Pamene zokambilana za aphungu ku nyumba ya malamulo zangoyambapo, mtsogoleri wa zipani zotsutsa a Lazarus Chakwera anena kuti iwo ndi anzawo ayambapo kunyanyala zokambilanazo.
Malinga ndi a Chakwera amenenso ali mtsogoleri wa chipani chotsutsa cha Kongeresi, iwo ndi aphungu awo ati ayamba kunyanyala zokambilanazo ngati a boma sabweletsa mu nyumbayo nkhani yokhudza zisankho.
A Chakwera adaulula izi pamene amayankhapo pa zimene a Mutharika adakamba potsegulila nyumba ya malamulo lachisanu.
“Ndipo a Mutharika ndi abodza, anatilonjeza kuti abweletsa nkhani yokhudza malamuo a zisankho, koma mmalo mwake tikuona palibepo,” anatelo a Chakwera.
“Ndipo ife tikunena lero kuti ngati nkhani imeneyi siyibwela pano, ife tiyamba kunyanyala zokambilana mu nyumba ino,” a Chakwera anaopseza motelo.
Mwa zina, malamulo a tsopano ovotela akunena kuti munthu opambana chisankho cha President azikhala kuti wapeza mavoti opyolera theka la mavotiwo.
Zikuoneka ngati chipani cholamula cha DPP ndi a Mutharika sakukondwa nazo zina mwa nkhanizi.
kuganiza molakwika
LIKE FATHER LIKE SON SIMWANA WA TEMBO UYU PAJA OTATE WAKE ONKATERONSO
Achakwela timawadalila kma ayamba zawozawo i dout if from 2019 can help us
A Chakwera Timafuna Titakupatsan Vote Kom Aaaa Ndiweosokonez Ukuculutsa Kuyankhula
After all ever since this Parliament’s discussion are only on Politics not benefitting voters who cares the Raila crying group
koma bambo chakwera nangangati mukunyanya inuyo enawa apanga bwanji? kodi ndinu mtsogoleri wa anthu otsutsaa kapena onyanyala?Nanga mukonza bwanji zolakwika?Chonde khalani wachitsanzo chabwino odziwa kupilira.Munthu wamphongo sanyanyalazinthu amakhala pompo kukambilana zimatha.
Chokani mukutokota zopusa asiyen a thane akaziwana
That’s nonsense
Munyanyala zokambiranazo,ndiye mukuti tizakuvoteleni muzatinyanyaletso nafe Thawi yakeyo Aaaaaaah xatapu zanu takamvilanani Za mzulu apa
most people here are just commenting without following the news that is going on. what opposition are doing is really helpful as far as democracy is concern. how can someone be a president by having 36% of the total voters. what opposition are pushing is a 50 1%
Government promised the August House that the bill is going to be discussed in November and it is not listed to be discussed. So it seems Government is not doing what it promised the House thus why you see opposition doing like that. in summary it simply shows that Dpp is afraid of this Bill. What are they afraid of? Malawi yambani kupenya osamagona masanasana .
Foolish comments against Chakwera are as a result of not following this link, find out first y they are threatening to boycott. Umbuli kumalawi nde vuto
Mazira ake
Zonyanyalanyanyala sanayambe lero mkuluyu anayamba kunyanyala za chipembezo kuyamba za ndale pano ndi uyu wanyanyala Parliament mwina akuganiza zokayamba za mpira athera moyenda mkuluyu.
Pondani okoza zinthu osutsa kapena Olamula?
More fire Bwana Çhàkwera Tatopa kunamizidws
More fire Bwans Chakwera Ndinu amene mudzstit. ulutse mu Iguputo
More fire Bwans Chakwera Ndinu amene mudzstit. ulutse mu Iguputo
Chakwera ali ngati Times radio,sanakambepo chabwino or chimodzi cha boma la Peter Munthalika,kukacha makutu mmwamba basi
Chakwera sakusiyana ndi mphutsi yanchimbuzi, poti imangodikila munthu anyere iyo idye.Chakwera salankhula pa zabwino y?
Zamanyi!!!
Mbuli amaiti chakwera iyi??
Mxieeeee!
People are taking this as kunyanyala kopanda nako phindu and its your opinion,,zoti ndi M’busa sizikugwirizana coz Chilembwe analinso M’busa and tinamupatsaso Tsiku lomukumbukira M’busa John Chilembwe so za Ubusa muyambile 1900…
It’s not easy for others to accept and understand the necessity to change, but we need to know our country is still going under democratic process interms of governance. That’s why we need to take a serious change of our electoral process….
I feel we can develop because people will have the power and none will steal it from them Koma chifukwa cha anthu oganiza mwawo mwawo mosamvetsa kuti ndi chani do not see the substance in his boycott may be until the electoral process has passed mwina adzazindikira kuti
WE WERE NEVER DEMOCRATIC TILL 1994 when change came
Kumanyanyala kt olamula azipsa mtima?
I don’t think 50+1 olo atapanga pass ingatheke, coz zipani zikuposa number of districts in Malawi. Nd we shall be voting for second time pa zipani zomwe zizakhale pa competition that time as in kenya
100% agree with u
Ngati adanyanyala Baibulo kkkkkk
Kkkkkkk zozelezeka izi zisieni
Zitsiru kodi ovutika ndi ndani poti inu ndi ananu simulima
akanyanyala asamalandire allowance anthu menewa. … sakumapanga zomwe atumidwa ndi anthu awo…
Amalawife,mavuto tidakalinawo,chifuka chilungamochimawonekelatu koma chimaphimbidwa,chifukwa cha ndrama owinamavoti,anali chakwela,koma tawonani lelo,asusamo oweluza,aweluza akutulusa,misozi akuziwa chilungamo,kuti nchelewaana awo apezakale,ovutika ndi amalawi,ambili ndiye ngati akukana achakwela,sakulakwisa boza la achikulilewo,liwonekelebe poyela
ayambakale kunjenjemera osusa ndiemumvakuwawtu
Table 50+1 bill! Is it another that ATI? Ehhhhh! a Malawi, let us show we are civilized, ever time, things upside down, can’t learn from the recent bye-elections results, people spoke against impunity and we are not learning, hu!
Wachamba
Muzanyanyalenso pama vote kkkk uona kenya, this is politics pastor
anyanyale pali vuto
Ndiye kunyanyala kuthandiza chani? Munthu wamkulu azingonyanyala ngati mkazi, akufuna kuchulukitsa ma allowance awo
Chakwera always get 0 (zero) votes in the South so where are you going to get 50+1? You think general elections are the same as by-elections ? think again
Anyanyale koma ndalama alandire? Osanyanya ndalamazo bwanji? Makutu anu.
Kma chakwela nditcito yakedi imenei mot anthufe titakhala ambili wamaganizo ngat, WEL DONE NGULUBE aaaa ndithu zinthu zikanasinthad kma pot wannthu tilipo pangapo wamitima yosiyanasiyana ai ngakhale yesu akuuza ophuzila ake wenaso odalipo otsitsa okaikitsa ndpo mcifukwa cake akawauza kti ONE DAY… ONE OF YOU WILL BETRAY ME. so muganiza kti uleka ubusa ndie kti nditcimo pakut mulungu anakonda dziko lapas kotelo anampatsa mwanawake obwadwa ekha kti yese okukhulupilila iye akhalinao moyo osatha ndie anthunu anthufe tien tiziganiza komwe tacokela ndkimene tikupita osat umatukwana kunyoza bt was not gd at all tien tithandizane kti kod zafikapa tipangenazo motani osat umatukwana zipindula cian amalawi???
Akuona ngati ali kuchipinda, kuzolowera kunyanyalisana ndi madam ake kuchipinda kkkkk
Koma Chakwera ofunika kukamuyedzanso Ku mental hospa.Kuchoka pa nkulu otsutsa,kudzafika pa nkulu onyanyala ishiii,koma ndiye wapruva.
Vuto timathamangira ku commenter tisanawerenge nkhani yonse mpake timangotukwa zilizonse
ngati akunyanyala ndekuti aona kuti zomwe boma likupanga sizothandiza ai
Musiyeni galu ameneyo anyanyale
Bakili Muluzi, Munthu wa ulemu kwambiri, Enawa shaaaa aonjeza, munthu wosusana ndi Yehova sangapange cha nzeru koma kunyanyala basi. Mumvetsetseni, just in two weeks mutu unandikula, but now i know where Chakwera is going…..
Kupusa uku ndiye mavuto atha bwanji
#Or Munyoze Km Mulungu Akudziwa Mtsogoleri Wa 2019….# Musamangophuzura Pazinthu Zoti Sizingabweretse Kusintha Kulikonxe
Zazii osanyanyala bwanji?
Chakwela boma boma 2019
Man chakwela apandiye sakuwonetsera kuti ndimunthu wanzeru,mukamva kuti ndinu wosunsa mudzingosutsa basi.Chokani kundale mubwelere ku um’busa,ndiyambisa mpingu wanga mukhale tsogoleri.L.Banda alikuti? taphunzitseni ndale munthuyu.Sindilimbali ya muthalika koma apa wandionjenza,akuyang’ana zake tsopano.
palibe nkhan ya nzeru apa
Nanga Ndi Mtsogoleri Wanji Otere? He Must Be Very Stupid,he Will Never Rule Ths Country!!!!
Nanga Ndi Mtsogoleri Wanji Otere? He Must Be Very Stupid,he Will Never Rule Ths Country!!!!
BILUI NDIABWINO AYENELA KUNYANYALA
ngati ananyanyala za uzimu nde mukati ndale…kkkkkk.koma
anyanyale tilibe tchito. kupusa kochokera nako kwao. alibe manyaz kuyankhura publically zopusazo
Pamene palichoyipa ndikofunika kunyanyala kumene,sakulakwisa ayi
Padziko lapansi kulibe ndipo sikudzapezeka munthu wabwino,inu amene mukunyoza Dr Lazulus McCarthy Chikwera atangokupatsani udindowu Kodi mungasinthe zinthu? Kodi inuyo mumati ndinu odziwa zinthu bwanji nanga osawauza zochita Dr Lazulus Chakwera.Achewa amati,mkadakhala ine adang’amba ng’oma.
Ndiye zimene akupanga achakwerazo zimenezo, akufuna kulamula nthawi isanakwane, angawaphunzitse anthu kunyanyala? Mesa amakambilana nkumapeza mfundo zomveka bwino amanyanyala? Olo a JZU Tembo ankapanga zimenezo??
leader of opposition amayenera azikhara okura ntima kumene boma limampasa ulemu not watulo amakutora mukundaura kunyanyara kkkk mufunse malema ku south africa every day ndeu mu parliament , so ur complain wat , lack of education u guyz
Nyanyalani koma ife dzisatikhuze
Chakwera is thinking lyk a dog no a human bing uphawi alinawo ukumusowesa mtendere that’s y sazalamula Malawi coz he is a fool
Let them walk out and leave those fat allowances. If one walks out after pocketing allowances then an injunction will be served to them.
Asiyeni anyanyale! Empty tin always makes a lot of noise!!!
Abambo amenewa ankatukwana presdent kuti wanama kuti wagula ma generator,koma dzulo tamva kuti katundu wabwela.SHAME MR!
Kodi tikati opposition ndiye kumangosutsa chilichonse ngati??? Kkkkkk muwapeza Tembo akubwelekeni notes kkkkkk
Ask your former useless opposition leader #TEMBO…..!!!! APM will move so much better in your absence!!!!!!
nde kupanda nzeluko kumeneko
Kkkkkk Chakwera akupusitsika ndi masankho achibweleza aja,mwina sakudziwa kuyambila kale zachibweleza zimakomela osutsa
DPP more fire a MCP aziphya mtima, ayamba kuwopa etiii kkkkkkkk sizachilendo mkulu ameneyu adazolowela kunyanyala chopeleka mu Church.
That’s counter productive. They should stay there and map away forward. Real Men face the enemy head on!!!!
Bambo Chakwera anali presdent wa mpingo wathu koma palibe chomwe chinkayenda or chimodzi,ndiye angayendetse dziko???
Koma Lazalo Chakwela ndiomvetsa chisoni. Chikhalireni leader of opposition anatsutsapo za nzeru koma? John Tembo and old MCP anaononga chipani. You don’t entrust such kind of leadership in hands of somebody who is not a good conversationalist. Chakwela is a coward. Kunyanyala kuthandiza chani pachitukuko cha dziko lino?? Akamfunse Joyce Banda m’mene anavutikila ndi DPP ikutsutsa. Akanakhala iyeyo atanyanyala dziko kumapita kwao ndithu. Mxxiii
Akanalithawa… Kkkkkkkkkk
achakwera mukatero mumati mwachitako za zeru machende ako
Kkkkk koma zina ukanva anthuni!, nde mukufuna aMalawi azavotere osogolera anzake kunyanyalayu? Chakwera ndimawana gyz boma sangaendetse alibe nphatso yausogoleri he is lk an empty tin, he don’t know wat to do, how n when to do it. Mark my words hon. Chakwera 2019 chanu palibe mukawafutse aTembo adazichitaposo zomwe mukuoangaz. Amalawi ngochenjera koopsa, take extra care!
Sakudziwadi kuti tikumuwerenga kae,apa ndie bola kuvotera ung’onoung’ono mwina ndalama za fegi zija zizabwerelaso kkkkk
Chomwe ndidaonapo ine amalawi tilindivuto,timalephera kupanga chiganizo patokha n sitidziwa chomwe tikulankhula komaso kuzindikira komwe tikuchokera ndikomwe tikulowera.Ambiri mwa ife timangotsatira anzathu akalemba ma comment onyoza tonse timayambaso kunyoza mmalo mopeleka maganizo athu pankhaniyo ndibwino kukhala chete kapena kufusa ngat nkhaniyo sitkuimvetsa bwino kotero tithakumapeleka maganizo othandiza not kunyoza coz ngakhale timanyozana eni onyozedwa alibe nthawi yowerenga manyozedwe akowo kut mwina mkuyamikiridwa insteated tizipatsana maganizo as ayouth here in pages,Chakwera ndiotsutsa ndintchito yake kutsutsa ku parliament ngat sakugwilizananazo n sangaimbidwe mlandu komaso nkhan akunyanyalayi ndinkhan yapakanthawi kufuna kusintha ndondomeko yakayendesedwe kazisankho ndiyokomeya amalawi tonse osati chakwera yekha ayi,Ngat zinthu zidalibwino pazisankho za 2014 nanga boma likukaniranji kubweresa bill yi mparliament?Kod prezdent amamulumbilitsa usiku ndizoyenera kutero pamene lamulo limeneli tilibe?
But kunyanyala is not an option
Ofcoz koma ndimbali imodzi yot mbali ziwiriz sizikuvana,y pipo amapanga ma Demo?mesa amafuna ndondomeko yoyendesera zinthu isinthe?
Kongelesi Sizava, Nde Mumat Anasitha Awa???? Aaaa Ndakayika, Fisi Ndi Fisi
We’ll iweo ndakuvensa hvy ndiwe ozindikra. vuto ndlimenero 1st cmmnt ikakhala yonyoza the reSt amakhalaso onyoza and ikakhala yabwino the rest amakhala abwino. Chakwera kut angokhala phee muyambaxo kuyankhula kut ntchito yake ndi chan? peleken maganizo anu and chakwera SapangA chiganizo payekha amapanga ngat gulu la osusa iyeyo amangopanga repreSent ngat leadER of opposition.
Kkkkkk Gat Umazitsata Kaleso Azao Ananyanyalapo Kma Sizna Phule Kanthu Kd Iwe #Bakali, Panja Tsogoleli Otsutsa Anali Ndan???
Bakali anthuwa amangolankhuliramo opanda tanthauzo lenileni
@Nijo tiyen tisayendese dzikoli kudzera mmbiri yamakedzana dis is another generation
AISE bill iyi ndiyokomera andale osati amalawi, ndipo si amalawi anadandaula za bill imeneyi, dziwani kuti idzabweretsanso mavuto omabwereza mavoti dziko losauka ngati ili, munthu amene wawina wawina basi Maya wawina ndi modzi bola wawina tisamangotengera zilizonse
Ndiye akunyanyala chani malo mochita zithu zomveka
enawo akuchuluka mphamvu because ali pa mpando kale nde mukuganiza kuti iye atani kuti apeleke attention kwa enawo option nkunyanyalako , mumati basi azingoti ng’wee chilichonse chakwerayo? asasutsepo olo kukhonzapo polakwikapo ?
Anzao apeza njira yabwino ku Zimbabwe
Ngakhale zimaoneka zopanda phindu koma boma lavomera fundo ya chakwera
Iwenso ndiopepera bwanji ndiye ukuona ngati Chakwera Ali otsutsa.. Solution ndinyanyala?Akuluakulu mmene alili a Chakwera azikana zokambilana Nanga Ife ma supporter tipange chiani.. Tingasekerele zimenezo. Zopusa basi
anthu ena amAngopanga makan osusa apeleka bill ya 50+1 akukana koma akufuna kut. osusa azingovomera zawo et???????? its a good idea and malawi its nt a poor country bt we the citizens we are poor expt z
We need to change our electoral process and I would vote zisinthe,osati munthu aziwina ndi anthu 37 pamene 63 sakumufuna sizingabweretse chitukuko mmalawi muno,,,,
WE WERE NOT DEMOCRATIC UNTIL 1994, but has democracy really helped us?..we need to embrace the Democratic governance process and one of them is the “electoral process”
}»those in power. ndalama zomwe zikubedwa daily m’boma. zikuchoka kut ngat malawi ali osauka datz the evidence kut we are nt poor
Zimenezo zokomela iwowo andale wo ife tipindulapo chani ?
Chifundo tipindula iwe sungasiyanise zaka zambuyomu ndipano maluzi ake?
Bakali awunikilebe anthuwa azidziwa zoona zokhazokha pankhan ya dziko komaso kayendesedwe kake
Luckson kod anthuwa adayamba aganizapo kut bwanj pazisankho ma MP mcp imasogola nthaw zose koma prezidential pamavutrapo why?
Chakwera kwake nkupha,kuba ndi kuononga,ali ndi njala ya utsogoleri.Abambo amenewa azakhala leader of opposition forever
nanga mamuna amanyannyala
politics,, my foot! ever since I was a child, iv been hearing same old political songs but nothing is changing for a better,, and now m expecting grey hair to appear in my head but still more things are getting worse. Infact,, will not vote for anybody this time around. Thank God for the energy and power he gave to Malawians for they work so hard on their own and that they live at least better even though citizens produce are being robbed by these so called politicians. Mulungu sataya wake,, alinafe nganganga.
Koma chakwera ameneyu wafikapo ndithu pokwana bwanji
Mugabe amulanda samalani
Kma musamanyoze musanamve.nkhani yavuta chakwela ndi otsutsa nde mudziwe kut ngati wanyanyala zomwe iye amafuna sizikutheka. Boma la petulo mwaliiwala kod? Kut limamva zake zokha. Or ku south africa ngat sananvane D A Eff ndi ena amanyanyala kumene. Tsono chakwela akufuna kulongosola zinthu inu bas kumangonyoza. Simuziwa kut chilungamo ndi chipongwe
50 + 1 ndiya boh
Unathawa pamaso pa mulungu unathawa ku school nkhosa yosochela ,mbuli iwe usabwelese chisokonezo mudziko muno.
chakwera kutenga bonaza sizikuthandauza kt league watenga ai, so dpp still ruling
Mmmmmm musathaweyi sizonyanyalazo kkk
It’s not the best way these is a Country working together we can do more to develop our nation whereever your rulling or opposition these Country it’s for us and whereever your DPP,MCP,PP,UDf we are one with one motive to develop these our beautiful MCP becareful people are watching u
Misaladi iyi chonyanyalila nde chani
Muli blind simungaziwone
Anthu ansanje inu tiyeni uko!!;!
Ndaòna kuti anthu ambirinu simukudziwa pomwe mwaponda, muzakhumudwa.
Why?
Ulamuliro pa Malawi wavuta, lero kulonjeza ichi mawa kusintha….. Malawi wakeup
Did you guys ever thought of this only best government on earth found on DANIEL 2:44?
50plus 1 muno ndiyosatheka muli zipani zoposa 50 kale ndiye ovota azivota bwanji kkkkk mapeto ake kuzikhala zisankho zachibwereza kungoononga ndalama, Mcp yazungulira mutu ndizisankho zamakhansala zathazi mukuona kuti pa udindo wa u president mcp siingawine nde mwati mulowere ku 50plus 1 hahaha Koma ndaseka, chisankho ndi anthu,,ena amavotere Mp wa chipani chosiyana ndicha president ndekuti mukuti anthu azivota bwanji
Komatu itheka Ndipo ngatiyukubayani Ndipo ikutumbulani
Inu ndiye mbuli yambuli zonse mu evil dpp yanuyo, 50 + 1singatheke chifukwa chiyani?
kkkkk simple and straightforward bola mwamva nanga poti akunyanyala ngati kuti ayamba kale kukambirana mfundo ndatchulazi nzochepa chabe zoletsa ndizambiri, UDF, AFORD , DEPECO, MAFUNDE, FUKO, PP, DPP zonse zikung’ana pomwepo? kkkk mcp ichenjere coz iwapezetsa anthu chokamba
mbuli ndi uyo akuti muno mukhale mukhale 50+1yet akudziwa kuti muli zipani zoposa 50+1yo
Kkkkkkkkkkk
Km uyuyu amandidabwitsa kodi amazitenga ngati ndani?
NDI otsutsa tsono umati axingovomela zili xonse
Loma tikadzawavotera Anthu amenewa sadzatinyanyala?
That’s evidence that DPP is the party of Great vision,,,,, always DPP ikakhala m’boma imakumana m’mavuto,,,, this broaden the minds of the leaders.,,,, expect something great to come out after these problems,,,,, mind you, the best & suitable food 4. The brain is a problem,,,,,,! The only problem I see on chakwera is that,,, he is not tolerant,,,,, too much talkative
Keep on dreaming about your devil dpp, real Malawians are tired of this satan and mark my words 2019 is your evil dpps dooms year
To u kachikopa, will 50 + bring development to the nation? Dont b fooled by ur chakwera. Since he attained his seat in parliament, what developmental measures has he contributed so far? What ne knows is to oppose. Kumangoweweta basi, eee apresident apa alephera, iiii koma boma izi zawakanika. Tanenanitu kuti mavutowa tingathane nawo bwanji 0/10. Onse amene ali ku legislature anasankhidwa ncholinga choti athandize kutukula dziko lathu. Kunyanyala nde kulepherako. Malawians need development.
50+1 means the winner is chosen by a majority which is real democracy,, i see nothing with it,, nyanyalan a oppoztion
A. Kachikopa. Ndi a president anuwo Ndi nthawi yoti muzipanga outline zomwe mukufuna kuzachita mukazalanda boma osamangoti mfwemfwemfwe Ndi ng’ona party yanuyo,,, mwamva.,,,, chipani cha nyaucho kkkkkkkkkkkkk
50+1, a DPP mukuiwopa? vomelezani kuti mukambirane bill yosintha ndondome ya chisankho kuti mukawina zikhale zovomelezeka ndi anthu onse azipani zosusa pezani njira ina yothesera kusamva kupatula zonyanyalazo
Game a DPP yakulira..kaya asewera 90min + 5min yowonjera..mpilirawu uli 6-1..komabe MCP ikubwera wave after wave..uyu mmati ndani uyu..aah! ndayiwala ..CHAPONDA defender wangogwa..Dausi ndi KUSAYIRA midfield yavuta..kutsogolo nako kwabutha wochinya uyu..pitala waleka kale kale kutimwetsa wamkaka..MCP yangubweretsa timaplaye tachisodzera kutsogolo kuli waluso wodziwa kukhethemula njomba paja mmati ndani kodi chakwera..ee abale ..ATUPELE MULUZI WANGO CHINYITSA ALI PHEE!.achina ulemu,sosten,mia ndi sitolo ayivinitsa gule wakazukuta dpp..it never rains but it pours..kuno ku malawi zithu zavuta..kumagona mudima kutabwera alendo..
Chakwera wati anyanyala zokambirana. Si otsutsa onse angavomere mbwererazi
Msogoleri wa anthu sakhala onyanyalanyala ngati mwana bolanso a Tembo omweajatu
Those who are ignarant cant understand because evil dpp has influenced their mind, Chakwera is for real Malawians not cowards who are corrupt and evil supporying the failed dull professor
Kungoti president timasintha koma maudindo ena onse anthu ake ndi okhokhawo okuba
Chakwera sakulakwisa pamenepa.
Msogolo sakhala onyanyalanyala ngati mwana bolanso a Tembo omweajatu.
Or Mutanyoza Bwanji A Chakwera Kma Dziwan Mukungotaya Nthawi Coz 2019 Akulowa Basi
Adzalowa bwanji poti amakonda zonyanyala awa! Adzanyanyalanso tikamadzavota.
kumeneko ndikunama choncho nkhalani phee kt mudzaone
Lidangokhala khalidwe lanu lonyoza azanu enanu ngakhale sadalakwe.
Why walkout? Hw wl u say wht u thnk is right? Its tym u ppl grw up n build ths country, dnt b childish. Ur job is nt jst to oppose bt gv positive inputs for betterment of Malawi. If u nt careful u wont win
Well said Mr Maposa?……
Achitabwino,asiyeni abale any akambilane okha okha
Chisilu Niamene Akavotele Dpp Ineyo Nimapeleka Nsonkho Wokwana K5000 Pamwezi Koma Mwana MWana Wanga Akadwala Mankwala Sapezeka Kuchipatala Chaboma Msonkho Wangawo Ukulowa Muchithumba Cha MUTHALIKA CHILIMA CHAPONDA KASAILA DAUSI KALIYATI NI Nduna Nzonse ZA PETULO Wanuyo
Anyanyale zawo izo
chakwera akufunika ku zomba mental coz salibho just like zakeuja
chakwera zokodzera zako wava ife daily tizivera iwe
Ohh!!! if Mr Chakwera is showing this character with 5-1 how about if he wins? we will be in hot soop I tell u pple. True that a lion bares a lion.
A chakwela ndimunthu omvesa chisoni kwambili maka potengela kuti ndimunthu yemwe saziwa chomwe ali ndip samamakhulupililabe mpaka pano kuti akulamulila mcp
He must be vry unwise thats being selfish
KKKKKK ACHAKWELA ETI.OKY.zukufunika akatenge zelu kwa tembo awa.kmaso muwauze kut DPP ndiyovuta kuigwesa pa pepala.asadeweze
Inagwetsedwa bwanji pa 17 October paja? Umbuliwu ukuvutani ndi evil dpp yanuyo, real Malawians are for Chakwera and mumva kuwawa simunati, ngati ndi mabanzi a cashgate akusokonezani mutu ndiye munsanza because real Malawians akumva kuwawa muulamulilo wa your evil satanic dpp
Hope chakwera akazawina zithu ndikuyamba kusalongosoka azakhalaso evil satanic mcp reader coz palibe amakhala president osapezeka kumalo kumenekuja kumachitika evil kuja ndie say watever makes u fil gud binniwell kachikopa
This is one of the reason that will make me not voting 2019,i dont see the difference neither the benefits of voting.Am still sleeping on a mat,going to bed with empty stomach,on the same thatched house.Drinking dirty water no hope for the poor.
Blessed are those pple ,selected by God that they wont participate on the deriberations of parliament procedings but at the end of a day they will pocket huge allowances,receiving full salaries haaaaa Dziko is not for the poor indeed but the reach.
Sell you phone and buy a bed. Food and a place to sleep are basic things you need not facebook.
Wabodza ameneyu chimanga k5000 ndye aziti sakudya ha ha ha wasowa mfundo ameneyu ukufuna zonsezo zingobwera ngt mana ha ha ha ha ha
you dont know what you are talking about,if you hv bread and butter on your table dont think the rest hv it.Go round on your villeges see how pple are struggling with life my dear friends.
che lomoliwa wanuwunso ndi ulesi!. tin lachimanga 20litres ndi mk1500
guys, be serious. Enanu mukayenda nkuchoka kunyumba kwanu, wa ku office kapena ku business zanu. I am not speaking about myself here, but for the people in the areas you dont even wish to work in. there is real poverty in this country not that you see on the streets of fake beggars. people are living with absolutely nothing to call food, shelter or clothing. have some time and go to the remortest part of the city you live in. its not that they are lazy. they have land to cultivate, and they do. but with no fertilizer. they manage to harvest little and try to sell some for other needs. what do you people do? you send your goons in the name of buyers and rob them of their produce through buying at the cheapest prices possible. when they have nothing left to sell, or to eat, you start calling them lazy and ignorant. do you see such people getting better someday? what could be the reason for such people to vote, when all they get is this poverty? all in the name of politics.
Thanks mr Botha,these pple hv never been in such state thats why they are speaking like this.if the tin of maize is as cheap as per wat u hv said do u think one could roast it and eat everyday?Lord hv mercy on u pple.
Another Wandale, needs some mental test
Koma chakwera mwina simudziwa kusutsa kwake nkopanda nzeru with no benefit becauz tikati kusutsa sitidati kunyoza ayi! komanso wosama demander zinthu zoti munthu ukuziwa kuti MW lero ndirero singapange ayi! kuwolokera ntchito ya anthu chakwera akukhala ngati wa ACB/ wa Police who is he it means udindo wake sakuwudziwa kodi ku Mcp ko kulibe wina wanzeru? awatu akufuna tiwone kuperewera nzeru kwawo asanakhale mtsogoleri! miseche too much that guy!
Dpp sorry!! Truth Pains
And look at you! Amati kusutsa? You are ignorant and evil as your dpp and dull professor
U have spoken well, u said Chakwera is like ACB or Police, that means he is the true son of Malawi. He knows that Malawians r in trouble with the big tareted idiot APM
Yes whether u like or not but our opposition in Malawi is a foolish! cauz he don’t know his responsbility! akakhala mavuto/umphawi ndiwakale ku Malawi ask ur grandparents! we keep on blame Mutharika no! ndi tulo tanuto khalani choncho but 4 those who knows the trueth chakwera ndiwopusabe!
Achita bwino, theirs noway mumwenye adzinkhala ndi mphavu kuposa eni ake adziko. Zoona aziti vutitsa amwenye.
A MCP asananyanyale awerengenso chigamulo cha mulandu Wa Press Trust Reconstruction Bill
Ambirinu munali muli ana kapenanso musanabadwe.
Zingowonetseratu kuti Chakwera nzeru zake ndi zochepa, chifukwa iye yemweyu akumakhala ngati akufuna kunthandiza dziko. Koma nanga izi ndi chiyaninso, ngati mutayambe kunyanyala chimene chiwapindulire anthu ndichiyani? Nthawi ija mulikunja musanakalowe ku paliamentko, mumalankhula ngati wanzeru anthu amakudalirani kuti awa atinthandiza koma nanga izi ndichiyaninso? Malo moliwuza boma kuti mwalephera kunthandiza wanthu, ndiye apa mukuliwuza dziko kuti mukufuna kunyanyala kungowonetseratu kuti nzeru mulibe. Ngakhale, 2019 kuzakuvoterani nanunso anthu azakhala kulira basi. Ndiyensotu munyanyale malawasiwo, musangonyanyala zokambilanazokhazo.
Wanzelu zochepa ndi imwe sakuyatsa magetsi osati kukambilana zapakamwa inu munyozepo apa takambani za blackout apa ndi wanzelu wanuyo
A Jafaliii! Ochepa nzeru ndi Atupele ndi dull professor wanuyu, Chakwera is for real Malawians amene tikumva kupweteka ndi umbuli wa evil dpp yanuyo. Mark my words, come 2019 real Malawians are for Chakwera no matter what and mumva kuwawa simunati because truth pains and always prevail
Iye ndi otsutsa tsono ngati sakumvan nde mumati atani mumafuna mpaka amenyane. Chakwela sakulakwa or ku rsa ngati sakugwilizana munyumba ya malamulo otsutsa amanyanyala kuzolowela kulankhula ngat ndinu ochenjela pomwe muli odontha ngat petulo hiya
Ndiye ukhaula nayetu, chifukwa iye ndiye akulamula mpaka 2019 ukachitanso masewera ndi Bomanso mpaka 2024. Iweyonso kukamuvotera kawiri, wakuuzatu kuti sanakalambe adakali mnyamata chita masewera akowo ulira naye ameneyo. Umadziwanso munthu akakhala pampando umenewo, kumuchotsa simasewera ayi ameneyo amalizadi ma period ake onse Chakwera wakoyo akulira. Umufunse J.Z. Tembo, anaulilira mpando umenewo tsitsi loyera lisanayambe mutu mpaka lathamo tsitsi m’mutu akuulakalaka. Iwe amenenso mawa lomweli, utembenuka uyamba kumusapotanso Peter.
Achakwera kunyanyala si nkhani even nthawi imene adali mwana amalonda kunyanyala nsima akayambana ndi munthu. Mchifukwa adanyanyalanso ubusa mkulowa ndale. Mutu mwawo nthawi zambiri suyenda bwino.
You will never go anywhere ndi nthano zanuzo, Chakwera is real and doing it for real Malawians not cashgated people like you dpp evils
Amene amasapota chakwera chimodzi modzi kusatira munthu wakufa.koma inu taganizani muluzi adanena kale kuti masiku ano uzipita kusogolo osati mbuyo ayi . Kupeza munthu wankulu Ali kwachaaaaa kwachaaaaa kwachera amako?
????
KKKKKKKKKKKKKKKKKKKKK
Childish!!!
Abusa tsopanokkkkkkkk manyazi bwa
My vote is for chakwera,i was a strong member of Dpp but since 2015 i joined malawi congres Party
Ntumbuka opanda nzeru unakhalako liti wa dpp iwe ndi wa pp
dpp ili nfi eni wake osateketseka ngakhale ku opposition amakhala nayobe ndie uti chani galu iwe?
Kkkkk
Ahebri 10vs31 kugwa manja mwa Mulungu wamoyo kowopsa chakwera wantha ntchito ya Mulungu.
Umbuli wanuwo musamanamizire Bible quoting, Chakwera is real and backward never forward ever, inu tapitilizani ndi dull professor wanuyo tikuwonerani mmene zikuthereni because Chakwera is for real Malawians
Tizangoona akazawina chakwera 2019 kuti Mulungu anamuitanira ku utsogoleri wa dzikodi kumchotsa ku utsogoleri wauzimu that wil be seen in 2019 when he wins ??
Ndi chisiru umuuze kkkk
Akufana azabweletse mankhadi galu ameneyi etii.
Inu nde atinso mumakhala kuti khadi yabwela kale inu monga simukudziwa zomvetsa chisoni ndithu kuti mbuli zilipo zambili ndaonela awa
bola macard kusiyana ndi misonkho pachilichonse tikugulacho, umbuli wanuwo ukupweteketsani because Chakwera is for real Malawians not evil dpp and your dull professor
Ndipo anyanyale kumene dpp ipse mtima
anthu ena kudana nd chinthu chabwino bravo Chakwera!
Bro udont talk rubbish to big ppo like this they will block your account n u r too young for politics leave them
Thats a non starter, your thinking is below par and directionless
Kkkkk zoblockernaso kkkkk
Kkkkkkk,kachikopa ndimwana wachakwera kodi kkkkkk
To big people my foot….
ambiri ndinu mburi zophunzira ,sichakwera amene adauza amalawi eni Dziko kuti mu November abweretsa zankhaniyi.pano Ka 6 – o, mwadwala nako.anthu amene mumakana zipani zambiri ndinu mukutukwana chakwera.kodi pitalayo mumamutenga ngati Mwana wa mulungu,siyani kuopa kavalo wanu amalawi.
tikukwezerani malipilo pantchito yanu yonyanyala ife tidazolowera
Kodi zachitika ku kenya sadazimvee
they are bunch of losers come 2019 kudzavotera dpp kuti mcp idzapyse mtima zenizeni
Hiiiiii mukuchedwa kuvotela usiku 48hrs
Akhaula achakwera anathawa mpingo ndale azivaso kuwawa sanati wangwanayo
Chakwera is not dull as your evil dull professor who even fail to understand the basics of the economy
Zonyanyalazo! Sign yopepera!
Malipilo osapasa akanyanyala zamalawasi
Zawooo zimenezo aaa
wth tht headline mungofuna anthu atinyozere chakwera wathuo apa
50+1 ikufunika kumene.. thy hav to force the govt iwo akuopa chan
Zipani zopikisana ndiye mpaka 112 ndiye wina nkumati 50+1
Zipani zikuoneka ndi ziwili bwana
Kodi alomwe akuwopa chiyani ndi Billyi?
zipani 12 mukuwerengera ndi tizipan ta briefcase. ?
@ Phiri.. eti eti… akudzikaikira 50+1 sangaione
Chakwera Kunyanyala Popanda Any Reason Kod Uli Nafe Limodzi Kapena Ungova Kt Kuli DPP Uli Vwiiiiiiii
komatu chakwela ngati ili misala ndiye avula ndithu kunali tu Tohn Ungapake Tembo akuti S 65 No 1 and Budget no 2 tiyeni kutabwela chisankho zomwe zinachitika ndikhulupila wina aliyense adaona zomwe amalawi adachita ndipo anayankhula osati pa fb koma pa movoti tiyeni tizingoyangana kuti zitha bwa
man pac is meeting the same issue, vuto ku dpp there is full of mafias pls take note, may be you are one of cashgators
mmmmmm iwe Gama ingokhala chete ku mcp ndiye kulibe mafias ukunenao Pac yakenso ndiye iti ukunenayo yomwe inaxaza ndi mcp yo umaona ngati ife sitimaziwa
Mumva kuwawa zenizeni Chakera is real and for real Malawians not your dull professor who even fails to understand the basic economy and fails in everything, truth pains and mulira simunati. Tikufuna chilungamo osati macashgate anuwo, go yo hell with your evil fail dpp and dull professor
Kkkk koma binniwell kachikopa akuoneka kuti chakwera akazawina 2019 azampatsa udindo ndithu.UDF boma !!
M’bale raymond ngat ulibe coment pepa ingokhala ukupangacho ndichibwana,ukushosha mitundu yolakwika.
DPP has been in that shoes during JZU era but nothing worked.Kunyanyala?
50+1 angafike?zonyanyala amufunse Tembo zomwe anaona
Palibe munthu amanyanyala popanda chodabwitsa. chitsiru chidaimba n’goma ochenjera nabvina.
mkukhala kwao awa, ali kuubusa ankakondanso kunyanyala nthawi zonse amanyanyala mzosadabwisa mkhalidwe lao kuwasogolela ana kuti aziziwa kunyanyala ndiye abusa amvula za zino ameneo
Kkkk ndizofunika mesandiotsutsa.
Chakwera need some psychatric check ups….
50+1 yikufunikilaɗi…angopeza solution yina rather than kunyanyala…i personally woulɗ like to see that ɓill pass!president asamalowe ku state house with 38% of the votes…at least he has to go into office with majority votes..of 50 +1
But majority always win even if it is 10% achakwela adakakhala kuti nawo ali m’boma sanakalola bill imeneyi kuti ikambidwe
Kodi ndi ndani yemwe anapezako 50% napanda kulowa m boma? Yemwe wapeza ma vote ambiri wa winer basi. Lamuloli likhaleso la ma mp
zipani ndizambiri muno ndi 50+1 ndiyosatheka opanga zimenezo ndima states omwe amankhala ndi zipani ziwiri basi
moti 50 plus 1 izapangisa malawi kulemera ngati america
kkkkkkk simon
Mot Ife, A Umodz Party Mukut Tithese Chipan Chanthu Kt Tizamuvotele #Lazalo, Aaaaa Ife M Y P Toto
Olo munyanyale inu ndi anthu opanda phindu zisiru
Nyanyalani malipilo anuwo apite kumagetsi kutsutsa ko poila kumeneko
ndiye choncho akazawinamo anthu akazayamba kumunyoza, kumugemula azatinyanyalansotu uyu ,zamugundika chakwela vuto anthunu mwamukweza muntengo wa papaya that’s why akuzimva kwambir komanso akuchita Boh kut khalidwe lo tizilionelatu
Sikoyamba kunyanyala. Adanyanyala nkhosa ku nyumba ya Yehova
Enanu ndi agong’oli simungamvetse what Chakewera wants, its good for Malawi democracy and only fools cant understand that
Tell them, ndi mbuli za anthu
Mamuna weniweni sanyanyala
Kunyanyala Ngat mkazi ????
Osati mtengo wa tsabola kapena wa tomato?
Kachikopa fool ndiiweyo,ngati ulipambuyo pachakwera usaganize kuti nditonse,choti udxiwe nkhani imene akunyanyalirayo njokhudza andale 50+ siikutikhudza pamene budget yo njatonse amalawi ndiye sitingasekelere zofoirazo kt wina akwaniritse zokhumba zake
Ndagwirizana nawe m’bale Chiluzi
Zomalumbiritsa President ku court usiku i think sichinthu choenera, Ndidalimva boma la dpp kt bill imeney aikambirana november, so hw cme kt alephere kuibweretsa? tinene kt amalawife timakondwera zinthu zizichitika mosaenera? kulira kwa malemu mbendera kunadabwitsa amalawi ochuluka kulumbiritsa usiku presdnt ku court nd chimene amalawi tinadabwa nacho,so to end this nonsese abweretse 50+1 ku parliament simple.
Which budget Chipiliro Chiluzi? And is budget an excuse to ran away from important bills like electoral reform? Or you even dont know what that electoral reform is? Arguing or debating for the sake of debating or because you benefitted from cashgate will never defeat the truth. Most Malawians are at pains today because of poor decision making of your evil dpp and its corrupt leaders. We need a president chosen on the basis of 50 +1 not 36%, 50 + 1 or any political process affects everyone whether wandale or not. Dpp has very selfish leaders, highly corrupt, egocentric and nepotistic, people are tired of it and real Malawians cannot go for this your dpp, mark my words come 2019, dpp will be booted out. Tikudziwa kuti mulimbalimba but where truth stands it always prevail. How can you improve macroeconomic conditions without improving micro economic condition? Your failed leader Mutharikas recent speech was rising above macroeconomic stability yet our microeconomic situation is down? Those that have subjective poverty like you chipiliro chiluzi and your fail clueless and directionless dpp cadets cant see the sense in Chakwera points, reread Chakweras speech and compare it with you failed leader speech. TRUTH ALWAYS PREVAIL, LOVE OR HATE IT
Ireen koma muja inalili nkhani yachimanga lero akhale oipa ndi Malunga?Even me,I support Malunga ndipo adagwira ntchito mokonda dziko lino
Zoonadi Akachikopa,mabill omwe adasiidwao ndiofunikiraxo kwambiri pofuna kukoza malawi wabwino,ACHAKWERA akunyanyala pofunika kunyanyalidwa,mabill enawo akawaikapo pandandandawo otsutsa abwereraso mnyumbai.
I reen , Malawi is in a democratic transitional process and I see we can do better kuti zikomele aliyense pa Malawi pano….kunyanyala kwa munthu uyu nkofuna chilungamo cha a Malawi chiziwoneka osati mokuba.
Kaya anyanyala kaya atani inuyo mayi ndinu nzika ya dziko lino and zamalamulo mukuyenera muzidziwe let change come as it came in 1994 not focusing on a simple gesture yonyanyala yet mukukanika kuwona reason behind the movement
By the way it’s not kunyanyala but movement
Mumuuse chakwerayo kuti machende ake.
Pa udindo wake palibe chikuoneka kuzintha. Amene akakwanitsa kusuza ndi tembo yemwe uja basi.
Amene uja amaimiladi anthu ovutika.
Osati za lerozi.
Mzuru ndi mzeru panyini bas??
nothing to gain hope chakwera z not reading ur foul words from ur stinking mouth respect urslf u cardet
Sorry am not career me,!!!
Ndipo ngati paling chindu chimene chimandinyaza ndie ndidpp.
ok koma kutukwana sikwabwino pagulu umangoonetsapo umbuli chabe pliz pliz dont repeat such mistake
dont forget during hn Tembo kunaliso section 65 and budget
A uzufu apatu mwatukwana bambo anu ife olo patavuta chota muthu wamkulunsikhu sitimunyoza ayi sibwino inu okhala amuna mwazivulatu apa
Koma chakwera guyz mwina simukudziwa kutsutsa kwake nkopanda nzeru ndi kwa no benefit a Malawi sitikufuna kutsatsa kwa mapokoso/ konyoza kodi a Tembo ankatero? sikuti muziswa malamulo iyemweyo wotsutsa koma akugwira ntchito ngati wa ACB/ wa Police who is he chakwera?
zotukwanazi si mfundo.
kungoonetsapo umbuli basi kumatukwana pa gulu ngt pano kumankhala ndimanyaz
Yusuf ndi mwitha tafotokozani chimene watsutsa pamenepa inuyo mukuti amamgokhalira kutsutsa ndipo zimatheka bwanji kuti chakachilichose bajati yaboma amayiveza mnyumba yamalamulo ndipo sindingavepo kuti ayikana.
Ndizimene ndikunenanzo mbuzi iyiyi ilibe phindu lililotse.
Ingobwerera mkachizi.
Ndipo ndie imandinyaza koopsa.
Ndine mwamuna koma. Ndikuti mundiuzire kwaiyeyo chakwerayo kt mapazi ake ..
Kumalawi kwachuluka mitembo. Wamoyo ndi peter ekha.
Osuza maliro.
Mzika zap mzikomo.
Maliro.
Yonse mitembo yokha yokha.
Mchifukwa chake kumalawi utsogoleri akamalamulira munthu wakwa amereca amapanga zoti ine ndiobwera.
Ndipange business yi
Ndikhapindura ndizipita.
Kwathu.
Machende anu.
Maforena nonse including chakwera.
Chinziru chamunthu.
Mbuzi eni eni.
Kwanu ndikuti chakwera iwe mapwara akho
kkkkkkk koma yaaa kumalawi kumeneko! ndye wabwino ndan? mwati olamula mbuzi zamapwala kukamwa otsutsa anamachende? mmmm apa ndiye che yusufu akalipadi ok zikavuta zedi ingosamukan mumulondole jb
Ai abraz panopa sndili ku mw
Ku comment bhobho kunaveka osawonjezelaso kutukwana apo sunachite bho.awe awe skeem saam
Watch your mouth braz…….kunena kwa ndithe nditheku………..watch out
ati kuona ngati ayakhula dza nzeru chifukwa atukwana mmmmmm
kusonyeza kupepera kumangowasiya awa ana otembereledwa
Ngati mukufuna zoyambana ndie tiyeni.
Cd chakwera or peter si ambuye anu mwamva agulugunyinda inu.
Sizakuwaweni ngati kt ndakukwana abambo anu machende anu nonse
mukulimbana ndiine.
Ngati mukuona kulakwika osandipeza ku in box bwa. ???
Kubadwa mopuza eti.
Ndilibe chipani ine ndipo sindisazapota chipani mpaka kutsogoloku.
Kwathu ndiku mocambique.
Ndimangomva chisoni ndiubulutu umene uli kumalawi.
kungogwira kaganyu ndikupita ku shop kukagura ka fn ka itel mwati muxipereka malangizo pa Fb kuoneza kuzindikira???
pa mtumbo panu.
muziona ndi anthu ake.
osati ine.
muli ndichani agulugunyinda inu.
kuchipanda zipani za mcp,udf,pp,dpp,bwenzi muli ndani??
ana opuza.
kulowa mnyumba mwanu kupeza ma ticheti azipani zonse.
mcp,udf,pp,dpp.
atidye nao.
opanda chipani cheni cheni.
mbuzi zawandu.
kumutukwana chakwera mukakhuzidwe??
nanga munakandiona ndi maso ndie munakandipanga zotani???
ngati mukusowa mtendere apapa.
anthu odya zachipani samasowai.
Yusuf idont doubt you are coming from vitsilu family and including your grandparents. Komaso nukhulupira kuti ndiwe mwana wa mchigololo.
kod kamachende iwe vuto lako ndichani???
Kuganiza mopepela,zomwe mugwilizane pazokambilanapo ndizothandiza olamula okha??,Ochakwera mukufuna kulamula zikoli koma??.Mukamamva kuti kulozedwa ndiye kumeneku.Pitilizani tione mapeto ake.
MBUZI YAMUNTHU, ANTHU ANAZOWELA KUNYANYALA MKUTE ALI ANG’ONO NDICHOMCHO. POMWE ANAKUSANKHANI NDI ANTHU IWE UKAMUNYANYALE MUNTHUWOTI AKULANDILA NDALAMA MWENZI NDI MWENZI POMWE MMALO MOKAMBILANA ZAKUPYA KUTI DZIKO LIYENDE BWINO.
Ine chiyambireni sndinaone pindu lililonse pazokambirana kopoza kupsa mtima ndimanyi aku paliyament
Akanyanyala akuyenera kukabweza ndalama zomwe atenga ngati ma allowances opezekela Ku Parliament pa session imeneyi.Konzani zinthu osati kunyanyalako
Mbuzi ndinu bambo mukukanika kuzindikira ndikuvomereza chilungamo
BINWELL, MBUZI NDI MUNTHU AMENE ANASIYA KUTUMIKILA MULUNGU KUTHAMANGILA NDALE IWE SIUKUONAWEKHA KUTI CHAKWELA ANAPANGA UMBULI KWAMBILI??? YESU SANALOLEZE MUNTHU WA MULUNGU KUTENGA NAWO GAWO KU ZANDALE ZANDALE ZILI MUGULU LA KAISALA. NDICHIFUKWA CHACHE AMANGONYANYA ZILIZOSE. KUNYANYALA KOKHAKO KUMAWONO NGETSA CHUMA CHAMBILI M’BOMA KOMASO KWAPHELA UFULU ANTHU ZIKA ZA DZIKO. PAMAKHALA ZINTHU ZAMBILI ZOMWE ZIMAWONONGEKA M’DZIKO CHIFUKWA CHA WANDALE WOTSUTSA KUTSUTSA KOPUSA KOZUNZITSA WANTHU MZIKA ZA DZIKO. ANGAKHALE IYE ATATENGA DZIKO PADZAKHALASO OTSUTSA WENA AMENESO TCHITO YAWO NDIKULIKOKELA BOMA M’MBUYO UKU KUMAKHALA KUBWEZELA CHITUKUKO CHADZIKO M’MBUYO.
Kd nde akt anyanyala chifukwa chan
Amenewa kunyanyala ngati ana zowona koma ktiseweretsa uku
Trade carefully guys otherwise someone most might use it to decampaign you.
Chakwela wayamba kuzimva ndi ka 5-1 komweka kuona ngat bas 2019 m’boma kkkkk
Kkkkkkkkkk inu mumapitilakonji?Ana opusa.
Ok s fne
who cares? That idiot is really irritating. That’s a sign of a loser. He will not make it. i domt want any reply but let me air oit my views…. MCP;Chewa people m tumbuka people are the ones behind our poverty.
Me too i dont want to call you a fool…
Me too i dont want to call you a fool…
Nanu Inu
Misala iposela apa
dont attack achewa or mtumbuka,ur peter hve failed to be honest.how far hve gone wit ur education umbuli basi,cant see dat malawi is in a crisis.
Ndopengadi akuluwa akusankha mitundu
who is talking aboit peter here? some people dont reason
man pls dont point achewa and atumbuka, kodi maize-gate ndi achewa?, blue night-gate ndi achewa or atumbuka?, ESCOM generator-gate ndi achewa or atumbuka?, 577 billion cash-gate ndi achewa or atumbuka? pls think before you post yr comment
machende alhomwe
Koma Mbuli Iyi Ngat Ayituma A Dpp Bwanj
tigawanepo dzikoli alomwe ndinu atsankhu.chigawo chakumwela mukhale komweko ndi vin wandale ife atumbuka ndi achewa tikhaleso patokha period
lets fight for federation alomwe mwatikwana tiwone ngat mungalimbe ndikumwera kwanuko
nkhan ndi umbuli ndi ulesi amaganiza ngt Pitalayo Adziwapatsa Ndalama Pa Manja Make Lomwez
Eeeee koma alomwe mukanasithako moyo osankhanawu
Simunati muyithawa nokha
You are one of the useless people among your very evil dpp
Ife kumwera kwanuko sitikufuna,mukamalakhula mwamwano tigawanapo tiwone komwe mukagulitse thochi zanuzo, mbuzi!
ada usamale,tidatopa kalekale ife, tingokuika mchigayo ife
A lhomwe ndiye kuti chani mungopanga matukutuku ngati muli ndi polima nd pomanga bwanji? mwangozazana mma estate aazungu
Alomwe ndi mbuzi za anthu, olo zipite ku school umbuli sukutha mchifukwa akupopana magazi. Asiyeni athana okha
I even dont get the whole issue here. Why calling names the lomwe people? I dont know why you are doing that…. But you must change. Am not a lomwe or whatever you may think.
Panyapako kumwera mukuipisa mbiri ya malawi umbuli basi ngati pali chigawo chosauka chomwe kuli UMPHAWI wazaoneni ndikumwerako
okie.. but why are you angry as if i have said something bad? am not angry. But you can’t compare BTZ n Mzuzu.
Kumwera kwa mbuli mwati???? Inu nonse opusa mmaganizzo eti??? Kumwera ndiko mumalilira agalu inu kulimbikira sukulu kuti muzaponde dothi la kumwera. Komwe kumachoka olamula dziko ndiye kumwerako, 2019 alowanso wa kumwera kuno. Ukawerenge wamva Kamuzu adanena kale.
Iweo u need to admit that wayankhula zopusa, its not an issue of pointing finger to tribals here. Ukati achewa ndi atumbuka ndiomwe akuyambitsa umphawi ndekuti ndi mtundu wanji omwe ukupanga zolongosoka?? Sonetimes kumayankhula ngati mzimu ulinawo.
Raymond G Chimbalah, your language seems you are a useless fella who is debating based on your cowardice, staying or being from south doesnt mean you are superior and if the country can be shared the southern region can be in great problems because even illiteracy level is very high in your south, we booted out old MCP because of such cowardice and nepotistic thinking. So the best thing if you dont have facts is just to shutup than making your nepotistic, tribalistic and regionalist silly comments
One day people will eat me.Why all this. I just jolted something sensible but hatera are hating.
kungonyanyala basi?plz admin muzika nkhan yonse si nanga enafe tili pa free data
Eya d kaa….
hahahaaa nanga pot ife tawerenga nkhani yonse apa
Ndr kutsutsako or ku RSA otsutsa amanyanyala akapanda kumvana
Achita bwino