Inu nonse amene mukutchukitsa kuti mtsogoleri wa dziko lino akudwala ndipo akuganiza zotula pansi udindo, akuti muzimangidwa.
Anthu ena omenyela ufulu wa anthu wa chibadwidwe ndiwo apempha boma la Malawi kuti liyambe kuunika bwino nkhani zimene anthu amaika pa Facebook ngakhaleso mu ma WhatsApp.
“Anthu akuchulutsa bodza pa Facebook ndi pa WhatsApp, papezeke njira yowalangila anthu onse abodza,” anatero a Billy Banda amene m’mbuyomu anali patsogolo kumenyera ufulu wa anthu.
Iwo anagwilizana ndi a Undule Mwakasungula amene nawo anapempha kuti boma lithetse chibwana pa Facebook ndi pa WhatApp.
“Anthu akumangonena bodza basi, pakufunika malamulo okhwima oti azilanga anthu otelewa,” a Mwakasungula anatelo.
A Banda ananena kuti m’mene anthu amanenela za umoyo wa mtsogoleri wa dziko lino panthawi imene anali ku America kunali kongoyenela kuti ena alangidwepo basi.
Anthu anatchukitsa kuti a Mutharika akudwala pa nthawi imene anatchona mu dziko la America, ena anati atsogola ndithu. Pamene a Mutharika anabwela dzanja lawo lamanja liri looneka lopuwala ena anati a Mutharika angobwela ngati chiphimba mmaso ndipo usiku atengedwa kumka ku chipatala.
muzimaga wokuba mwasowa chochita
Nanga onama pa MBC?
Pepan Ninalakwisa Ngat Cinapiteko SCHOOL Polemba Kut FACEBOOK
Ended Limanga Anthu Otelew Zikom Pa FESIBOOK.
Boza ilo
pitala akudwala kumene zosachitaso kufusa or kuyitana a prophet kuti atitsimikizire kuti akudwala, iyeyo ndani pitalayo kuti asadwale za ziii
Ndinu opusa
Guys kungot chilungamo chimawawa koma likulephela kunena chilugamo
Kkkkkkkkk freedom of speech remember
Mumange kaye Ndawu ndi Azake Akunamiza kuti Simukudwala
Onama kapena Ochuu !
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kumangana pa Facebook…. umbuli upose pamenepa kkkkkkkkkkkkk……. mukamamva kupusa kapena kusowa zochita nde kumeneku…… I wish mtakhala omangidwa oyamba ine ndithu
Alomwe makomment iii kumuyikira kumbuyo galuyo yanyanyisa too much mmxxmmmm
koma boma lopepera ngati ili sindinalione ine.. Chovuta ndichakuti this government doesnt have that confidence kuti ayendese boma chomwe akungotaya nacho nthawi ndikulimbana ndi anthu instead of planning zaphindu.. Asa educated savages. With empty brains
Sorry sitidzayambiranso…… bola asadzapitenso kwa UNGA next time oloko adwalenso adxipita ku kamuzu central hospital
ine si wandale !!!.
za zii
Ayambe inu a malaw 24 pot ndinu agalu. Mmafalisa nokha osat mnthu winai . Chupiti
Osamanga matchende akewo bwa?
Eya amenewo amangidwe ndithu conz sibwino choncho.
Eya amenewo amangidwe ndithu conz sibwino choncho.
Kodi iyeyo kuti asadwale ndan,ine ndimangeni ,president akudwala ndisanilika pa Tchesamu via kakwewa
IDIOT
zankutumbo bwanji sakumanga anthu amane akuba ndalama zabomawo
Boma lichita bwino kutelo anthu amasowa chochita tsiku lina anthu azakutamani ndimabvuto ,kamba kabodza.
loading…………………
A Mabvuto,munali yani inu….kkkkkk!!!koma abale ndaseka ndithu…
chaaaa malawi wafikapo pano
kod anthu asowako chochita kumalawiko@?
Muyambe kuzimanga inu, Kodi mukamati boma mumatanthauza chani? Mesa mumanena ife timavotafe? Kkkkkkyambani kuzimanga nokha
Nyamakazi simatenda? Nanga ndichan nyamakaziyo
Fuck dat fucken boma
Ayambe kumanga amalawi 24
Umeneo nde usiluuuuuu
Ayi zoona zawonjeza ndithu
Muyambe kumanga Peter wanuyu
Kkkkkkkkkk kusowa zolankhura eti
Fuck u
U just think we r still in 1970’s zaugalu
Hehehehehe is better to arrest government official and then news reporters not us .
zachamba eti imange kaye anthu abodza onama kuti alikunsonkhanoakudwala kkkkk
Kkkkkk wakwamba kumangika uwe iwe walemba nkhani iyi, chifukwa mukutemwa kubisa vinthu Yeo
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk mayaz
Kkkkkkkk nde aziwapezela kutiko anthuwo?
Stupid……..
Kd Ndpa Facebook Pokha Muonenso Ma Media Enawo
Kkkkkkkkkkkk
pa fb munthu akamupezerakuti ? alemba mumazi
.Are you good in bed ?Do you really need a rich sexy sugar mummy or sugar daddy that can change your life completely with money and influence, so get the opportunity to meet sugar mummies from all works of life,politician,bankers,oil ladies,executives,directors,gold ladies,cash money ladies,Global Network group friends,doctors, ladies, willing to pay as much and get the best exclusive VIP arrangement anywhere in Nigeria,LAGOS,ABUJA,CALABAR,DELTA,ANAMBRA,PORTHARCOURT,,RIVERS,KOGI,KADUNA,JOS,ABIA,KANO,BAUCHI, SOKOTO,BAYELSA,ONDO,OSUN,OGUN,BENIN,IBADAN,ONDO,BENIN, call admin on 09036713792 or 08117333727 for your connection,like page before calling.
No one shall be arrested. Opposition party & NG0 s argue DPP not arrest anyone who post info on social media saying that pple hv right to access info.
Kulephela kumanga oponda dolar zinja mkuti za cashgate amanga ndani kupenga ettiii
Osamanga amene amadwala nyamakaziyo bwanji
Ndiye Amanga malawi yonse…
Ayambe kumanga okodza pa mtengo,,,odya mizimbe,nthochi dowe mkumangotaya zinyalara paliponse ,,kenaka amange ma minister 7 akuba aja …..pomaliza onama pa fb
Palibe zomangana apa kukhuta zigege kod et
One sindifslitsanso pa fb pano. Ndiyamba kufslitsa Ku tweetr ndi WhatsApp.
Ofunika ayambe inu a24
Aboma amati sakudwala koma iye wanena dzulo kuti nyamakazi yakhala ikuvuta kwambiri and zinafika povuta kwambiri aboma akuyenera kumangidwa chifukwa chotinamiza.
Crazy story.
Nde wamisala akuteloyo umbuli basi kodi mwatani amalawi?
Madela anapita iye ndani
Oyamba ndikhale ine bwa?
Ndende yake yikhale civotu.
Kkkkkkkkkkk kusowa ntchito eit .
Kkkkkkkkkkk kusowa ntchito eit .
mmalo molimbana ndiçhitukuko mulimbana ndi ànthu mupezàpo çhani dzeĺu zatha tsopaño
za usamunda iizoo
Inu malawi 24 ndi yemwe akutumaniyo pa ujeni panu shupiti muuzane. Obwera kwa ine akhale olimba chiwindi. Magetsi, njala, umbava ndi zina zotero mukulephera kuthana nazo. Koma mwaponda gear pa fb. Fuck u all. Demet, tidakali kutokota, poyamba pitala anagwa kamba ka njala pa msonkhano, pano dzanja lake lalowa ma virus. Kod ife tiziti munthuyu za umoyo zilipo? Ndalama za amalawi ovutika zinabedwa zankhani nkhani palibe mfundo yeni yeni ikuoneka. Inutu inu ohooo. Musamatenge ngat mukamakhala mu ma office mwanu aliyense ndiopusa. Kumanga muyambire atolankhani coz ndamene amafalitsa nkhani za bwampini. Ndipekenso ina.
Pitala anati ziii ku america, a malawi 24 anapeza umboni woti abwanawa anali ku holiday ya mothers day. Amakasangalala ndi amayi awo ku america. More news clink here >>>>> malawi24.com
Zoona God in control worry not
Mmaso mothinamo
Ndito tulo mwiniwake wanena yekha kuti akudwala nyamakazi ndie Musil is drank in so apa ???????
Inuso amalawi 24 mumangidwa nawo
Mmmm abengo ndi nkhani zake
kodi akulipempha Boma kuti liyambe kumanga onse amanama pa fb ndindani? Inu a Malawi 24 mwazitenga kuti tufuna nafeso tikawafuse amene amaterowo, nde pamenepa inu a Malawi 24 Lies ndi kuyambanitsa mulipati pofalitsa za bodza ndikuayanitsa a Malawi kapena ofalitsa zoona ndi zoluzanitsa mtundu wa a Malawi?????? Be a tool of Peace u Malawi 24 not of destruction pls!!!!!
Masendi masendi masendi ya boma
Tiyeni tigwiritse ntchito face book pokamba zokhuda iwe mwini. osakhala za mabodza kapena kutukwana pa FB.
Mmmm inu ok
Kusowa chochta.
Segulani ndende zambiri kuti mumange amalawi onse. Koma choti muziwe ndi choti tizavotanso 2019. Mpando umenewo timakuikanipo ndife amalawi,siwamuyyayaaaaaaaaaaaa.
Nyamakazi simatenda? ngati tikunama atimanga kangati til kale ku ndende
Aaaaa inu mesa ine ndikukhala kuno Ku Pretoria moyandikana ndi chipatala chachikulu. ndizoona wabwera kuno kodi muzabisa mpaka liti ? Aaaaa oky yambani kumanga ine bisani matendawo koma maliro nde tizamva
And i can help you the harcking
Mumangeko Magetsi Kmso Njala Zisamatimvute Then Mudzatimange,we Need To Say Truth To Shame Devil
Boma limange kaye kape ameneyo after that limangenso ndi mkaz wake komanso Bwampini
Bull shirt come and arest me
zachamba zokhazokha inunso a Malawi24 chilunga mukuchdziwa kaya mukupepelanso nd chan kaya, poyamba ndnkakudailan koma ndaona chanzeru palibe!
So the issue is to arrest pple who lies, n what about him Peter he lied to us that he’s gonna change things while we’re still getting poor and poorly and also worse? tell me!
Eeeee nkhani zovuta izi nanga tsopano zanja lija ndi chani si utendawo umeneyo
Kumangidw kkkk koma ndiy zafikapo kumalaw,muyambe mwamang kaye onse anaba ndalam zaboma aja kenaka amene azilengez zabozawa,kkk komans mutuluse kaye anthu onse omwe ali ndimilandu yocepa amphaw ali kundendeko coz ndikuth kuona kuti tonseeeeee timangidwa malo ndiamene atakhale ocepa
He’s arleady old he doesn’t fear death.He should know that he is in injury time and therefore he should ask God to forgive him his sins of geting GVT by stealing.The living God is not happy with his leadership.we want 2019 to be tomorrow so that we can take him out together with chilima.
UYU MUKUTI BILLY BANDA NDI MMODZI MWA AMALAWI OPUSAA WOMWE AMAFUNA KUWONEKERA PA ZINTHU ZA ZIIII!!! NGATI ALI WOMENYERA UFULU WA ANTHU BWANJI ZAMAGETSIZI!? sukudzgg566f
kkkkkkk koma abale nde amalawi tonsetu kundende, boma liwonjezere ndendende zina coz apapa chifukwa chakuchuluka kwa anthu mapeto ake adzidzangoti takukhululukirani kuli kusowa kokatiyika kkkkkkkk
asah zopusa eti osakamanga amene anagulisa ma tractalar bwanji mbulizophuzira inu!!!
Mangani anthu onse amanenawo.bola musa ngwilisile ndalama zamisonkho.
Asakane anafabe ameneyo wachita kuuka
Ndizowona tizikamba zowona vuto amalawi timawoneka ngati anthu owopa mulungu koma ndife achinyengo okonda boza
Nde chambacho umange akwanu
Mitu yanu idadzadza mamina ndithu kusiya aja anapha ma aludino waja ndi awo anasololawo kulimbana ndi amphawi akapuntha buye aaaa ndiye mumanga anga angati poti ndiwa zaka 4 zomwe mwana akudziwa bwino kuti bwampini akudwala kkkkkkkk koma kwathu kuno umbuli siudzatha bwanji kupachikidwa ambuye ndi khanda lomwe lidadziwa ndiye kuli bwanji mbava nhgati imeneyi sangadziwe 4 seck un emputy tin think nothing & react
Pazinthu zopusa nde kumakhwimisa malamulo milandu yeniyeni ikukukanikani
Koma abale munthu m’modzi wakuzunguzani mitu osamangodya bonya bwanji kaya wamwalila kaya sana mwalile what is ur business
Kodi ufulu uja udapita ndi Bakili eti?
Zosatheka zimenezo
koma nanga ndizaboza?
Zakumachemde zimenezo, ine ndili ku Kenya Naku Toun mubwera kuno
Kkkkkkk zaziiiiiii,,,,amene akuteroyo machende ake abwele andmange ine…..I’m here in mozambique…ndzabwera ku mw unless pitala amwalire shupitiiiiii
Billy Banda let me say fuck u
zoti akupapereka moni ndidzanja lamadzere ndidzabidza? akudwala mvomerani tsikuti ndioyamba kudwala iyeyo.ngwazi ija amkati mkango yamuyaya inadwala ndikufa ndiye inu zinsinsi zake ziti apa.
Koma onama pa Radio bwanji eg President akukumana ndi ma investors pamene alikuchipatala
kkkkkkkkk Fk pusy
Kkkkkk atipezera kut chamba nose amene akufuna kumanga abozao ndiodwara uyo pint
Dziko lopanda mtsogoleri ndi chomcho,alomwe ndi ndi ntchito zawo,amawona ngati kulamulira dziko mkophweka ngati kubela mavoti
Bwanji Osakhoza inu magesiyo olomutatenga achabambo wanu sangakwanise
Mumakamba mau oti inu olopang’ono simungakwanise bwanji azikumangani kumene athu opanda chikondi inu mulungu azikukhululukirani ife wathu ndiyemweyo basi mufune musafune. Ky akukutumani akupwetekesani
Nanga onama za bushiri???
Onse abodza Tate wawo ndi mdyerekezi chifukwa iye sadanenepo chilungamo
Eish #Malawi wanyung’unya mpaka wamiseche azimangidwa?Yambani kumanga a Malawi 24 ndi #Lazarus_Chakwera amenewa ndiye oipa oipisitsa safunira anzao zabwino.
Uzeleza pera
sanadwere kma osamanamizan apa
Mmalo moti muziti mupanga bwanji kut magesi aziyaka, mukunena izi…. demet… ngat amanama omuyankhulirawo awone mkwiyo basi… u think malawianz ndiogona eti?? Hahaha thesan njala kaye ndi kuzima kwamagetsi
APM ndi presdent wathu.
Mukulephela kumanga mbava zikudyerela thukuta la a mphawi ku DPP kooo ndiye mukamange wotiuza zochitika kwathuko? mwasowa chochita. Muyambe mwamumanga Mutharikayo posauza mtundu wa a Malawi komwe anali ndipo amataniko? kokudya misonkho ya amphawi ndiye mukubisa? kungomva kuti akakhala pa nkhate sapheka Khoswe? Ndiye mumanga angati? Boma la Malawi likufunika mzika yeniyeni ya Malawi osati Man wa ayi ndi okonda ku maiko a Zungu basi ndimangani
Ikakwana 12 mundiwuze ndimwe kaue ma ARV
Boma liyambelamanga gwenembeyo peter
Boma ili lazazana ndi agaru okha okha ngati mukufuna kumanga muyambepo ineyo chilingamo chiyenda basi
akunama samgakwanise zimenezo there iz no way can b taken anthu tatopa nanu mugosiya udindowo mwawulemu
Mukandifunsireko kuti mukwanitsa?
Amange ndende zambiritu
Zopusa izo amupeza kuti munthuyo eyaaaaa
Kkkk ndende izaza
Machende anu akumpando inu mundimange ine agwape inu iyaaa
Ndebwino amange kumenene ndipo boma mukafuna kafukufuku ndikuthandizani mundipeze,chabwinomukhale oyipa koma mubwezeletse chikhalidwe ndi Ulemu
Ndiye mulanduwo uzitchedwa kuti chiyani bwanji osamanga akulu akulu a ku escom bwanji kuchokera thawi yonseyija tinatenga ufulu odzikamulira mpaka pano simunapenzebe njira zothetsera mavuto a magetsi mmalawi muno ndiye pano mukufuna mulimbane ndi social media bwanji tinavotera multi party kuti tiziyakhula za kukhosi lero mukufuna muyambe za chipani chimodzi sithani
Oyamba ndinu amalawi24 too much bodza mukalowe basi, president wathu ali nyatwa inu kumati akudwala sibwino chomcho
Munyanya ma comment ,khani simukuyiziwa mwinaso simunayive bwino inu ma comment mpaka 500MB khani yake kunyoza tsogoleri malo 500MB kupangila chaphindu lyk kuyitanila malonda,kulengeza za uthenga wabwino Wa Mulungu,kufusila tchito,even kuchezetsa ndi tapambali,muli busy kulowelera za ndale ngati kuti amakolo anu even agogo anu
Need civic Education .Let people know what is going on with their leader whether it is bad or good through fb.
Machende anu nonse akuluakulu am’boma
Yambani ine
komanso aboma nganiyo sakuyitenga bwino chifukwa ngati anthu akunena kuti akudwala mwina sakudwala koma ngati sakudwala kungoyamika mulungu osati kumanga anthu alakwa chani?
Oyamba kumangidwa ndiye mukhalatu inuyo
Kkkkkkkkk koma zavuta et
ayambe kuzimanga okha ndimabodza awo
ayambe kuzimanga okha ndimabodza awo
Palibe dimocalanse ilipo
Mukayambe kumumanga yemwe analenga Facebook then kenako muzizatimanga ifeyo
Misala imeneyo muyambe mwa gonjetsa njala agalu inu
kwaine fb palibe bodza kukakhala udwala mzoona yekha wavomela kuti nyamakazi. nde wabodza ndani? ine nuona aneneli amtsogoleri nde abodza amabisa matenda amunthu wamkulu. nde omangidwa akhala ndani?
Kupepera
Mawa ndiwamanga a presdent popeza amanama kuti akukumana ndi anthu ena zakhuza chuma cha dziko pomwe amadwala
Ndiye mumanga dziko losetu pamenepo kkkkkkk
Kikikikikikikikikikik
tandipatsani fone number ya emwe wanena kuti adzitimangayo. akuona ngati ndine size yawo apuludzu amenewa
Kodi ndiye kuti zimakhala zochititsa manyazi kuvomeleza kuti President wathu akudwala?
Aaaaaaaaa
Mwaine ndekha kaya inu mumadziwa kumanga anthu kamangeni koma ngati pali chomwe chanve anthu ayenela kukambapo kanthu ngati inu aboma simukukamba chilungamo ifeso tidutsa momwemo komaso kodi kuopako tidziopa inu chifukwa choti mutimanga timangeni ngati inu muli achilungamo pankhani komaso ngati kuli kuopa ine sindimaopa humanbeing I only fear Almighty Allah and Allah alone none of you’s ndiye ngati kuopyeza awopyezeni omwe mukuwaona olakwawo ndipo amangeni komaso ngati inuyo simmafotokoza reality ndiye munthilidweso zingwe ndinu osokoneza ponama mulungu sakuona mbali2 ayi chiweluzo chiyende same manyaka aboma anthu opanda pabwino*******
what the fuck to government of malawi
Nyaope
Ok
Manganiso onse omwe mukungowasiya Ku ma chita externalise magesi Ku Escom…
koma muwakwanitsa anthu wonse amene akugwiritsa ntchito facebook kkk iwe ukunenazimenezi ngati akupatsa yogula bread wagwanayo pitalayo
koma muwakwanitsa anthu wonse amene akugwiritsa ntchito facebook kkk iwe ukunenazimenezi ngati akupatsa yogula bread wagwanayo pitalayo watizuza mokwana
Ndimangeni ine apulezidenti athu akudwala
koma muwakwanitsa anthu wonse amene akugwiritsa ntchito facebook kkk iwe ukunenazimenezi ngati akupatsa yogula bread wagwanayo pitalayo watizuza mokwana
ngati ife amalawi tikukamba kuti akudwala nanga azodiac mmakaniziranji kulowa kuti asakhalenawo?
Ayamba kumanga iwe amene walemba post woyamba ukhala iwe kamaboza wankulu
Kkkkk kkkkk hede wandigirigisya iwe
Schupiti!!!!!!!!! Fuck!!!!!
Oky tiyamba akunenao nthawi yoopa inatha tinachenjera
Kkkkkkk azimanga anzake mndani ?poti boma likumanamaso kwambiri!!
koma ziliko heeeeee
Amangidwe kaye president chifukwa chowanamiza anthu omwe anamuvotela, ngati ukudwala ungovomela kuti ukudwala sikuti tikuchosa pampando mwinanso anthu omwe ukuwanamizawo atha kukuthandiza mankhwala.
moti zomangana zikanalipo ndiye democracy ndichani? zopusa sinthawi ya kamuzu ino ai mulephela zopusa
mumuuze pathako pake munthalikayo mfana wa usiru akulephere kuimanga njala apa!
Kkkkk wadya chamba eti!!!?
akumandionjeza
Kod Tandithandizeni Boma Ndichani Amene Akudziwako Izi Andiuzeko
Oyamba kumangidwa nde ndinuyo,coz mwayesesa kupeka #Mabodza koma mwaona kuti sizinatheke izo munkafuna.f***ck M24
Never ! Never ! Never ! Ngati mwasowa chonena kungowutura pansi udondo chifukwa mulibe fundo zotukula dziko ( stupit officials)
Nde zausiru zimenezi akuona ngati ife ana awo eeeti mutu wake amene wayambisa zimenezi ndipo andisamale nditha kumu……….. Mbuzi
zamba
Ngat Kuli Anthu Ofunika Kumanga Ndi Onse Amene Ali Mboma Pamodz Ndi Nkhalambai Peter Achuke Eni2
Bodza likuyambitsa ndi Boma lanu lomwelo. Yambani mwakhala olungama pofotokoza zowona ku fuko laMalawi. Mukatero chilungamo chanu chidzakutsatirani.
Zazi kusowa chochita eti
Muli ndi ndende zokwanira kuti tingakakhale?
kkkkkkkkkk hahahahaha kikikikikiki odi ukoooo!!!!!!!
koma ndiye kusowa zochitatu? kuleka kumanga anthu a cash gate mulimbane ndi anthu aziii apa FB be ashamed
Za chamba musayiwale kuti kuli ufulu opanga zomwe munthu akufuna
zankutu
Midnight 6onse ngakuba!!bwerani mudzandimange agalu inu!!
U r stupid with u dead presedent, who is he? And where waz he? Many pipo sacrifice them selves, to take this malw in the hands of whites guyz, fuck u
OK?
Boma liyambe lamanga Mbuzi za 24 chifukwa ndizomwe zikufalitsa nkhani za bodza kkkkkkkkkkkkkk.
Anthu aziwopa kunena chilungamo kukuwopani inuyo? zausilu zopusa basi. tizinenabe sitisiya. iweyo amene ukuyambisawe kuti anthu azimangidwa pamnyopako.
akamange eni ake oyambisao
Mumanga amanu zakumaliseche basi
Akadzafa joyce banda malawi idzapumula chifukwa ndamene amagwirizana ndi buchiri wasatanik pofuna kuononga malawi.
Stupid leadership
Mxiiiiiiiiiiieeeeeerrrw
Dzamange Grace anandiniza kuti ali single.
kkkkkkkkk
Kkkkkkkkk
Poti boma ndi ifeyo anthu ndiye tizizimanga tokha
ayambe a malawi 24 kenako kwa ineyo zafodya basi ndiyetu mupange ma cell ambiri coz tikadzadzanako kkkk
Nonsense mangani ineyo
Boma si anthu kodi? Osayamba kumanga a cash gate bwanjiiii? Mwasowa chonena? This is not Zimbabwe kuti ukanena za Mugabe a kumanga chamba chimenecho
Osamango yankhulatu kuti zikuchokeni. Muzimanga? Ife mumati weva
Hahaha zakumachende eti
Atimanga bwanj pot ma 4n timagula ndi ndalama zathu en palibe chifukwa cholesesa kuyankhula zmenezi ndipo pomangapo muziti tatan pot nkhanio wina aliyese akuiziwa zot president wa dziko lovutika la malawi akudwala ndye poyankhula muziganiza muzizitukwanisa zithu zazi ngat mufuna kumanga anthu aboza ndye kut hall malawi ikuyenera kumangidwa mmalo mothesa umphawi mkumalimbana mza fb mwanya ndithud bozalo lipitilila
ZA ziiiiiiiiiiii ndani akuteloyo
Build them pliz
aaaaa zaziiii!!! akandipezera kut iwowo? dzina langa lapansonkho lisali limel kkkkk adzitan kumanga kwake?zachamba ife nde sitisiya kma kunena pomwe tikuyenera kunenapo iwo ngat sakumanena chilungamo kuliuza dziko amat ife titaa? alongosoke!!!
Zaziiiiiiiii mwasowa chochita mumdzikomo? Ntchito zogwila zakusowani? Anthu amanamizilidwa aja kuti amwalila ndindani anadandaula kapena kumangidwa? Ngati mwasowa chochita dzikalimani
Ayambe kumanga pitalayo ndi nduna zakezo wononga ndalama za boma,
kkkkjkkkk chilungamo nchipongwe ndithu
Kkkkkkkkkkkkk pano guru rakwiya tikangokumana ndimutharika apandidwa umuziretu iwe zachambazo anthu wakana
Zaulamuliro wa asamunda basi,mwasowa ntchito chani,mukusiya mbava zomwe zacashgate,ndalama yomwe mukanagulira magenerater amagetsi amakono,malawi nkutukuka,ndiye kulimbana nzazii inutu inu mutilankhulitsa pobowoka!!!!!!!
Moti ayamike Mulungu APM wachira akuyambaso nkhondo yapakamwa. Amaona ngati sazadwala? Iyo ndioning’i chenjera pemphera
Kkkkkkk bomalo liziwapezera anthuwa kut
Onse abomawo mitumbo yao
Kuli Zigulu Zamaufulu Zimenezo Nimbiri Yamake Dzana Zomaopsezana Patsani Timaudindo Timene Anyamata Muone Kukoma Kwake Dzikoli
Liyambire kumanga #banet meke pa Malawi cashgate update group
Anthuwa ndi zitsiru ,,fuck them
Kkkkkkkkk Nde Mudzamanga Dziko Lonsetu,
Kkkkkk Koma guys ..mmmm tazandmangen ine pano ndkadye zaulele pa prison kkk zachamba iz wadwala wadwala bas szobisaso apa kut munaona plzdnt akupeleka Mon nd reft hand mmmmmmm
Tell them all they are stupid,,stupid n stupid
simu kwanitsa muma nga anthu angati?koma zoti present aku dwala simana vomelezebe
Kkkkkkkkkkkkk sindiwerenga nayo amanga agogo ake ameneyo umuziretu sitisiya taaaa
Ayambila pa inu kumangako kenako enafe.
Its a welcome development may be these pple can have a lesson zanyanya heavy
Palibe Akunapo apa.wavomela kale yenkha kuti mkono wake wayamba kuvunda.
Ayambe ndi petulo ndi maministers ake onsee ndenkhokwe zamaboza ka
Zausilu ifeyo nde mutimangadi ngati mukufuna chotsani facebook kumalawi kuno
Amaufulu alipo oyamba kunamizilidwa kuti wamwalila pano padziko lapansi si peter yekhayo tiyenazo bola chipepeso musungeso bcs mabungwe adzakhala mbali ya olangidwayo
Kkkkkk mwapangaso lamulo latsopano koma zirikunyasaland zindizo.
Mwapenga ndi boma lanulo
Amange kaye president waononga ndalama zaboma lathu kulibe achina mutharika kumalawi R.I.P Kamuzu Banda
Za zii Malawi 24
Ine nde ndizinamadi osati sewelo tione ngati andandimange ,zitsiku zopanda mzeru m’malo mwakuti azimanga omwe anaba ndalama za cash get ndiyeno muti manga ife chifukwa chani? Eeeeeeee!!!! Ndizoonadi ineso ndinamva kuti wamwalira ndiye bwelani pompano muzandimange agalu inu, ngati ndanama
Ndie maganizo opusa amene iwe Billy Billy Banda
Ayambe kaye amanga ana a bwapini a malawi voice ine azandimange ndilikuno nkhata bay bwapini akudwala asiyire chilima bcz iye zanja lafa kuyakhulaso sakuyakhula zamukanika pitala
Maganizo odzikonda don’t scared us on our own soil
No guyz, nkhani ya boza iyi .dzitsilu zaku mw24 zomwe zimangopeka tinkhani tawoto , kut tizida m’boma . Agalu inu a mw24 ,
Zikhala bwino coz akuonjeza maka pomunamizira munthu kuti wamwalira koma alimoyo pa nde mmmm zaonjeza
anyani inu ,a Malawi24 ,mwayamba kuzemba ?? mesa ndinu nomwe mumatiuza zonsezo?? 1agalu, 2 afiti .Manyaz bwanji mukamakamba zaboza zanuzo??
mapaz amakolo anu nose wadwala wadwala bas watokhala iyeyo ambuye chan or atafa
Oti samakweza dzanja lamanja tsono bodza lili pati? Abodza ndinu a boma mumanama kuti Mutharika akunjoya thanzi pamene munthu akudwala inu khalidwe lanu ndilotani? Muyambe kumanga amene amati he is enjoying robust healthy chifukwa a Manama.
Bomalo ndilauchitsilu ndipo ndikuchalenja kuti ine sangandimange.ndipo mwauze amene ayambisa kulipemphwa bomayo pachakuti pakepo sindikumuopa sukamnyoko yakeyo
zoona zake ndizomwe zanenedwa kale sitingalole zimenezo ngat liriboza pangani lanu mutinamizile.e
R.I.P PETER…..REMAIN IN POWER PETER KKKKKKKKKK
Kkkk ndiwerenganso atimangano liti?
kunamatu ndi mtima wamunthu bola usamanene zabodza za munthu wina , chifukwa mwini akadzafuna kunena chilungamo zidzakhala ngati kukuchititsani manyazi. zonamizirana kudwala ndikumufunira munthu moyo wautali. heeee ife tinanenedwa kalekale kuti tili ndi aids koma lero tilibwino, tikadwala kupita ku chipatala, amangopeza negative. tsoka kwa onena kuti tili ndi aids.
Kkkkkkkk mwina mumasitha amuna ngati Chitenje
hehehe munthu wa Mulungu abale, kungoti ndili ndi mwana, bambo ake anamwalira, ndiye mumadziwa munthu akamwalira amati wamwalira ndi aids, nkhani imeneyo nditaimva anthu amangokanirana kumangoti anayambitsa nkhani ndi wakuti, winanso akuti ndiwakuti, mafunso akamabwera timangoti tiyeni mukapeze zoona. mwa modzi yemwe nkhaniyo inamupeza ndi modzi amene ndinamuonetsa ma result. ndimafunitsitsa nditatenga pomwe analemba ma result koma amakaniza kuchipatala, South Africa ukadwala ndikupita kuchipatala yimasiya ma file, timangopita kunyumba ndi mankhwala basi,koma ndinafunitsitsa kuti nditenge ndidzaonetse onse amene amanena, poti ena mwa iwo ndinapanga mark.
Miseche Yakwan Nd Pa Fb Pomwe Kma Kwanko Sory
Zopusa Zimenezo Mumanga Anthu Angati?Kuli Ufulu
Kkkkk dzuwa salozelana aliyese amaliona ekha
Iya
Hahahaha
Ayamba ndi iwowo kumangidwa amanama kuti president sakudwala, lero wanena yekha kuti amadwala:-P囧
Malawi 24. pelekani umboni wankhaniyi wanena zimenez ndan? nduna yake iti? muzipeleka nkhan zogwira mtima.. mwakula
fb idzakalako mpaka muyaya iwowo angomanga maprison oti adzawasungile antuwo. mgaiwaso uzapezeke wambili woti tizadye
Galu uyu
It dosnt make sense, ngat boma komanso pita angamauze guru chilungamo then pipo wont lie
Muli ndi nthawi
Muyamba kuwamanga. Liti athuwo? Ndinenele chile bozalo. Kuti mukamayamba kumanga. Ndikhale nditasiya
Inu ndy kaaa
Walipemphayo ndani popeza limanamakwambili ndi Bomalo osapemhpa kuti nawonso azimangidwa bwanji? simunanamizidwe nsapato inu amapemphayo ndi mbalame
Pulezitemti Or Tamwalila Ch
Ok nde omanga mzakeyo muuzeni ndizamulondera ana ake akazi onse
A mange kaye a cashgate
Amalawi Tamavomerezani kuti President yu satha ku lamula. Iyaa inu hamuona
Kkkkkkkk koma asovenge
Xoona zake umfiti too much amalawi
muyambe kumanga ine ndikupasani address yanga …. kasungu TDCC P B x yasenya airport .mwandipeza .President pitala anamwalila kale guys . koma mundibwelele bwino plz .musandibwelele ku mazele
Gwepe iwe,…, nyeni iwe,…, pisi iwe,…
Gwepe iwe,…
Gwepe iwe,…
Do think that we are in one party system. We can’t go back but go fore
The word says, aliyense wabodza ndi mwana wa mdyerekezi coz satan is a father of lies kotero akanena bodza iye amaona ngati wanena chilungamo popeza mwaiye molibe chilungamo. Nde onse amakonda kufalitsa nkhani za bodza pa fb bambo wao ndi satana
Kkkk athu akufa ndi njala inu mukulimbana ndi zazi basi
Boma lipemphedwa liti? Tamaphunzirani kuyankhula chiyankhulo chathu chabwinochi inu. Lipemphedwa? Ndie osadikira lipemphedwe then uzichita report bwino bwanji?
PaChitsiru Pako Iwe Wava
Zofunika kumalalata yemwe sadziwa za mankhwala kuli jackson othandixa mwa ma hrs akubisabe zimveke
Iweyo aboma kabudula mwako choyamba chachiwiri amene wabweretsa nkhani kapena amene adayambisa adzingokanda paipi yakeyo
Section # chan imeneyo yomanga wabofzayo??
U r all fools with boma lanulo
kkkkkkkkkk ndiye oyamba kumangidwa akhala iyeyo kenako Admin omaliza ndizakhala ineyo Chokani.
Boma losowa zochita
Sizimene mukutokota apa ayi zakuchigayo kwadzadza tonse tidzafa monga mwanthawi yake.Koma tiyeni tichepese boza basi
Sizopusa zomwe timanena zimenezo
Boma linapenga misala ndi pitala
Aaaaaaaaaaa palibeee zimenezozooo
Kkkk yambani purezideti, kenaka onse amuboma , andale chifukwa sakwaniritsa malonjezano kenaka muzalowe mmafoni mu fb. Kkkkk pamutu panu mwapanga nzeru pamenepo eti.
Kodi azindikira liti kuti anthu akunama pa fb, adatani kulankhula muja adali ku American? Ngati ndi zotero nanu a Malawi 24 mumangidwa chifukwa mumaika zanu pa fb.
hihhhhhi! kumangidwa? kusowazochita eti? tikuwuzeni zoti muzichita 1>njala m malawi 2 > mankhwala mzipatla 3 >Pelekani fert mwamusanga
,,,,,,,,,the Government
ayambe ine pano kkkkkkk uziwa uziwa akufabe
sidzomangana zo ayi nkhani ndiyoti. ndichifukwa chani magetsi akudzima tsiku nditsiku
KKKKKKKK chilungam kuwawa abwere adzamange ine awone kanyama kakudowa tmatamba ife
fodya eti
Kkkkkkkkkkk koma abare kodi nkhuni ina paribe
Nanga dzanja linafalo sikudwala kumeneku? bwanji mukusewela ndi mulungu.mulungu akuwonen mukuyambisa kubisa matendanu.sadwala ndan mesa ose anafawo anayamba ndi matenda.
Za Ziii
ukuzembera a nbb takuwona kkkkkk chifukwa amanama kwambiri,kkkkkk
Zimene akunenazo ndizosaveka ai,ndipo cndikukhulupilira kt angazikwanitse,dziko la Malawi asalitenge ngat Zimbabwe kt anthu azilephera kuyankhura zakukhosi kwawo,bomalo likamatero ndiye kt likuwatumira tumira anthu kt asasiye kunena za President mapeto ake anthu sangasiye kukamba nkhan imeneyo
Ok kutanthauza kt anaba mabillion aja zinatha basi osawamanga kma afuna amange anthu osalakwa amene akungozichezera pa fb yawo kodi nanga matsiku onsewa ku US ko amataniko awawuze anthu?
zomangana zinatha ndi kamuzu .Tisazuzike ndi kadegree ka Peter komwe anakarenga ku america ifenso tilinayo koma sitidzikundikila .Analanda boma ndi Bakili ndi Chihana awa anabwera ataona zothaitha Anali kuti ?Zopuaa eti mukagwere uko .
Mangani ine ngati sakudwala opusa inu
Just open Ur TV u 24 idiot and see..
abomawo akuganiza kuti anthu nkhanizi amazipeza kuti . freedom of experesion ili kuti . atiuze kaye asanatimange
Ana anjoka inu kungo kula mutu koma maso awili okha tamakambilanani zanzelu prz atsogoleli mutapanga chonchi wina ata tenga part ya magetsi wina ndikutenga part ya madzi kuti zisama vute wina ndiku tenga part ya aziphuzitsi kuti azilipilidwa mosavuta kapena kwabela ndalama zawo ayi ndibwezi ana aku phuzila wina ndiku tenga part ya school fees kuti isamakwele mwapa n.gong.o wina ndiku tenga part ya mavuto omwe ali nmamidzi wina ndiku tenga part ya zaulimi mukhoza kupindula osati zopusa mukukambilana zo mamanga anthu aku malawi osamakamanga anthu akwanu ku zimbabwe bwanji zausilu eti nthawi zino ndinthawi yoma uza anthu kuti prz prz ntundu wanga malawi mvula yayandikile tiyeni tizipita kumunda kuti mvula yoyambilila yo tizave zoti chimanga chatuluka koma nkhani ndikuva apa za ma buzi zokha zokha yen.yo ndi chitsulo kodi ine ndi dwale nzanga ndikudziwa zoti ndiku dwala ndingaka musumile chifukwa choti aku mauza anthu ena zoti ndadwala ine ku mwalila anthu akhoza kudanda ula end anthu amafusa kuti wamwa lila chifukwa chani nanga bwanji simunati uze zoti munthuyu amadwala matenda sama chititsa manyazi mwauze a bro anuwo kuti kuno siku zimbabwe siti mabisa matenda atsogoleli achifolenawa prz kumawa uza musana wapatse mwayiwo kuti pepani inu ndalendo kuno timadana ndizopusa ngati nkhani mukubudula apazi zandinyasa nkhani zama buzi zi bwanji ndikakhale kundende ine chifukwa chama tenda awina hahahahaha kunali aphwanu ankadzi tcha chitsulo cha njani koma ifa ilibe kuti uyu ndi shakazulu nde ali ndi anyamata owayang.anila koma nyumba yomwe amagona munali ma camela koma pano or muta kayang.ana muma memory card anuwo simu ngaka iwone imfa nde dolo padziko lose ndemuka mati muziti manga kwa merica ko mu nchipatala ana kugonekani inumo muna libemo odwalaso ngati inu baba muthalika from zimbabwe
Aaaaa akuluakulu mukuiwala kt nd democratic gvm? Ngat mukufuna zimenezo sinthan dziko libwerere ku 1 party system. Bwanj osamanga akuba osewa ndalama zipezeke
My dear Kondwani, u re right that we re democratic, mind u democracy goes together with responsibility, tisamaswenso ufulu wa anzathu.
Kuteroku akhala ndi ntchito yomanga ndendetu mmalo mokomza magetsi. #MudakanaKamuzumululinji?
zandale tatopa nazo. kwezani maminimum wage. zinthu zadula kwambiri. magesi asamatima.
eeee,nde timangidwa ambiri
Kkkkk koma yea
Bamalo nde loyambulila kumangidwa too much maboza…
Bwerani muzamange ine kuno ngati mungati opusa inu . Boma lakulephelani ndiye mwasoba chochita . Chifukwa chache timakuthani Ku Malawi Chifukwa chaumphawi . inuso ma pulezideti muzimangidwa Chifukwa mumanama kwambiri nthawi yakampeni malonjezo anu sitiyiwala ife agalu inu
Moti muzigayila anthu chimanga njala yavutayi,muziamanganso asaaa shame on u galu
a ndiye ndende zizaza ndi anthu osalakwa
Mulungu a k anakhala kuti ndiwapolosi,anakayamba inu kukumangani
Chabwino ndaona pakhota mchira nyani achinyamatawa akukunyozani coz akusowa chochita muyambe mwachotsa nkhalambazo kubomako then muike achinyamatawa, nkhalambazo zikagone basi sadzakunyozanixo kkkkkk
aaaaaaaaaa mutsaopyseze athu ngati ma phone akutenga awulele ku boma fakosheee ngati akunama bwanji iyo bingu akugwiritsa ntchito mkono umodzi kwa anthu wabwela ndi ebola ameneyo
Zake izo amene uja aziona jadgement yamupeza. Mulengi wakwiya naye,tsono asatiopsyeze palibeso angamangidwe olo atabweretsa ma contaner 10000 aunyolo, fotsek m’mene zikubedwera ndalamamu kumati amange munthu ot akungogwiritsa ntchito ma units a K50 za usiluu…NDAKWIYA NANU.
so funny….
Mwina nkachoka pano nkameteko ndenvu zachulukitsa,hohohoho 14: 30 ndiyonthawi pano pa malawi 24 news
kodi press conference yayamba?
Enafe tiri ndi ma account awiri pa FB, inayo tinaikapo dxina komanso Galu wa #ALEXIS-SANCHES pa profile,, nde ngati tinganyoxe Mtsogoleri kudxera pa account imeneyi,, mukundiuxa kuti mudxapita ku England kukamanga Galu ameneyu?
Ndiinunso malawi24
Amanga anthu angti ndipo akasungidwa kuti?mwina state house
Ayambe inuyo bwaa a mw24,
Akulephera kumanga omwe adaba ndalama za boma ngakhale akuwaziwa ndie amanga bwanji muthu oti sakumuziwa…akuwona ngati aliyense amaika zowona zokhuza iye mwini…
Kumanga anthu sikuthetsa mphekesela zabodza ai, koma president apange misonkhano ndipo anthu amuone okha, aleka zokambazo.
kkkkkkl
Kukhala pa malawi pano ndi ku ndende kale zikusiyana pati
Kuseka mwa njala hohohohoho, koma inu.koma inuyo asaaa mpaka kumangana?ndie anthu ose muwatha?
Tiyamba kumanga bomalo ponamiza anthu kut prezdent sakudwala
this is bulshit till,out of older how come thet are not anouncing on gvt radios its already 2mp now huh?
Eish my malawi
Hahahahaha zautsiritu mumangapo m’pweyaapatu
FB linayambisa ndi boma la Malawi ? Pa FB anthu amalemba zomwe akufuna ngati zamunyasa achoke pa FB azipanga zina
Inuso muli mgulu
Get well soon mr President
fundoless post
Osakamanga a Escom akungothimitsa magetsiwa bwanji usikuxo andiotchera computer yanga yomwe adandipatsa azungu, azungu atandiphwanyira mphika wanga umene adandipatsa agogo anga atandidyera mbatata yanga yootcha adandipatsa a Phungwako? Zausiru
kodi azichita kusaka ngati nkhwali kkkkkkkkkkkkkkkkkkk akunama amenewo / koma zoti salibwino/ ndi za bodza???
onama pa fb azmangidwa, how about them who are always lying to citizens, tipange chathu nafe chilango? ok then wa ndale aliyese yemwe sazkwanisa malonjenzo ake will be executed… Sounds good right?
Ndikakhala Ndi Ndalama Bwezi Nditakupatsan
Kkk yamban ine
A Malawi 24 ndinu anthu opusa kwambili ķodi mumusowa źolembà eti mumatega anthu ģati zitsilu ndinu nomwe kunkati muthaliķa wamwalila , aķuďwala mukukambaso ziña agalu inu a malàwi 24 musova
Atola nkhani ali pa Malawi pano ndi boma onse nzelu zungofanana, amene akufalisa mabodza pakati pa inu ndi amumphepete mwa APM? Inu ndinu mbuzi
following
Kumangana chifukwa choti wayamba kupezako bwino ? Inu ndi nkhono et. Ok koma mawa musadzati sokosele.
Boma liyambe kuzimanga lokha, then litimange ifeno. Iyeyo asadwale ndi chisulo kapena ndi ndani? Muuzane kuti kunali munthu amaitanidwa kuti wamuyaya, kodi akadalipobe? Mulungu akamufuna leo kapena nkucha amutengatu or popanda kudwala zopusa bas, kagwireni zigandanga mudzimage.
Yo such a brainless idiot.. First the msg here says spreading nkhani zabodza about the president or any other issue that risks national security will be punishable by law..and man you need to go back to school..yes kamuzu was called life president..but not immortal president you idiot..there is a difference..life president means someone who will legally stay in power till his death..not that he can’t die…you got that you dumb ass??next time think first before commenting
Fortune, Musatiopseze Ayi.Zomwe Zimakambidwazo Ngati Ndizabodza Muyambe Makoza Ndende Zambiri Chifukwa Mumanga Dziko Lonse.
Uyo wachambayo kodi angatiopye ife? Nae uyo farune akungokhala ngati sanamve chomwe chikunenedwa nanchidwe.
Fortune usandinyase ma Thousands of pipo suffering just becoz of one Person Mr IBu,,ameneyu si Munthu ngati sasintha aziona za Brother wake,,,,,,Mlungu sangakondwere anthu azivutika ambiri Chifukwa cha one Man,,,,,,
Fortune D Boy Simmons akukhala ngati amakhala zimbabwe kapena kuti ndi khungu saona. Mwina walozedwa ndi anzakewa. Mwina ndiodwala mutu.
An argument with idiots…waste of time…what do u know
Yourself idiost, stupid you do know what are you talking about Fortune D Boy Simmons
kkkkkkkkkkk no comment
#Fortune*wanena Zowona Musamutsutse,inuyo Mwangozolowera Moyo Waufiti.
But you cant control gossips and in this case you cant catch anyone here …fact remains he’s our leader elected by people and evryone shud respect hm.
Eee Nde Nd Ambilit Nyasa Times Zodiak Plus Malaw 24 Eee Amanga Ambili Kkk…Kwanthu Kumalaw Simungakumvetse
heeee kkkjjjk
Choyamba ndipereke moni kamayi anga kudedza uko!!!! Mayi tchito munagwira pondilera bwino mulungu akpasen moyo wautari,ndimakunyadiran Mayi……..mwana wanu ine pano…miss u mom
Mwati nchani? I read the post 4rm Malawi 24 this morning that the president is sick. They heard rumours. First arrest Malawi 24 then the rest will follow.
Dats de point braza ayambe amanga a Malawi 24 cos ndi amenexo akumanama heavy
Aaaaaa zabho ine sangandigwire poti ndili kubt komkuno ku ndilande sangandipeze anamwaliradi kma azuka mwachisomo ok
Tiyambe kuwamanga mr ndawu poti nawo ananama kuti pitala sakudwara pomwe pitala. Tingoyang’anira padiso
Asakamanga akuba bwanji nde akamange munthu chifukwa choti wanena kuti Peter akudwala,chamba eti
a malawi 24 zitsilu inu mesa ife timava inu shit
Tiyambe kuwamanga mr ndawu poti nawo ananama kuti pitala sakudwara pomwe pitala. Tingoyang’anira padiso
Nde ngati amene wanama alidziko lina mupanga bwa????
kkkkkk @ http://www.#mamangidwe.com
Stupid. Osamaopsyezana
ayamba kumanga amalawi 24 poti nawoso nkhani zawo ndi zabodza
Kikik dont talk about left handed. Have u forgot he was in America all cars are left handed u drive on yo right lane and keep left. Kwaaah
Akuyambe kaye iweyo admin coz ndi iwe amene umatiziwisa zonse,Chachiwili uliuze bomalo kti bisani matenda maliro tizamva.Matenda sichinthu chomabisa coz wina aliyese amadwala.Ndikatelo ndamaliza
Bwanji osalipempha bomalo kuti limange anthu omwe asakaza chuma chathu (public funds)? Mwasowa choti mutchuke nacho. This is cheap point scoring…
Iwe kupepha boma ndiwe ndani tikuziwe boss
kkkkkk eeee muzimangadi mwina maboza athe athu anatailila fb sinyozera muthu koma yokambilana za chitukuko tsopano iwe mbuli kwako kulalata
Hahahahahahaha
Ayambila inuyo poti Ife mabodzawo tikunvera kuchokera kwa inu
kkkkkkk zomwe ndikuseka zoti kodi amalawi24 ali pachani..mesa iwoso ali pa fb bwanji akazipeleke awamange….zipangizo zamakono ziti zili padziko lathu zoti munthu angamupeze komwe ali….nanuso olengeza mumangolengeza zamutu mwanu.ngati msogoleliyo amaona ngati sazadwala pamoyo wake onse aziwe kuti anabadwa kwakadzi wauchimo ndipo matenda azimusata monga mumene tonse tikupezekela ndimatenda….kaya ndi ifa naye ikumudikila monga mene tonse tizafele.asaope ifa koma aziopa kupanga tchimo lomwe limabwelesa ifa yoti osakhalaso ndimwayi okhululukidwa ndi Mulungu,monga kunama,kusowa chilungamo zonsezo zoopsa.
eya ena ali pa fb ,mesa amanenera pa fb. athawa chifukwa chamanyazi
Ngati a president amasoweka panado zipatala za mziko lawo nanji zipangsizo ……
#chiyesa ooo ndimanyazi agwiladi nane kuona chocho.#Lucky J zoonadi panado weniweni kusowekela muzipatala nde angapange scan pa satilite munthu??
Kkkkkkk
Malawians u r far behnd wth technology dats y u r sayng so.arrest ur mediaz first
Malawians u r far behnd wth technology dats y u r sayng so.arrest ur mediaz first
Kod abale ndingatani kut ndisamaone mkhani za malawi 24?????eeee coz zandikwana hlp plz
Kkkkk kushosha amalawi akuyankhani2
Childish mind” kodi pakati pa inu ndife wabodza ndani? & muzitimanga bwanji popeza izi ndizapa air? ok ndayambapo ine president Peter Muthalika akudwala ndipo dzanja lake lamanja silikugwira ntchito linafa ndione ngati mungandimange
Liyambe kumanga ambuyewo fotsek !!!!!!!!!!
Kumalimbana ndi nkhani za pa fb si kupepera kumeko. koma sakudwala?
Zaziii
Basi nkhaniyake imeneyo nankha aja ananama kuti Mulungu anakwiya nkuuza Ngelo kuti angoyimbilatu Lipenga lomaliza ameneja nawo akuyenela kumamangidwa
amangeni makape amenewa ndikanakondanso kuti mukawagwila muzingopha bas zisilu zimeneeeezi muzisowese zopanda khalidwe
Ndikugwirizana Ndi Malawi.24.Com Popeleka Ulemu Ku Boma Pamene Zitsiru Zonse Zolemba Zonama Pa FB Zizimangidwa…Zimangidwe Ndithu!
Nde muyambe mwamanga plezdntyo cz ndamene amatinamiza kt ali ku msokhano k USA chonsecho akumva nyunyunyu ku hospa.kenako omwe amamuyanganira onse cifukwa amatiuza ife amalawi zonama.
Ingovomelezani kuti a president athu sakupeza bwino,ndipo nkofunika kuti tiwapemphelere osati zimene mukulembazi..
Akwizingeni basi.
Some of these things are easier said than done, it may be a good idea to regulate social media but prosecuting those suspected to have violated the law may be a mountainous task. I wish the govt could try to implement that, but authorities shd also be ready to be dragged to court for providing false information, its strange that official lies are just too many these days. The bottom line is that the govt triggers some speculations from the public sorely bcoz the former seem to be allergic to the truth,. Why shd pipo be hunting for information when there is an entire ministry responsible for that? The ans is just simple, untruthfulness!
No wnder mulungu akulanga malawi mkusiya akuba ndala za boma mukamange wa facebook, nanga bwanji samapereka kono wamanja bwa popeleka moni kuwanthu it means alibe ulem iyeyo powapatsa moni wa kumadzere sinchoncho ?
azayambile ine kuno mbuzi zachabechabe iwowo ankatibisira zakudwala kwake ankati anthufe tiziganiza chani malamulo opusa
Face book ili ngati kuonera movie, 98% zimakhala zaboza munthu ozindikira amaziwa, mbuzi yosazindira ndi imene ikuyambisa zopusazo, nanga akanama munthu oti ali kunja, umbuzi basi
Kkkkk alibe zochita eti?
Zoona
Nanga onama pa misonkhano Ya ndale komanso pa wailesi Za boma?
Ok ayambe ine “NAZI NKHANI MWA CHIDULE”
President Peter Mutharika akudwala mwa kaya kaya moti pano akumapereka moni ndi dzanja lake la manzere,Izi zikuchitika chifukwa Chakudwala komaso posachedwapa akhala akupereka udindo wa u President kwa wachiwiri wake a SAULOSI CHIRIMA….
Kkkkkkkkk muli bho man
kkkkkkkkkkkkkkkk akudwala tiziwopa kulakhula ngati akufuna kuti ndikhale chete andibwezere votiyanga..
Hahahahaha Umaitha,,
Kkkkk umakwana
Hahahaha muli bho man
ndipo pano wamwalila dzulo kkkkk
Kkkkkkkkkkkkkk nde amanga malawi yosetu kkkkk
Kkkjk
mmmm akuti akuyendela ma juction aphavu kwambili oposa maARV amapangisa muthu ukali phavu zikangotha amangogwa thi kuti azuke pamenepo eeeee ma drip a mazi 4
Ati akufuna ayambe boxing kkkkkkkkkkkkkkk
Akumenyan2 Paja Akufuna Chilemba Amuphuzitse Kumenya
Lol
moti president akudwala ndizabodza ? osamatipusitsa ife ndi ozindikila f.b ili bo inatiziwitwa kuti president akudwala mwa kayakaya
Kkkkkkkkkkkkkkkkk mwati chani?
mnaiwala 5mins to 2 pano
Tiyamba inuo poti zomwe mukunenazi mzaboza;
Musatinyase Agalu inu
tsano ozimanga individual or nomanyuzipepa omwe? nde muyambile kunjata o malawi punch,Malawi 24,Nyasa times, face of malawi ,zodiac online,maravi post kenako ifeyo mtinjate tonse poti phone mdatigulira ndinu
Musatinyase Agalu inu
Inuxo mukutumidwa ndi zopusa zomwe eti nanga apa twitter, watsap angovomereza mabodza akuyamba ndi iwowo
Amayankhulira alikuti messa akuti sangayankhule kaya kuwanthu , kkkkkkkkkkk . Wayamba kuyankhula namwali?
Pepani ine sindinenapo kanthu pa nkhani imeneyi
Iwowo Anene Kut Azimanga Onse Onena Chilungamo Nanga Palinso Zobisa Apa Ndi Mwana Yemwe Kufunsa Kod Mon Ayamba Kupelekela Ku Manzere? Mwinanso Adangotibweletsela Chiloboat Chofanana Ndi Mr Ibu! Coz Chimaenda Mwachangu Komanso Chosayankhula
kkkkkk bwino man
Palibe Man Chilungamo Chiende Ngat Madz Akut Anali Nyamakaz Siwaulula Nanga Ndife Mveran Speech Yake
wachira eti?
zachamba zimenezo nde xakudwala
no comment..
ndiye atsamunda ayambiraso kulamulir2
ndani anayambapo wagwirisa ntchito mkono wa left popereka moni even you unapangapo …………!???&/$%
nde liyambire inetu kumangako
Mmmh
atimange sinanga tikunama km ngati kudwalako tikunama sakuyakhula bwaji
Mangani ineyo ndikhale oyamba kumangidwa,koma musanandigwile muzandilole kuzagwila dzanja la apresident la kumanja tizawone ngati sazakuwa pa gulu.
zazi!!! yambilani ine ,nanga amachoka osasazika ngat ulendo osalowa fisi kkkk.
amange kaye nkono wopanda ntchitowo kuti uzigwira ntchito
Mpake Akudwaladi
Mukuyambitsa Ndinu A Media Tsopano Ife Titani Poti Tikuma Comment Zomwe Mukutiuza Pa Post ,if So Ayambe Kumanga Inuyo , Koma Dziwani Kuti Matenda Amabisika Koma Maliro Muzatiuza !
asaaa,zambiri zolembedwa pa fb ndi zabodza,ayamba kumanga poti ananena za president??…..iwo pomwe sankanenapo kanthu amaona ngat tziganiza zichani ifeyo??…..to be continued
q
Hand over bas tione zina
Ndizosatheka nkomwe zimenezo.
okie
okie
kkkkkkk koma anyani apeter(mapuya) akusowqa zochita bwanj
ngati lero mwadzuka bwino ingoyamikani #chauta ndipo musathe mawu poti simudziwa kuti mawa libalanji
Greating pipo using left hand its a lie too
kkkk komaso ndi mwano umenewo kkk
Kusowa zochita eti.
Zausilu…
Chamba Chamba Chambaaa! Nanga Moni Wakuleft Mchaniii?