Zomavala mabamushoti, kumadikula, timiyendo ngati machesi, zithe – wabweza moto JB
…wati Lulu ndi Tay Grin ndi ‘mingochana', anaba ndalama zothandizira ovutika ndi namondwe …akuti dolo ndi Namadingo Mamuna mzako mpachulu; kwavuta ndipo kwatelera, awawa apwetekana. Oyimba Jolly Bro wasambula Lulu pomunena kuti ali ndi timiyendo… ...