Anandiyimitsa udindo popanda chifukwa: yadandula mfumu yaikulu Amidu ku Balaka
Mfumu yaikulu Amidu ya m'boma la Balaka yadandaula kuti akuluakulu a khonsolo ya Balaka adaiyimitsa pa udindo wa ufumu pa zifukwa zomwe sakuzidziwa. Poyankhula ndi Malawi24, mfumuyi, yomwe dzina lake lakubadwa ndi Amina Gayesi, yati… ...