that they have completed the signing Kamzere who has signed a two year contract that will keep him at the Nomads for the next two seasons.
The legend has come out of retirement to sign the contract after the Nomads goal minders have been struggling between the poles.
Since returning between the poles Kamzere has guided the Nomads to the Fisd challenge cup semifinals and has also helped the Nomads to move to position six on the log table in the top tier.
Ironically Kamzere debut for the Lali Luban side this season came during the Nomads four nil thumps against Karonga United in the super league.
Kamzere is one of the most celebrated goal minders in Be forward Wanderers’ history, having been a key part of the team that won the super league title in 2006 and many other trophies for the Nomads.
A Bullets mungozivuta uyu ndi mdoro amatha ife za2 zikuenda nanga inu zanu mwayamba kale kuzizimuka muziona ana mwachepa.
Mmmm wayamba kale azingonyeredwa kkkkkk yake [email protected]
Nice move chipuwa akhoza kuona msana wanjira kaye goalkeeper okanika kudula ma set-pieces ngati ameneyi sinnamuone
Koma zikubeba
Mpake malawi mulibe mpira kodi kulibe ana?
Okey, nice!!, I, m looking for motivated ladies & men that want to earn some extra money!
~NO experience needed, full training and support given
~No CV. You just must just be willing to learn
~Also have a business mindset!
~Work around your current commitments. You decided your hours
~Start earning immediately
~Even more once you move up within the company
~FREE to sign up, No kits to buy,
Interested? Leave your telephone number below or whatsApp me on +255763232431..
5 games clean sheet. Neba don’t comment zopusa apa!
magemu 5 wosachinyitsa uliboh takulandila khalawomasuka wafikakwanu kumanoma valesi
Kkkkkkkk koma inu ndi anomadi? Zoti anali komko kale ngati goalkeeper trainer simukudziwa? Ndiye apa mukuti khala omasuka wafika ku Noma kkkkkkkk.
Kkkkk
Aaaaaaaaaaa!i iweeeeeeeee as a player or what?
Washington Malata come again anyeledwenso uyu.
Washington Malaya come again anyeledwenso uyu.
Kodi neba ukumva bwanji ? ine ndikumva kukoma ndi Nyerere
amene uja akufuna adzakhale goalkeeper trainer, inanso ndinjira yosungira ma legend, neba sungazimvetse!
What for this granny?mafuta anatha kale mu tank !!
Nyerere more fireeeeee
zosangalasa kwambiri tamulandira ndimanja awiri
Musatilowelele noma ndiyathu
koma umphawi sizinthu manyazi onse kutheratu kkkk zoti anazinyela ndi bomba kuiwalira ndithu hahahaha
Walcome nyrele
Yawo ija kkkkkkk
Admin nthawi ili bwanji pano?
wakalamba adzingogulitsa diesel pa Limbe depot basi yake ija.
Sanakalambebe
That pic is not Vales Kamzere…that is Noah
Jst bcoz he didn’t conced goz wen u wer playin lake valley & zolozolo kkkkkk dikilan kaye mumumenyanso ngat Chi poor
Isiyeni NOMA neba manyazi ya 2 cup tiphula pamene aganyu mphuno biii kulira.voméléza unazisiya mu FISD manyazi kasuté CHINGAMBWE
once a soldier still a soldier. welcome back
Manyaka ini eni
This is nonsense, that is why our national team is not performing, why can’t you try new blood so that we built a good foundation for the national team?
my dear friend sometimes experience matters most. it doesn’t necessarily mean that he is the only goal keeper to be featured in all games.
Let us just wait and see
man! national team siizatheka! tiyeni tizingosewera super legue basi
INE SIWA NYELELE KOMA VALY IS A GOOD GUARDA REDE. WELCOME BACK KANZELE!!
Tanthauzo la welcome back mumalidziwa? Munthu wakhala akugwilila magame chichokeleni Chipuwa ndiye mudziti welcome back?
Amatha ameneyo ndi Dolo
Be Old Socialz Backward Wanders, Youngsters?????
Thats awelcome idea very encouraging….!
Thats awelcome idea very encouraging….!
Neba mavuto umawayamba dala kkkkk kammzere mpaka
kkkk……Sizampira izi
WELCOM BACK AVALY
Mmmm Welcm Nkhalambayi? Kkkkkk
Mukanena kt kulibe akulu mkutukwana,mukapha nkhalamba zonse adzakulangizen mndan(welcom back avale).
Kkkkkkkkkk Bola Asazapange Zijazi Anapanga Ku Lilongwe Zija
M’MAGANIZA ZOMWEZO BASI?
Yaaa! That’s History He Made In Field Of Football
KALE salelera ana nawe!
nkhalamba fc ndinu tsapanotu
Juju ameneyo tisulusa ife kuponya kamozi izifika mipira 7,kusowa oti agwire
Chaka chino tiyimbanso onyeredwa,onyeredwa mu ground..tikumbutsire pa dzana..
Zakuvutani a mogo FC Zisiyeni NYERERE ziphule ya 2 cup manyazi kagutseni makeni.
Kodi uyu siuja ananyeredwa ndi buleti pa silver stadium, kkkk Koma nkhumba izi mpaka nkhumba 41 mu super league izi ndi nkhumbadi..kk
Bola nkhumba anthu amadya and they r
in semi-Final of FSID.Kodi inu a CHINGAMBWE FC mwaledzera naye mogo.kathirireni nazale.
Mumugulire matewera or ma pampa
…kkkkkk iweyo akulembe ntchito yomamunkoza akanyeledwa mu ground…
Blessing Tembo,, chilombo choopsvya kwa” neba
Kodi paja mkuluyu adabibidwa ndi bomba landani ?kkkkkkkkk
Ndi yemweyu, koma mmene wakalambamu azivala ma pampa pa golo.
Old soldiers never die
Kodi chipuwa alikut?
Ukaipa dziwa nyimbo
Ine ndingoti ayi ndithu pagolo pa noma ndi ntchentche yomwe idzigoletsa nanga si pabooka
Ameneyo Suja Amanyeledwa Pogoloyu Mwasowa Otenga Kd
Azazinyere kawiri mu ground
kkkkkk chipongwe eti
Alibho welcome back mr
Kodi chipuwa alikut?
anathawa ndi banja lake from blantyre.after zija zinachitika ku civo after game ndi kb
Eish kunalizotani abraz inandiponya imeneyo?
Inenso ndikufuna nditaziwa komwe ali chipuwa
Komwe ali sikukudziwa paja masapota anoma anamukuntha akuti anachinyitsa zigoli zopoila pa game yomwe amamenya ndi KB pa Civo.Ndimmenemo @ Alinane Unyolo
Kkkkkkkkkkk koma …nkhalamba iyi sizatifela m,galawundi?
Nyelele My Team
Kodi chipuwa alikut?
good news
NOMA YOMWEEEEYOOOOOO
analikut ameneyo? musakhale mwangomutenga kolima mphonda
My TEAM # B4WARD
Bola Malikebu,a Valley akagulixe mu hardware ya Malikebu’umuuze admin