Malawi Super league giants, Nyasa Big Bullets must really be considering of fetching new players as just days after two of its players headed to Tanzania for trials, it has now been revealed that two other are leaving for South Africa to try their luck as well.
The two are forward Muhamad Sulumba and defender John Lanjesi are heading to South Africa’s Premier Soccer League side Polokwane City F.C.
This comes just a day after goalkeeper Owen Chaima and defender Sankhani Mkandawire both left for Kinnah Phiri’s Tanzanian side Mbeya FC.
However Technical Director Billy Tewesa and Chairman Samson Chilunga have said he does not know that Sulumba and Lanjesi have left for South Africa.
Recently, defenders George Nirenda and Miracle Gabeya were in South Africa for trials Chippa United where it transpired that Bullets went furious because they were not consulted.
It is reported that one of the Bullets top officials called Chippa United spitting venom at the club for picking the players without following procedures.
Kayeseni mwayi wanu guyz, gud luck
Khaniyabwino nebour
Kkkkk I like your diction….”spiting venom”
Mwapanga export kuti azikamenya ma penalty…. Neba
Bola akayesedwe mapenaty koma akakayesedwa mugraund ali M’madzi atipezaso ameneo
How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my deities, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before a month my body start developing my skin start coming up after 2month I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via whatsapp +2348162447651
You ll never walk alone, much luv.Die hard suporter .
Im behind you.
Neba tulutsako maplayer osamangosunga mmnyumbamo wanva kapena mwina zaka zawo ndizosakwanatu kt akamenyeko mpira kunja kkkkk km neba
All the best maule players.
Wa bankers 4 life,zabwino zonse a Nijo,koma anzanu mwapita nawowo mpira wawo ndiwazikhulupiriro.ndiye nyanga zawo zikadumpa nyanja zimasuluka.koma inuyo madala ndiakatundu.pitani kapangeni ma rand.remember to put God first and dont 4get indurance also pays.all the best.WA BANKER 4 LIFE
Do worry guyz as u know dis year God has planed something interesting to us n believe me guyz dis year we wll take alot of cups in Jesus name wat u know z we r going by miracles.
Kaya kususuka ndi ndalama executive ya bullets team yisokonekera iyi how can you do that yet you know that hav you plenty injuries
Abwelako amenewa posachedwa pompa.
All the best bafanaz . #team:NBB
all the best
The Peoples team. Neba m’mimba kuti puuUuuuuuuuu
Maso tilinawo zidzawoneka
Aneba mukhalira njiru yomweyo ndichifukwa simupita pa mtsogoro anzanu zikuyenda. …………. siswa mazira. please fill the gap
Goodlucky guyz.
Ziku theka zikuthe afana ndihlu ndiyo mweyo basi ansanje akakwilile doko lansanje hahaha mawule ndi dihlu mumanyanya makwela kwela muna kwela hule wa priodi
Pachoka mzako pali malo
muyende bwino bola muzikachinyabe ma penalty ine ndi wanyelele uja,
Mbuli mu mpira za chuluka ndikona amalawi abili tili osauka vuto ndi nsanje
hahahaha tiyeni nazoni,
Ma Ref Akumangopeleka Ma Penalty Kwa Mfitizi Kuopa Kuphedwa Kkkkk Koma Abale Kkkkkkk Chingambwe Bullets!!! Kumango Oopseza Ma Ref Eeeeeee!!!
ahaha paja Noma 12 years league osatenga
ahaha paja Noma 12 years league osatenga
ahaha paja Noma 12 years league osatenga
ahaha paja Noma 12 years league osatenga
Noma ndi mbuzi zachabechabe
kma we supporterz shud learn 2 knw our role in sports az far az football z concerned…the role of a real supporter in football z to support hz/her team not to underate other peoples team team…kma kuno ku malaw supporter weniwen uzamupeza aku2kwana supporter wa team ina..its high tym we must gt 2 knw our role supporterz…ine nd wamaule so..cbho kut ndkamayamkla team yanga wna zzmunyaxa..am just playin ma role!
Kkkkkkkkkk usova ase
Zabwino zonse 4pakamodzi iliposo ina ingatumize 4 pakamodzi muchikhala inu tikanatsekura m’mimba ndikudzitamandila munthu sadzathekadi. #Viva maule
mmmm osadandaula paja inu anu ndi mapenaty ndiye sikuti akuchoka ndi mareef ayi alipo ndipo azipelekabe,mungopeza omenya basi,kodi simunagwirizana ndi mareef kuti magame achaka chino mapenaty azingokupasani.
Hie Bravo, Do you know why this team get more penalties? Its bcoz ma team enawa amaopa mbiri. Amatanganidwa mpaka amalakwa zochita. Team ina idzangoyesa kusewera mtima uli mmalo. Ndithudi bullets sizapulumukira penalty
chakula apa ndi nsanje. Maule woyeeeee
Akulu mudziwe kuti Penalty its a part of the game and imabwera coz of pressure!!!!
Umbuli winawu kodi kugwira mu 18 box ndi penalty every where komaso Lucky malata samuziwa ndani kuti ndiwamablanda yoooooo neba ndichifukwa chake akutibula
Akupita ku SA osadandaulanawo abwelelako ose
Koma ngati mapuleya athuwa apitadi kunja panthawi iyi. Ndikokuti kunalembedwa kuti Mulungu ationetsele china chache choti tiphunzilepo chifukwa ndinthawi yovuta kwambiri pankhani ya mpikisano sabata ino2
Koma ndiye khani yabwino manyasa mumalimbika kwambili guys chifukwa chake dzabwino dzikukusana
Mpake Kukafuna Pofewa Kumene Ma Player Angawapatse Ndalama Osati Kuabela Ngati Mmene Anakwiira Ma Sponsorz A NNC
Plz plz ngati ma players akupeze mwai wa choncho let them go musamawakhomelere coz ndi tsogolo lawo
Sakhani and Owen Chaima will also goes to Polokwane fc
Yah,will go to polokwane fc
Sure guyz
kkkkk will also goes to polokwane fc yomweyo
Kkkkkkkkkkkkk chonchi tikamati xool ndiyofunika,,,koma makani thoooo hahahahahaha
Kkkkkkkkkkkkk chonchi tikamati xool ndiyofunika,,,koma makani thoooo hahahahahaha
kkk other wil goes tanzania kma xul ndi dilu
John Lanjesi and Sulumba
kodi maplayerwo nd ndan guys tandiuzan
Sulumba,Sankhani,Lanjesi and Chaima
musakhale ndi mphuma apita kukadya ndalama za a president
Mmmmm APA ndiye zitivutatu
Chairman wakana akuti ma prayers sanachoke adakalinawobe mwina apita kokayenda basi.
aaaah muzingowinira MA refuwa. kkkk
plz be civilized, football is not netball, we use legs not hands and only goalkeeper is allowed to use hands only in 18 yard box. Bullets strikers are giving pressures to defenders hence penalties. umbuli ndi matenda mix nsanje,vuto losapota team yolephera.mudzingolira simunat.,
ngat amawinira ma ref, inu game yanu ikumakhala opanda ref? ndye akumaimbira ndan? Bullets nd Barcelona yakumalawi!!! walira neba!!! shame on youuuuuuu!!!
vuto ndi katangale ndi mu pitch kumene. amalawi sitidzatheka. kkkkkk mpira PA Malawi
aaaah ndipo pali katangalepo. kkkk
Bird in hand worth two in the bush, all the best!
replacement arledy