Katemera sakhala okakamiza – boma
Boma la Malawi lati katemera wa mlili wa COVID-19 amene akuyembekezeka kufika mdziko muno kumathelo kwa mwezi uno sakhala okakamiza. Izi ndimalingana ndi nduna yofalitsa nkhani a Gospel Kazako omwe amayankhula lachisanu pomwe akuluakulu a… ...