Boma liyamba kukakamiza anthu kuvala zotchinga ku nkhope
Boma lati liyamba kukakamiza anthu kuvala zozitchingila ku nkhope ngati njira yochepetsa kufala kwa covid. Mlembi mu unduna wa maboma aang'ono a Charles Kalemba anenaizi ku Lilongwe dzulo ndipo ati boma liyamba kusatila ndondomeko zomwe… ...