![Kondwani Nankhumwa Malawi](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/01/Kondwani-Nankhumwa-Malawi-276x176.webp)
Tsoka likalimba: Bwalo la apilo lakanaso Nankhumwa, Jeffrey
Yalimba nkandilo! Pomwe a Kondwani Nankhumwa, a Grezelder Jeffrey komanso a Cecilia Chazama amafuna bwalo la apilo liwabwezeretse pa maudindo awo mu chipani chotsutsa boma cha Democratic Progressive (DPP) komaso kuwapatsa chiletso kuti asakaonekere ku… ...