Kongelesi sidzalamuliranso Malawi, watero Mutharika
Mtsogoleri wa dziko lino, Peter Mutharika, wanenetsa kuti chipani chotsutsa cha Malawi Congress (MCP) sichidzalamuliraso dziko lino. A Mutharika alankhula izi posachedwapa pomwe amayankhula ndi imodzi mwa wailesi za kanema zodziwika bwino pa dziko lonse… ...