Ogwira ntchito za Boma ku Balaka alonjezedwa kulandira malipiro awo lero
Bwanamkubwa wa boma la Balaka, Darwin Mngoli, wati anthu ogwira ntchito mu nthambi zosiyanasiyana za boma mu khonsolo ya Balaka alandira malipiro awo a mwezi wa May pakutha pa tsiku la lero, lolemba pa 5… ...