Former Speaker of Malawi Parliament Henry Chimunthu Banda on Friday escaped death in a car crash in Mchinji.
The car Banda was driving, a Toyota Prado, was involved in a head-on collision with another vehicle causing it to overturn several times.
Reports show that the other vehicle left its lane in a bid to overtake other cars but ended up crashing with Chimunthu’s Prado.
Chimunthu told the local media that he was fine and would seek medical help in Lilongwe.
“I thank God for he has saved my life. I feel okay but will seek medical help,” he said.
Chimunthu was on his way to his farm at Kapiri in Mchinji when the accident happened.
Kumukhumbila kuchila luwiro
this must be viceversed to the president of DPP so that people can drink water
I will make Brai kkkkkkk
we thank God
All old adge in political must die atinzunza mokwana from 1994 f****k
RHGCHVGGUCHC
Tisaphatikize Ndale Ndi Ngozi Guys.
Thank God he is fine
Was he drunk
Thax God 4 ur survival………God’s good.
anthu oipa awa, nduna zokhomerera zonse machende awa pamodzi ndiabwanawo.Achinyamata ife tikumavutika pamene inu mukudyerera ,nthawi yamavoti ikamafika kumangoti ine ine kunyerokwanu mumanyera zokazingirako ,mukamachita ngodzi chonchi muzitengerapo phusiro ,ndatopananu .Mukamatinamiza mulungu amaona,komaso chilango chilipari pasipompano,oipa nonse akulangeni .Chapondayu akumusiya pati? watilizauyu wokumvaamve ondifuna andiimbire pa09 ,ndatopa ndiuphawi tizingoomva zachumachanu ine phawi ndimayesesa mumatikhomerera ,ine malawi
sorry big
God must be praised, Malawians still need your services
Be careful of opposition.
I saw this accident yesterday
Very sorry for these accident may god bless you?
God is Great ! Chimunthu is our History in Malawi. He was handling debates with lovely commending voice with no bias mind. Kuno Kumzimba tikuti Chiuta nimuwemi pakumunthaskani Ku ngozi yikulu na yakofya! We wish you all the Best.
Praise God.lt means u r stil usefull in this world.its no easy to escape.
Oh shame sorry Mr
Koma mmmm mulungu ndi wankulu basi.
It happens, its a secret between u and ur God, even non politicians, Christians Muslims, cadets, presidents can be involved in road accidents, It wasn’t his time to loose his life,,Chiuta watumbikike swiiii
Car crash survives Chimunthu Banda
The car cannot drive itself
Umafuna afe?
kodi antu amenewa,amaganizako bwanji,zamulungu wakumwamba ntcito kulota ndale basi
What type of car is this? Thank God
It’s time to turn to God
Thanks god thanks jesus
Ofunika amudziwe yesu ndi ophunzila ake ndiithuuu
Thank
God
Leave driving carrier to professionals that’s my advice to all bosses
Thanx God
Alemekezeke wa mmwambayo
Mulungu ndiwamkulu
Madala Ngati Simumapemphela Kuyambila Lelo Muyambe Kupemphela Mulungu Alinanu Cholinga.Ndalezi Izi! Madala Zitayeni.Mutsateni Yesu Mwaiye Muli Chipulumutso,chitetezo Komanso Chigonjetso.
amen mwandilimbikisa nane
Zikomo.
Ndekuti opemphera samapanga ngozi yapagalimoto eti!
mafutso enawa oduka mu2 ndithu kkkk
kkkkkkk!Ndimafuna Mundifunsile Ndinu.
Thanks be to God
?
Thank God
Amen
oosh
or akanafa ndilibe nao vep athu andale akumalawi ntchito kuba bas mmalo mopanga chitukuko achina Dausi anayamba ndale ndikamudzu banda mpaka lero koma kumwa kulibeko chitukuko cholozeka shupit zanu inu athu andale nonse kupatula abwana lucias Banda koma ambirinu ndinu apumbwa
Moyo wanzako umenewo?
eya abg zamoyo wawina sindimasamala athu andale si athu amazikonda okha bas ndiye zimandinyasa wava bg
Bg athu andale amatikonda pa kampeni bas kungowi ndiife chikondi chimatha tym yomwe
Ngat Mmalawi Muno Muli Munthu Wina Opanda Chitukuko Ndiye Lucias Banda Ndimmoz Mwaiwo Koma Toney Ngalande Osat Manyowa Akowo Wapangako Chani Bandayo Tel Me Braz
Moyo Uliwonse Ndiofunika Palibe Moyo Oposa Umzake Ziwani Zimenezo
Big mwayenera kukhala mfiti yoopsa inu!
Ndipo big ngati ufiti mulibe koma matewela okha mumadya
Koma zoti wampulumusa ndi Mulungu ukuziwa????
ndiwe chisilu, opusa, kupepera. ziko silimasitha ndi atsogole okha ngat malaw siotukuka you are also rensponsible mumakavotera nokha, lucius wakoyo palibe cha nzeru chomwe akuchita. chimunthu sakupanga nawo.usamale
isaac iwe ndiye kaya kaya bas iweyo or utawavotera andalewo palibe chomwe ungasithe pa moyo wako mpaka uzalowa mmanda uli mphawi mmalo mot uzilimbikira ku vepa kut mwina uwone kuwala kwa ziko lapasi uli busy kusapota zipani usova fana
Alipo a ndale angapo kumpanjeko sindimawaonera kukondwa anayamba ndikamudzu koma mpaka lero ali m boma koma palibe chadzeru chomwe anapangapo mudera mwao
Kuyankhula mopepera ulibe uzimun’bale wanga
Ngakhale leronawe uthakuyambandale tionezitukukozako kkk ndkusekangat zabwno mmm. Ukumayendanjomba ngakhale akazako n anaako kulibwanj zko kapena dera?
Lucias Banda ukumunenayo anaba certificate. Iyi ndi mbava grade 1.
Chigimbuli cho chibila chibuka wayuuuu
Man mukutanthauza chiyan sindikuvetsetsa bwinobwino zimene mwalembazi
Amakonda kuendesa okha, apeze batman or driver lija ndikale
thank god!!