Apolisi apha mbava poyiwombera
Apolisi ku Ndirande mu mzinda wa Blantyre, awombera ndikupha mzibambo wina yemwe akumuganizira kuti amafuna kukaba ku nyumba kwa wachiwiri kwa wamkulu wa apolisi m’chigawo cha ku m’mwera cha ku mzambwe. Malingana ndi ofalitsa nkhani… ...