Phungu wa dera la pakati mu boma la Lilongwe a David Bisnowaty aputa mavunkhomola.
A Bisnowaty dzulo lolemba anajambulitsa ndi Mafumu a mu dera lawo ati atatchena ma suti amene Phungu’yo wawagulila.
Polemba pa tsamba lawo la Fesibuku, a Bisnowaty analemba mozithilamo amvekele: “sindilonjeza zinthu osakwanilitsa, onani ndinalonjeza Mafumu ma suti. Awa atchena apa awa.”
Koma a Malawi ambiri sanakondwe nawo a Bisnowaty ati kamba koti anali kuzitamandila pa zinthu za mkutu zenizeni zopanda ndi mchere omwe.
A Malawi ochuluka amene anathililapo ndemanga pa nkhaniyi anasonyeza kukhumudwa kwawo ndi khalidwe la Phungu’yi.
Ena anadzudzula a Bisnowaty kuti bola akanamazitamandila pa chitukuko chooneka ndi maso osati kamba koveka nsanza Mafumu basi.
Choseketsa chinali choti Mafumu ena anavekedwa ma suti aakulu.
*Ma suti a Bisnowaty autsa mapiri pa chigwa*

bisnowaty ndi khuluku alephera kutipatsa chitukuo mmalo mwake wangowagulia aunjika magogowa
Mubwele ndikuwuzeni zokuti mupange post osati khani zopanda tathauzo zanuzo
That’s insult to the greedy chief’s kkkkk
Vuto La Amalawife Kunyoza Too Much.Pamenepo Mafumu Ena Analibe Suit Apa Aipeza.Akunama Akulu Mwachita Bwino Mwathandiza,kp It Up
Vuto La Amalawife Kunyoza Too Much.Pamenepo Mafumu Ena Analibe Suit Apa Aipeza.Akunama Akulu Mwachita Bwino Mwathandiza,kp It Up.
Akuona ngati makolo athuwa ndi ogona?
kutchuka ndi ulele bola kuztenga bwino
akuona ngati agawine chifukwa cha masuit wapelekao akunamatu ameneyi muuziletu
mwatchena koma?
Bisnowaty watichotsa manyazi, ,, mafumu akuwoneka bwino, ,,
Ana anjoka nsanje, ,, mufanazo
Phiri lina ndakumana nalo mu zombamu sindimadziwa kuti lachoka kwa a bisnowaty
kkkkkkkkk km abale mesa azimvumu akas wo ali nd azibambo awo,,azivala basi
Kodi zithu zikamavita timasiya apa wa std 3 atha kulemba zazeru
Nanunso a #Mw24,,the issue is,,#bisnowaty wapereka ma male suit kwa ma female chiefs,,bac izii ndzomwe mulephera kuuza anthu ,,zamanyaz buanj!!!!!!!
Mukanati wagawa chimanga ndikanakumvetsani koma muti chani suti aaaaaaa asandiyankhulitse pambali ndithu
Akatelo wagula ma vuto koma lol
Kkkkkkkkk mafumu kwagulila kaunjika ndikumati ndachita zampavu jekete lakelo kuliona mpa anthu awili kuvalatu
Nhkani yopanda nzeru …
This story of yours is senseless doesn’t have meanifull
koma ndiye afunda ma jeketewotu
Kenaka azapereka ma shirt
Kkkkkk mpaka ma jekete
Kkkk ma ovolosi
nanga nsapato yake? ndi sports shoe sikugwilatu
basi kulawira ku post nkhani ,mwati mubwereze kulemba ngat mwana wa grade R , zazi sizikumveka kut mukutinji?
Kodi walakwitsa chani munthuyu?moyo waufiti basi amalawi.
Bisnowaty ndiolephera palbe akuchta mnzeru ai
Mmmm, Nanga Masuit Wagawawo?
Mmafuna Peter azitchena yekha?…apapa ndi draw game,aMfumu nawo atchene n in 2018 it will be more…
nanuso @ Malawi24 mwalemba zopanda ntchere,,,,, nkhani sikumveka bwino bwino iyi
Si chitukuko chimene tumafuna ife povota chimenecho