Mutale watutumutsa gulu ndi uthenga okhudza bwenzi lake Tay Grin
Ubwenzi wa Tay Grin ndi Mutale Mwanza ukuoneka uli pendapenda potsatira uthenga omwe mkaziyu walemba pa tsamba lake la mchezo. Uthengawu ukusonyeza kuti mkaziyu wasweka mtima ndi zomwe bwenzi lake la muchita ngakhale zifukwa zake… ...