Amid political squabbles in opposition Malawi Congress Party (MCP), President Peter Mutharika has called for peace in the party arguing that the country stands on pillars of democracy.
The call comes at a time when there has been internal squabbles in the party that have witnessed some members losing property while others being threatened.
Speaking during a dinner and dance for Democratic Progressive Party (DPP) in Mzuzu on Friday, Mutharika urged MCP to resolve all the differences with peace.
“We are democratic and Malawi can only develop with the participation of every citizen in our democracy. No citizen must be intimidated, threatened with death or their property set on fire for expressing their political views.
“As John Lynch reminds us, we will not agree on every issue, but let us respect those differences and respect one other, let us recognize that we do not serve an ideology or political party, we serve the people,” said Mutharika.
Among the reasons for the infighting is MCP members’ displeasure over the leadership of Lazarus Chakwera.
Some members who claim to be fed up with Chakwera’s leadership have been asking him to resign and seek fresh mandate at a convention.
But the party accuses the disgruntled of working for the ruling DPP.
Mlendo abwera bwanji pakhomo ngati eni khomo mungokangana.
Njoka muudzu
Akukwerezera moto ndi iwowa kkkkkkkkkkk koma NDALE ,its dirty indeed
Nzelu ngat zamunthu wamayi [Nangondo] kungot adakhuta mbewa ndi zitete remember alhomwe sasankha or fieces amadya
Chakwera is a dictator
Jumbe lost to chakwera and is thr one trying to distabilise mcp he has external support from opponents of th mcp
. Who fear the party
Wapereka ma bread nde uziti peace sichipani chakoso
Old man again???
But mcp will never have a leader like chakwera.mark my words
Uyu ndiye president ,. Big up Amwene Pitala. Auzeni abusa. Mwina ngati zavutisisa angobwerera Ku ulaliki akawalandira MULUNGU sataya mwana wake.
Asatipusitse iye kuchipani kwawo kulinso mavuto
murders careless party.(mcp) will never change.mbiri yanu sidzayera mpaka kale.
Gogo Pitala has called 4 peace ku chipani cha MCP. Akutanthauza Chani? Pangani Kaye zanu agogo
Kkkkkk koma Pitala ndi dolo akuyankhula zimenezi pa gulu koma kuseli akuyishosha kuti chipani cha MCP chithe ngati chikolopa
Bodza ndale chabe mawa atukwanana angofuna kuyalutsana sangakoze akulepherera Ku dpp
Ife basi yathu yomweyi Malawi crocodile party MCP 4 ever. ..
satirical
Congrats Mr Presdent
Hello my name is john I want to give a testimony about my HIV virus that was cured by a great spell caster. Since last 4years I have being a HIV AID patient. I never think I will live long again and am so grateful to Dr sule who help me cured my HIV AIDS last 3 weeks. I was in a great pain so I told one of my best friends; he told me that there is a great spell caster that can cure my VIRUS. I asked him if he had his contact, he gave me his contactl, I contacted him he talked to me and he perform the necessary things and sent it to me through corrier delivery company and deliverd to me at my place and he told me that after two weeks I should go for a test. Which I did, when the doctor told me that am now a HIV negative I couldn’t believe myself I went to see another doctor the result was still the same, I was human on planet earth, so I emailed him and thanked him. Please if you are having a similar problem please visit him/contact him via whatsapp +2348162447651
That’s a good leader
Peter leave MCP a lone dont pretend as if there no problems in ur DPP
yes no problem in dpp
U r just thinking u dont no
Awa alibe nsannje ayi mpamene awo ati abusàwo ali busy kukumba maenje kuti mugweremo koma yehova akungokuolotsani nàmupitabe chitsogolo
ha ha ha ha ha………! very laughable!!!!……
Auzen zochta anawo amapwya mulhupalhe bwana presdent,tmakunyadran heavy.
Ungobwera ndi bodza basi pa tsamba limeneli, iwe akhale kuti akusokone chipani cha MCP ndi a DPP usamve pa news/ pa radio kuti dpp ndi imene ikuyambitsa. Akasokoneze anthu oti akuvutika apindula chiyani, iwenso ndilipoti lako labodzalo bwanji wabwerensa mochedwa?
Dpp
Chipani cha MCP chithe chifukwa phindu lachipani chimenechi palibe chinatembeleledwa
Amakanika kumpanga acknowledge Chakwera ku ma function a boma apa nde waona ???
Democracy must not be words only but put in action. How can u clean someone’s ass while u haven’t clean yours? Ndale ndibodza eti. Chotsa chitsotso chako b4 chamdzako.
How can peace prevail pamene mukutuma anthu kuti akatiotchere office?Are you serious?Kuti tidziti simukudziwapo kanthu?Takonzani kaye dzikoli za MCP mutisiyire tokha akakhala Jumbe posachedwapa tikupatsani wauleleso ndipo osati ogula ok.
Utsogoleri ngakhale utabela ma votes koma Mulungu ngati sanafune sizingatheke. Choncho ndikhulupilira nonse onyoza mtsogoleri sindinu Akrisitu ngati ndinu akristu ndiyekuti simunawelengepo 1Petro 1 Muzilemekeza atsogo anu
Even if utsogoleri woti wapha ndi kulanda dziko mzako or oti wabera mavoti just like u have said,alemekezeke basi.Its from God.
APM auze abusawo ndale sikuphana ayi
Njaunju,Chasowa, anaphedwa ndi Dpp ya peter. Chakwera is clean.
man kunena zowona kulibe nzeru olo imodzi
Lev Nyondo is back to power in the north.
Sweet news about Nyondo “landslide” comeback. Pepani MBC. Campaign munamenyera ena aja mmadzi. Pepani, maswewra oterewo inu a MBC muzichitira Ku Blantyre syndo komweko
ine ndingofusa nawo..zija munati kagulu kena kalosela zakutha kwadziko pa 29 mwezi watha…bwanji simukutiuza kuti zinatha bwanji?ndimadikila kuti paduse tym yokwanila,inu mumapanga post zinthu zongofuna kuononga maganizo aanthu basi…mbuzi anthu amene mumapanga post,nzeru mulibe kumangopeleka nkhani zodanisa amalawi.mwandikwana kwabasi.
Mau a akulu amakoma akagonela
Financier
kkkkkkkkkk
Petro angataniso kodi? adakhalapo wa mcp chiyambileni cashgate ndi mbale wake,azipusitsako mbendera yemweyo mwamva,amulekeletu chakwera wathuyu ndipo siwamtundu wakwao.
Zaziii chikukukhuza ndi chani bwampini tathetsa njalai tombolombo iwe.
iweso ndi mbuzi eti?
Eya ndine mbuzi.
Mumakwana Man Pitala… Auzeni Manfanawo Kut Agonjelane Otherwise Adzangoonetsanapo Ma Blow…. Inu Man Pitala Ndinu A Bg Man Ozitsata.. And Za Inu Timakamba Ndiife! Tikudziwa Kale Inu Kut Ndinu Coolman Thats Why Atumbuka, Achewa, Ayao, Alhomwe Plus Asena Akungohalla Kut Pitala 2019 Bomaaaaa!!!
Lomwee belt fo ever
Hahaha kuponya bomba nkumawuzilira???
Kkkkkkkk uyu wakalambadi mutu sukugwilaso ayi. Tatiuzeni za Cashgate apa osati kulowela nkhani zoti ukupangisaso ndiwe
cash gate ndiye kuti chani?
Cashgate ndiye kuti chipata choposa makina a Atm…munthu umangotapa mmene ufunira. Ndithu bwana
Hooo!, chikopa nkhosa, nkatimo fisi? ayi tiye nazoni.
Chikome kome cha nkhuyu mnkati muli anakulapsa
Ati inu? nyenga ndiyemweyu uyu.. aaa!
Kkkk
Nyenga fusadara
hooo! inu.. pusi pusi umakasisita pamsanapa apa, ikoko mchila weteweteee iwe kenako gwiiilu… mkasaka chiii!
Kkkkk, koma ndoda, mwanikumbutsa kamwathendo wa pa zodiak radio.
Amene uja ndi zolowere mkudyele mwana.
Kikkkk ndizo yuluchita ndodai ka, nanga lero ndi lero ukayankhila za ku MCP mpamene ali iwo omwewa playing the game under the ground?
Akuti ndale imeneyo.
Mfiti simafuna kuonekela kuti akupha ndiye mcp be careful
I used to love this page koma pano ndimangodutsa coz mwachulutsa bodza kwambiri
Big up Mr Big
Thats why i lv u mr pzdet.Ndale si ku nyozana but kutsogolera anthu potukula dziko.BIG UP MR APM.The pzdent with vision
iwe ukati ndale sikunyozana mmene dpp ikunyozeramo, apm, patricia, kudontoni, do yo follow dpp well koma iwe…….wamasewera iwe eti
kamuuze Kaliati zimenezo.
Koma mmadziwa kupusitsa anthu ndithu mutavala dzigoba. Opusawo nkumaombera mmanja to such crap of propaganda. You are the masterminds to mcp squabbles with your foolish style of divide and rule. You can fool some but not all
iwe chapani chidapita nkamuzu ichi.kusapota mcp nchimozimozi kukhala mulova.makangano ku mcp sinkhani thats why a gadama.matenje.sangala. chiwanga.chisiza. mphakati.chipembere lero kulibe. ufunse kuti zinatani.then come and comment
That was my opinion how i see and understand politics pamalawi. I don’t impose it on anybody and that’s yours too
Yaa thus democracy.Teach them professor
kkkkk akosonkhezera ndiwowo a DPP akufuna kuoneka madolo kkk mmm Ben Phiri ndi amene ali engineer wazimenez
choka apm iwe, ungafunile zabwino mcp iwe??? stupid propaganda
choka apm iwe, ungafunile zabwino mcp iwe??? stupid propaganda
Satire
big up mr president!, amene atakunyozeni pankhani iyiyi andimva lol
Akuvani ndichani dpp mcp zipani za Mbava
Ndipo atimva
MCP, UDF, DPP and PP ndi zapani zambava, so just shut up and enjoy popcorns
hahahahaha ndati mundimvatu kkk
zake zikumukanika!!
Akhazikeni pansi bwana anawo aphana, auzeni agonjerane
PRESEDENT OZINDIKILA AMAFUNIKA AZITELO THATS GOOD APM
Ife kwathu ndikuyamikila zabwino basi komano we wll never find another presedent like this one in malawi ngati alipo tamutchulen timve kakena akamulepo kapena
Waiting government from, untill when? President by votes action than wining with mouth
Yamukanika kuisokoneza MCP