Cassava farmers in Nkhotakota are worried of low harvests due to monkeys that are invading their farms to destroy tubers.
Malawi24 caught up with some farmers in the district who said the situation may lead to hunger.
In an interview with this publication, one of the farmers Latifa Chisisili said the situation is worrisome since cassava is their staple food.
“The situation is really bad since monkeys in large numbers are invading our farms. They are destroying both fresh and dried tubers.
“Here in rural Nkhotakota we rely on cassava for our survival since maize doesn’t perform well due to environment,” she told Malawi24.
She added that currently some farmers are spending daytime in their fields to chase away the monkeys.
Nkhotakota district is one of the districts in Malawi that takes cassava as staple food.
The problem is serious in villages of Mbalame, Chizili, Chamba, Thandaza and Nkhandwe which are under Traditional Authority Malengachanzi in the district.
Otumidwa. Amenewo asakudya chamba bwanji
Fundi muli bwanji ku Nkhotakota? Paja mwafikako ma week apitawa eti? Nanga iwe Marion zoti anyani avuta ku Nkhotakota ukudziwa?
Fundi Francis wanyamula the forbidden leaf kuwasutitsa anyani onse ku KK. Shaaaa i pity my anyani
Ndikuphatikizani nonse
Kkkkkk anyani simawasungira chakudya ndife malawi yonse
Alekeni Anyani kumeneko ndikwawo musawaphere ufulu munawatsatira dala nokha kumenekuja sikokhala Anthu koma Zinyama
What A Very Yummie Meat! Eat It
Pakufunika civic education kukhalangoko
Saidi Tiuzeni zoona.
A Mfumu you are in Nkhotakota hahaha
Brother babs
Brother babs akuononga kumeneku?
Hahahah leading a coup
Hahahah he’ll be caught before he knows it.
Hahaha smh this guy. Athawa ndekuti ku zoo
???? nthawi yomweyi? Kwagwa chilala
Hahahah Kaya tawafunseni. Inu a Mfumu musakhale ngati simukumva
Hahaha akumva koma nkhani ndi yomwe yavutayi. Akabwera poyera anthu ammudzi alusa??
Hahaha nde asiya kuyenda?
Hahaha eya, kwavutatu. Most Wanted Babs.
Hahaha smh tinkanena ife. Siizi
Hahaha kusamva Mfumu!
comments from vis post Eeeh! !! so funny indeed
Azidya anyanio,food chain
Icho mchidziwitso chabe kuchitira kuti alibe miezi iwiri kutsogoloku asowa mkudyedwa ndie boma lisadzabwe kkkkk
Alenje a boma akagwile ntchito tsopano kkkk
pakufunika civic education because that’s vandalism
Just start eating them the population will be reduced
Too bad
Give them 7yrs imprisonment with hard labor…
Ofunika life imprisonment
Anthu adakalowa malo a nyani popanda chiloledzo. China chilichpnse cholimidwa pa mthaka yawo ndi chawo. Umbombo bwanji,mtima psafuna kugawana.
Give them beer,and when they get drunk,they won’t be able to dig and destroy cassava
Panopa nkhaniyi ili mmanja mwa apolisi akufufuza.
ndiyeno bwanji wosamanga ameneyu komandi kanakhalayine zaka zitatu ndilikundende nanuso mukasowa nghani muzingokala ndikumacheza ndibanjalanu kusowazonena mufuna mutiyanghulise pambali zawucsilu
Verani izi, zomwe mungapange kuti vutoli lithe .mugwire nyani mmozi ndiye mu mpake penti ya Red thupi lose ndiye mu msiye ,ndiye akamasatira anzake aja azimuthawi basi ndiye kuti dera limenelo achokapo basi mukatero mwaitha
What is the Department of Parks and Wildlife doing about this issue? If it is like the situation at my village then the answer is nothing at all, even though Regional Headquarters is only 8 kilometres away.
but how many r the Monkey to lead pipo to hunger!
Atipange hire anthu aku Dedza ndi Ntcheu paja timadya zimenezi
Effects of climate change? I thing if you destroy natural forest where do think they will find food?
This has nothing to do with climate change. It is because there are plenty of crops being grown for people that there is no need for the monkeys to search for food in the forests. Why should they bother when it is far easier to steal food from the villagers. As we continue to do nothing about these vermin then their numbers just keep increasing, and the new ones see that there is no need to bugger about all day searching amongst the trees when there is food just waiting for them in the villages.
Nkhani ndi zikwanje
Yllka Bojku
sorry
Ndi ndiwo, nyama ndithudi.
Anzake a Chaponda amenewo
Asiya kugwira switch ya magetsi nawo ali ku casava aziwona.
Anyani tell them kuti anayambitsa ndi chaponda zoba zakudya nde inu ndiayani kuti musabe chinangwa
Ndi ufulu wawo salima alibe manja olimila kmanso makasu,azidya nawo basi sakulakwa ayi
ziwan kuti nyan simunthu kulibwino kupha anyaniyo or kuwathamangisa
oky
Alibe munda atani asiyeni sakulakwa
Invite people from Nkhata bay. It’s good meat to them
Kod olo muwanene anva? kkkkkkk mukumuimba mulandu pusi akunvani? ;amalawi sazatheka basi
Kkkk zoonad Achimwene sazathekad amalaw kkkk
Nkhotakota farmers are not for Cassava they ar for Ganja y r u accusing monkeys??
Choka mulomwe iwe, udzapite Ku Nkhotakota sudzapeza amasikini openga ngati mwadzadzila mmataunimu, Chambacho China mule gets an I inuyo anthu opanda malo,Nyani ndi nyama ya mbuzi kwa inu
Here in zambia,a baboon switched off electricity in livingstone making two provinces to go blackout
Anyani A Masiku Ndi Ophunzira Man
Leave them eat free
asaaaaa
Tangotumizani angoni aku ntcheu 20 akathana nawo ndi ndiwo zimenezo ngati anamaliza afisi kanyani mkachanixo!!
Scare them away using makombola. Ngati mungachite mwayi kuphapo mmodzi mundiyitane, ndindiwo yabwino kwabasi
Just killed
kkkkkk
Vutcha Mngale amathililila zongendawo ku guguza
Kkkkkkkk kukasamba amalima guguza koma Ku nsanja Ku saneti kwawo kwachina MAVUTO ndiko kuli mwaya
Mufuna potukwanira munthu
Kkkkkkkkkkkk watha manyopola kukasamba
kkkkkkklkkkl be serius guyz r u telling me that u hav nothing to write here only for monkeys?
monkeys? not goats?
NOT DESTROYING BUT EATING LOL
Lol comment reserved………………
koma Malawi wafika powawa tsopano kt uzale Chinangwa tikuopa anyani, chimanga tikuopa chaponda
oh kk you see ..this humans they ‘re worried about us ..they say we’re the distroying their staple food …….let us eat also is our food too …
monkeys
Kkkkkkkkk koma people,
Kkkkk kodi apusi akadali uko paja nawoso amadya nawo chamba chakumaliwa akatero ndiye atumbwe kunsanja
Nanga azipanga chani ntchito simukuwalembanso ku teveta simukuwatenganso koma ndi a Malawi
Fireworks . Plus misampha mugwire mmodzi wamoyo and paint it
Dramatic comments. Kkkkkkkk. I have enjoyed them.
Sanayambe ndiwo kuba thipula ku nkhotakota nanga chaponda
kkk Cassavagate
Mmmmm ndiabale athu asiyeni akudya za abaleawo
I that the news that you can give us, please please give us something better
They are eating as well!!!
Tameki kodi anasiya kupanga fakani munda wonse tameki
Koma aise waganiza bwanji?
Nanga timeneti tizivuta why
Akawasumile koma chidakwa kkk
They are not destroying. To them they are making ends meet
Bola asakhale Gomani awazundula kkkkkk!!!
Tumizani agalu achiwewe akathane nao.
Don’t kill them. Just scare them away with dogs
Akatenge Chaponda Awagaire Zakudya
Jus eat them asaaaaa
They are eating not destroying.
Eeeh tinangozolowera sizinayambe lero..
Emma Gondwe thus the point. Chifukwa chachikulu ndichimenecho basi
Kulozedwa?
Anyaniwa akusamalika bwanji iwo omwewo akazimise mages apa mukuti akuononga chinangwa
Munawononga nkharango yomwe amkapezamo zakudya popanga minda.These are some of the deforestation results coz anyaniwa nawo ali ndi ufulu
That’s conflict between animals and people that’s wildlife thing bac
evry coment funny thou
But you monkeys why this???
Koma ndiye kukhala kubelekana koopsya paja akudya chosaphika . Banja la Mtsogolo must hear this .
Really??
Nawonso amachifila m’beduu
Deploy dogs dammit!!
Ndiye ngati mukuona kuti akupanga zolakwika muziwapatsa zakudyazo akapitilizabe agwire ntchito yakalavula gaga kundendeko mwina angakaphunzireko chikhalidwe
do you think that monkey where can find food becouse this animais can found food through youre fam jast reve them
kodi tidandaula mpakaliti kodi balame ziyimbibwa mulandu chifukwa zimadya mapil
Kkkkk abale athu awa, adye nawo izi osawakhomerera
I think gov’t must own the problem and compensate the farmers
Akadye kuti?
Koma ndithu kulima anthu azilimila anyani? Aaaa
Aziphulitsa makombola
Imenyi sinkhani mindayo munachita ku walanda tsono mumati apange bwanji?kawasumileni kwa mfumu muona ngati ati abweleko
Akathana ndi chinangwa akabande nawo nganja
Ndiwo izi,kumangodya bac
Tingokhalana nawo pansi kut asiye cikhalidwe cimeneci,bola ngat sakutenga ndi mbewu yomwe or report them to the nearest police station,or the gvt shud set an inquiry comision
Koma adha I we kkkkkk
Ndi conco man
Maganizo Abwino. Contact And Dialogue Basi
Kkkkk
Pot amangodziwa the setting of an inquiry commi opanda tsogolo
kkkkk koma inu muli ndi mfundo
Mmmmm malawi wathu ameneyi
Awa ndabwana ndthu lkkk
Ndi achibale athu omwe awa asiyeni adyerere basi.
MZONGOFUNIKA KUKAMBIRANA SIDZOCHITA KUTENGERA AGALU KAPENA MKONDO MZAPACHIBALE.UNDUNA WA DZAULIMI UYENERA KUFUFUDZA NGATI MINDAYO YOMWE ANTHUWA AKULIMA ADAITENGA MOSAWABERA ABALEWA
tazikhalani serious guys…
Kkkk
mmmm mpaka kufika pamenepa?
Hahahaha koma iwenso ndiye wandikomola ndikuseka ndithu.
Its means more birth rate than death rate :-):-):-)
They Also Hav No Food.
akagwidwa adyedwe basi…
Mukufuna azidya chani anyaniwo? Chinangwa chomwecho mpaka kuchita kuwakumba, kuwalengeza pa social media ngati aba ndalama za cashgate?
KKKK KOMA GUYS
Kkkkk koma adha iwe
Sukudziwa kuti anzako ndi nsima imeneyo eti
They must employee more guards
Scaring them away with dogs or just guarding the farm is a solution. Mvula ikagwa kwambili tidandaule njala, ikachepa tidandaule njala, ndi anyani omwe adzikhala pa list yoyambisa njala abale??
Nice meat try it?
Zilombo zimenezi zimasokonezanso bwanji. indeed farmers must guard their farms zisamangotivuta nthawi zonse ayi
ndiye kut mindayo ndi yawo munachita kuwalanda kkkkkkk!
Koma pokadikililapo Samalani coz naonso akakwiya timva kuti mwini munda wakhadzulidwa ndi anyani ndithu.
Kill them all
Hahaaa
Let them survive
yes , ofcourse koma ndikupempha apolice kut akaponye tear gas kwa anyani omwe akuononga kasavao
Akwee tidya chani ife anyani inu
Kkkkkk koma anyani amenewa akufuna tife ndi njala eti
Kkkkkkkk eti
That’s how God created the earth!! Just need watch alert.