M’modzi mwa akatswiri pankhani za ndale m’dziko muno a Wonderful Mkhutche ati mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika mwanjira ina iliyonse anayenera kupezeka kumsonkhano wa atsogoleri maiko a mu Africa.
A Mutharika sanakhale nawo pamkumano wa atsogoleri a bungwe la African Union (AU) wanambala 29 omwe umachitikira ku Ethiopia.
Kumsonkhanowo dziko la Malawi linaimililidwa ndi kazembe wa dziko lino ku Ethiopia a Chimango Chirwa.
Poyankhula ndi nyuzipepala ino, katswiri pandaleyu wati chiganizochi sichabwino kwenikweni potengera kufunikira kwa msonkhanowu ku dziko la Malawi komaso kwa mtsogoleri.
A Mkhutche anena kuti chifukwa chopulumutsa ndalama chomwe likupeleka boma pakulephera kwa a Mutharika kukhala nawo pamsonkhanowu ndichosamveka.
“Pali zinthu zambiri zomwe boma lingachite pofuna kutitsimikizira kuti limasamaladi ndalama za ife anthu opereka misonkho osati kulepheretsa ulendo ofunikira ngati uwu.
“Vuto ndiloti dziko lino muzaka zapitazi lalephera kugwiritsa ntchito bwino mwayi wopezeka kumsonkhanowu ndichifukwa chake lero msonkhanowu timauona ngati opanda ntchito ndipo kupita kwathu kumangokhala ngati kukakwanilitsa chiwerengero,” atero Mkhutche.
Munkuonjezeraka kwawo a Mkhutche ati a Mutharika anapanga izi ngati mbali imodzi yandale komanso ndi cholinga chophimba anthu m’maso ndi kupewa zoyankhula za anthu.
Iwo anamaliza ndikunena kuti zinakakhala bwino mtsogoleri wa dziko linoyu anakapita ku msonkhanowu kuti akapereke dandaulo lake pankhani yolimbilana gawo lina la nyanja ya Malawi pakati pa dziko lino ndi dziko la Tanzania.
Musiyeni sabwelera msanga kwao akapita m’misonkhano ameneyi,,kulita kwambiri,anzake onse amakhala kuti abwelera mwakwao koma iye amakhala kuti akanali komweko or kuti msonkhano watha,,kuzipita achangu kuti azibweresa zotsatira msanga
Munthu alibe pabwino satha kuyamika.
Kkkkkkkk ndimadz lamulila ndekha kkkkkk wanga wapita ku au ist on jonz or lusaka kkkk
ameneyo si katswiri ndawona,umunthunso mulibe,mwina sukuluyo kapena,ndiye pamenepa chalakwika ndi chani kusapita,amakudyetsani ma buns kapena andalewa? akanapita mukanayankhula zambirimbiri apanso wajomba walakwanso,Malawi sadzatheka ndithudi.
Mukati kuononga ndalama ,kapenakusunga ndalama m’boma
msonkhano wopanda ntchito..it lost its purpose way back..kukanika kupeza resolution ya issue ya nyanja ya mw,..nde tidziti azitsogoleri amenewa can they be trusted?? ninsense
Iyeyu akufuna akhale ngati dolo ponena zimenezi. He is very stupid idiot.
He was busy with blood of unsiner
Akapume akalamba madalawa
itsateni bwino nkhaniyi osangofulumira ….
Kunena zoona I don giv a damn whether he goes or not it remains the same. The punchin bags we are, u get a salary u get punched (tax) and u go to buy tings Mr tax is there, wha the hell!!!
maybe they get paid when they happn to oppose anytin, u don knw.
tha’s what it means by being an opposer
ku Nyasaland ndichifukwa ali proffessor tizamumvetsesa bwino pazapita zaka 10 chifukwa tilibe nzeru zokwanira bwino
If busy or sick can send a vice isn’t a punishment ,even if he can go or not, will never boast our economy…..never!!
l think we malawians now what l can see is just a heart of jealous why alwez we like blaming our president thats not true and this is not only here in Malawi but all countries in Africa we like this let these leaders lead us its there time
Akajomba walakwitsa! Akapitanso walakwisa! Malawians what should a person do for your satisfaction? Our leaders are not problems, we are the problem and that can end only if we change our jelous mindset!
Am 100% sure this is not political analyst……how dere are ?? Munthu mufuna atani?? Aaaaaaaaaah Malawi sanje
Kkkkkk just fireburn wicked politician
Basi ifeyo choona tachidziwa munthu yu Ali bwino ndipo dzikoli akuliyendetsa bwino kuti zikupwetekeni kwambiri tizangomuvotera kachiwiri kuti inuyo muzingolira ndi nsanje yanuyo choncho
Apite or asapite mphindu ndichani kwa ine,munthu wa kumudzi?..
Its outstanding to go as all African leaders are involved
Your massage l like it
Komano uwu ndi msokhano ofunikira kodi nanga mwina akambirana zoti azungu akufuna atithire nkhondo AU or mmabukhu anthu akuphunzira zabungwe limeneri
amene muti aMunthalika akula dzeru zikubwerera
Maganizo ako amenewo
I Love Peter So Much Becoz Of The Way He Is Misgorvening Our Country
Ameneyo ndi Pyere mphwake Muthalika sizibwana
Umh ayi munthu olo atatani sangaoneke ubwino wake in government chilichose criticism? umh umh shame on you Malawians bizy trying to still pull our nation down,go to hell
Ufiti ? It just prove that what ever we do in life there is someone somewhere who will find a fault kkkkkkk
Mm munthu atani guys ndine wa mcp koma apa pokha wayetsetsa
Lucious once sang; mundu jwangali pa mbone,akanapita mukanamvanso ena akuti walakwitsa akuononga ndalama
Apapo ndipamene ndadzindikila kuti peter alibe vuto lililonse Ku mtundu wa amalawi anthu mukumamutukwana chifukwa cha jelasi yofuna kungodana naye anangapita mukananena zambiri kuti akuononga ndalama za misonkho yanu a Malawi taonjezanotu.
Malawi akanakhala ndi akaswili bwenzi zitawoneka kalekale,,,,akaswili kulibe
Sometimes political analyst are very stupid
Aaa munthu musiyeni ngati sakufuna mukuchita kumukakamiza ngati ndi m’bale wanu amenewo ndiye masewera mwava
Pokhalila pano mufune musafune DPP ndi boma basi mpaka 2019 woooooo!!
Aaa munthu musiyeni ngati sakufuna mukuchita kumukakamiza ngati ndi m’bale wanu amenewo ndiye masewera mwava
A Malawi sindikuziwa chimene mumafuna kwa asogolele athu, kaya ndi ufiti kaya ndi kusuta kaya ndi nsaje, anakapita zokamba za mbiri mbiri mimba zanu musiye ku nyoza asogoleli kuyambila lelo.
Even though it can’t change the mountain,we are already stupit happy we are that we are second leading in africa interms of baby manufacturing and early marriages that doesn’t last long.happy independence 53
koma Malawi sadzatheka sure.. akanapita tinakamva imweyo akuti walakwisa kusapitayo,akunenaso kuti akuononga Ndalama zaboma…A MALAWI TINAKHALA BWANJI????
Learn 2 appreciate wen 1 z doin good thinz 4 u akali moyo.
Mmmmm mkului kujombako amafuna akondwelele 53,independent, unluckily kunachitikaso ngoz and it’s not his 4t it happen s,koma hw much did he spend on independent day compared to he could go to AU summit,Tanzania Skip’s the freedom day to avoid expenses, y my Malawi z still expending on the day while eni ufulu akuvutika ulova,
inu guys,mukudabwa chani kodi? anthu akumunena kuti why sanapite komanso akanakhala kuti wapita bwenzi atalandira ma phuzo anthu kumutukwana right? the answer is that majority of malawians doesn’t like him,take or liv it but mak my words..
The main reason it’s most pple are savages the fact that you don’t like his policies it’s not reason enough to insult him.. I hope one day we shall learn to disagree respectfully and with dignity.He is president
yaa ur right erick,but the problem starts with you cadets always,kukonda kutukwana ndikuyankhula zoduka mutu always..
People have always something to say.
No anachita bwino caz sakutithandiza pa nkhani za nyanja
Akadapitanso mukadalankhuranso zambiri kut akuchoka anthu atawasiya ovurara mkufa pa indepence celeebration…
Damned is he goes, damned if he doesn’t . Lol
Kodi a Mkhuchewa ukatswiri wa ndale anautenga kuti?
Zangozi ndi khaniyi sizikugwilizana amalawi chakula pano ndi mtopola basi ndikona sitikutukuka uphawi ukuchita kutifinya kamba kokamba zopanda mutu akanapita mukanati walakwa kusapitanso mukuti walakwa ana afa pangozi mukuti wapha ndi pulesideti mumaganiza bwanji amalawi azanga ?ngati chonena mulibe pena kukhala chete sikulakwa ayi.
Kungoti a Malawi vuto lanu ndichani? President akayenda mumalankhula zambiri, tsono lero sanapite ku msonkhano mukulankhulanso kwenikweni mukufuna chani. KASWIRI WA NDALE ndiyekuti chani? Dzina lodyera
malawi sadzatheka kodi munthu wabwino atani abale/apite mwat wapita ndi gulu akuononga ndalama,wakhala zokambaso bwee akula ndi mabodza.
Mulungu yekha athakuyamika osati munthu
palibe timapindulako za ziii
Mkhutche nde chichaniso, ali nchani,,akagwere uko
Wapanga Dala Amafuna Amve Kuti Chani Ulendo Uno. Ndiye Mwati Walakwitsa? Kk
He should surppose kuti akaonekere nangano mfundo zomwe akambilane kumenekozo iye azidziwa bwanji zomangilira Africayi kuti akhala wabwino tikamati kusemphana nazo zochitika ndiye uku, wakhala ndiye pano akuchita chiyani kumalawiko?
Akanapita bwenzi mukutukwana, lero sanapite mukuti sanachite bwino! Munasuzgo mwe! You don’t know what you want! Winawu ndiufiti tsopano.
Kkkkk mwe kuwa nga ntchewe kkkk
Kod wabwino atan?, akadapita bwez mukut akuononga ndalama za misokho yanu eish
Mixiuwww!Zachamba
Ndi #Robocop peter
Adzapita kumangalande osati izi zamu Africa. Zilibe phindu kwa bwana wathuyu.
Poti sikwaazungu ndiye kujomba koma kukanakhala kutsidya lanyanja ya mchere kunalibe zojomba. Katswiriyu palibe chomwe walakwitsapo apa.
Apite mumvekere akuononga ndalama ….za boma…akhalenso osapita ….ntchito sakuitha yotukula miyoyo ya amalawi.!!! Eshiiii..mukufunano chiani agalu amaliongo?
amalawi ndinu mbuz za athu last tym muthalik anapta ku america ndpo munakamba zambli kt akutha ndalam apa wakhala mukuti aiso amayenela kupta mixewww nde ife tive zit? kmas akatswli enawa akungofun kutchuka
Ndife mbuzi chabwino iweyo nde ndan ? pumbwa i guess
kape iwe shit
OUR PRESIDENT WENT TO SCHOOL AND HE KNOWNS WHAT TO DO AND NOT TO DO. HE CHOOSE NOT TO GO TO THE SUMMIT AND AS A NATION WE HAD TO ACCEPT IT NOT CRITICISING FOR THE SAKE OF TO BE HEARD
Ndakunvani
Akulu akulu pepani munthuyu wathawa ku mento
za nyanja adandaula maulendo angati
Akulira maliro.
oky
Akaswili akumalawi ophuzila kwambili kkkkkkkk
Akanapita eeeee koma akuononga ndalama bla bla kkkkkk a Malawife
I don’t have problems with the president travelling but Iam a bit uncomfortable with the number of people who accompany him for the sake of pleasure
Kikkkkkkki wasuta kwambiri chamba iwe,akadapita wekha ukadati akuononga ndalama za msonkho,amalawi mulibe pabwino maka inu andale mmafuna popezera campaign kugwesera anzanu ngati ngolephera,choncho sitingatukule dziko lathu
Dziko lovuta ili
Ok
Koma kukanakha ku kuzambwe ku Ulaya
Aaaaa munthu asajombe? Ndiloboti!!! Chani
pali akatswili ena openga. ngati amenewa
Nde chabwino ndi vichi
kodi kumalawi kuno tili ndi akaswili ochulukabwanji enawa tu siakaswiri
Inu alinadzo ntchito dzimenezo alibe chokanenako kumsonkhanoko.
Akatswir Opusa Mungochtapo Zilizonse Kulowetsa Ndale Ndye Wabwino Ndan Mwatkwana Tsopano Wabwno Tmudzwa Ndfe Tsopano Fwetseke
AL IN AL BIG UP HE FOR SERVING million S OF KWACHAS ….
Very Stupit,what Variety Of Person Is He?When Peter Skipd The Senarial Ur Lameting Hhhh Like Un Own,now Ur Hissing Like A Snake,so What Do You Want To Him?I Can Say That Peter Is Doing Something Better,and Comming Election He Is Going To Be Re Elected
Mention 2 things mutharika is doing better?To be a Dpp member doesn’t mean you must support everything.Wheither u like or not,Peter is waist president we had in Malawi.
Like Or Not 2019 Boma!! Am Out Side Malawi Since 2012 Bt Media Inform Me Everythn Peter Wil Re-ruling Until 2024 Wamva…?
Munthu ndi ovuta basi
Ur teacher will ask u to write an essay about ADAY U WILL NEVER FORGET. At the end he give u 17/ 50 as if that day he was with you
kkkkkkkkkk
Muzinena momnveka kuti katswili pa nkhani za maphunziro a Ndale. Munthu sanaimilepo ndi u khansala omwe. Sanapangepo campaign mkuona kuti wayankhulako za mzeru anthu amukonda, Yake ndi theory mkalasi basi. Akhala bwanji katswili pa nkhani za Ndale. Mpira omango fotokoza pakamwa kapena osewela wekha popanda okumaka aliense akhoza kuoneka dolo.
Inu ndinu abodza sopano. Muziyamika. Sikuti poti mulimbali yina muzingopanga critisize everything. Apa ineyo ndawayamikila kwambiri a President.
Koma mwati akatswiri enawa ndi eni eni koma? Anakapitanso munakati akuyenda kwambiri akuonongonga chuma, eeeeeeeeeeh kkma yaaaaa! Kuyendetsa dziko sizochedza guys.
Sakanakwanitsa kupita, amadikila sacrifices yomwe amakapanga kulilongwe kukapha miyoyo yosalakwa kamba ka kukhwima #luminat
Apa timva zambili apa
Shame on u.
Iwenso ulin’gulumo how do you know.
President Was Not At Bingu Stadium. You Should Have The Clear Evidence On Your Comment!
Ufulu ukupwetekesa
Demon class imeneyo kumangoyankhula mene ukufunira wati kuli ufulu basi zachisoni.
Malawi @50 everyone can insult the President in the name of democracy
U wil b traced 4 ua fucken comment…we r mourning as a nation and ua here commenting zopusa
Javas ukuyankhula zimenezi chifukwa omwalira siabale ako bwezi ukulira komano wazitengera molakwika nchifukwa coment yako ndimwano kwa Presidet & ofedwa ufulu kupekerana nkhani
Javas ukuyankhula zimenezi chifukwa omwalira siabale ako bwezi ukulira komano wazitengera molakwika nchifukwa coment yako ndimwano kwa Presidet & ofedwa ufulu kupekerana nkhani
Zaziiiiiii shame on you
iwe moo
Iwee ndi Chome, mphaka, nanthesi, nanchidwe, Chule, nazikambe, tombolombo, gwape, finye, nkhululu yamunthu. President chikumukhuza ndichani 6 July yayamba lelo
Ofcorse I don’t like mutharika but on this matter its not because of him that’s what is happening for every stadium but don’t point a finger to somebody
Hahahahahahahahahahahahahahahahahahahahahahahahahahahah kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk koma iwe Mike Mvula eeeeeeee ulemu wako
Kkklkkkkkkkkkkkkk wamisala anaona nkhondo
eeerr makoment enawa kungochimwapo apa msembe yokhwima?
Our leader should go to Summit
Ati pazifukwa zingati
Nonsense,Akanapita bwenzi inu nomwe mukuti akuyenda yenda (akuononga ndalama zaboma),kodi inu ndinu ndani?inu ndi ndani?,anthu osaganiza koma kusintha sintha zoyankhula.
Chilipo chomwe anaopa uyu. palibe chomwe akutithandiza.
Mukufuna mudzikalandila Sima ya ulere ku state house?
I have now comfirmed that man is indeed difficult animal to deal with. Abwino ali kumanda basi
Katswiri wopusa ameneyo.
We also have big problems we Malawians, had it been anapita something differently zikananenedwa. I am not his fun but let’s appreciate wen some1 dd a gud job. Envy won’t take us anywea. Let’s unit to develop this country but izi zomango pointing fingers will not help us and the this country.
Okoma atani onga fungwe
He is afraid of being ashamed with what is happening in the country. His gvt is full of blunders. Alot of …..gates within two years of his rein. Shame.
okoma atani abale?mutapasidwa mwayi oyendetsa dziko kwa mlungu umodzi mungakwanitse inu?why always criticising , without appreciating other people’s ďeeds?yóu fault finders tatopa nanu tsopano.
Anthu simudzayamika akadapita mukanayankhulabe ndiye chabwino ndi chiti??? Shame on u.
Musaiwale kuti munthu ndi ovuta amasusa chilichose
Akapita mukuti he is destroying our tax money akhale mukuti akanapita,what kind of pple are u?
I wonder ooooo!!
nde a Malawi amenewo…Everyting the President does is wrong..
They should simply work hard to become a president one time rather than pointing a finger to somebody who is rulling
Anthu!
Kkk mitu ya AmaLawi ena siyenda bho.
ndiye muli ndi umboni woti wakhala chifukwa choti akuwonga ma tax money zachamba
Tiuze Ndiweyo then,am not a politician
Mukuchiziwa inuyo chambacho
Asiyeni angokhuta awa
I Like Ur Comment Mr Master!
chamba ndiweyo zophusa
Munthu ndi mbatata
I agree with u master
I suport u mr Master akanapita anthu bwezi kuti akuonanga ndalama mufuna atani kuti mumuyamikire
Munthu ngoipa kwambili apite ati akuononga ndalama asapite walakwa maso mwao ndithu
kkkkkk,do you know why people are acting in that way,kuti wakhala or apite akumunenabe?? the answer is that majority dont like him.
that’s wat happens when u are in power because of 36%.
The funny thing is really voters are in villages not pa social media kkkkkk
Am agree with you boss
Musaiwale kuti satopa ndikusutsa nditchito yawo tinawapatsa chifukwasitinawa votele timadziwa kuti ngati kwachitika gozi azati ngozi imeneye wachititsa ndi peter kusowa khani