Musanyengeke ndi zotsatila za chisankho chapadera, ife tigwetsa Kongeresi mu 2019 – atelo a DPP

345

Amene amayesa kuti chipani cholamula cha DPP chatha ndi kufelatu basi kamba koti chathibulidwa ka ‘5 kwa 1’ ndi chipani chotsutsa cha Kongeresi, ati aganizenso kawiri.

Malinga ndi mneneri wa boma a Nicholas Dausi amene alinso wamkulu wa chipani cholamula, kusachita bwino pa zisankho za padera sikukusonyeza kuti iwo afa basi.

Sidik Mia

Dausi: 2019 tiphukilanso.

“Mwanna, musanyengeke ndipo musakomedwe konse. 2019 tiphukilanso ndipo Tambala wadya Chimanga uja timupanga phwando. A Kongeresi alilanso kuti Mayi wawaye,” anatelo a Dausi.

A Dausi anaonjezelapo kuti kugonja kwachitika pano kupangitsa chipani cha DPP kuti chilongosole zinthu kuti pa 2019 azamwe wa mkaka.

“Mbamba khulupilila, pendapenda sikugwa. Ife tachita pendapenda apa sikuti tagwa tonse ayi. Mtunda udakali,” anapitiliza motelo a Dausi.

Chipani cholamula cha DPP chaonetsedwa mbwadza pa chisankho chapadela chomwe chinachitika mu madera osankhika lachiwiri.

Pa madera asanu ndi limodzi, Kongeresi yapambana madera asanu ndi kusiyila DPP ka dera kamodzi basi.

Share.

345 Comments

 1. Mr Dausi dont cheat people of Malawi, its only those who do evil like DPP .vomelezani kuti chipani chanu chilibe mwai ku Malawi and people hv lost trust in u becouse of corruption,

 2. I have a message for my beloved hon Dausi. The man is so talented that I wonder why he is sticking to a sinking boat. He is in the wrong boat. He is like Jonah in a boat that is sinking whose only solution is to throw Mr Dausi in the waters so that he swims back to MCP. He was with Kamuzu, and the spirit of Kamuzu is not happy that he damped the party. Mr Dausi think twice, repent and come back to your father’s party. I liken him also to mwana olowerera

 3. osayiwara kuti woonelera umaphweka mpira amatha masapota kuchinya messi asanamenye buluti pa golo ,DPP i zawina chifukwa anthu amafuna chitukuko cholozeka ndimaso,kuyipitsana mbiri cholinga inuwotsutsa mukhare azeru .kwa athu aluzawo zoti kwawoko sakuwafuna

 4. osayiwara kuti woonelera umaphweka mpira amatha masapota kuchinya messi asanamenye buluti pa golo ,DPP i zawina chifukwa anthu amafuna chitukuko cholozeka ndimaso,kuyipitsana mbiri cholinga inuwotsutsa mukhare azeru .kwa athu aluzawo zoti kwawoko sakuwafuna

 5. This loss it’s a bad sign, myself I voted for DPP, but frankly speaking anthu akuchidandaula chipanichi, some of the leaders kudzikonda kwambiri, even campaigning materials kumawumila e.g nsalu osagawa zokwana bwanji? Don’t expect to win in 2019, if you’re not going use the grassroots team.

 6. bvuto mu dpp ndikuchenjera mopusa azitsogoleri ake.Mumaoneka ngat anzeru pomwe munachoka ku#udf panopa uchitsilu wanu inu a dpp olo mwana akuudziwa.Yafikano nthawi yot mukukute mano.Apa mpango ndimaso mphenya chabe apa tiyeni ku 2019 muzakomoka.Agaru inu mwatikwana over and over

 7. bvuto mu dpp ndikuchenjera mopusa azitsogoleri ake.Mumaoneka ngat anzeru pomwe munachoka ku#udf panopa uchitsilu wanu inu a dpp olo mwana akuudziwa.Yafikano nthawi yot mukukute mano.Apa mpango ndimaso mphenya chabe apa tiyeni ku 2019 muzakomoka.Agaru inu mwatikwana over and over

 8. Tizavotera dpp yomweyo mcp yaba kwa nthawi yayitali zaka 30 ndye mkumati mukufuna kulowa m’boma muzachitamo chani komaso mukati new blood mukutanthauza chani ? Popeza anthu ake ndi omwe aja ankaba ku mcp kalekale aja ndye mukufuna muzabeso zaka 30 sizinakukwaneni asaaaaa

 9. Mudzagwetsa ndi chiani? Simukunena kuti tidzayetsetsa kukopa a malawi kuti adzativotere koma mukungoti tigwetsa kapena ndi yomwe IJA? Mdzina LA Yesu Khristu tikukaniza machenjelero a mdierekezi pa chisankho cha 2019, amen.

 10. Kwaine sindimaona wachilungamo pakati pawandale if u want our country to develop tiyeni tisinthe kaendesedwe kaboma chifukwa onsewa posiya zomwe ankapanga kulowa ndale cholinga sichina ait koma ndalama zoti alemele .

 11. No chance DPP in 2019 because it is good for nothing, Whoever say DPP Will win in 2019 He/she is wasting time, people hv notes that the only way of getting rid of problems we have now is to remove it from power, you will see when 2019 comes.

 12. Mpaka Mcp Kuwina Ku Nsanje.Koma Zomakhomera Unzika Tili Nzika Kale Mukufuna Mutinzunze Dziko Lokhala Lathu Sitilora Its Beta Kwa Falao, Dpp Paulendo Mu 2019.

 13. Mpaka Mcp Kuwina Ku Nsanje.Koma Zomakhomera Unzika Tili Nzika Kale Mukufuna Mutinzunze Dziko Lokhala Lathu Sitilora Its Beta Kwa Falao, Dpp Paulendo Mu 2019.

 14. Ngati mumatha kubera muja mudachitira 2014 uja zachiteninso tero koma ziwani kuti Malawi wa lero si ogona ngati mudamuseweresa uja phunzirani ndikudziwa kuti Malawi adaona kuti kunja #kwacha , siogonanso ayi ndithu sanalani ndimau achibwana anuwo.

 15. Does it mean that people from central region and northern region have no blood ?Are these people the statues or else they have no life pls goverment take note and think

 16. Kumalankhula kwambiri kuti Dausi azipsa mtima tiye nayeni namapopa ameneyu a malawi amawatengera kuntoso ngati nyama ya galu kkkkkk MCP ikulamula 2019

 17. Kukanika kuvomereza basi a DPP bwanji chimanga mukugulana pa ubale wanu Soya tikungosunga mitengo manyaka mukut 2019 boma pano security palibe

 18. Nde akamati ndale mesa ndi mpikitsano? Akamati mpikitsano, mesa amafuna pakhale wowina Kodi? Nde inu Mr Dausi, dzitsakho mwaluza! Koma your telling us kuti titsanamidzidwe cz 2019 mudzawina ndi, munalekeranji kuti muwine idzi mwagwanazodzi? Nde 2019 mudzachita kubera? Remember Mr Dausi, analanda ufumu kalero na wupereka kwa iyo, oyenera nchani chingamulake ambuye Mulungu ngwachirungamo!

 19. Who gonna vote in 2019, I think is the same people who reject dpp now. What happened on this election is a warning call to dpp. Malawians have just showed dpp that they are regreting for putting Peter Muthalika on position in 2014. So enough is enough. Kabelatuni chabe musayembekezere za second term.

 20. Kunena chilungamo zindunazi sizimamuuza chilangamo APM mumamunamiza kwambili
  dpp ngati mukufuna mupitilize kulamulila do something presentable to malawians otherwise zitsanzo zake ndi mmene zayendelamu

 21. Dausi Muzazionela nokha 2019- yafikatu oponya vote ndefetu paja musaiwale ma business athu sakumaenda magesi akuvuta NDE tingakuvotele ……. Come 2019 tikumuona kuchedwa zathu zaima.

 22. Chokani apa anthu oipa inu. ichi ndichitsimikizo chokwanila kuti anthu sakukufunani ndimakhalidwe anu oipao kusasamala za anthu anu.. muziona chakachino.

 23. Kumulanje vote yanu musawelengele kulibeko zanu zinaipa kale…
  Muto ndiloti mwapanga athu mkhaza kwambiri mumatuma asilikali kumazunza anthu kuwamenya mpaka ena amaphedwa osalakwa ati mkhani yamatabwa.
  .munthu

 24. MCP 2019 boma,tikufuna tione zinthu zina than kumangokhalila kuhasula misonkho ya amphawi,pano mukuti tikhale ndi chiphatso cha udzika(Citizen ship ID) then it will expire after 5 yrs,after that tizikhomelano tsonkho lyk a motor vehicle insurance.

 25. Sinanga mukufuna kudzaberanso ndi chilima wanuyo nde musamaletu chifukwa nafenso tracing with computer ndifenso machine mutu sukugwira iwe neba

 26. Good job Bwana Dausi our underground mafia,tikudziwa kut mulinafe,mupangenso chimodzimodzi 2019 azikomedwa nanu kumakuonani ngati ndinu a DPP chonsecho muli a congress.

 27. Kodi paja amati munthu ukamafa umayamba kugontha mapilikaniro.tizawin 2019 Azavote ndi ambuyako kapena amako.akukafuna ka jelemusi ka chipani kakoko ndindani? mukuona ngt anthu akumakuonelan kukondwa et?makape zopusa basi.

 28. zaziiiii,mcp szalamulila zkoli mulungu sangalole chakwela azikalalikila osati azipanga zandale,paja2 mcp imawina kulilongwe ndie musanyengeke ndi timasankho tachitikachi,ngat mukufuna kuzabesa mavot anu zavotelen mcp yanuo muzaziona

 29. Usamat ndadala usanawoloke tsinje wutazadza madzi.All days are not sunday they will see.Pira ndinthawi ya game ndipo nthawi ya practice c mpira.Agalatiya Woyamba ndizabwino koma matherowo

 30. A DPP Musadzataye Nthawi Ndikubwebweta Kuchita Kampeni Chifukwa Apa Za Onetselatu Kuti Amalawi Atopa Nanu.Dyelamtuni Komaliza Chifukwa 2019 M C P Boma!!! Tazuzika Mokwanila Tioneko Zina.DPP Inali Kale Ndimalemu Dr Bingu Osati Inu Mulipo Lero Yanga Vote Simudzaiona

 31. mare words can not fight ballots talks! Dausi has ran out of ideas, the DPP words has lost its fresh instead has arrested metaphorical values! Ankati mu boma lathu tizapanga service reform ya civil service, anthusazalandila ma chenji ankatanthauza kuti azatulusa k2000 note yolumala, amanena zoona kuti anthu zalandila yogwirana otsakhala ma chenji koma sikuti zizakhala zambiri mumene amganizira anzathu agwira ntchito mboma!MCP is sendi amessage! Wake up the sleeping government,

 32. mare words can not fight ballots talks! Dausi has ran out of ideas, the DPP words has lost its fresh instead has arrested metaphorical values! Ankati mu boma lathu tizapanga service reform ya civil service, anthusazalandila ma chenji ankatanthauza kuti azatulusa k2000 note yolumala, amanena zoona kuti anthu zalandila yogwirana otsakhala ma chenji koma sikuti zizakhala zambiri mumene amganizira anzathu agwira ntchito mboma!MCP is sendi amessage! Wake up the sleeping government,

 33. Inu tazifusani za mmadera mukunyadilawo kuti mwawina,Dpp imavutika kupeza mipando.Apatu kukanakhala ku Mulanje,Phalombe,Chiradzulu,Zomba kapena Thyolo ayi apo ndiye tikanaziwa kuti Mcp izalamulanso,Inu mukunena za Nsanje ndi Lilongwe ayi melani mapiko MUZAZIONA.Chosangalatsa amzanutu sanapite ku Court,choncho tisazamve kuti wina wathamangila ku court.

 34. If u want to win 2019 General Elections please solve the Electricity problems firstly if not so.. ng’ooooo….!! vote yanga xmuzaiona

 35. A Dausi musadzinamize, omwe tagwetsa DPP ndife ovota omwe zomwe dpp ikuchita zikutinyasa. Mumangolankhula osakwanilitsa zomwe anthu munawalonjeza. MCP is here to rule come 2019. Zanuzo tatopa nazo. Ndi chiyani chomwe simunachite chomwe mupange kuti anthu adzakukhulupilireni 2019? Nthawi mulibe. Zibwebwetani choncho. Ikakhala black out izi ndi zomwe dpp timazidziwa nayo ndipo blackoutiyo ipitilire kuti 2019 muczalire mayi wawaye.

 36. you can lead a horse to the river, but you can not force it to drink. mutha kuesetsa kukopa anthu ndi zilizonse zimene mulinazo, but u can’t force them to vote 4 u. if u don ‘t scale a mountain, its too hard to sea the plane. so if u have failed to success over this elections how can u false urself that u will win the game?

 37. ine ndikanena zinthu zimachitika i told u the pple tht dnt b fooled wth the gathering ya dpp chifukwa ama user anthu ambiri ochokera kutali chifukwa ali ndi access ya transport ya ma cars aboma ndiye ena anthu amabwera kudzaona ma cars woo take it all or leave it all its yo choice

 38. Izizi ndizaulendo uno,chofunika kukhala maso tione kuti adzapanga chiyani kuti awine , popeza amuthalika ndi chipani chawo ife tadanazo kukhosi mavuto anji osatha kuyambira 2014 mpaka lero kumangoti zyenda mpaka liti. Tiwayesekoso anzanu tione kuti nawoso achita zotani.

 39. Izizi ndizaulendo uno,chofunika kukhala maso tione kuti adzapanga chiyani kuti awine , popeza amuthalika ndi chipani chawo ife tadanazo kukhosi mavuto anji osatha kuyambira 2014 mpaka lero kumangoti zyenda mpaka liti. Tiwayesekoso anzanu tione kuti nawoso achita zotani.

 40. Mwana, listen to me….I am a DPP supporter, but if u really want to win the MEGA 2019 elections, u must(DPP) consider Wht Malawians are crying for. It’s almost everyone is complaining abt this GVT. Stop promising the people n start acting, time is not on ur side DPP. Solve these problems we are facing now, fulfill all the promises u made now b4 2019. U promised us abt University in Mzimba, a university in Bangula, a university in Nkhotakota, and now u keep promising us a university in Machinga/Mangochi….give us those Universities AND u solve electricity problem NOW!!!! I LIKE u mighty DPP thts why am giving u this kind of advice………long live NYASALAND!!

 41. Adausi tiwakumbutse kuti amayika munthu pampando ndimulungu kudzera mwaanthu chisankho chachitikachi mwina kutheka samadziwa kuti angaluze ckoncho sibwino kutha mawu

 42. Mudzawina munjira yanji kubera kapena anthu kukuvoterani? its a big warnning watch out Peter Dautsi asakupusise angofuna akukawe choona chili ndi anthu kumudzi ndipo adzayankhula 2019.

 43. Mwatikwana.Agalu inu ine yanga simudzaiona soya,chimanga chikusowa msika pameme mukatiuza kuti tilime mbewuzi misika ilipo nandolo uyunso ma Indian’s amati akumufuna pano akusowa nawo kolowa ndiye mkumati mudzawina? Kapena mudzabela? Zakuvuta Kwa magesi pano tinangozolowela.

 44. Koma muzizindikira kuti, simiyala mumaitsogolera ndi anthu omwenso amafunanso kumapindura ndi zinthu zomwe dziko liri nazo.Osati Kumangoona m khuto wanu ndikungomachalira 2019.

 45. get off! DPP bunch of thugs. Iwe Dausi nawenso ukupanga maplan obwelera ku MCP. Iwe weka sitikulandila wa chewalised english ku MCP ayi takukana

 46. PPLE MUST KNOW THAT, MCP IS GOING TO BE INCHARGE OF MALAWI. AND ALL OF DPP MEMBERS THEY MUST KNOW THAT THEY ARE ALSO GOING TO DIFETED IN 2OI9 AND EVEN THE ANGELS IN HEAVEN ARE ALSO SUPORTING DR L CHAKWELA AND TRULY IS 2O19 L CHAKWELA BOMA!!!!!!!!!!!!-

 47. 2019 I will be at my home town k u i will vote to who ever i want no 1 can tell me who to vote so politian be awere this is not usual story now is next generation that means no one can cheat who ever win u will be hold accoutable 4every thing remember we as people we are the 1 put u there and me have power to take u out we are ur booooses.

 48. Tiyeni Amalawi Tidzakhale Tcheru Mu 2019, Chifukwa Gulu ili likukoza mapulani odzabera, mmalo mokoza mabvuto a dziko lino.. tipemphera ndi kukhala tcheru kuwonetsetsa asadzabe mavote, chilungamo chidzayende ngati mtsinje 2019 ndapemphera mu dzina la Yesu.. Amen

 49. zoonadi a malawi talankhula Mulungu adalenga anthu ambiri anzeru ,ena atsogolerepo anthu tikulira koma mtsogoleri zosamukhudza akapume zatikwana .

 50. Ok mwene che Dausi.titere masamu ake:anthufe ambili tizavotera MCP ndpo izakhara nd mavot ambiri zed than you DPPs. koma koma muzawine ndiinuyo basi ngati zimatheka.Paja malemba amati chiyankheni chitsiru mogwilizana ndi uchitsilu wake.

  • Amwene olo atati MCP yawina nde mulemela? A MCP azigawa ndalama? Kuti musamavutike m’banja mwanu muzingolimbikira kugwira ntchito yo basi osati usogoleri wa dziko mudzalemela nawo

 51. We don’t send our messages thru the mouth, we rather use a ballot, talk whatever you want, pitilizani propaganda mmene mungathere, but come 2019, we will use the ballot again and you can’t stop us- if you are thinking of your usual style of getting into the government, then ask Kenyatta! Africa ain’t the same!!!

 52. m’wanna mmmmmm, sichisankho choaintha boma ichi kuti chingapangise kukhala jenkha mmmm iyah asanyadile apapa mpomwe panels mangolomela tsopano kungowina uu m p mkumati eeeeeee ife kuunoo aaaa dza dziiiii

 53. Zikuonetsa kuti a Dausi tanthauzo lakugwetsa sakulidziwa.
  Timagwetsa chinthu chomwe chili choima kale ndiye mukuti come 2019 mudzagwetsa MCP kutanthauza kuti ndiyomwe ikulamula panopa eti?
  Auzeni zoona anthu kuti talephera ndipo atibwenyula ndipo vomerezani kuti 2019 nkhondo iliko

 54. A DPP ndi zinkhalamba sizingatukule MW e.g Goodal Gondwe,Chaponda,Henery Musa,Ntaba,Dausi etc amagona mpariament ikangokwana 10AM Zimikonono kumachita kumveka pa TV let them out of office bola ta anyamatati tochita kuwala ngati maluwa mzimu woyera ukugwira ntchito

  • kkkk km cc wawaonjeza mpaka maloto mupaliament km m’busayu ndm’busa wathupi not uzimu khosa zauzimu zataika zambiri adzalipira mulandu umenewu kwa mulungu ukuona bwnj cc

  • Felister! ngati mukudziwa mfumu David(banja limene anabadwira Yesu) ndi mfumu Solomo yazeru amachita bwino pa ufumu wawo chifukwa chodziwa ndi kuopa Mulungu.Ufumuwuso ndi Utumiki chifukwa umasunga anthu a Mulungu inu simudziwa kuti Mulungu amagwiritsa ntchito mafumu ndipo ena amawadzoza ,Sauli bwa?

 55. Ili ndi bodza la mkung’unthiza dpp uwu ndi ulendo, ngati akuluza ma by elections ali mboma zimene zoti sizitheka wamba kuluza ichi mchiyambi chabe kuthasamuka mulira simunati balimbitsanani mtima

 56. Ayi Osamatukwana koma vomeleza ni abwana mwaluza chipani cha DPP chitha ngati makatani.Mwaluza ndiku lower shire komwe 2019 chipani cha dpp chizakhala chipani chachikulu chosusa boma kumalawi.Dpp WoooooooooYeeeeeeeeee!!!!!!

 57. Kkkkkk koma zikundipasa mphwete,ndipo ndakhulupilira kuti mawu akulu amakoma akagonera zoona izi zikuchitika mmalawi munozi? Palibepo ochokera kunja ayi onsewa ndiamomuno okhaokha ndithu.kukanganira zimatumba zandalama misokho yathu ndithu zafikapa ndi mtundu ndimtundu uzaukirana.wamaso apenye wakumva amve ndithu zapherezeradi.

 58. Dausi Ndati Usalakhure Ngati Ukuuza Akazi Ako Kuchipinda.Uziganizila Za Anthu 17 Million.Sikuti Mudzatikakamiza Kuvota Tifunaso Sitingadzavotere Aliyese Chifukwa Mumachitayi Ndi Njuga Agalu Inu.

 59. inu simumaziwa mpaka lero!! kkkkk ndani analuzapo pa kwao kkkkk chikanakhala kwina bwezi tikut MCP izawina koma LL hahahahahaha pakwao ndkumalalata choncho kkkkk mwagwanayo!! DPP ikuwina muziwe zmenezo

 60. Nanga zakupatsani picture yotani zomwe zachitikazi???????

  Tiziti anthu akukondwera ndiutsogoleri wanu????

  Simukudziwa zokut amalawi atopa ndikulamuliridwa ndianthu achikulire??????

  Phunziro:a DPP stop counting chicken while eggs are hatching

  Musakopeke ndichikhamu chopezeka pamisonkhano yanu pakut simudziwa zolinga zathu

 61. STERN WARNING!!

  The DPP GURUS Are Now Pressing A Panic Button,,,,They Have Smelt A Rat At Length…Their Days Are Now Numbered,,,,They Are Forcing Themselves Out Of The State House..The Government Which Has Failed To Impress Local Citizens Out-there..Talk Of “OPOPA MAGAZII Saga” Ku Mulanje Which Has Sparked Debate Country Wide…

  Now Their Failure In The Just Ended By Elections Is A Clear Indication That They Will Be Booted Out Of Government Come 2019 General Elections..

 62. I Can Agree With Hon. Dausi: My Free Advice Is; Please Go Back To The Round Table, Re-think, Re-adjust. Most Importantly, Listern To The Cries Of The People. DPP Has Sound Policies: What Is Now Needed Is Not To Talk About Them, But Act On Them! It Is Not Too Late For The Party. God Bless Malawi.

 63. Iyi ndi 21st Century mwene u were trying ku zemba koma mwapeza zitseko zotseka ndipo muyerekeze 2019 kubera u will court red handed anthu akuona

 64. Mcp Izalamulira zidzukulu tudzi za ine, osati m’badwo wa ineu uli moyo muiwale!!! Sindikuona chipani cholongosoka choima ndi dpp, sikoyamba mcp kuwina ma by elections! siine wa ndale ndangodutsamo,atawina mcp ndiye kuba, kungathe? ukulephela kugwila ntchito molimbika kudikila Chakwela Ng’ooooooooh!

 65. What you should know is that action speaks louder than words. You can say what you want but come 2019 you are leaving the office for the New government.

 66. Munya kulibe zakuba mu 2019 . Ufulu was democracy tinaupeza movutikila. Mwauseweletsa agulukunyinda inu. Dausi zimenezo uzimunamiza petro wakoyo koma iwe pansi pamtima ukusangalala ukuona ngati mu 2019 ungazalumphile yowina unyaaaaaaaaa

 67. HA HA HA HA HA HA OLEMEKEZA BAMBO DAUSI UKU NDIYE KUMIRA PACHIPANDEE NDITHUU INUU MASOMPHENYAA AKUKANIKANI Tambala wakuda akubweraa WAVE AFTER WAVE kumeza chimangaaa Samalaa iweeeee

 68. Kubwebwetaku Z An Indicator Showing That Dpp Z In A Direma Towards 2019 Elections.Zikuonetselatu Kut Mwapweka Ngat Sima Yosapsa. Muziona Lelo N’chabe Koma 2019.Boma Losasamala Za A Malawi Ngat Dpp Ife Ayiiiii!!!

 69. Kkkkk kodi ovota azakhalanso ena,mayesa ndiomweo amawinisa mi pando 5 ku MCP,nde a DPP azawasintha kuvotela iwowo,iwale zimenezo,ine ovota ndiamene ndi kunena pano Kuti MCP 2019 BOMA!!!!!

 70. mcp ..dpp…pp..amathandiza chani kodi mu malawi muno still mene tinatengera ufulu mpaka pano andale amangobwera kudzaba kumapita ife busy ndi zadzii makolo amene anamenyera ufulu atati adzuke akhonza kumva chisoni mwina kutitenganso kuti ananu tiyeni bola kumanda ….tisiye kupeleka ulemu kwa andale tikamagwadira timawapatsa matama

 71. Kkkkkkk kuzilmbitsa mtma et? ovota ake anzakhare ndan,mwna ngat zizavote nd tchetche muzawina kma na anthu oganizafe mwaga nayo iy ynal chabe sample.

 72. Ngati chipani chanu sichisitha tchito zake yiwalani mawu amenewo osamayakhula ngati adzavote ndi ambwiyako okha ayi ovata ndi a Malawi omwe akuwona mmene chipani chanu chikuwonongela dziko…… foolish government

 73. chipani chikamaluza chimaluza ndi anthu ngati amenewa amene amakhalira kumanamiza azitsogoleri awo kuti zinthu ziri bwino pomwe siziribwino nkomwe. inu taganizani 5-1 nde wina aziima pa chulu nkumanama? kkkkk

 74. DPP MBAVA INU NSITINGAKUVOTELENI, NGAKHALE VOTE YANGA SINDINGAKUPANSENI MBAVA INU,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,, MCP BOMA 2019