Joseph Kamwendo targeted by thugs

278

…robbers ransack his car

Be Forward Wanderers midfield maestro Joseph Kamwendo managed to escape a robbery at his residence in Blantyre last night.

However, his vehicle has had parts stolen and windows smashed.

Kamwendo’s car in bad shape.

Pictures circulating this morning show the vehicle in bad shape after the purported attack on him failed.

Reports say he managed to hide while the thieves turned to his car parked outside his house in Chigumula Township.

The thieves have gotten away with a radio, windows and other items that were in the car.

Apparently, it is reported that police have ignited a probe into the matter.

Night robberies are on the upsurge owing to lengthy power blackouts that have rocked Malawi.

Just last weekend Kamwendo extended his popularity among the Nomads family when he scored a screamer that saw Wanderers win 3-2 against a rather resilient Dwangawa United side at Balaka stadium adding to the lifeline of the Tnm super league title chase for the Lali Lubani side.

Share.

278 Comments

 1. umbuli ku Malawi kuno wafika pachimake, ndikudziwa kuti zinthuzi zikukambidwa chifukwa chosaphunzira kwa anthu amene mukuti ndimasapota a Bullets amene amubela kamwendo. ndikuona kuti suspect wankulu mukukhala inu amene mukunena kit

 2. #Joze where ever you are, forget about the past and focus for the future, #which_its_the_game_against_mzuni….Neba chala cha #YAWE chikaloza chaloza
  #Noma_pachiwongolero..

 3. Aliyexe ndiwakuba apa enanu ndikuxalulika ngat mukut ndi abullets pot enanu bambo anu ndi a maule nde kut amakaba nawo?my sory goes to kamwendo he is ois amalawian guy’s let s love one another

 4. Oyamba Kubeledwa Kumalawi Kuno Ndikamwendoyo Taona Anthu Akubeledwa Magalimoto Ikhale Galimoto Yolongosoka Akanangobamo Wailes Yokha Bas

 5. Koma Anthu ena zikugwilizana bwanji ndi Bullets zimenezi? Eneya Banda anakhapidwa ali Ku bullets sitinanene kt nda Noma koma poti ndi Kamwendo basi ndi Abullets apanga attack, Ma savage ndinuyo, anthu amabeledwa daily sizachilendo,

 6. Mmmmmmmmmmmm guyz zonenanena kuchuluka mvula ikagwa chilichose chikachitika ndi BB bwanji adaleka kupangidwa robb m’mbuyo mu mudzilakhula bwino kuti mawa tiinene zina shame on u ukulimbana ndi BB

 7. Kkkkkkkk anthu oipa inu!!!!!
  Kwa khama kulibe anthu?
  Koma ndilande ya ana akachaso ngati imene ija,
  Ngati mumafuna kumupha,
  Mwalephera!!!!
  Noma inyamula chikho basi
  Mufune musafune
  Ng’oooooohhhh!!!!!!

 8. AAA KOMA ABALE, TIZITUKANANA TOKHA TOKHA CHONCHI? Page iyi analero lokha aaa landiopsya. Aabalee ndichani chikuchitika mpaka kuyima pachuru kumatukanizana? Nkhani ya galimoto la chekamwendo labeledwa.

 9. Makape masapota anoma,,,player azikakhala kwa KHAMA koma abale,,mmene anayendela iwowo maiko onse aja kumalephera kumanga nyumba kumakhala pa rend.Mayesa kwa Khama ndi kwa masapota anoma.

  Ku SA 3yrs ago Senzo Meyiwa anaphedwa ku chibwenzi wa Orlando pirates,,munamvapo akuti ndi ma rivals awo a Kaizer Chiefs?
  Kodi umbuliwu uzakuthelani.,,,okuba amaona nkhope?.Iye ngati amamwa mowa mwaumbuli mumati asabeledwe

 10. Umboni oyamba mumafuna kumumenyesa duka,mwatuma a Dwangwa kupanga complain nkhani ya Kamwendo.kachitatu mukutiuza kuti munthu oziwika sangakakhale kwa Akhama,mukufuna kuthandauza chani??.Anthu ena akhala kwa akhama ndioziwika kuposa kamwendo.Winanso akutukwana.muyaluka nazo zimenezi.Zinani kuti zonse mupanga tikuziwa powona polekera.Neba sazatheka ndi achule awo ali kusulom kowo.

 11. Ndikhulupira kuti amene mukunena kuti ndi abigbullets muli nawo umboni wokwanira,ndipo ndi nthawi yabwino yoti mutibweretsere umboniwo.

 12. Panthawi Ino Nkoyenera Kut Ma Player Anoma Akhale Ndichitetezo Chokwanira Chifukwa Adani Ndiambiri Kuphatikizapo Neba Wathu

 13. Mmmm a BB nd a Sulom aaaaaa mwayamba kulonda ma players athu mmm koma ngati jealous wanu anyanya aaaaaa cholinga mupweteke asakasewere game ya Mzun huuuuuuu Chauta wakana manyazi bwanji awooooo hooooooooooo

 14. few years ago, thugs killed Meyiwa in S.Africa but I never saw comments like I’m seeing here from uncivilized Malawian supporters who always encourage their teams in Juju/ngunda and misconduct during games. Mpira wathu sudzatukuka mpaka ………………..

  • we learn from others…with this resistance to change eeeeee mkulu keep kulimbikira kukodzera magolo, zithumwa, kunama zaka zakubadwa and the like….lol. Sorry if my comment has disturbed your peace of mind

 15. It seems thugs are afraid of mob justice than anything else because Police is not there in residential areas. You get more on them along the roads. So basically a Chitetezo seem to be taking the lead

 16. Thus why l don’t support football teams,they lack discipline, love and Peace but full of backbiters pull him down, JUJU beliefs, drunkards, osuta kanundu full of woes just to mention a few, Learn to love peace and unity

 17. Aliyense wa inu amene wanena kuti a bullets mitumbo za amanu kwa zaka ziwiri kaya amako anafa watukwanitsa mafupa ndipo apanga bwino kumubela

 18. apa tikuwonetseratu umbuli ndipo amalawi ndifedi mbuli,chomwe a bullets angalimbanire ndi kamwendo ndi chiani? udani umakhala mground,mecium muhone adapangidwako chiwembu ku south africa,zimachitika izi kamwendo sioyamba. ndiye anoma tamayankhulani ngati anthu ozindikira pajatu mumati ndinu ophunzira.Tiyamike Mulungu Pomuteteza JK.#nbb_supporter.

 19. Kusowa nzeru kwa munthu ,wabwino bwino aganene kuti ndi a bullets? Anthu onsewa akubeledwa mu dziko munowa sianthu? Bwanj timasiyanitsa zinthu, aliyense akhoza kubeledwa osati zopusa anthu mukunenazi, Ali yense ndi wofunika chimodzi modzi ana a mulungu

 20. Mukamakhala kwanuko simukuva bwino mukava dzi loti NYASA BIG BULLETS.Bullets ilipobe kut mupsye mtima,mupwetekana mkumanamizira BB koma mbiri yathu sidzasintha.

 21. This is very bad indeed I hope Bullets fans are not behind this attack just to make sure that Jk doesn’t play in our must win game against Foolish…educated salvages called Mzuni

 22. Iwe Rhodney Mandala ndiwe chitsiru ndiye kuti mbava ndiiweyo muti tathokoza chauta kuti Kamwendo wapulumuka pa chiwembu iweyo kumalowetsa za mpira zikukhudzana chiyani

 23. Koma wa bullets ndi chigawengadi guys akufuna amuvulaze then tilephele kutenga lig inu musangalalele ng’oooooooooo muli m’madzi Mulungu akasankha wasankha ngakhale mubele ma penalty palibe chothandiza kkkkkkkk Manoma patsogoloooooooo

  • iwe anakulesa ndani kuti usamasute moyo wako ndi wako basi panga zosamala moyo wako posausutisa fodya bwina ungakwanise zaka 100

%d bloggers like this: