November promises to be a good month for Malawians and Chaponda.
Comedian Daliso Chaponda will be in the country in November where he will entertain comedy lovers in the city of Blantyre before moving to Lilongwe.
Chaponda who was a finalist in the British Got Talent competition is expected to entertain patrons at Victoria Gardens in Blantyre.
In Lilongwe, he is expected to do the same at the Bingu International Conference Centre.
This will be the first time that Chaponda will be performing in Malawi after his newly found fame that has come owing to his appearance on the BGT show in United Kingdom.
why is he going to Malawi now??…..is it because he is a tv star??
Akuzatenganso ndalama zina……. i cant guess gate imeneyi ikhale chani kaya
His home coming has nothing to do with his father’s atrocities. Remember, he is simply an entertainer not a politician
Nkhuyu zodya Bambo chimanga zidapota mwana chaponda..azikabwebweta yekha..sindizavayako..
Home sweet home Dalitso
Akuzabaso chimanga ameneyo ngati abambo ake
Zimayamba choncho, kenaka tikuva akuyima u MP, Ku mulanje, kenaka nduna, kutilamulira ife tili vwiii kumawomba m,manja.
KKKKK!!bola mukudziwa
Balamanthu watulukira kaloswe 2 undisamare ndikanabwera komweka koma ndalama ndizomwe adaba kaloswe 1 zo
guyz pali ubale wanji iyeyu ndi. a chaponda omwe tijuwaziwa
Witchcraft is sending your son overseas to study medicine only to come back as a stand up comedian
Kkkkk
Mukamalemba mitu yankhani mudziyamba bwino maina enawa mukamangofikira kuwatchula mitima yathu imalapuka nkuyamba kusaka palimwala wachilengedwe kuti tiuvunge.
Cde mwandipatsa phwete with your wording
Nanga kungofikira “Chaponda”. Alaaa maina awa siabwinonso kuwamva. Mtimawu umayaka moto kkkk
Ine kungomva kuti Chaponda matumbo anga akuchita kulumpha mmimbamu moti ndikusakasaka pamene ndinayika chibonga ndimkondo ndikathane naye basi anandimvetsa kuwawa tatewake
Ha hahahahshshshshsh. …. some journalists are not serious with their professional
Kkkkkkk mpaka” kulapuka “ndaseka
Eeeetu ukamva dzina lamunthu amene anakubwitika mchenga mkamwa mtima umachita kulapuka. Kufuna kubweza mowawa kkkkk
Akulu mwandisekesa eshiiii
U made my fridy….chamba mchabwinodi kkkkkkkkkk
Kkkkkkkkk
Kkkkkkkk koma
tikaseka bwanji atate ake atizunza ndalama kumamphunzitsira iyeyu.shame
Al the time Blantyre and lilongwe what about mzuzu
ku Mzuzu ndikuti???
You r not serious I don’t have time for
Ha ha ha
Ku Mzuzu sitimakuziwa ife
Kkkkkkk
Sorry for your ass then
Kodi ku Blantyre WhatsApp imagwira ?????
Ku Blantyre ndi ku Town
All the best peace be with you
Welcome, and forget about ur fathers maizegate
Tsopano kudzatulukira mwana wamacholowe
Ndiye mwati chaponda ali ndimisonkhano Ku Lilongwe ndi Ku BT? Aaaah asamatero sitinayiwaletu ife kkkkkk
Like father like son
Welcome home Chaponda….. Feel the warm!
eeeee ine ndikangomva dzina loti Chaponda Bp yanga imakwela
is he related to the Chaponda we know???
Former Minister Of Agriculture’s{ Hon Dr George T. Chaponda, MP} son.
What a question? Say something good for this young please!
For this young gentleman please
Funso lalakwika pati Mr.Muhuro
Mainz get
Bola azanenepo ya chimanga
They write deliberately such WITHOUT crality to confuse the already confuse minds.Team Dalitso Chaponda.
See you there!
Ths guy is good kind remind me of chris rock
He is shameless
Why?
Why madala
No explanation needed
You have missed the point!!