![Part of the game between Nyasa Big Bullets and Mighty Wanderers](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/12/IMG-20231224-WA00032-276x176.webp)
Boma lati ntchito yomanga mabwalo a Bullets ndi Wanderers iyambilaso
Boma kudzera ku ndondomeko ya za chuma cha dziko lino ya chaka cha 2024/2025 laika ndalama zoyambilaso ntchito yomanga bwalo la zamasewero a matimu a FCB Nyasa Big Bullets komanso Mighty Mukuru wanderers. Ntchitoyi inaima… ...