Amene amayesa kuti chipani cholamula cha DPP chatha ndi kufelatu basi kamba koti chathibulidwa ka ‘5 kwa 1’ ndi chipani chotsutsa cha Kongeresi, ati aganizenso kawiri.
Malinga ndi mneneri wa boma a Nicholas Dausi amene alinso wamkulu wa chipani cholamula, kusachita bwino pa zisankho za padera sikukusonyeza kuti iwo afa basi.
“Mwanna, musanyengeke ndipo musakomedwe konse. 2019 tiphukilanso ndipo Tambala wadya Chimanga uja timupanga phwando. A Kongeresi alilanso kuti Mayi wawaye,” anatelo a Dausi.
A Dausi anaonjezelapo kuti kugonja kwachitika pano kupangitsa chipani cha DPP kuti chilongosole zinthu kuti pa 2019 azamwe wa mkaka.
“Mbamba khulupilila, pendapenda sikugwa. Ife tachita pendapenda apa sikuti tagwa tonse ayi. Mtunda udakali,” anapitiliza motelo a Dausi.
Chipani cholamula cha DPP chaonetsedwa mbwadza pa chisankho chapadela chomwe chinachitika mu madera osankhika lachiwiri.
Pa madera asanu ndi limodzi, Kongeresi yapambana madera asanu ndi kusiyila DPP ka dera kamodzi basi.
MCP up! Up! Up.DPP down down down
Mr Dausi dont cheat people of Malawi, its only those who do evil like DPP .vomelezani kuti chipani chanu chilibe mwai ku Malawi and people hv lost trust in u becouse of corruption,
Mr Dausi, be assured that it
only jehovah z my president and his vice p jesus thats all, ma mps mbwe mbwe mbwe acina nowa ndi anzake. zanga phee zamdziko zacabe
Inu mwatha basi tione zina
I have a message for my beloved hon Dausi. The man is so talented that I wonder why he is sticking to a sinking boat. He is in the wrong boat. He is like Jonah in a boat that is sinking whose only solution is to throw Mr Dausi in the waters so that he swims back to MCP. He was with Kamuzu, and the spirit of Kamuzu is not happy that he damped the party. Mr Dausi think twice, repent and come back to your father’s party. I liken him also to mwana olowerera
Kaya ZANU izoo!!
Wait& sees Malawi is listening bwana dausi
osayiwara kuti woonelera umaphweka mpira amatha masapota kuchinya messi asanamenye buluti pa golo ,DPP i zawina chifukwa anthu amafuna chitukuko cholozeka ndimaso,kuyipitsana mbiri cholinga inuwotsutsa mukhare azeru .kwa athu aluzawo zoti kwawoko sakuwafuna
osayiwara kuti woonelera umaphweka mpira amatha masapota kuchinya messi asanamenye buluti pa golo ,DPP i zawina chifukwa anthu amafuna chitukuko cholozeka ndimaso,kuyipitsana mbiri cholinga inuwotsutsa mukhare azeru .kwa athu aluzawo zoti kwawoko sakuwafuna
Kkklkk
Hon Dausi your saying this coz you have the time yo say.
This loss it’s a bad sign, myself I voted for DPP, but frankly speaking anthu akuchidandaula chipanichi, some of the leaders kudzikonda kwambiri, even campaigning materials kumawumila e.g nsalu osagawa zokwana bwanji? Don’t expect to win in 2019, if you’re not going use the grassroots team.
bvuto mu dpp ndikuchenjera mopusa azitsogoleri ake.Mumaoneka ngat anzeru pomwe munachoka ku#udf panopa uchitsilu wanu inu a dpp olo mwana akuudziwa.Yafikano nthawi yot mukukute mano.Apa mpango ndimaso mphenya chabe apa tiyeni ku 2019 muzakomoka.Agaru inu mwatikwana over and over
Sorry Dpp zamanyazi ng’oooooo
bvuto mu dpp ndikuchenjera mopusa azitsogoleri ake.Mumaoneka ngat anzeru pomwe munachoka ku#udf panopa uchitsilu wanu inu a dpp olo mwana akuudziwa.Yafikano nthawi yot mukukute mano.Apa mpango ndimaso mphenya chabe apa tiyeni ku 2019 muzakomoka.Agaru inu mwatikwana over and over
Tizavotera dpp yomweyo mcp yaba kwa nthawi yayitali zaka 30 ndye mkumati mukufuna kulowa m’boma muzachitamo chani komaso mukati new blood mukutanthauza chani ? Popeza anthu ake ndi omwe aja ankaba ku mcp kalekale aja ndye mukufuna muzabeso zaka 30 sizinakukwaneni asaaaaa
Dausi, I hope u r counting.
How many comments are on ur side?
Mudzagwetsa ndi chiani? Simukunena kuti tidzayetsetsa kukopa a malawi kuti adzativotere koma mukungoti tigwetsa kapena ndi yomwe IJA? Mdzina LA Yesu Khristu tikukaniza machenjelero a mdierekezi pa chisankho cha 2019, amen.
Kwaine sindimaona wachilungamo pakati pawandale if u want our country to develop tiyeni tisinthe kaendesedwe kaboma chifukwa onsewa posiya zomwe ankapanga kulowa ndale cholinga sichina ait koma ndalama zoti alemele .
Zazi!! Mukupenga tizaberedwa mpaka liti? Zisithe basi
No chance DPP in 2019 because it is good for nothing, Whoever say DPP Will win in 2019 He/she is wasting time, people hv notes that the only way of getting rid of problems we have now is to remove it from power, you will see when 2019 comes.
Mpaka Mcp Kuwina Ku Nsanje.Koma Zomakhomera Unzika Tili Nzika Kale Mukufuna Mutinzunze Dziko Lokhala Lathu Sitilora Its Beta Kwa Falao, Dpp Paulendo Mu 2019.
Mpaka Mcp Kuwina Ku Nsanje.Koma Zomakhomera Unzika Tili Nzika Kale Mukufuna Mutinzunze Dziko Lokhala Lathu Sitilora Its Beta Kwa Falao, Dpp Paulendo Mu 2019.
Ngati mumatha kubera muja mudachitira 2014 uja zachiteninso tero koma ziwani kuti Malawi wa lero si ogona ngati mudamuseweresa uja phunzirani ndikudziwa kuti Malawi adaona kuti kunja #kwacha , siogonanso ayi ndithu sanalani ndimau achibwana anuwo.
Koma ndiye nzosekatsa ndimaliro omwe ku mortuary mutangoyerekeza kuti tivotenso tonse mawa ngati ena simungadzinyonge mcp 2019 bomaaaa!
Ofcourse but someone else
Does it mean that people from central region and northern region have no blood ?Are these people the statues or else they have no life pls goverment take note and think
Comment reserved but why is it that blood suckers attack the people from southern region only?Does it mean people from central region
Kumalankhula kwambiri kuti Dausi azipsa mtima tiye nayeni namapopa ameneyu a malawi amawatengera kuntoso ngati nyama ya galu kkkkkk MCP ikulamula 2019
Uku ndikukula mtima
Kukanika kuvomereza basi a DPP bwanji chimanga mukugulana pa ubale wanu Soya tikungosunga mitengo manyaka mukut 2019 boma pano security palibe
Shame on you Dausi,,,shame on you!
Mwakhaulabe
Tabalotani mr Dausi ndi anzanu tambala wakuda ndiye wanyamuka ulendo wakusanjika…kayaaaaa!!!muzigwiraaa
Maso a atsogoleri a DPP ali pa chisankho cha 2019 mmalo mokonza mavuto omwe dziko likukumana nawo. So sad
we are the voters bear in your mind
Achedwa Atalawirira
Tamakanganani ine zisandikhuze
Akupenga ameneyu,,khala ndi DDP yakoyo mwinaso ndiwe modzi opopa magazi
Nde akamati ndale mesa ndi mpikitsano? Akamati mpikitsano, mesa amafuna pakhale wowina Kodi? Nde inu Mr Dausi, dzitsakho mwaluza! Koma your telling us kuti titsanamidzidwe cz 2019 mudzawina ndi, munalekeranji kuti muwine idzi mwagwanazodzi? Nde 2019 mudzachita kubera? Remember Mr Dausi, analanda ufumu kalero na wupereka kwa iyo, oyenera nchani chingamulake ambuye Mulungu ngwachirungamo!
ndichani chingamulake
DDP boma 2017 mufune musafune maliro akatuluka nyumba sabweleraso nyumba guyz
Adpp ni itsilu venven mbala
oky
Who gonna vote in 2019, I think is the same people who reject dpp now. What happened on this election is a warning call to dpp. Malawians have just showed dpp that they are regreting for putting Peter Muthalika on position in 2014. So enough is enough. Kabelatuni chabe musayembekezere za second term.
chakwerA z nt a foreiner
Mukunamatu bambo dausi
Kkkkkkkkk
Dpp ndiyofoila
Kkkkkkk dausi dausi. Munapusitsa bwana wanu kuti ntchito mwagwila kale? Tsopano mwayambaso kunamiza kuti koma 2019. Mmmmmm adausi muzavota mavoti angati?
Accept the defeat papa n there z more to come pull up ur socks n tuck in ur teeth
Kunena chilungamo zindunazi sizimamuuza chilangamo APM mumamunamiza kwambili
dpp ngati mukufuna mupitilize kulamulila do something presentable to malawians otherwise zitsanzo zake ndi mmene zayendelamu
Every journey starts with the first stèp even adownward one
Write a comment…wamkulu akamemyedwa savomeleza kut wamenyedwa sifusenikaya mumtimamwenumo ndiye muzoyankhula bwinozopandazeruzo.
Write a comment…
Odwala a Dausi ,olila samugwila kukamwa
Mudzabele2 Kmanso Ma Demo azagwira ntchito
apa ndipamene ndlama zitasowe mmalawi muno chifukwa azidziwiratu kuti mpando wapita
Chipani chilichoxe chikamalowa m’boma chimalowa bwino koma akakhala kathawi amaonetsa zintchito zosalongoxoka and izix from MCP. UDF. And DPP ruling
Dausi unless mutasiyakuba kumenye anthu mwina zikatheke
Chisonkho cha Mk250 000 chomwe mumandivulaza nacho chija, ndiye ndidzakupatseni inuyo vote yanga ? Misala, chani?
Dausi Muzazionela nokha 2019- yafikatu oponya vote ndefetu paja musaiwale ma business athu sakumaenda magesi akuvuta NDE tingakuvotele ……. Come 2019 tikumuona kuchedwa zathu zaima.
Zilimbanani mudzitizuza ,mmene mungathere
Chatsazo pankhani yomwei muone makomenti ngati atapezeka atatu ambaliyanu mulindimwayi.
Chokani apa anthu oipa inu. ichi ndichitsimikizo chokwanila kuti anthu sakukufunani ndimakhalidwe anu oipao kusasamala za anthu anu.. muziona chakachino.
Kumulanje vote yanu musawelengele kulibeko zanu zinaipa kale…
Muto ndiloti mwapanga athu mkhaza kwambiri mumatuma asilikali kumazunza anthu kuwamenya mpaka ena amaphedwa osalakwa ati mkhani yamatabwa.
.munthu
Mbuli izi abale ,can’t u see that people have spoken here through ballot paper,,wash ur linen at home,,wamkaka 2019
MCP 2019 boma,tikufuna tione zinthu zina than kumangokhalila kuhasula misonkho ya amphawi,pano mukuti tikhale ndi chiphatso cha udzika(Citizen ship ID) then it will expire after 5 yrs,after that tizikhomelano tsonkho lyk a motor vehicle insurance.
Sinanga mukufuna kudzaberanso ndi chilima wanuyo nde musamaletu chifukwa nafenso tracing with computer ndifenso machine mutu sukugwira iwe neba
KUGWA KWA BABULO UKO! EEEE SURE !
Mwatizuza kwakwana pano kwao gule kwao gule tione zina isaa!!
Kkkkk Zasintha mpikisano wa zipani, nanga zikanakhala dziko lonse mukanatani?
PALIBE ZOWINASO APA
Its 2_late dpp ituluka boma mboni ndi mulungu,and yemwe adzabele zisakho mulungu anzamulanga musatinamize a dpp but now taseguka maso
U know that iz not true,it iz my prayer that 2019 congres it iz going to became the lulers,but any bady who iz againest
Kodi Dausi kuyankhulila chifukwa chokula kamwa kapena kuti asakuchotse?your days are numbered in the government,
akuteteza udindo, kufuna kumupusitsa pitalayo.
Zilibwino abapusitsaana chomcho
ngati chipani chaluza by election chikulamula,ndiye kt nd chokf 2019 DPP chanu palibe.
Good job Bwana Dausi our underground mafia,tikudziwa kut mulinafe,mupangenso chimodzimodzi 2019 azikomedwa nanu kumakuonani ngati ndinu a DPP chonsecho muli a congress.
Kkkkkkkkkkkkk asaphyatira muwuze amvetse kkkkkkjkk azakhala spokesperson wathu hahahahahaa
waganiza bo kk.koma sitidzamulola
alibe malo mu mcp ameneyo!
Ndiwachisokonezo ameneyo ku MCP adzakhala munthu wamba basi
Never don’t think people are fools they got sense they got eyes and ears and they using their minds to vote
Kodi paja amati munthu ukamafa umayamba kugontha mapilikaniro.tizawin 2019 Azavote ndi ambuyako kapena amako.akukafuna ka jelemusi ka chipani kakoko ndindani? mukuona ngt anthu akumakuonelan kukondwa et?makape zopusa basi.
Ngat azavote ndiwowo azawina koma ngat ovota ndife omwe tavotera mcp pano 2019 ikutenga boma kut a DPP azipsa mtima MCP HOYEEEEEE!
zaziiiii,mcp szalamulila zkoli mulungu sangalole chakwela azikalalikila osati azipanga zandale,paja2 mcp imawina kulilongwe ndie musanyengeke ndi timasankho tachitikachi,ngat mukufuna kuzabesa mavot anu zavotelen mcp yanuo muzaziona
We will vote for MCP kumene DPP vindere vekhavekha mahule inu
mcp ndiyosusa mpakana kale ndie sngawine masankho olo zitavuta maka,kut ilamulile boma atamazasuse ndani?azawina kulilongweko basi
Khalamba zonse out in Jesus name.
Maloto achumba awaaa
kkkkkk apa bwana ndiye basi talimba mtima ndithu kuti DPP itule zida pasi ndipo 2019 idzaluza mochititsa mselu bomali tatopa nalo
Usamat ndadala usanawoloke tsinje wutazadza madzi.All days are not sunday they will see.Pira ndinthawi ya game ndipo nthawi ya practice c mpira.Agalatiya Woyamba ndizabwino koma matherowo
2019……
5 – 1 yomweyo kuti wawawa
Mwati 5 chani! Kodi ndi ma penalty
Chisankho Ichi Ndiye Chatitsegula Mmaso Ndipo Chatiuza Oyenera Kuwavotera Mu 2019.
Chisankho Ichi Ndiye Chatitsegula Mmaso Ndipo Chatiuza Oyenera Kuwavotera Mu 2019.
Achipasula Kambani Zoveka Ubusa Wake Ut Umeneo
Zikufuna zibeleso mbuzi zimenezi mwatikwana a DPP tioneko zina
RIP DPP
Makani inu mukupitiriza? Kunamiza anthu?
Akumva nyunyunyu….Ndepoti tangoyamba
A DPP Musadzataye Nthawi Ndikubwebweta Kuchita Kampeni Chifukwa Apa Za Onetselatu Kuti Amalawi Atopa Nanu.Dyelamtuni Komaliza Chifukwa 2019 M C P Boma!!! Tazuzika Mokwanila Tioneko Zina.DPP Inali Kale Ndimalemu Dr Bingu Osati Inu Mulipo Lero Yanga Vote Simudzaiona
Tamuzen avomele ameneu kuti 2019 sawina akunamidza insogoleliwayoo aawina akanene akafasa kwao
MCP coming wave after wave samala
Mcp 2019 Boma!!!!
Kulila ndi sample kkkkkkk
Kulila
Choka iwe bodza basi, kodi mtaba alikuti…kkkk
mare words can not fight ballots talks! Dausi has ran out of ideas, the DPP words has lost its fresh instead has arrested metaphorical values! Ankati mu boma lathu tizapanga service reform ya civil service, anthusazalandila ma chenji ankatanthauza kuti azatulusa k2000 note yolumala, amanena zoona kuti anthu zalandila yogwirana otsakhala ma chenji koma sikuti zizakhala zambiri mumene amganizira anzathu agwira ntchito mboma!MCP is sendi amessage! Wake up the sleeping government,
mare words can not fight ballots talks! Dausi has ran out of ideas, the DPP words has lost its fresh instead has arrested metaphorical values! Ankati mu boma lathu tizapanga service reform ya civil service, anthusazalandila ma chenji ankatanthauza kuti azatulusa k2000 note yolumala, amanena zoona kuti anthu zalandila yogwirana otsakhala ma chenji koma sikuti zizakhala zambiri mumene amganizira anzathu agwira ntchito mboma!MCP is sendi amessage! Wake up the sleeping government,
Mugwetsana ndi pp
Bola osazatibela, paja inu mumakonda zogogodana
Akunama amenewo 2019 mukupumabe
Akunama amenewo 2019 mukupumabe
Inu tazifusani za mmadera mukunyadilawo kuti mwawina,Dpp imavutika kupeza mipando.Apatu kukanakhala ku Mulanje,Phalombe,Chiradzulu,Zomba kapena Thyolo ayi apo ndiye tikanaziwa kuti Mcp izalamulanso,Inu mukunena za Nsanje ndi Lilongwe ayi melani mapiko MUZAZIONA.Chosangalatsa amzanutu sanapite ku Court,choncho tisazamve kuti wina wathamangila ku court.
Palibe kubera mu 2019 atolankhani adzakhalapo, kumaliza kumaliza kuwelenga nthawi yomweyo dziko lonse kudziwa M C P M P C ayiyaya
If u want to win 2019 General Elections please solve the Electricity problems firstly if not so.. ng’ooooo….!! vote yanga xmuzaiona
2o19 Iku Chedwa Bwanji,Adaus Ndi Azawo Atitopetsa Kwa Mbiri.
Kkk Mcp Boma Ana Achepa
KODI INU ADAUSI MOTI MUKUPITILIZA KUMANAMIZABE AMALAWI MALO MOKOZA MOLAKWIKAMO AAA CHITAMKONI MANYAZI ADAUSI
KODI INU ADAUSI MOTI MUKUPITILIZA KUMANAMIZABE AMALAWI MALO MOKOZA MOLAKWIKAMO AAA CHITAMKONI MANYAZI ADAUSI
DPP my foot
Kkk Kulira Kumeneku Adausi Mcp Woyeeeee 2019 Boma.
A Dausi musadzinamize, omwe tagwetsa DPP ndife ovota omwe zomwe dpp ikuchita zikutinyasa. Mumangolankhula osakwanilitsa zomwe anthu munawalonjeza. MCP is here to rule come 2019. Zanuzo tatopa nazo. Ndi chiyani chomwe simunachite chomwe mupange kuti anthu adzakukhulupilireni 2019? Nthawi mulibe. Zibwebwetani choncho. Ikakhala black out izi ndi zomwe dpp timazidziwa nayo ndipo blackoutiyo ipitilire kuti 2019 muczalire mayi wawaye.
Adausi mwasowa chokamba manyazi akugwireni
you can lead a horse to the river, but you can not force it to drink. mutha kuesetsa kukopa anthu ndi zilizonse zimene mulinazo, but u can’t force them to vote 4 u. if u don ‘t scale a mountain, its too hard to sea the plane. so if u have failed to success over this elections how can u false urself that u will win the game?
Mutha kuyankhula kuti mudzawina coz of yanu yija ya tsizina ntole,koma apa ingovomerezani kuti mwakanthidwa
u r leaving the office 2019 no matter what?
Muzakawina muzandidule ichichi
Kkkkk MCP sngazawine izingochedwa
Bulutu wamkulu m’dziko muno, ndameneyu
Njoka ikamafa imaphuphaphuphabe ndiye alekelenji a DPP
Agotomara a dpp alimbeso mau tikuyeniyeni pa 2019
ine ndikanena zinthu zimachitika i told u the pple tht dnt b fooled wth the gathering ya dpp chifukwa ama user anthu ambiri ochokera kutali chifukwa ali ndi access ya transport ya ma cars aboma ndiye ena anthu amabwera kudzaona ma cars woo take it all or leave it all its yo choice
Hahahahaha mwina akuganiza kuti njuchi zawo zija zinzavotaso njeee mwene bapakilani tatopa nanu
Kicks of a dying horse
Izizi ndizaulendo uno,chofunika kukhala maso tione kuti adzapanga chiyani kuti awine , popeza amuthalika ndi chipani chawo ife tadanazo kukhosi mavuto anji osatha kuyambira 2014 mpaka lero kumangoti zyenda mpaka liti. Tiwayesekoso anzanu tione kuti nawoso achita zotani.
Izizi ndizaulendo uno,chofunika kukhala maso tione kuti adzapanga chiyani kuti awine , popeza amuthalika ndi chipani chawo ife tadanazo kukhosi mavuto anji osatha kuyambira 2014 mpaka lero kumangoti zyenda mpaka liti. Tiwayesekoso anzanu tione kuti nawoso achita zotani.
Kulila kwa Cadet wamkulu
lets wait 2019 its nt far mch…
Mr Dausi pitilizani kumunamiza Peter timasangala ndizimenezo yankho 2019 tikupatsani zikomo
All I can see is denial and lack of self collection. Which killed MCP long ago. Now its face the real bosses the voters.
Mwana, listen to me….I am a DPP supporter, but if u really want to win the MEGA 2019 elections, u must(DPP) consider Wht Malawians are crying for. It’s almost everyone is complaining abt this GVT. Stop promising the people n start acting, time is not on ur side DPP. Solve these problems we are facing now, fulfill all the promises u made now b4 2019. U promised us abt University in Mzimba, a university in Bangula, a university in Nkhotakota, and now u keep promising us a university in Machinga/Mangochi….give us those Universities AND u solve electricity problem NOW!!!! I LIKE u mighty DPP thts why am giving u this kind of advice………long live NYASALAND!!
Hahahahahahahah musandisekese adausi hahahaha
Last kicks of a dying horse
Tiyeni uko inu Che Nicholas Dausi.
Korona pakhosi but still talking mabodza Bambo hahaaaaa
okufa anasiya mawu chachilendo palibepo apa dpp ulendo!!!!!.
DPP yachapidwabe 5 kwa 1!!!!!!!!!!!!!!
Adausi tiwakumbutse kuti amayika munthu pampando ndimulungu kudzera mwaanthu chisankho chachitikachi mwina kutheka samadziwa kuti angaluze ckoncho sibwino kutha mawu
Dausi kunyatsa ndi mtima omwe kkkkkkkkkk iwalani za utsogoleri mu 2019
Your tym z over now apa tkungodikira 2019 tione zina
Mmaloto anu a Dausi
Anthu Panopa Ayamba Kuzindikira Democaracy Yeniyeni Osati Kunamizidwa. 2019 Mcp Boma!!!!!
A foooooool Dausi napawpaw fufu man osaganiza
Mumalimbana ndikubweretsa mpungwepungwe ku MCP mmalo mokoza zofooka zanu. Shameful
dpp pansi … Mcp woye
Mudzawina munjira yanji kubera kapena anthu kukuvoterani? its a big warnning watch out Peter Dautsi asakupusise angofuna akukawe choona chili ndi anthu kumudzi ndipo adzayankhula 2019.
Kamwa sisiya mbuyake akufa. Ine chisankho chitabwera ngati ndi pa MCP po chonguuuuu ndipo sindinachongerepo yoluza.
aaaah maloto amenewo, mukuwona ngati tayiwala za maize gate? pita uko iwe!!!!
Mbava zakwapulidwa
Munazolowera kubera koma chaka chamawa nde muwona mbonawona….Mcp woyeeeeeeeeew,,,,,,
Mwaonjeza a DPP TNakukondani koma inu simukutukonda
Ukunama Dausi,uzalira iwe uzawakumbuka a Kamuzu
A Rasta gona laf hahahaha!!! wen babylon down falln
Zopusa Dausi palibe ntchito wagwira pa mwanza kuposa phungu wa kale inu ndiye mwaononga Mwanza bwenzi pano Blantyre itakumana ndi mwanza.
Uko kunali kulira kwa anamfedwa kkkkkkk
Koma akulu awanso
Mwatikwana.Agalu inu ine yanga simudzaiona soya,chimanga chikusowa msika pameme mukatiuza kuti tilime mbewuzi misika ilipo nandolo uyunso ma Indian’s amati akumufuna pano akusowa nawo kolowa ndiye mkumati mudzawina? Kapena mudzabela? Zakuvuta Kwa magesi pano tinangozolowela.
Ngati mukufuna kukonza DPP thamangitsani Dausi mwamva agalu inu
2019 mudzawinira kubera zitsilu lnu tchito zanutaziona mulibe zelu
Koma muzizindikira kuti, simiyala mumaitsogolera ndi anthu omwenso amafunanso kumapindura ndi zinthu zomwe dziko liri nazo.Osati Kumangoona m khuto wanu ndikungomachalira 2019.
No kaya yaluza inu si mulungu wait 4 2019 muzaone zimene mulungu wakonza dont judge fast
get off! DPP bunch of thugs. Iwe Dausi nawenso ukupanga maplan obwelera ku MCP. Iwe weka sitikulandila wa chewalised english ku MCP ayi takukana
DPP 2019 bomaaaa sitikutekeseka ndiwathu omwe mwangwilitsa ntchito ma blood sackers pobera mavoti
Ife Youth League timwa wamkaka 2019,munthu wa Mulungu waitha,mabanzi a Youth tadyanso.
Mukumunamiza Peter Mutharika inu.
PPLE MUST KNOW THAT, MCP IS GOING TO BE INCHARGE OF MALAWI. AND ALL OF DPP MEMBERS THEY MUST KNOW THAT THEY ARE ALSO GOING TO DIFETED IN 2OI9 AND EVEN THE ANGELS IN HEAVEN ARE ALSO SUPORTING DR L CHAKWELA AND TRULY IS 2O19 L CHAKWELA BOMA!!!!!!!!!!!!-
2019 I will be at my home town k u i will vote to who ever i want no 1 can tell me who to vote so politian be awere this is not usual story now is next generation that means no one can cheat who ever win u will be hold accoutable 4every thing remember we as people we are the 1 put u there and me have power to take u out we are ur booooses.
Tiyeni Amalawi Tidzakhale Tcheru Mu 2019, Chifukwa Gulu ili likukoza mapulani odzabera, mmalo mokoza mabvuto a dziko lino.. tipemphera ndi kukhala tcheru kuwonetsetsa asadzabe mavote, chilungamo chidzayende ngati mtsinje 2019 ndapemphera mu dzina la Yesu.. Amen
Sitizagona. Ma monitors sadzagona ndipo tizakhala cheru.
tidzamaka man palibe kupeleka mpata, adzalira kut chiiiiii!
mene atopera Amalawi azabeledwe azalola???
Anayesa kut abere ma by elections omwewa akanika…..tili mmaso 2019
I think Akufuna azagwilitse ntchito za registration makape amenewa, thats why akukakamiza kuti anthu alembetse.and anthu akulembetsa ndi azaka 16 kupita mtsogolo. Chilipo chomwe akufuna azachite makape amenewa
If u can’t beat them join them,,,Team MCP
Chisilu uyo galu ndi DPP yake
zoonadi a malawi talankhula Mulungu adalenga anthu ambiri anzeru ,ena atsogolerepo anthu tikulira koma mtsogoleri zosamukhudza akapume zatikwana .
Watch out DPP,ITS TOO LATE NOW.
Ndipo 2019 DPP ilamulanxo wina afune asafune vote yanga ndi ya peter
Ok mwene che Dausi.titere masamu ake:anthufe ambili tizavotera MCP ndpo izakhara nd mavot ambiri zed than you DPPs. koma koma muzawine ndiinuyo basi ngati zimatheka.Paja malemba amati chiyankheni chitsiru mogwilizana ndi uchitsilu wake.
Zimafunika kuwina kuti DPP izipsa mtima .2019 MCP boma .dausi akulota uyu mtayeni guyz
Koma aMalawi tikufunika kuti tidzuke, sinthawi yomalamulidwa ndi ma foreigner yino ayi…thats old fashion.
A malawi atopa nanu ,simukunvaa pati ?
Koma kt awone kt tatopa nawo, we should go in large numbers and vote them out!!! Agalu adpp awa.
a Dausi,”tsamba likagwa,manyazi amagwira mtengo” hahahaha
Kicks of a dying horse. Dausi ndi openga, uyu!!!
Amavotatu ndi anthu osauka amene akuvutika kumidziku osati inuyo kumipandokooo
Amwene olo atati MCP yawina nde mulemela? A MCP azigawa ndalama? Kuti musamavutike m’banja mwanu muzingolimbikira kugwira ntchito yo basi osati usogoleri wa dziko mudzalemela nawo
We don’t send our messages thru the mouth, we rather use a ballot, talk whatever you want, pitilizani propaganda mmene mungathere, but come 2019, we will use the ballot again and you can’t stop us- if you are thinking of your usual style of getting into the government, then ask Kenyatta! Africa ain’t the same!!!
Tibweza chipogwe chomwe mwatipanga,vote yanga inandipwetekesa this time sindipangaso mistake.
Hehedeeeee tionana 2019 MCP tinene kuti kwaaaachaaaaaa
ngat anagwa Belisazara,Mutharika ndan.Siku lokupha nyan mtengo umatelera.Chenjeran mukupita.
ADAUSI MUKUWONONGA CHIPANI APRESIDENT MUCHENJELE NAYE DAUSI .2019 IS NEAR
18 months to go!!
Nice
Kkkk DPP YATHADI ,,,,,,MCP TAKULANDIRANI TENGANI BOMA ,,,KULUZA PA HOME GROUND KKKK ZOCHITISA MANYA,,,,,,,,ZIIIIIIIII
Dying horse DPP
Ameneyo wanya nayo musiyeni bro @Denis
m’wanna mmmmmm, sichisankho choaintha boma ichi kuti chingapangise kukhala jenkha mmmm iyah asanyadile apapa mpomwe panels mangolomela tsopano kungowina uu m p mkumati eeeeeee ife kuunoo aaaa dza dziiiii
Zikuonetsa kuti a Dausi tanthauzo lakugwetsa sakulidziwa.
Timagwetsa chinthu chomwe chili choima kale ndiye mukuti come 2019 mudzagwetsa MCP kutanthauza kuti ndiyomwe ikulamula panopa eti?
Auzeni zoona anthu kuti talephera ndipo atibwenyula ndipo vomerezani kuti 2019 nkhondo iliko
Wailesi ikamatha ma batire ndi pang’onopang’ono zayambikapo apa. A Dausi tisiyanitsa bwanji ndi pumbwa mu mtengo wa kacher e abale
You can’t fool all the people all the times.
Uko kunali kuli kwanafedwa,anamalira patsogolo kenako ampingo pambuyo pakepo adzukulu onyara chitanda ena tonse pambuyo.kkkkkkkk 2019 mcp bomaaaaaaaaa.
kkkkkw
hahahaha…
Mwna sukudzwa Panop M C P Yatengak Kale Boma Inu Adpp Muperesekeko.
A DPP ndi zinkhalamba sizingatukule MW e.g Goodal Gondwe,Chaponda,Henery Musa,Ntaba,Dausi etc amagona mpariament ikangokwana 10AM Zimikonono kumachita kumveka pa TV let them out of office bola ta anyamatati tochita kuwala ngati maluwa mzimu woyera ukugwira ntchito
kkkk km cc wawaonjeza mpaka maloto mupaliament km m’busayu ndm’busa wathupi not uzimu khosa zauzimu zataika zambiri adzalipira mulandu umenewu kwa mulungu ukuona bwnj cc
Felister! ngati mukudziwa mfumu David(banja limene anabadwira Yesu) ndi mfumu Solomo yazeru amachita bwino pa ufumu wawo chifukwa chodziwa ndi kuopa Mulungu.Ufumuwuso ndi Utumiki chifukwa umasunga anthu a Mulungu inu simudziwa kuti Mulungu amagwiritsa ntchito mafumu ndipo ena amawadzoza ,Sauli bwa?
Zoona Joice kodi analemba pati kut m’busa sangakhale mtsogoleri…?????
Ili ndi bodza la mkung’unthiza dpp uwu ndi ulendo, ngati akuluza ma by elections ali mboma zimene zoti sizitheka wamba kuluza ichi mchiyambi chabe kuthasamuka mulira simunati balimbitsanani mtima
Truth Is pain dpp ili ngat njoka yomwe waimenya mutu ikungodupha dupha kuthatha ndi imfa dpp yalira ndi mkodzo wake omwe
Ayi Osamatukwana koma vomeleza ni abwana mwaluza chipani cha DPP chitha ngati makatani.Mwaluza ndiku lower shire komwe 2019 chipani cha dpp chizakhala chipani chachikulu chosusa boma kumalawi.Dpp WoooooooooYeeeeeeeeee!!!!!!
MIKHOZA Kufuna kuti muwine ngati DPP koma ovotafe sitizakuvotelaninso tizivotela MCP
Dpp Iwina Andichotsele Chaponda
Kkkkkk koma zikundipasa mphwete,ndipo ndakhulupilira kuti mawu akulu amakoma akagonera zoona izi zikuchitika mmalawi munozi? Palibepo ochokera kunja ayi onsewa ndiamomuno okhaokha ndithu.kukanganira zimatumba zandalama misokho yathu ndithu zafikapa ndi mtundu ndimtundu uzaukirana.wamaso apenye wakumva amve ndithu zapherezeradi.
Aaaaa mutuluka basi matikwana
You are like Mkango wopanda mano
Mwatibulidwa basi 2019 ndiye wakumanda basi.
Dausi Ndati Usalakhure Ngati Ukuuza Akazi Ako Kuchipinda.Uziganizila Za Anthu 17 Million.Sikuti Mudzatikakamiza Kuvota Tifunaso Sitingadzavotere Aliyese Chifukwa Mumachitayi Ndi Njuga Agalu Inu.
inu simumaziwa mpaka lero!! kkkkk ndani analuzapo pa kwao kkkkk chikanakhala kwina bwezi tikut MCP izawina koma LL hahahahahaha pakwao ndkumalalata choncho kkkkk mwagwanayo!! DPP ikuwina muziwe zmenezo
Mmmmmm mulibe ndimanyaz omwe….macadet opusa inu azakuvoteren ndan…. mukaganiza zobera zimenezo iwaran.. .
am not cadet!! don’t be stupid with your stupidity!!
Izawina pot iwe ulikujon abale ako ose olemela kale ana akwanu ose ophuzila bwino kut muzalinyenye zenzen tsopano dzikoli
I don’t care whether UDF, MCP, UMODZ, NDA, DPP……… I will support it!!!!! chomwe ndanenela kut munthu saluza pakwao kwa onse ondmvesa I think sipakana khala ndkumatukwana!!! for what?
Bwana Mulli!!! ndkanakonda zikanakhala choncho koma mukulakwisa, Agogo anga anabadwa before MCP time till today, she is poor and I was born in Muluzi time and I struggled to get this frog life! I don’t see who will be the president of Malawi only GOD know the one who will get us out of this life!!
MBAVA ZIMENEZI ZATILIZA MOKWANA ZIKUENELA UKAPUMa
Azakuvotereni nd ndani?
Kkkkkkkk Zitsiru Inu Ichindichiyambi Chabe Mukunya Nd Ka Pitala Kanuko.
DPP woyeeee!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
Kkkkkkk kulila namalila
Nanga zakupatsani picture yotani zomwe zachitikazi???????
Tiziti anthu akukondwera ndiutsogoleri wanu????
Simukudziwa zokut amalawi atopa ndikulamuliridwa ndianthu achikulire??????
Phunziro:a DPP stop counting chicken while eggs are hatching
Musakopeke ndichikhamu chopezeka pamisonkhano yanu pakut simudziwa zolinga zathu
STERN WARNING!!
The DPP GURUS Are Now Pressing A Panic Button,,,,They Have Smelt A Rat At Length…Their Days Are Now Numbered,,,,They Are Forcing Themselves Out Of The State House..The Government Which Has Failed To Impress Local Citizens Out-there..Talk Of “OPOPA MAGAZII Saga” Ku Mulanje Which Has Sparked Debate Country Wide…
Now Their Failure In The Just Ended By Elections Is A Clear Indication That They Will Be Booted Out Of Government Come 2019 General Elections..
I Can Agree With Hon. Dausi: My Free Advice Is; Please Go Back To The Round Table, Re-think, Re-adjust. Most Importantly, Listern To The Cries Of The People. DPP Has Sound Policies: What Is Now Needed Is Not To Talk About Them, But Act On Them! It Is Not Too Late For The Party. God Bless Malawi.
Your Stand Is Not Our Stand…
Oo! I don’t Need Yuor Stand
wateta boy apo
Iyi ndi 21st Century mwene u were trying ku zemba koma mwapeza zitseko zotseka ndipo muyerekeze 2019 kubera u will court red handed anthu akuona
Mwene Mwalasa,wakuba Mau Amat Afe Ndithu Ndiye Chilima Akabelaso Tidzamutentha.
Mwayiwala zimene mumatukwana pa campain yaku LL sopano nindani wangwa
Mcp Izalamulira zidzukulu tudzi za ine, osati m’badwo wa ineu uli moyo muiwale!!! Sindikuona chipani cholongosoka choima ndi dpp, sikoyamba mcp kuwina ma by elections! siine wa ndale ndangodutsamo,atawina mcp ndiye kuba, kungathe? ukulephela kugwila ntchito molimbika kudikila Chakwela Ng’ooooooooh!
auze sakudzwa ndiotembereredwa mu2 wangwro ungasiye ulemerero wakumwamba kusankha zadziko and azalipira mlandu omwaza khosa zamulungu m’malo mozikokera kwaiye
Panopa akt ndiowina wina koma azakhumudwatu
hahahaha awo anali anafedwa nawo kulilapo
Ine ndiye ai dausi ndi mzake azipakila basi ulendo ulipo azao alamulepo
Mumayenda mbali, mwakumana nazo
Paja olo nsomba ikafa imaphupha ndithu
Olira sagwiridwa pakamwa
Man ndikumamganitu chibwezi changa ndi chapolicetu ok?
Kkkkkkkk namalira
Uzakabela ngati 2014 uzawina koma pano Malawi inawona
Musinthe khalidwe tatopa kulekelera
What you should know is that action speaks louder than words. You can say what you want but come 2019 you are leaving the office for the New government.
Akalambanso awa we need new blood hiyaaa
Dr Laz mtima mmalo ma vote tiponya ndife
No more dpp we’re all tired of this sheet government.
Munya kulibe zakuba mu 2019 . Ufulu was democracy tinaupeza movutikila. Mwauseweletsa agulukunyinda inu. Dausi zimenezo uzimunamiza petro wakoyo koma iwe pansi pamtima ukusangalala ukuona ngati mu 2019 ungazalumphile yowina unyaaaaaaaaa
Mozambique
Kkk a kuziwa kuti athibulidwa eti kkk
DPP is died
Mupeze kosewela mwamva? tikudzavotela Chakwera ife!
Dup yatha amaona ngati bziko lino angathe kuye ndetsa ndi okha apa totse tiku ona otsatsekelela athu owonongawa titsawapatse pata.kkkkkkkkk
HA HA HA HA HA HA OLEMEKEZA BAMBO DAUSI UKU NDIYE KUMIRA PACHIPANDEE NDITHUU INUU MASOMPHENYAA AKUKANIKANI Tambala wakuda akubweraa WAVE AFTER WAVE kumeza chimangaaa Samalaa iweeeee
These idiots r making plan kuti adzabere mavoti
Uko kunali kulira kwa anafedwa dausi usamulimbix mtima peter apita amene uja
Walephera ku maka ndipo sudzamakanso
Kodi inu A DPP muli mutulo kodi amalawi musawasebelese 2019 zivute zitani muzachoka 2019 chakwera boma
Yes presidential polls will favour dpp come 2019, we can afford to hve kongelesi MPs but not president
Mmmmm inu ndi mulungu
no more DPP in 2019 and we dont love dausi thats why analephela pa zisankho za mp
Kubwebwetaku Z An Indicator Showing That Dpp Z In A Direma Towards 2019 Elections.Zikuonetselatu Kut Mwapweka Ngat Sima Yosapsa. Muziona Lelo N’chabe Koma 2019.Boma Losasamala Za A Malawi Ngat Dpp Ife Ayiiiii!!!
Tionana 2019 yomweyo!
Ma by election so ankat awina onse
Za ziii osangovomereza bwanji kuti ayamba kugwa pang’onopang’ono MCP 2019 boma basi phsyiiiiii!
Mutu sukugwira Mr
Ena amafa bhobho koma ena mavuvu mwina chifukwa chotamba
kkk koma ndaseka
Kkkkk kodi ovota azakhalanso ena,mayesa ndiomweo amawinisa mi pando 5 ku MCP,nde a DPP azawasintha kuvotela iwowo,iwale zimenezo,ine ovota ndiamene ndi kunena pano Kuti MCP 2019 BOMA!!!!!
Mwina kuzabwera ovota ena kkkkkkkkkk
Kkkkkkk,koma ndie
Auzeni!
YEMWE ANGAVOTELE KUZIMA KWA MAGESI NDANI?
Umbava wanu autulukila Kale. Kudzikuza kwanuko
ngat azavote okha
Already fall but vanish there party except bad history
Adausi vomerani kuti amalawi ayakhula kuti zomwe boma lanu likuchita anthu atopanazo
Tizunzeni mmene mungathere koma tsiku lina tidzaima mzere umodzi kudikira Chiweluzo
Musatengeke ndzokamba za dpp tipitiliza kuiponderera mpaka 2019 yatelo mcp.
last kicks of a dying mbuzi……..
Kkkkkkkkkkk uku nde kuwerengera madzi amphutsi
Izindiye Za Manyi Bola Sports Izi Ndi Zongolemetsana Zazi
mcp ..dpp…pp..amathandiza chani kodi mu malawi muno still mene tinatengera ufulu mpaka pano andale amangobwera kudzaba kumapita ife busy ndi zadzii makolo amene anamenyera ufulu atati adzuke akhonza kumva chisoni mwina kutitenganso kuti ananu tiyeni bola kumanda ….tisiye kupeleka ulemu kwa andale tikamagwadira timawapatsa matama
chomwe chimandinyasa heavy muzaona mcp kuzawina zomwez za dpp zizajoinaso mcp kumazabaso
exactly bro chifukwa chake sititukuka
sangavomere or atanyera pogona iye yemwe dausi
boza iwe palibe akulota zayinu 2019 kwatarika tikuwona kuchedwa
mdalayu akumupusitsa bwampini..
Mukunama
Kkkkkkk kuzilmbitsa mtma et? ovota ake anzakhare ndan,mwna ngat zizavote nd tchetche muzawina kma na anthu oganizafe mwaga nayo iy ynal chabe sample.
Kusafuna kuvomera. Yet they campaigned very hard with the entire President using the scarce public resources taking part. Choncho angasinthe awa.
Et boma kuluza,waku LL kno anampatsa 17M.Et amayendera makomo kumagawa soap nd mafuta.Amat door to door campain,
kkkkkkk
5-1 TEAM MCP
eee guyz just open and see!!! tiyeni nazoni km ndili. sure kt mcp 2019 bama kale!!!
Chokapo iwe
Ngati chipani chanu sichisitha tchito zake yiwalani mawu amenewo osamayakhula ngati adzavote ndi ambwiyako okha ayi ovata ndi a Malawi omwe akuwona mmene chipani chanu chikuwonongela dziko…… foolish government
Ameneyo ndi talking parrot
Kwachaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaa
Kkkkk aganizenso ka 2
Olira samutengera zoyankhula zake… chimakhala chisoni
Zoona braz kkkkkkk
Ndavetsetsa
Zowona man olira samutapa mkamwa.
Adzathawa awa
amayankhulira kuti izizi? komaso kuwina kuli madera aketu,eg-dpp singawine ku lilongwe south,mcp singawine ku mulanje/tcholo,izi mukuenela kudziwa
chipani chikamaluza chimaluza ndi anthu ngati amenewa amene amakhalira kumanamiza azitsogoleri awo kuti zinthu ziri bwino pomwe siziribwino nkomwe. inu taganizani 5-1 nde wina aziima pa chulu nkumanama? kkkkk
They loose 2 Parliament seat at piliament for Lilongwe and nsanje ndiye akuzilimbikisa chani we will vote DPP out
hhh wa dpp apse mtima
Kukana kuvomeleza kkkkkkk
Wasuta chamba eti.?
will be silent just waiting for 2019,,,this must be a warning to all DPP. Malawi akuyankhula yekha apa
Mudzachita kuberatu
Yeah azachita kubeladi ndi chimene akudalira sakuvomeleza zazi
Kkkkkkkkkkkkkkkk anthu lero adadziwa choonadi. Ukadziwa choonadi chimakumasula
KKKKKKKKKKKK akunamatu amenewa tell them
Ma vote anu mpando wanthu team #DPP
kubatu,.,.
sizikutengera zimenezo #Dpp
DPP MBAVA INU NSITINGAKUVOTELENI, NGAKHALE VOTE YANGA SINDINGAKUPANSENI MBAVA INU,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,, MCP BOMA 2019
we acan’t vote for DPP ONLY CORRUPTION: MCP BOMA
Just accept Mr Dausi.2019 MCP Bomaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaa.