Ndazitaya sindikapezeka Ku convention ya UTM
Monga muja tinalembera cha ku m'mawaku kuti m'tsogoleri wa chipani cha UTM a Michael Usi sakapikisana nawo ku convention ya UTM, iwo atsimikizadi masana ano kuti sakupanga nawo convention yi chifukwa kwachuluka phada. Usi akuti… ...