Mkulu wa Reserve Bank wachotsedwa kamba kokanika ntchito
M'tsogoleri wa dziko lino wachotsa mkulu wa Bank yayikulu m'dziko lino ya Reserve bank a Wilson Banda kamba kolephera ntchito. Malingana ndi anthu ena ogwira ntchito ku Capital Hill omwe atitsina khutu, panatsala miyezi 6… ...