Mwawaona ayambilanso zawo zija magetsi? Ndiye ati ndi chabe chifukwa posachedwapa magetsi akhala akuvuta monga muja amachitila kale.
Malingana ndi akuluakulu a kampani ya Egenco imene poyamba timaitcha kuti ESCOM, vuto la magetsi layambilanso ndipo posakhalitsa likhala likufika pa mpondachimela.
Akuluakuluwa amayankhula izi atayendeledwa ndi komiti yak u nyumba ya malamulo.
“Vuto ndi madzi omwe aja, ngati munaona pakati apa kuti zinthu zinasintha ndi chifukwa cha mvula inagwa ija. Koma pano madzi aja ayambanso kuphwela ndiye kupanga magetsi kupitiliza kutivuta,” anatelo akuluakuluwo pouza aphungu.
Iwo anaonjezela kunena kuti madzi akamapitilila kuchepa, nawonso azipitiliza kupanga magetsi ochepa ndipo zotsatila zake ndi zoti a Malawi azipitilila kulandila mphamvu yochepa ya magetsi yoti akati ayigawe mwina aliyense azipeza kuti si tsiku lonse ali ndi magetsi.
Malinga ndi iwo, anthu adikilenso kuti mvula izagwe kuti vutoli lichepe.
Mwina tinzingopemphela kuti mvulayo ikati izagwe, izagwe bwino.
Zachambatu…wats da problem timatcha
Malawi
thus malawip
tinazolowera
Ndiye bwino candlex ilemere pogulisa candle
mmalo mot ndigule passpot ndizilimbana nd ma candle?
Manyaka ameneo
tikhalira yomweyi football kudximitsidwa
ubwino wake ndinatemetsa khwangwa pa mwala kuti nsidzavotanso .
No need to worry or panic we are used to black out. We have already started enjoying no electricity all day.
campaign
kodi mesa amati ma LED BULB athetsa ma BLACK IN wa??
Inu kutereku munaiwala kuti ma power generation alipo ndi omwe anasiya gogo Kamuzu ndi MCP aja? Enawa akumangosintha ndondomeko za kaendetsedwe ka makampaniwo koma sakuonjezera mphavu za magetsiwo
Ndiye mkumati bweraniko ku joniko zanziiiiiiiii!!!!
Shaaaa! Barber shop tapachika. Komano uyu akutokota za Marep 8 angosiya ndi2. Sopano ku Malawi ma Trading centre 382 akhala akuwunikila ma candles kkkkk
Zamanyazi ndithu
That’s the way we live here in MW..No astonishment at all.
Tidazolowera
Khato civil engineering company contract ina iyi …tap water from the lake to nkula ….nzotheka basi
Magesi akumalawi kuvuta sanayambe pano ayi kuchokela nthawi yakamuzu kugula fridge ya R8000 kumati ukagwilisa ntchito kumalawi is just waste of time fridge ikawonongeka ukataya ku scrap
Malawi24 Mwasowa Chokamba,koma Management Yanuyo Muliko Anthu Adzeru?
Kodi Ndinu Opusa Nose?
Zayamba Lero Zakuvuta Magetsi?Nanga Kodi Akugulani Ndi Ndalama Zingati Osusawo.Beliv Or Not We Shall Never Never Never Develop If W W’ll Continue Ths Fuck Stories
Chokani iwe, kukonda zoipa basi
koma dzina limeneli ndi lenileni??
I used to cry everyday thinking I will die of HIV virus. After 6 years of contacting the virus and taking Arvs, I came across an article of an herbal doctor who cured HIV/AIDS. I was terrified and decided to contact the doctor with the number provided.(+2347085071418). I saw other patients the doctor have cured and I got the herb and exactly after a month after I started taking the herb, I went for my monthly test and was completely negative. It was too good to be true that I did series of test in another hospital but the test results came out negative as well. With joy in my heart I share this testimony. If you need help just like me you can contact DR ABUMEN via email [email protected] or whatsapp him on +2347085071418 thank you once again for your healing.
Palibe chabwino boma lipeze njira zina mwachangu osamangodalira madzi popanga magetsi tikhaula nazo
No stress! I gat a Telkom Solar panel 250 watts,.. Ngati nanunso mkuifuna mkhoza kuipeza pa mtengo wabwino. Ku Malawi ndi konkuno Ku RSA.. Just inbox
Akuti dziko la mkaka ndi uchi “fuck tht shit”
Kadziko aka angokaseka
AMALAWI KHANIbasi kachigeti ukamika kukozamagetsi aphavu
Kukhala Malawi ndikulimba ntima tinazolowela ku Mpanje ndichoncho.
Chiwamba Sananame Kukhala Malawi Kulimba Mtima.
Chiwamba Sananame Kukhala Malawi Kulimba Mtima.
Better to buy solar pannel than electricity
Mavuto wa anachokera ku Escom united
Mwatsala pang’ono titsikiranso komkotu pano zikawawa kupita komko basi
Poor Escom
Thats wat Malawi wanga amadziwika nazo
iiii koma chiziko ichi!!!kuvota NDE chivoterenicho koma zimavuto zosantha,mukawina upresident WO mukumapanga chani kodi?ndigure TV ndizingosunga?za chamba eti!!!!!
zakumtayanthungo basi
at what price should we exchange with dimba la mizimbe
Osamaiwala kukhala malaw ndikulimba tima,, kaya ine patheba pano pheeeeeeeee
Imeneyi News? Usatikhumudwise aise
Pansana pako :>
ka page ka opposition aka
Ife tinayiwalako zimenezi,we hv our own
mundigula sola ulendo uno basi
I got 250 wats solar i even use when is raining f**k Escom
Boma lagona kaye mavuto kobasi
malawi24mwaiwala kut kukhala mmalawi ndi ntchmo
Kama kawaida, tumashazoea saiz
correct one; gulani nyali,ma kandulo ndi makala……..
Za ESCOM kaya mukuti EGENCO ndizosakambika mpaka Yesu adzabwera wooo!
Zafikano poipa zedi
Tidazolewela paja kukhala kumalaw nd chimo
Ndie fodyayo
Kaya zawo izo tikakhala enafe ndye mwinanso zikhala bwno tigulitse kwambiri candle wathu
Nkhani Yabwino Kwambiri.
Ati Magetsiwa Samazima Vuto Lake Nchani Kuti Azizima Panopa?
mtolo wa mavuto udabwera tsiku lomwe ndidamaliza ku vota mpaka ndiza voteso
Utadzawavoterewo adzaika madz mu shire kut asamazme
Utadzawavoterewo adzaika madzu shire kut asazime
Adxapeza mzeru zina zobweresa magetsi anakuza kut magetsi amachokera ku madzi okha ndan iwe Lazaro wakhatedi ndithu
paja ma cadet ndi mbuli school saidziwa.cadet amawona ngati magetsi amapanga ndi madzi okha,kumangowakhululukila basi
Mmmmmmh kod zot olo mphepo imapanga magesi simuziwa??? Mukufuna kundiuza kut mvula mene yagwwra chaka chinomo mwagwilizanaso zina zot muinamizira shire??? Chaka chino nde mubwera ndiiti yot mtundu wa malawi ufoile nayo? ya zinyalala kapena makina alowa mchenga??? Malawi sazatheka at chilichotse anachilowetsa ndale
TSOKA WANYUMBA YAMAGETSI
True akuti ndipo musavutike ndikumafunsa
good news..
ineso ndava zimenez pa radio one
iweyo wakuza ndindani zimenezo? 🙁
nothing new, we are already used
zachamba