A 32-year-old woman told a court in Nkhatabay on Tuesday that she was selling marijuana because her friends told her that Malawi government legalised the illicit drug.
The woman Rute Makuluni was on 1st August, 2017 found with Indian hemp weighing 28 kilograms at Mukwiya roadblock.
When she appeared before Nkhatabay First Grade Magistrate court on Tuesday, she pleaded guilty to the charge of possessing cannabis sativa.
But during mitigations, Makuluni claimed that she looks after seven children, has no husband and was deceived by her friends that Indian hemp has been legalised by the government hence she would make a lot of money by selling the drug.
However, first grade magistrate Anthony Banda told the convict that Indian hemp remains an illegal drug in Malawi.
He then slapped her with a six month jail term.
The convict was facing a ten year jail term but the magistrate showed some leniency bearing in mind the fact that Makuluni was a first offender and that she has a huge responsibility of looking after seven children.
Makuluni hails from Bula village, Traditional Authority Kwataine in Ntcheu district.
Ligalised it & sell it, don’t stop becoz muli chuma mu chamba osafowoka ndipo sitifowoka!!
Ndakuwona kkkkk uzatiguliseko
Ganja yomweyi kumangana?
Chamba is not a drug nanunso. Eish!
Apolisi muzingotuwabe chomcho….
Makhothi ayamba kugwila ntchito?
chuma chaziko lino chili muthaka. apolice a malawi muzazindikila liti, badmind pipo
Mukayambe mwamanga ma rasta ku temple kwawo amapemphera kwinaku akusweka kkkk
Munajayila mpaka kumataya madzi muli mupamti. Indeed it was legalised with sum reason. Anali pusi pusi ameneuja ncolinga agwire anthu amene akumalima cambaco. Cangamukani acikumbi nonse kenako ndinu
Kodi ku America kuli company imeneyi moti kuti amve kuti kunonso zili choncho ma order tilandila,chimangachi titha kupumitsa kulima nkuyamba chamba chifukwa pa chaka chokha aliyese m’malawi ma mitre angapo atawapeza,dziko litha kutukuka koma no Akumtundawo amafuna basi adzilemera okha,inu osadabwa anthu akumapita kukatengako akagwidwa pa boarder akuwalanda and komwe chimapita m’madziwa akawachitenga chogwidwacho? Amagulitsa oha akulu akuluwo,nanga monse muja adayambila kugwira muja bwanji sapita kukatetha mindayo ku KK? Malawi wokondera kwabasi
Chamba Ndi Chamba Basi.Chozunguza Bongo
ineyo ndikadzangoti ndabwelela ku malawi strght kuboma komko asiye kulesa chamba….apolisi mumandi pinga…..
Free dis woman asaa
Kkkk anamvera mbasi kkkk
Arimbanendi anthu omwe akubandarama zaboma amange amenewo amusiye zimayiyo
https://www.facebook.com/IndustrialHempMalawi/
https://www.facebook.com/IndustrialHempMalawi/
It is already legalised for industrial purposes, is it not?
It’s still under research. I wonder what they are researching when they already know the results haha
Wina wake is holding them back!!
They know ? ?
SHUT UP
azatimasula lite kuti tizigulisa ndi kusuta
Kkkkkkkkk,,, koma
Looks like we are cool as a nation to see foreigners come to collect our herb and make millions of dollars out of it while we are regarded as one of the poorest nations in the entire world. This makes me sick every day I wake up. Legalize marijuana especially for industrial purposes asap. It can absolutely build up our failing economy
Mulimba ndi achamba anzanu akudya dolla ya boma thru cash gate ,maizegate hahahahahahah leave that woman alone othr wyz ayamba uhuletu ameneyo oho
Akawagwire kaye ma ministers onse kuphatikiza petala muthalika ndikuwaika mundende awulure kunasiya iwo ma million ati cashgate kaya basket i don’t know eya nde akamaliza pamenepo azigwira bwino ogulitsa chambafe apo biii pavuta Sure !!!
Kuteroko matumba anga onse 30 ndigulitsa bobo balibe angachite mnyooo ! Kodi a police akuyerekedwa akulandila zingati m’boma ? Kkkkkkkk Wapolice ndi player wa mpira nde bolanso player wa mpira ali ndi makobiri kusiyana ndi wa police , angoopsa muchipewamu awa kkkkkkkk popeza akalanda Chambacho nawo amasuta .
If you can drink and drive what can stop me from smocking and fly…..?
Hi Admin, imiss you
Maiko anzathu akugulitsa mopanda cheu-cheu izi komwe ku Ethoipia kwa Hailer Salasie kulibe zimene olo mwana amakhala ndikamunda kache ma chamba agulitse apeze ndalama yogulira zosowa zake koma Ku Malawi kwachuluka #achiphanzi mumalanda chamba koma komwe chimapita palibe amadziwako zazii.
Gen 1vs29.ndapeleka zomera zonse za njele kwa inu kuti zidyedwe.
zoona kumanga anthu chifukwa cha chamba
Awauza ndiye Atani apa?
Ndimomwe wavutira ulimi chaka chino apolice agwira anthu ambiri ndi busnes ya chamba.wina ndine ngat chimanga chilekeze pa pa k60 ineso ndiyamba
Mo #knowrg/grt #courg/no #damage.plz free up d #black #people
Mmalo momanga anaba ndalama za Malawi akulimbana ndi osalakwafe koma zko yili,vuto ndi driver wanthuyi salibwino
Hahaha! I just likes the comments.
Alolen anthu alime chamba bcoz ulimi wenwen womwe ungatibweletsere ndalama zochuluka.
She must bring those friends to court
Wagwida ndi chamba a police buzzy kumanga munthu, koma akaba ma million anandarewa palibe amaima pa chulu dziko lochititsa manyazi iliii.asiyeni anthu azigulitsa chamba, mmene zikubvutila zinthu ku malawi kuno anthu agwira mtengo wanji?
kkkkkkkkk when kkk
Aaaaa,,,ganja yomwei mpaka kumangana??? Chamba is nt a drug its a plant,,,,bwelani muzamange ine kuno,,,
Legalise
She is innocent, release her immediately.kkkkkk!
Marijuana Its An International Herb And It Doesnt Kill Thats Why It Cures More Than 100 Diseases Across The Globe And It Is Also A Very good Source For Industrial Purposes.Let It Be Legalised But Terms And Conditions Must Be Applied To Avoid Uncertainities.
Amalawi akufunika kulimba mtima kuthana ndi anthu awa a bomawa basi,alemere iwo basi and nkasa sananame” Amphawi
akuti K5 itikwanile-tikalemera
tingautaye ulemu
Vuto Ndi Mitima Yomweyi Yokuti “Let Me Be At First And Have More” Posaganizira Apansi.
Court liime! Kkkk
Tisute,tibande,tingaze,tisweke,dzitiphweteke.Mesa #Munaloreza Kodi??Mudzimanganaso Hahahaha.
makape inu.musiyeni mukulephera kumanga mbamva zen zen mukulimbana ndi.mphawi ngat uyu fokof
Marijuana activated 100%
Chamba ndi makobiri , auzeni zitsiru za police zo nane business yanga ndi yomweo asa tikawadyere kuti malawi wache wathapoi ? Panopa ndili ndi matumba olemera 90 killo grams okwana 30 ndikupitanao kunauchi kkkkkkkkk tikakumane cha ku ntaja kooo ! Bola azibwera atakodzeka failing which , wina azaluza mano .
kkkkkkkkkk
Ine nde sangandigwire , zauchitsirizo azipanga ndi azimai omweo , Achina Joicy ati khaya banda kaya nabanda i don’t know ee ameneo anaba ma billion gulu la achina peter wamuthalika zonsezi mbabva nde kumalimbana ndi wogulitsa chamba kuti chani?
ine zikandiphwanya ngini ndimayiponyera kutali bwanji
legalise marijuana
kkkkkkkkk
Mulandu palibe apa
marijuana should be legalise dont tell the people that marijuana is harmfull to our life, its healing of the nation
Kkkkkkkk koma kwavutadi
Pa malawi ndichocho amakodwa ukamavutika uzikhala kapolo kumayenda mumisokhani Ya DPP kkkkkk
So update us??? How was the judgment went down??? Kkkkk
anthu akumidzi akanamawasiya kut azilima ganja kut iziwathandiza mwina ndi mwina moti boma silimafikira..#free_di_plant
kkkkkk mayiyu awina mlanduwu
inenso ndikudziwa zoti anapanga legalize
Inenso kuno ndili ndi ma oda akufuna 70 bags koma
dokotala wa2 musiyeni…..
Ine Nde Sangandigwire Coz Apolice Onse Tinadziwana Kale Kale Mungololeza
legalise it… Then mumange mental hspto ku bt…
MUSIYEN ZIMAI AMAFUNA MONEY
Hahahahah thats what she heard & knows .
No comment
anapanga ligalise kalekale
Legalise it plz, even admn of this page like it a lot
Aloleni anthu azilima chamba please chili ndi ndalama poor people life would change.
Legalise Marijuana…Legalise!!!
Self defence
musamange2 mai ameneu ndalama paja mwazibixa manyumba anuwo
Kkkkkkk