Mu nyengo yino yachisangalalo yimene kumakhala zikondwelero za masiku a Khirisimisi ndi Nyuwele, mfumu ya zi Nyau sinalore kuasiyasiya oyikonda powapasa mphatso.
Mfumuyi imene dzina lake lili Limbani Kalilani, yapereka phukusi la nyimbo zisanu ndi imodzi kwa a Malawi amene amakondwera ndi mayimbidwe ake. Iyo yachita izi kuti anthu asangalale mwamkokomo mu nyengo yino.
Kalilani amene amatchuka ndi dzina loti Tay Grin, waimba mothandizana ndi akatswiri angapo amayiko akunja.
Ena mwa oyimbawa ndi Bebe Cool wa Ku Uganda, Orezi wa Ku Nigeria ndi Jay Rox ochokera mu dziko la Zambia.
Katswiriyu wayimbaso mothandizana ndi a Malawi amzake monga Sonyezo Kandoje amene amadziwika kuti Sonye, komaso Gemini Major amene amakhala mu dziko la South Africa.
Mphatso yi yaperekedwa lolemba usiku kudzera pa pologalamu ya pawailesi yotchedwa made on Monday. Ndipo analandira mphatso yi mmalo mwa a Malawi ndi bambo Joy Nathu amene ali muulusi wapologalamuyi.
Nyimbo zomwe zikupezeka mu phukusili nazi; 21, Tawe, Ssinaziona, One more touch, Hallelujah ndi Balenciaga. Ndipo anthu apereka maganizo osiyanasiyana pa nyimbozi.
Imodzi mwa Nyimbodzi, one more touch ndi yomwe ili yodziwika kwambiri kamba koti inatuluka mwachangu. Kanema wa nyimbo yi anafala paliponse mdziko muno.
Wangoyambatu sanati NXT yr ndi Rick Ross. Buffen muguliletu
Big man am always proud for that keeping it man
zichitikalit zimenezo
ndikuti kumeko abig man
zikachitikilakuti abig man
kusowa zolemba to uku a 24
Kukweza kamba mu mtengo man awa satha kuyimba ine ndiye ayi kwawo komweko bola ndizivera TSAR LEO fana waluso uyo wosati chitelera chomwe amayimba ada kaya amati ndi hip hop kaya ndi beni
Kungosowa zolemba 24
Mfumu ya kamano kkkk
Uyu ndi dolo wa oyimba kwathu kuno
ndimakufla tg
Kd ameney ndinaimba? Azingovara nyauzo bas osat kuimba zopanda nfundo zija
Yah yah proud to be Mchewa umakwana nyawu king
Aaaa bozali ine bwanji ndimamukonda koma sinnalandile
Komadi iyidi ndi mfumu ya zinyaudi sungafunsenso ikuoneka koma oikondao akuoneka ma babie ochuluka kusiyana ndi azibambo
Akazi kutengeka too much adha kkkkkk
Eeeeeee koma amaikonda ndi akaziomweo
Aaah my foot… I ain’t a hater though, I just hate copying already made styles…. #my_views
naneso ndimaikonda hvy mfumui.koma fuso mkumati iyoy imadziwa zimenezo,nanga oikonda ake ndiati omwe alandire mphatsoo? mwina ndine amene!
TAY grin, following Fredo’s footsteps in other way
which footsteps bra tay is far better than fredo
Hahahaha Tay Grin akatsanzile fredo zoona ??? iwe ndi nkhuku eti ….Tay Grin samakuopsani ndekuti ??
Hahahaha tay grin mkachaniso
ukafunse fredo y anasiya kuthoka za tay grin he will tell u coz he knw grin ndi fire
Fredo ali ngati bambo ake Kamlepo…. always making noise but has no legacy….
Nkona akumapanga tima show taulere kuli kugula fame…. mtchana wamakape
Mr fireeverywhere:……….