Tithandizeni ndi njira za makono za intaneti – Kunkuyu
Nduna yowona za Mauthenga ndi Makina a Digito m'dziko muno a Moses Kunkuyu wapempha dziko la Korea komanso mayiko amuno mu Africa kuti aganizire nkhani yokhudza njira za makono zomwe pachingerezi zimatchedwa kuti Information, Communication… ...