Gulani nyale ndi ma kandulo, magetsi ayambilanso zake zovuta zija ndipo ati mulimbe chifukwa avutitsitsa

ESCOM

Mwawaona ayambilanso zawo zija magetsi? Ndiye ati ndi chabe chifukwa posachedwapa magetsi akhala akuvuta monga muja amachitila kale.

Malingana ndi akuluakulu a kampani ya Egenco imene poyamba timaitcha kuti ESCOM, vuto la magetsi layambilanso ndipo posakhalitsa likhala likufika pa mpondachimela.

Konzekani ndi nyale zo.

Akuluakuluwa amayankhula izi atayendeledwa ndi komiti yak u nyumba ya malamulo.

“Vuto ndi madzi omwe aja, ngati munaona pakati apa kuti zinthu zinasintha ndi chifukwa cha mvula inagwa ija. Koma pano madzi aja ayambanso kuphwela ndiye kupanga magetsi kupitiliza kutivuta,” anatelo akuluakuluwo pouza aphungu.

Iwo anaonjezela kunena kuti madzi akamapitilila kuchepa, nawonso azipitiliza kupanga magetsi ochepa ndipo zotsatila zake ndi zoti a Malawi azipitilila kulandila mphamvu yochepa ya magetsi yoti akati ayigawe mwina aliyense azipeza kuti si tsiku lonse ali ndi magetsi.

Malinga ndi iwo, anthu adikilenso kuti mvula izagwe kuti vutoli lichepe.

Mwina tinzingopemphela kuti mvulayo ikati izagwe, izagwe bwino.

 

Advertisement

71 Comments

 1. Inu kutereku munaiwala kuti ma power generation alipo ndi omwe anasiya gogo Kamuzu ndi MCP aja? Enawa akumangosintha ndondomeko za kaendetsedwe ka makampaniwo koma sakuonjezera mphavu za magetsiwo

 2. Shaaaa! Barber shop tapachika. Komano uyu akutokota za Marep 8 angosiya ndi2. Sopano ku Malawi ma Trading centre 382 akhala akuwunikila ma candles kkkkk

 3. Magesi akumalawi kuvuta sanayambe pano ayi kuchokela nthawi yakamuzu kugula fridge ya R8000 kumati ukagwilisa ntchito kumalawi is just waste of time fridge ikawonongeka ukataya ku scrap

 4. Malawi24 Mwasowa Chokamba,koma Management Yanuyo Muliko Anthu Adzeru?

  Kodi Ndinu Opusa Nose?

  Zayamba Lero Zakuvuta Magetsi?Nanga Kodi Akugulani Ndi Ndalama Zingati Osusawo.Beliv Or Not We Shall Never Never Never Develop If W W’ll Continue Ths Fuck Stories

 5. I used to cry everyday thinking I will die of HIV virus. After 6 years of contacting the virus and taking Arvs, I came across an article of an herbal doctor who cured HIV/AIDS. I was terrified and decided to contact the doctor with the number provided.(+2347085071418). I saw other patients the doctor have cured and I got the herb and exactly after a month after I started taking the herb, I went for my monthly test and was completely negative. It was too good to be true that I did series of test in another hospital but the test results came out negative as well. With joy in my heart I share this testimony. If you need help just like me you can contact DR ABUMEN via email [email protected] or whatsapp him on +2347085071418 thank you once again for your healing.

 6. iiii koma chiziko ichi!!!kuvota NDE chivoterenicho koma zimavuto zosantha,mukawina upresident WO mukumapanga chani kodi?ndigure TV ndizingosunga?za chamba eti!!!!!

  1. Mmmmmmh kod zot olo mphepo imapanga magesi simuziwa??? Mukufuna kundiuza kut mvula mene yagwwra chaka chinomo mwagwilizanaso zina zot muinamizira shire??? Chaka chino nde mubwera ndiiti yot mtundu wa malawi ufoile nayo? ya zinyalala kapena makina alowa mchenga??? Malawi sazatheka at chilichotse anachilowetsa ndale

Comments are closed.