The ruling Democratic Progressive Party (DPP) secretary general Greselder Jeffrey has defended her controversial sentiments in political rallies saying they are driven by the ‘truth’.
Her remarks follow criticism from citizens on how she speaks during political rallies in the country.
The ruling party secretary general has argued that she gives honest sentiments to citizens though her remarks are described as insults by some quarters.
“Inetu sindimanyoza anthu, koma ndimanena chilungamo nde popeza chilungamo chimapweteka, munthu ndi povuta kuvomeleza (I don’t insult people I say the truth but because truth pains it is hard for people to accept what I say).
“Amadandaula ndi a opozishoni chifukwa amaziwa kuti watibaya (The opposition are the ones that complain because they know that I have spoken the truth),” said Jeffrey.
Wa Jeffrey came under fire last year for her remarks that a citizen from northern part of Malawi can never become president of the country.
Political experts faulted the sentiments and demanded that she should withdraw what she said.
Madam jeffrey ‘Lino ndi dziko, kunali a zanu maudindo omwewo, tukwanani m’mene mungathele, ndife ayani kuti tikuletseni,
Ndi a Bishop a *God is Good International Pentecostal Church*, the founder for that matter so touch not God’s annointed
Truth my foot
HULE LA MUNTHU ILI AKUONA NGATI A MALAWI SANAONEBE MUKHAULA COME 2019.
Mayiwa kuyakhula amatha koma problem ndiyoti zimene akuyakhulazo amangozindikira azitulutsa pakamwa paopo
Pazamusata uyu
Uakayenda udzisiya phazi coz pakamwa pamakutsata
And that truth will kick you out….
WAtha maplan uyu
Amayakhula the truth.
oooh yeah!her mouth will put her in a big problem!!!ukayenda usamasiye mulomo!usiye mphazi chifukwa mlomo udzakupeza!!!!
Koma anthu akwawowo nkumamuvotera ndithu…
uyu nde bola chavura mmh
But this woman, mmmmm our fellow man is in trouble.
She doesn’t even have a man, amangonyengetsa kwa amuna osiyanasiyana
Oho that’s why mutu sukugwira bwino ntchito eti!!
mmutu mopanda kanthu awa