From 2018, not even cyclists will be using the roads for free.
In Dowa, the district Council has disclosed that it intends to introduce parking fees for bicycle taxis (Kabaza) in a bid to improve revenue collections for the council’s service delivery.
The council’s new directive will see those involved in Kabaza business at Mponela, Nambuma and Lumbadzi trading centres of the district being licenced.
The Dowa District Council organised a learning tour of the joint Finance and Human Resource Service committees to the Blantyre District Council with a rationale of appreciating and learn how Blantyre District Council has managed to overturn deficit into a billion kwacha surplus over the past 5 years.
Speaking in an interview with Malawi24, the joint Finance and Human Resource Service committees chairperson Councillor Simeon Nyemba said the Blantyre success stories have led the Dowa District Council to come up with recommendations such as the use of targets and incentives in revenue collection in markets, signing of agreements with billboards owners, to ensure proper follow up on all site rentals and the development and operationalization of a revenue and enhancement strategic plan beside filling up the vacant posts in the Directorate of Finance.
Nyemba told Malawi24 that the other innovative ideas include sending revenue collectors on holiday to set new targets, no revenue collector to handle cash for business licences and the use of intact banking by all vendors in handling cash deposits for all business licences.
“The council will strive to see to it that all business licences are to be signed by the District Commissioner and Chief Accountant to avoid other people developing their own systems of gaining money by false pretence,” he said.
The councillor said business licences will only be produced on approval from the office of the Director of Finance to curb any arising malpractices saying the approach has resulted in growth of revenue from Mk40 million, 5 years ago to Mk397 million in the 2016/17 financial year for Blantyre District Council.
He expressed hope that if they fully adopt the success stories of Blantyre, the Dowa District Council’s service deliveries will no longer be the same as of today.
In 2015/16 Financial year Dowa District Council was the highest in revenue collections among councils.
Thanks to Dr.momoh who saved and cured me from hepatitis B.. virus. with his herb medicine you can also reached him for similar
*Or any other….virus…like.. Hepatitis…..C… Virus….
You can reach him through this number…you can add him on WhatsApp believe me you will never regret it
+2349068579672
Your cure is here for you !!!
Kkkkkkkk malawi
Ameneyu ndi mbuzi ndi boma lakeli, kodi mwati munthu ameneyu ndi m’malawi? Koma ine ndakaika mwina mkutheka ndi waku Zimbabwe. Akabazawo sikuti mkufuna kuti adzinyamula anthu koma chochita chikuwasowa. Kapena mukufuna adzikuberani? Apatseni chochita chomwe angapange kuti chidziwapatsa ndalama zothandizira ma banja awo pa moyo wa tsiku ndi tsiku. Kapena adzikaotcha makala? Mudzawalandanso mukuti akuononga chilengedwe. Kapena adziphika Thobwa mkumagulitsa? Agule ndani Thobwa lotentha poti magetsi chizimireni sabata yathaaa. Tizunzeni koma dziwani kuti kufuula kwa nkhalamba yomwe siili pantchito komanso madandaulo aanthu mtheradi mudzapita ngati m’bale wanu uja……….
Bola la Pitala limenelo, Munthuyu ndi mbuzi ya munthu. M’mene kumawawira kupalasa njinga
Ku Malawi kuli vuto, kaya ndi kusadziwa kaya,muona 2019 akumuvoteranso,kaya vuto ndichiyani kaya
Aaaaaaaa xweeeee kma inu mbuzi etiiiii AAA kma
Ban kabaza,ngolo in the cities why we don’t have city standards?
propaganda at its best
kenako oheda matumbaso timva kut akufunika ma licence kkkkk koma boma ili.kundichitisa dzakaka mate nde
Eeeeehh….. this is so sad.
stupid
Stupidity on it’s best
Kkkkk
Mukudziwa inu tidati voterani ife zaukapolo izi bwezi kulibe
I wish we had another malawi somewhere!
This spirit of stealing now is walking barefooted in malawi. Malawi government please we didnt want to be poor but the spirit of poverty dont wantvto release us. Its pity kuti evrn government nowcisctrying to help this spirit of poverty to attack us
NDANI PAKUPELEKA MAGANI OPUSA NGATI AWO AMALAWI AKUCHITA IZI NDIUPHAWI GO TO Hall THIS GOVERNMENT
Dpp natural deaths
It will be reversed anyway
Koma nde kuzisaka, kenako tizilipiraso misewu yathu yafumbi yomwe popita muliyenda…
koma malawi iiiiiii
zoputsa bas
Kkkkk pachema apaaa
This is sad,these people are trying to make a living instead of being thieves,thugs ,and really the gorvment wants them to pay?? And cycling wt extra weight it’s no easy,this isn’t fair
That’s totally wrong I think the government is mad!!
ufiti ulipodi sure and kutamba masana.guyz mmene amavutikira wakabaza muziberanxo? do u.know hw much they get per day?enanxo njinga sizawo amagwira ngt ntchito.mmmmmm whr z Malawi heading to now? eishhhhhhh God hv mercy.
Apa ndemwaziphelatu aDPP 2019
Hahahahaha fack de government
Kkkkkkk koma boma la alomweli ndiye lafika penapake uyu akufa ngat mkulu wake
kkkkkkk koma ziko ili gyz kenaka tivaso kut gule wamkulu
Asaaaa, kod cashgate siikukukwanan
Paying taxes wen using these pot hole roads
You Cruz you don’t known what to do
awakonzera malo oti azipanga park? if so its okay.
Koma dziko ili likhala apolisi a pamseu, you won’t to collect every thing. Ngakhale woyenda pansi akama lowa mtauni azilipira entry fee. Eeeeeee. Za chamba kulemeletsa apolisi .Asilikali ndi alonda a G4S akusaukilabe. Zaziiii.
Kenako tidzamva kuti onse oyenda pansi ayamba kulipira msonkho,known doubt about that
mmmmm koma gayez njinga tikanike kukwera mpaka lincence koma yah
Kukama mkaka yowonda kale kkkkkkkk
Ayi mmatiimilira mrbossman
Kukama ng’ombe yowonda kale mwaganiza bwanji? Think 2 ce
nosense
Za Chamba Zopuxa Cndingaxekelele
Mulibe chisoni
oxapanga kaye zA Magexi bwa?,.
mmmmm
Which roads? Bumpy, potholed tars don’t deserve a fee. Sizomangobera anthu ayi tamapangani zinthu zooneka plz
We r pure Malawians not from Mozambique & let’s follow our rules & regletions
Infact kabaza is more expensive than minibus so atha kutero
Malawians osasekerela zopusazi malo athu omwe mwatilanda kale mwati tizilipila nde mufunanso tizilipira ndi pa mphavu zathu zomwe kofi mumatifyesera ndinu mmakomo mwathumu
Ukakhala pa bwino usamati kunja kulibe mavuto, sichifukwa kuti ndinu a nduna kapena muli ndi udindo wabwino ma allowance dairy nde muziona ngati zobse zili bwino ndi ena onse
Kkkkk this one will be suspended as well like road traffic fee and 5000..kkkkk
Uku ndiye kumuvulaza m’phawi
Aaaaa so everything you need the poorvto digdeep their pickeks how will they survive
mmmm yalakwa
Next will be pedestrians.Kkkkk
Dziko lapànsi lili mmanja mwa satana ndichifukwa chakeso anthu zachisoni anasiya nanga wakabaza abale mmene amavutikira kupalasa njinga mkumati azikhomera a!!!!!! akuika malamuloyo pokhala pake ana ake xool fees galimoto yoyendera zonse zaboma ali phee!!!!!! Angakhale ndi chisoni uyu a!!!!! mulungu akakunyekezani ngati muzamwalire musanalape.
Guyz tikakudyelani kuti mpaka pa njinga yomwe mmmm malawi zoonadi kunkhala mmalawi mnkulimbadi mtima
It is welcome
Maskin wa mungu had baskel aweanalipia hee
Uyu ndiye ayinso
people are unhappy.
people are unhappy.
MALAWI WASANDUKA KUDZALA NDITHU EISH
MALAWI WASANDUKA KUDZALA NDITHU EISH
Mmmm smh, nkhanza izi
Mmmm smh, nkhanza izi
kenako timva aliese ali ndi smartphone msokho.
kenako timva aliese ali ndi smartphone msokho.
economy yavuta pamalawi
economy yavuta pamalawi
ngati dziko likukuvutani kulamulira muwapase ena ali ndi mnzeru za u munthu ndi utsogoleri wamaso mphenya agalu inu mwatikwana sono kuzima kwa magesi dairy,apanso mwatulusanso K5000 yapepala lero muli pa akabanza mkuncha mudzafika pa okhoma mabosi.kagwereni uko mkamwa mwamatewemo.mbuzi za atsogoleri inu
ngati dziko likukuvutani kulamulira muwapase ena ali ndi mnzeru za u munthu ndi utsogoleri wamaso mphenya agalu inu mwatikwana sono kuzima kwa magesi dairy,apanso mwatulusanso K5000 yapepala lero muli pa akabanza mkuncha mudzafika pa okhoma mabosi.kagwereni uko mkamwa mwamatewemo.mbuzi za atsogoleri inu
iyi nde iti itinso?
iyi nde iti itinso?
Adzayambe utolela msonkho akamata phula miseu .Miseu yamawenje .Palibe chifukwa chopelekela msonkho.Ufiti sungapose apa .
Adzayambe utolela msonkho akamata phula miseu .Miseu yamawenje .Palibe chifukwa chopelekela msonkho.Ufiti sungapose apa .
That’s nonsense
That’s nonsense
Gyz kod ndan ameneanapta kusukulu kut akadzaphuZila azakhla wakambaza nang zabwela nd yanizot AKABAZA azayambe kulipila nsokho ngat kut tchito yawo amangokhla, sindiye kut zimene linanena BAIBULO akukwanilisa zot (Munth azAdya thukuta lake) npaka kuyamba zomawalipilisa ngat kut Njinga zimene amagwilisa tchito amachta RENT…..tiganizepo bwino………..
Dpp iiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii
hahahaha malawi uyooo kwavuta
sopano kwasala kuti munthu akanyera mu toilet yake azilipila msonkho ku boma anyani achabe inu asaah
Good one
Money has become problematic in this government
My Malawi is really rotten. …..don’t lie to the devil this time. ……
zoopsa
Kkkkkkkkk atsogoleri a kumalawi mukuba mosabisa ndithu wakabaza mumubereso kkkkkk
Dziko lili mmanja mwa agalu ili.
zaziii
are we in a democratic country o nog
Apapa END OF TIME basi
Manyi anu!
No it’s not right, let them lead their lives, do u want them to be robbers? Too much.
Ingotiphani amphwawife agalu inu tichitenji kuti tioneke abwino Kwa inu?????? Kungoyamba kuna ma voti mpaka pano mubenso Kwa wakabaza????? Eeeeeeeh chitaniko mantazi anthu inu ndithu aaaaaaah mwaonjeza.
Ok
Hell earth mxiew
Koma mwalephela kuba,,mpaka licence yakabaza hahahahah
kkkkkk kwatsala wonda pansi mmsewu azitengaso malince
Yusuf Chothia Mo Larry Ahmed Waka Zaheer Ahmed
I was about to tag u people aswell
This is not the first to hear it ask people from balaka they pay to city council
mmmmm zaka 52 malawi adakama ndalama pano mwayamb kulimban ndi akabaza malawi kd watan ok tiwona 2019,km chifundo mulibe atsogoleri inu kenako tiyamba kudula mtsokho udzu omwe timaika panyumba pan2
Every Jim and Jack should also contribute to the budget. Osasonkha asadye. But shameless individuals will squander this money and go untouched. Shame. Are you really Malawians?
Ngeke,thats sounds pity,mpaka pamenepo
Usakwa amalawi…mpka parkin fee
Dziwani Paul inva izi
In a country where there is a social and economical injustice its only poor people who pays penalties of few rich and greedy people. The vast gap that currently exists between the rich and everyone else is not the product of some inexplicable natural phenomenon. It is, rather, the result of “unfair economic policies that benefit those at the top at the expense of those at the bottom. Hence the gap between poor and rich goes wider and wider.
If we go in houses of these bicycle taxis drivers its when you will understand the evil chain of reaction of corruption and greedness.
If you go through on second paragraph, it end with very pathetic reasoning “…a bid to improve revenue collections for the council’s service delivery”. Its like what again!? Malawians are already paying too much taxes that can be used to do more about so called town/city/district concils. Thats robbery done by government through its startutories to its citizens who have left with a single drop of life to survive. I mean,,,There are already fees that these KaBaza drivers pay to their respective councils before operating their businesses…are those fees not enough for them??
Mundiuze kuti alembe zikwangwani nkuika malo amene akaBaza asamaime ndipo opezeka ataimapo(atapangapo park) adzalipitsidwa.That makes sense. Some of these by-laws are nothing other than blackouts.
My opnion: they(councils) are doing it kuchepetsa chiwerengero cha akabaza. But thats just an aftermath of economical crisis. They should get along with it.
Yoh kulipo kulumana ndithu
Romana Raphael jus look
Lmfao what’s happening to Malawi ?
Dnt ask
Vuto ndilokuti,mitchona yonse imakhala italemphera kumene imayenda,BASI amalawi akuti timuzotera,we are still in crying.
Manganizo abwino, tidziwadziwa
Ooh
Watsala oyenda wapansi timvanso posachedwapa.
Its only humans who pay to live on the planet, rent, taxes, tariffs, toll fees etc.
Kukama yoonda kale
Mbuzi
Koma pa malawi nde kwanyanya! Kenako onse opha mbewa azipanganso register, total madness feel sorry for these poor pipo and tax these bloody indian tax dodgers!
Ma lamulo amenewa akuchokela kuti kwenikweni?
Dziko mukulinyenyadi ndithu ngati sewero
Malawi for sale
Koma ndiye mkhanzatu pali wini yanji pamunthu wakabaza ?2019 tichotse bavazi
Koma anthuwa mukanawamverako chisoni…..kabaza alibe engine and they use their own energy eish
trouble pa mw tizit ndalama zikuwakwanabe kenako oyenda pansife tizidulaso nsokho kkkkkkkkk iiiiiiii guyz.
Mmmmmm koma boma lawonjedza mene amavutikira wa kabadza
Zilipo
Kkkkkkkk koma nde zafikapo eee ndani ameneyo akupanga ixiyu
No stone will remain untouched under president PETER MUTHALIKA
Took late Ku LIWONDE zinayamba kale
Khanza
Machende anu agalu inu
Big mwaonjeza iiii kkkkk
Kkkkkkkkkkk
Big amapanga chocho nakha AAA kkkkkkk
Zachani soprano izi?
Kkkkkkkk Boma ilo
Ku liwonde amalipiratu ndipo opanda kulipira mawalanda njinga Ali mma license
Shame on you All So-called Top Government officials. Thats what really happens when you vote for Leaders outside Prayers. Because of high rate of Poverty, we are easily fooled and brown away by Perishable Campaign materials. When a politician comes with A packet of Sugar and Two fritters (mandasi) then we all run and vote for him. Because of foolishness which is interwoven with Grinding poverty at large made us vote for leaders with no hearts for people. There is absolutely nothing we can Do on our own without the help of Prayer. We need to have a Discerning spirit on our leaders when they come for campaign. We must not forecast on what he has carried materially for us but what he is going to offer beyond Sugar he is willing to give us today. Only if these leaders can strip down the Pants of a Kabaza Man. They will have the shock of their life to See Zikundu mmatako kulimba because of trying to put Bread on the table for their Families. Remember life is all about the choices we make everyday. If we continue to vote foolishly we will alwez reap foolishly. This is as a result of foolish vote we casted yesterday. So the ball is in our court in 2019.
Thats bad..anyamata awo asiyeni kodi aziba kapena bwanji?
Malawi is poor shame we aren’t even going forward but backwards
Koma nde kutikamatu, mukama magazi kenako
Mmmwahahaha
Mmmmm zafikaso penapache isaa !!
Zilibwino…komanso kuli ma business ambiri mu dziko muno omwe enewake amangopanga phindu osapereka mnsonkho. Boma lichitepo kanthu. Mnsonkho usangonkhala Wa anthu ogwira ntchito, Malawi ndiwatonse.
I hate u
Tiye nazoni kenako mulemba ma Civil Servants omazapempha cash m’makukamu.
Achitabwino there no future in this business, it just promote laziness, during Kamuzu time these people were having good life through farming and related activities instead of spending the whole day alongside the road looking for peanuts, get a life. Please government, ban Kabaza in Malawi it’s degrading
Where did you keep your brain?
you think everyone was born in your family?
Am just passing
Iwe Pano Malo Akusowa, Iyi Sifundo Ata! Ndi Wakabaza Kma Zavuta Kuboma.
Mfundoless #Moses
Choka galu,nyani kutereko akupasa ndlama abomawo etiiiii,,,,,,,? ndisazakuoneso pa pubic online pa ukukamba mfundo zako zosapsazo @ #Chipeta moses
Odala Inu A Magalimoto Anuanu.Enafe Timadalira Kukwera Kabaza Yomweyi
Iwe moses chipeta ukulankhula ngati wadya manyi chifukwa chani usazakomenteso manyi ngati amenewa wava?
kodi mesa mukamapita ku ma lodge mmahule aja mumatenga akabaza omweo? bwampini iweti!
kodi mesa mukamapita ku ma lodge mmahule aja mumatenga akabaza omweo? bwampini iweti!
Mungakwere chani kabaza atatgetsa
Muli shit man very shit may thunder strike u amen
Wayenera kukhala cadet iwe mind ur words kuno ndi kunja kumayanja lichero
hahaa nose mwakhoza khalani pasi
Zopusa basi, zikuoneseratu kuti akabaza mwachuluka pano, and you talk shit, next time I see you on the road I’ll run you over. We don’t want those rotten bicycles of your on our roads, amfiti inu??????
Ndi zimene mmafuna po votera galu yanuyo
OK bwanji kuzisaka boma kkkkkkkkk
Misewu yake yonyasayi
mmmmmm too bad, we are buying our own country. hahahaha. registercard expiring date,driving license, nanga chiphanso chauzika!!!! Malawi wandikanika bola akagwere kudoko la Msanje,kuti mwina bomali alamuleko awa
stupid plans,,,, Mr ibuu
Kanundutu uyu, shame.
the revenue collectors are always tasked with a challenging job, but interms of allowances they only got a peanut
Uku ndiye kuwabera amphawi
It has started in eastern part of Zambia
mloooo
This show me that bike is a real transport in malawi ne ? Lol what a joke
Nde poti amalawi mumangovomeleza zilizose, zimenezi zichitika basi !!
Nkhaza zimenezo kwa amalawi osauka
Kkkk ths gvt is depping so high in poor people’s pocket.
kukama yoti ikufatu uku!!!
Kwasala oyenda pansi.
Azitilipilitsanso.
Azitchinga misewu.wosalipira,osadutsa.kkkk!
nkhalamba izi chamba,vomelezani kulephera kwanu.
bomali bac angofuna kuyamw athu basi
Kusowa zochita uku osakhonza Kaye ma black out bwanji
Iyi ndiye misala yeni yeni
Wow good news
Zachambatu izi tikumachita manyazi ndiife tilimaiko akunja anthu akuno akangoona izi tikumachita manyadzi kwambili
Plz don’t do that it’s not gud for as
Boma silifuna untax payers. Koma kwacha wake ameneyi mpaka kabaza licencing?
Aise pena zochitika Ku Malawi, u think of it as jokes, there r serious problems for the Malawi government instead of closing all windows of opportunity 4 the poor
Well spoken Daud Mbewe. The more the people are taxed the more they’ll complain thus less votes.
zachamba kodi mwasowa chochita et zuto ndi chati kuti muzaberannso anthu uvutuka ndalama
Wa trafic tidzakwapula baba zasilu eti pamanu nonse t man akakunyelani kuti agalu
fakeni mutharika achoke Bushiri woyeeee
Uku ndiye kubera anthu osauka
Hahaha kugulitsa ma company aboma mkusauka kenako mkumalimba ndi anyamata a kabaza. You old people you should be ashamed of this nonsense you did to this country. Sheeee
Zachamba etii .
Mmmmmmmmm koma 2019 ukhaula
Ichi ndiye chamba mwamva
Ndimanyazi omwe mulibe??? What a shame!!!
I do agree on Kabaza because these people raise a lot of money,If a barbershop man pay so wat about kabaza.even landbill should go a head ,they dot pay tax but manage to raisen mk 90000 at a months.
Pangani zomwezo basi tilipile zimenezo basi mbuyanga tinakuikanipo ndife tokha
KKKKKK guys zoopsa, nkhalamba izi ziribe nzeru, ma plan akuba ongofuna anthu osauka azisaukabe,
A Malawi tili mmavuto. Abale misonkho yonseyi sikukwanila
Zinthu sizikuenda pa nyasa mpaka wakabaza choncho eshiii
DPP why always milking a thin cow,sucking from the poor pipo.This is money hungry party.Shame on U!!
ndikukhulu pilira kuti apa boma lamva maganizo aanthu osauka kuti nawoso a njinga wa adzidula msonkho
Kodi Akuyambisa Zimenezi Ndindani.?
wayambisa zausiruzi ndndan??????kod kwenkwen akufuna kt OSAUKA AZINGOFA asamakhare mkathu kalikonse?????zofoira basi………
amalawi mutengerepo phunziro kuvotera aGALU kuti azikusogorerani .mbewa zanji zopanda manyazi mupakana njinga yakapalasa musonkho .zayamba kusowa ndalama muboma zija mumaba nthawizonse eti …..mwanya nayo pakamupeni akazabwera ameneyo miyala gayezi ….paja kumalawi mifuti zimasowa
Kkkkkkkkk dziko la malawi losauka basi olo mutorere misikho nothing changes
Kkkkkkk eish zovuta zed
Kkkkkkk eish zovuta zed
Kubela osauka uko mwasowa zochita
hahahahahahaha malawi ndi anthu ake
Madness mumisewu yafumbi?
Nonsense
Mmmmmmmmm !!!!! Foolishness..
Chonena ndilibe chomwe ndingapephe ine tell a immigration apange fast ndi passport yanga ndizipita theba ine.chifukwa apa ndye bola kumakasambisa khalamba
l
Tangomangani misewo yamakono nkuyika ma toll gate or ngati mukufuna kumapeza ndalama mokwanira ku traffic department. Koma kumbali ya a Kabanzawa mmmmmm, I agree azilipira msonkho komanso ena mayendedwe a pa msewu sawadziwa mkonze njira yowaphunzisira kayendedwe ka pa msewu ndikuwapangira ma licence awo awo.
Boma lipeze minda lizima. Osamangodalira kulanda anthu.
Aaaaaaa licencing yachan ?shut up
Mwasowa kodyera ndalama mpaka njinga, shame my Malawi
Zoti ntchito ija ndiyathukuta mumadziwa?Simulesana pofuna kuchita zinthu chifukwa chani?
Kwa Ine makamaka vice President Saouls Chilima ndi mamuona ngati wachinyamata koma chidebe cha munthu zili zonse eeeeeee bwana
APM kusowa mapulani
Kkkkkkkk kanthu akoooo!!!!!
Boma uli silikukondwa kuopa muthu osauka amanyamusofi ngakhale kajumbo ka bonus,koma koma shine ndinjala basi kuti aziwalambira bwiino.
MMMM ndiye kusowa chochitanotu
Kkkkkkkkkkkk tiziona amalawife mpaka njinga yakapalasa nde zausilutu kodi ku tsogoloko simtsutsana mkamakambilana nkhani ngati izi kkkkkk
Kkkk mavotelavotela mwavotela nazo mavuto iyeyutu akutengela za kwawo Ku mozambiki akufuna azibwelese kuno sopano
Shayra Jo-anne Fernandes
I can see even a farmer milking a cow while a cow is so thin thin
Kudyela aumphawi,,,.,., Koma Mulungu wakwiya nanu heavy,
before long something wil hapen against u stupid-nonsense plp.
Ngoloso ndiyetu kkkk
Koma mwafatsako kuDPP kwanuko eti
Tiziyenda mutchire utsiru wanuwo ayi
Nsewu uja awusandutsa olipilitsa tsopano….Timvanso pompano kut amene mukungoyendamo ,muzipereka kenakake….Ndalama ili pa minga ndithu….Awa ndingawapose ndithu kupeza njira zotukulira dziko….Anyamata a machenji ngat awa kuchita kuwafinya pakhosi chonchi mmmmm….kkk
Had Dunduzu and his brother Yatuta Were alive, for sure wouldn’t hav hesitated to shoot arms
Koma boma lilibe chisoni ndithu
Ine ndimodzi wamakani ndi boma ili koma apa pokha boma likufuna kupha anthu.Inu munthu akuyesesa kuti mwina mwake apeze thandizo,mukugwira pakhosinso.Mmalo mowalimbikitsa aziwala umphawi wawo kuti anakuvoterani mukudya bwino iwo akusauka powapatsa njinga zamoto.Ine sindikumvesa:Wakabaza azilipira CHANI??.Tsiku linatu amalawife tizatopa ndipo chauta azatithandizira mkwiyo.AYI ZABWINO ZONSE TENGANI ZIKHALE ZANU.
everyday things ar getting worse,worse under this government;k5,000.00 bank note,blackouts,corruption,low maize prices,now msonkho wa njinga,mawa azalamulanso aliyense wobvala nsapato azikhoma msonkho,CRY 4 OUR BELOVED MALAWI ,
let wakabaza atukuke kuti maybe azagule galimoto Kut muzayambeno kumudula bwino msokho osati kuyambira level imeneyi ndie you expect kuti angatukuke
Ndipo mukadzawavoteranso 2019…msonkho udzakhala mpakana pa oguza wheelbarrow; ngolo …
First of all, boma adziunika kaye kuti anthuwa patsiku amakhala akupanga ndalama zochuruka bwanji; nanga akachotsa ya ma spareparts plus kukonzetsa amakhala kuti atsala ndi yochuruka bwanji;
Zimawawa kuti amalimbikira chonchi kutolera misonkho ya amphawi ndipo ndlamazi nkumasunga mma Expand mnyumba zawo yet people are lacking conducive environment with well improved roads and infrastructure for boosting their business; better social services in terms of electricity; clean water ;etc.
Amvereni Chifundo anthu akumudzi…
well said
Kkkkkkkkk mpakana okupha nkhuku yako yomwe!????????
Kkkkkkkkk koma zoonadi azilipira
Tazimvani chisoni zinazi aaaaaaa
NO,THAT’S BAD,BICYCLES!!
Malawi hmmm
The government is failing to strike a balance in the economy, with these policies which are always aiming at reducing disposable income from people, not even big companies will survive coz pple will have no money to spend. Take an example of Sweden and netherlands, they knew that in timee of crisis the best way is to increase the disposable income of people and raise the base for indirect taxes. I wonder what our gvt thinks sometimes.shame
true.. Malawian economics are of 200AD
Kulephera uku or uyambe ya mandasi afunaso nsonkho
Koma yaaaa
thats good,we need that,,and dont forget awa ama burning centers and ma studio angoyambika wambawa,,
I think this will control the numbers of #Kabaza… they r too many eishhh
Aaaaa kodi ziko ili likupita kuti kodi inu peter ukupita kuti ndiziko
Don’t Be As If You Know
If You Were You What Would You Do?
YOU MOSES MULEMA,WHAT HAVE YOU DONE TO YOUR COUNTRY,MALAWI?
Which roads, are there any roads out here?
Which roads?
Good question. Misewu yake yomweyi amatukwanidwa ndi ma driver agalimoto ngati agaluyi? It can only work if special pavements are constructed for them like other countries do else it’s totally impractical
Thus an act of war!
Boma ili limuziwe yesu
kkkkkk
Tamalembani nkhani zoveka bwino chamba eti fees kenako free ndiyekuti chiyani?
Koma zinazi yoooh!
this is bullshit!
Kkkkkkkkkk
B
Kkkkkkkkkkkkkkkkkk wakabanza mpaka licence
Kkkkkkk Malawi gulitsa dxinali Ku maiko ena odziwa budget
Eeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee mpakana pamenepa? Ayi malawi wavutadi
Very unfortunate to make the poor suffer. This is not fair.
mwationera mmadzi akabaza numphawi sikufuna
Koma
Kkkkkkkk koma kwen kwen ndi chan abale
Wat,,, can’t get u????
Dats is very stupid
KODI INU A DPP NOKHA MUKAKHALA MOTI SIMUKUDZIWA KUTI KUKHWIMITSILA FUNDO ANTHU OSAUKA NGATI KUNENEKU NDI CHIMODZI MODZI KUWAWUZA KUTI ASADZAKUVOTELENINSO???????
ku salima kuno zinayamba kalekale.nthawi ua chair.amene amatolera ndi a council.
kwathu sipadziko tengani zonse zikhare zanu, Toy Car ya mwana wanga mufunaso nsonkho. mwalowanu kuba sopano mkaka ndi uchi wakumalawi uja ulikuti?
Kod boma likufuna kudya thukutha LA anthu??????zimenezo ndy zopusa bcz ngat tikugwilisa ntchito magazi popalasa njinga inu muli nenga mipando. Tizaona
achakulungwa mpaka ni njinga sya kapalasa komela nsongo wa pa nsewu kkkkkkkkk.Basi dziko langa lafikano pena pake,akutinso mpaka Bushiri akufuna kugula Eskom?sha !!!
Zobelana!!
So u mean mukubazi isnt enough to full up ur pockets you thieves Where Do You Get these foolish policies??
Nkhazatu iziiiii anthu apumire pati pulizi
Kenako muyambanso msonkho wachamwaka. Don’t re-introduce colonial laws in this era in the name of widening revenue collection. Think of other means not milking the poor people. This is outrageous!
Mmalo moti mudzikamba zoti anthu akabaza akuvutika boma ligawa njinga zamoto kuthandizila business yawo koma mukufunaso akugaileniko kochepa komwe amapezako God please help Malawi and take out its poverty
koma yah!. .Malawi akuyakadi moto wa lawilawi
Nde mukuti pitala ndiwophuzira??kuphuzira kukuonekera pati apa?
Mozambique have this already. both anjinga zopalasa and motorbike pay nsonkho but in malawi coz is new, look at the comments. ha..ha..ha..ha.
Wh@ do u do for a living Mr?
Thank u for your question. i might not dwell on it but let me remind u that for our country to develop, it needs u and me to contribute something. it cud be either money or any means. malawi is the only country in southern africa that gives most of its services free of charge. Malawians always depend on the government to do things for them instead of doing the opposite. we demand good roads,markets, hospitals and etc but we dont have them coz of lack of funds. Lets change our mindset.
these policies are not to be brought in when there is a financial challenge in the economy as it is now, your argument is perfectly ok but right now gvt should rather consider more on indirect taxes like VAT. coz powafinya anthu now kandrama kocepa kale akupezako it wont make any sense.
I agree with u Mr.Msokera. Let me draw your attention by saying that those responsible for formulation of policies have seen the need of demanding this fee from these people who are doing this business. I believe there is an advantage . we may think of life protection to the customers and safety of their goods.
it’s like we’re killing one another Mr kachimanga seems like u hv lose ur sense, ,malawians ndi anthu olimbikila ntchito but look akakolola they fail to sell their produce at a productive, ,, and you said our neighbours ara already doing this when comparing plz make sure to play a good siso not looking at one angle b4
That’s nonsense you can’t compare Mozambique to Malawi. if that is the case kuti it will be the way of sourcing funds, bomalo likulephera ku yika ma public transport why? likulephera ku manga ma toll gates oti lizitolerela ndalama bwanji? panopa ntchito boma likulephera kuthandiza nathu kuti apeze ntchito, then munthu pawekha ukupanga kabaza as means yopezera ndalama yozithandizira then boma likati lizidula msonkho kwa anthu amenewaso? thats nonsense. zinthu mdziko muno zikulakwika coz ambiri amene akutitsogolera ndi anthu osazindikira. nde ngakhale muyambe kuwadulitsa msonkho akabaza, that will change nothing. Ndalamazo azingotidyerabe basi…
Thank you all for your views. I believe our views are just as good as they will benefit all of us. If I have offended someone inside my comments forgive me but it has been a good debate so far.I have enjoyed all the views from all the angles.
Malawi is currently loosing alot of money due to thieving politicians and government officials therefore we need not to punish these kabaza operators to pay the money which will at the end benefit few greedy thieves.
iweyo ukat amalawi amangodalila boma kut liziwachitila zithu iweyo ndiwe m’malawidi??? kapena ndiwe somalia wangokhalitsa kuno?? coz palibe dziko lomwe anthu amadzilimbikilila pa okha kuposa amalaw, nde ngt usali mmalawi plz stay out dis!!!
ndufuna ndimuuze uyu akuoneka otaikayi amve mau awa ndipo ngati ndunama titsutsane pompano os qualker mocambicano qui tem mota ou bisicaleta tem direito de pagar imposto sim tou apedir osinhor para me imformal onde e qui provincia k os taxcista de mota ou d bisicaleta so paga imposto so nao esses outro e osinhor tek saber cada pais tem legra dere wamva?
Masulirani big, otherwise it will be greek to us the readers.
Kkkkkkkk
This is Malawi not Mozambique, bwanji tizitenglako zinthu za bwino sometimes
My time is over with this debate, …. we can not hold the same oppinion i suppose. All views whether positive or negative are equally important otherwise let us do things that will improve our livelihood. I have arleady accepted so iam wondering why others put a blame on me but its like that.
ok donton ndimaganiza kuti munthuyu alikumosco komuno ndunena chomchi malamulu akuno amalamula aliyense amene ali ndi njinga yamoto kapena yakapalasa kudula msonkho pachaka koma lamuloli silisankha wakabaza ekha koma aliyense yemwe alindizinthuzi ndipo ndinamupempha kuti andiuze ngati kulimzinda wina omwe amakhometsa msonkho akabaza ndipo pomali ndamuunikila kuti dziko lililonse lili ndimalamulo ake
Sure paulo wanena zooka koma nanga wa ngolo bwanji.
Mozambique and Malawi are two different countries,don’t compare them,Malawi government amayenera kumva chisoni ndi anthu ovutika ngati akabazawo,ena sikufunakwawo kuti azitero mmmh
Kkkkkk koma eeeeee
Nde muziti congress imalakwitsa msonkho or cadi inu nde no 1 nkhanza
Cut down on extravagance, unnecessary foreign trips & corruption if u want money & leave the ored impoverished pipo 2 b free in their motherland.!
zausilu zimenezi kufuna kumangoberana basii
Kenakonso muzayamba kutiuza amituta ife kuti tizikhala ndi ma lainsence onyamulira mituta ya pamutu yomweyi ,,Mayooo!!! Malawi wangaaaa!!!!! Atate ingobweranipo muzamuweluze ekhayi uyuyo akumatchulidwa kut MALAWIYI SHA!!!!!!!!!!!!
What is this so called presdent up to?? kenako atigulitsa a Malawi tonse coz he likes money too much..he doesnt care about poor people..samayenera kukhala presdent in the first place..SHAME ON HIM!!
Mwasowa kokubatu sopano
dpp mistake after mistake.mukuona ngati zisankho ndikale? pls ndinthawi yoiwalitsa mavuto anthu osati kuenjezera
This is cruel…..
Ndiuziren onse akumipando kti onse mitu yawo,ndipo asamationelere chifukwa chauphawiwu
Izi ndi nkhanza kwa eni zikoli sure
Si zoona kupalasa kuja kumakwanira timazilipirira tokha msonkho
ulipirabe basi usova
Kkkkkk mayazi bro thukuta lija nde msonkhowo
kkkķkkķ bro mukunena zoona thukuta lake limenelija alipirenso nsonkho??? kkkķkkķ kulakwa guyz
Kkkkk kufuna kutipha kangapo eti
Kkkkk zosatheka
Mmmmm likupita kt dziko lija bola kale ndithu chasala apa ndikutilamda zonse zomwe tilinazo.
Koma dziliko liko ku malawiko shaaa bola ine ndili kwa jacob zuma kuno ndipo ndizabwere kumene pitala muthalika akazamwalira kapena kutula pasi udindo muthu olephera iwe ndi sukulu yako ulibe nao dzelu
Ukakwera pansana pa njovu usamati pansi palibe mame.Kwanu ndi kwanu mthengo mudalaka njoka man.Mwina lero kapena mawa ugwidwa pa ukapolo wa kulindera(deportee) uzatan? Osamatha dzankamwa.
Bg akudziwa zimenezo ndi god bas koma ukuganiza kut wakabadza mpaka azilipira sokho mmalo mokagula zakudya pa den pake mmene ivutira kupalasa njinga muja ndiye muthalika wanuyo adzingowabwera athu kuterekoso 2019 uzamuvotera eeett
koma abale
TIbwereranso nthawi yakamuzu
Aliyense kusogoloku azakhale akupezeka Ndi khadi loyendela pa nseu
that’s crap ~ f<>k de gov!
My Mother Land Where R U Turn To?
Ha ha ha nthawi tsopano ndi nthawi yakamuzu dzikusiyana pati
Malawi
Mmmmm..Ok
Kusowa chochita or chisoni mulibe
Eeeee guyz be serious where money are going? Do you mean past years the government lost alot of money because there’s no much contributions like this time?
Ok and then maintain your roads first to continue your underground movement over poor people
Koma abale
KOMAAA?
mmmmm kupanda chisoni ndianthu shame Malawi wamoto
Mmmmm nde mukuti anthu wamba mavuto awo awachepetsa bwanji.Inu zoona muziwanyambitilanso akabanza anthu oti akukhetsa thukuta lochuluka kuyesesa kuthandiza mawanja awo ndiye muziwabelanso?.That’s witchcraft guys.
Kkkk where is malawi? Kwasala msonkho wa ma pedestrian kkkk
For free or for a fee? Ur shupit mwamva? Mukumalemba ma post anuwa osampatsa editor, this showz how unprofessional u r..!!!!
I will rather advise u to re-read the story.nothing wrong there.
Palibe chalakwikapo apa man vuto ndinuyo,,,,,,,from 2018 not even ………………………..
Wapala et kkkkk
This Is the reason why you should’ve paid attention in class
Zanu izo, inu mufuna nziganiza ngati inu nzanu ndiri pa counter…..
mr Nkhoma please say sorry to malawi 24, otherwise stupid will back to youserf
Hahaha ndumwa mowa mpepesa nkakhala sobber
Kkkk koma man…
Za mkalasizo izo nzanu pano associate finale ine
oyenda pansife we are next kkkkk
Hahahahahaha kuba basi
kkkk After 5 pin then mukameso wakabaza inu chikho ichi mmm Malawi wachilemela God have mercy on my mother malawi
Kkkkkkkk koma yah ena adavotera zimenezi ankati ndizophuzila kwambiri, ndiye tiye nazoni
kkkk eya zinaphunzila kuba kaaaa
Iweyo ndiye oipa chifukwa sunavote
Kusavota kwaiyeyu, ndiye kumene kunapangitsa kuti anthu amenewo alowe m’boma. Ndiye lero, ukulankhula moputsa apa futsek. l
Kkk! ANAYIWALA KUT KUPHUNZIRA SI NZERU… . Dziloli ndi latonse tiyem nayon
@jafali Tambala, inever mentioned your name in my comment before so don’t try to be aclever
and he has to
sakutanthauza kuti iyeyu sanavote ayi koma akuti voti yake sinapite kwa amene akulamula panoyu. Kuzolowela kutukwana basi. Bwanji ma member?
Mbava zopanda manyazi
YOKUMBIKA YOMWEYI????
eyaa muzilipila bwana
KKKK,
KKKK,
Malawi Watha Guyz
Milking the thin cow.
Kufun Mtsokho Chan
Ummmmmmmmmm tell us who has sayd this So that we comment nicely
hahahaha koma Malawi NDE wavunda shaaaa
yaaa
How to draw boys man?
at how to draw boys…..hihihi
Kkkkkkk
???????????
Zimatengera ma fon ake man