Patangotha maola ochepa anthu akukamba zangozi yomwe yachitika m’bandakucha lero, ngozi ina yachitikaso mu mzinda wa Blantyre.
Malipoti omwe tsamba lino lapeza akuti galimoto ya mtundu wa thilaki inaduka mabuleki ndipo inaomba galimoto zina zomwe zimadutsa.
Ngoziyi yachitika kwa Magalasi mu mzinda wa Blantyre.
Pakadali pano sizinaziwike kuti ndi anthu angati omwe akhudzidwa ndingoziyi. Nyuzipepala ino ipitiliza kukupatsilani zankhaniyi
Boma la Malawi chonde yets2esani kupanga miseu yabwino kuti ngodzi zichepe
is apower of Satan we need special prayers
pali madriver ambiri omwe sanapite ku driving school pepani ku road trafic chepetsa ziphumphu ngati anthu akufa ndi chifukwa cha inu a road trafic
Akuziwapo kanthu awowo!
Terrible news…the government are failing to control the roads and corrupt police
Sorry
Sorry
Mapemphero ndiye yankho lazonse
In time like this,I do remember Joseph Nkasa’s song CHEPETSANI UKALI.
Tiphwanye maBus ndi maminibus tizipha wapansi..
What is it going in malawi
Mmmmm
spiritual battle….we have to pray Malawi
Malawi need A strong prayer
Its time for government to review safety standards of the roads they must upgrade all the main roads in the country
Ayi pepani amalawi zomvetsa chison.
When a country is ruled by the wicked, this is the results, expect more until these pipo repent all atrocities committed to innocent blood and all corruption issues crippled all over them
Mulungu angatinvere bwanji pamene ndife abakha?. Mulungu yakwiya ndi machimo athu. We deserve this punishment.
Mukadzaona izi zikuchitika muzadziwe kuti chimaliziro chili pafupi.
Our days are numbered in the air
uchimo wapadziko lapasa ndiumene ukudzetsa mkwiyo kwa mulungu ngoz zikucitikaz ndkwiyo wa mulungu cifukwa chauchimo wathuwo
Its a spiritual battle Zikufunika mapemphero
misewu siyabho kuno kumalawi
Koma yah titha tose ndinthu
Timchotse bwampini pampando
Ngozi zinazi ndi chifukwa chakuti anthu ena akupanga upgrade ma licence awo alibe ukatswiri ndi ukadaulo obvomerezeka ndi malamulo apa nseu.
Dzikoli full of satanism tkuyenera mapephero bas
Bushiri akuwapo kanthu pa ngozizo
We nid special prayer for zalewa road ed let’s mek 1 bundle for those prayer to go back to the sender ed I bliv wat all my friends zomwe mwayankhura ndizoona Zake but 1 thing let’s unite ed put GOD 1st in JESUS name
Tinadya zamwini tikuyenela kubweza ngongole munjira imenei,kuphetsa anthu wosalakwa.Ambuye mutikhululukire.
Yes that s true bro
mh
we need to praye n fasting to stop dis evil deeds
A malawi we call God in troubles only why? In piece we drink, dance and so many. Satan tidamuvomera malinga ndi tchito zathu sangativere Mulungu
Vuto lina ndi loti ma driver ambiri akupeza ma driving licence mwachinyengo.God protect Me&my Nation . David Said’ Mau Anu Ndiyo Nyali Yakuunika Yapanjira Panga.Be My Light LORD.
Amalawi kukonda zotchipa timagula magalimoto okutha kale ma brandnew second nde zizitivuta.
Remember expensive cars are cheap the cheap ones are expensive they can break anytime and likely to cost our life ngati angatero tili mkati mwa ulendo.
Boma liletse magalimoto opanda zokwanira pamseu apa tili pa nkhani ya Cof izipelekedwa kwa galimotodi yoti ili bho
Magalimoto ena amaloledwa kuyenda panseu mabreak alibe amaimira engine break kapena magear . Izi sizodalilika
Atraffic atithandize moyenera osati msuzi basi pamseu magalimoto ophotchyoka mkumaendabe pamseu.
Miseu siyabwino ku malawi
It doesnt mata kut zikuchitika chifukwa cha nsewu ka chani but zonsenzi nzokondweretsa satana yemweyo chifukwa tili naye komkuno and akudziwanso kuti masiku anchepera. And Mulungunso amalora kut tionongeke ngat sitikumumvera but tikampatsa attention will find out. What i mean is osachedwa apa ndikuyankhula zambiri coz greater is the one who gave us life, lets just put our trust in him atiwululirani zinsinsi like wat yeremiya 3 vs 33 says. Palibe zosatheka ndiYehova tikathanga ufumu wake mathews 6 vs 33 chachikulu tidzichepetse 2 mbiri 7 vs 14 God wants us kut alamulire mmitima yathu, maka tatsalafe whachidule. thank you.
zizindkiro za masiku omaliza
Thoma Wanoma
Enaakudzitengela nthabwala chilipamzako mawa…….kutaya azibale ndikowawa nde chikakugwelani inuyo tionengati munganenekuti tigulitse magalimoto
the end of world’s be carful people!
There-many-ways-among-them-are;
1.Dont-drink-n-drive
2.speed-limit-must-be-observed
3.follow-road-sings-pliz
4.drivers-your-machine-alwayz-b4-u-boad-in
5.observe-carying-capacity
etc
zomwe wanena ndi zoona koma ma driver ambiri sanapite ku driving school ndipo amangogula licence ngati munthu wagula licence malamulo apamseu angawadziwe bwanji? tachepetsa ziphuphu kuti dziko liyende bwino
zomwe wanena ndi zoona koma ma driver ambiri sanapite ku driving school ndipo amangogula licence ngati munthu wagula licence malamulo apamseu angawadziwe bwanji? tachepetsa ziphuphu kuti dziko liyende bwino
Malawi watani abare
mulungu dalitsani
Our government must do something about our roads……we are still using miseu yomwe inapangidwa in the 80s pamene magalimoto anali ochepa.
Noo!, ndinthawi bas, bwanji nseu wa zalewa kuchokera pa bridge aupanga renovate 2mnths ago, bwanji dzulo bus yagwa
That’s primitive thinking…. We suggesting solutions here, we can’t jst seat nd accept that its time. Something is happening here nd we need to address this issue. Our gvt is doing nothing. By the way, how good is that road u are talking about nd is it a highway? These days in Malawi we need highways (freeways), more especially busy roads like Bt- LL road
Ngat mukuziwa kathu pa zangozi zomwe zikumachitikazo basi penzani njira yothesera ngozizo.
We need to have very strong prayers to these things happening including our friends ma Moslems fasting yao aponyere kwakuya kuti Satan asakhare ndigao
Reckless driving on poor roads of Malawi
Apolice Asiye Zopusa Amachita Akakhala Pamseu Zomalandira Tima K200 Ndicholinga Chot Galimoto Yomwe Siri Mu Condition Iduse, This Is Major Agent Of Malawi Road Accidents
sorry to ask, iyi ndi itiyo ngozi ikunenedwa panoyi?
Palibe njira zotetezera ngozi koma titha kuchepetsa ngozi ngati:kuchepetsa speed pamseu,madalaiva aziziwa kuti ali pamseu ndipo nthawi iliyonse moyo wao okhoza kutha,mahampu aikidwe miseu yonse pamitunda yosachepera 4 to 5km iliyonse.
Onse amabuasi asanayambe kuyenda pamsewu aziyamba ayezedwa bwinobwino
sad
Bushiri akupeleka msembe kwa satan
FIRSTLY AS MALAWIANS, WE NEED TO AGREE KUTI IZI ZKUCHITKA CHFUKWA CHA SATANISM VEN ORGANISE NATIONAL PRAYERS
But u need to b
may be ndingakhale ndi mtendere wa mumtima
Lord have Mercy…
Malawi bwanji kodi
Apostles,Bishops,Priests,Deacons,sisters and Brothers tigwilaneni manja ndipo tipemphere kwambiri kut ticotse ziwanda zomwe zikuyambitsa ngozi.AMBUYE odziwa kuteteza akhale pakati pathu nthawi zonse.
Burn all cars frm Dubai
ngozi kusonyeza kut palibe amayembekezera out zichitika palibe njira yotetezera ngoz ndichithu chosayembekezereka ngakhale oyenda pansi ama phumtwa pakumwalira ngozi
Sign of end days,tikuyenera kudalira kwa Mulungu molimba!!
Drink And Drive Must Stoped
ngozi ndi ngozi zimachitika zikafuna basi anthu anayamba kalekale kufufuza njira zochepetsera ngozi koma zikuchitikabe olo atati atraffic aziyendetsa magalimotowa zizichikabe
hahahahaha yambani mwaona kaye kuti chikupangitsa mchani kenako mpamene umabwela ndi solution
tikusowekela mzimu oyela akamangidwa chaponda ngozi zichepa mulungu wakwiya naye
mapemphero
We have to be careful when driving
Tiyeni Tigwirane Manja Popephelela Pazimene Zikuchitika Zokhuza Ngozi
WHY IS GOVT PENALISING MINIBUS OPERATORS WHILE THESE ACCIDENTS ARE ALSO AFFECTING BIG VEHICLES LIKE TRUCKS AND BIG BUSES??
Tingogulitsa magalimoto onse ku mayiko akunja zikatero ndeyekuti ngozi zidzachepa chifukwa timiseu takwathu kuno sitoyenera magalimoto.
APolice asiye chinyengo pa msewu!
Malo Ovuta Misewu Yathuyi Akhale Ndi Ma Arresterbed
Ngozi zikuchitika ku malawi kokha ?
kungozikiza mmapemphero basi n God is more than able & on top of that read #John 14v14
ngozi ndi ngozi imachitika pa thawi yomwe usakuyembekezera kuti ingachitike, kondomu izibowoka iwe nkumati umaziteteza kuti usatenge matenda ngoziyokhayokha
Kkkkkk mpaka condom kubooka ndi ngozi
Kkkkkkkkkkkkk
tixiyenda mothamanga atleast 100km/hr kupangira mimseu mabampu
A traffic azikhala penapalipose
Mmmmmmmm bwanji kodi chomwe chikuchitika ku malawi
Bad roads, reckless driving.. Nzovuta kunvetsa. Last month to this month nde zanyanya. Kapena tiziti kukhwima anthu
anthu azingoenda pasi tisiye kugwiritsa ntchito galimoto
The size and conditions of our roads are not worth for the cars
Mukamva za #miracle money zina NDE ndizimenezi
Xaonjeza sopano
Wina wopanda nzeru akuti kuchuluka kwa magalimoto ndiko kukupangisa ngozi zoona? Ku South Africa kuli ma galimoto ambiri koma ngozi sizifika pamene zafika ku Malawi. Munthu unganene kuti kulibe mizimu yoyipa ku Malawi masiku otsiriza ngati awa?
Ndiye ena mukumangovumbuluka wautali osapemphela chonsecho mukukakwela zokwelazi.
I pray for intervition mmmmmm
Zikusonyeza kuti chinyengo chakula
Mmh! Kuenda Kwaopsa.Usananyamuku,pemphera Kae Katatu
pangozi zonse zachitikazi ndizingati zakhuzana ndi minibus?
very sorry
chanikodi amalawi ngozipafupi pafupi titani amalawi ekhe
Eeeeishhh zawonjeza sopano pakufunika mapemphero apadera abale malawi waonjeza nchito zoipa
Vuto mukugwilitsa ntchito galimoto zakwmanje za mpanga wenkha
Season of accidents …dark cloud
koma mulungu zonsezi akuona ndikulilira dziko lathu lamalawi lili pamoto koma tonse titamanga umodzi mmatchalitchi mmizikiti kdziko lonse lamalawi kumanga chimodzi kusala kudya kukwera mapiri satana azolikila pansi iye ndiolephera basi akunama iye kwake ndi kuba kupha ndikuononga koma ngati mulungu anapulumutsa ana a israel mmanja mwa pharao angalephere kutipulumutsanso ife mkamwa mwa satana tiyeni aliyense payekha titengepo mbali mogonja ndimozichepetsa ambuye imvani kulira kwa ana anu
Ambuye mutichitile chifundo
Satana alowelera kwabasi
Mulowelerepo ambuye inu kopanda inu moyo wathu ulimmadzi.
Gorverment must construct new roads pliz,
Mmm ndi dilu 4m #major,1 sindkukayikiraso
Evils started their duties in Malawi, the end of happeness is near
Koma ya tikupitatu eeee ayi dzovuta sorry for that
Ohhh Lord have mercy on us
Mutidziwitse akulu ndithu
Achina Bushiri akubweza zawo
POOR ROADS with alot of pot holes =NGOZI BASI ..whether u like or not
Kumalawi zimesu zambiri nzophotchokaphotchoka zomwe zikudzetsa ngozinso…ndipo Si ma MINBUS OKHA OMWE AKUPANGA NGOZI …ALL CARS IN MALAWI INVOLVE IN ACCIDENTS NGALHALE ZI MA BUS ZIKULU ZIKULU ZOMWE ANTHU AMAZIKHULUPILIRA ZIKUCHITANSO NGOZ KWAMBIRI
NDE GOVT YALETSANSO MA BUS AKULUAKULU KUNYAMULA KATUNDU OR ANGOPONDEREZA A MA MIN BUS OKHA??
NGAT YAKHO NDILAKUT ALETSANSO MA BUS AKULUAKULU KUNYAMULA KATUNDU SO HOW PPLE CAN TRAVEL WITHOUT BAGS/KAPENA KUT ZIBINYIRA..KKKKK
Gvt construct Gud Roads to reduce Accidents…komanso ma Driver apa malawi muchepetse Mowa(Drink and driver its Dengerous
Ambuye alowererepo
But to me i have got different views in those accidents,this month of Musilim i hope these pipple has all the questions to answer.Nsembe maybe nanga tiziti nchiyani? Each and everytime these Moslem do their fasting,there are so many accidents believe me, but let us Pray in ve name of Jesus our Saviour so that this will never happen again.Justice imawawa you the Moslem simungandilodze coz am a son of Jesus ndipo sizingatheke olo mutachita kutani if my suggestions really true.
Am a Christian and I believe that Jesus is lord..he teaches not to judge for we will be judged and also to love one another.
Bro your how do u look on your comments…is it good???
thats why i said its my view!!Nanga zoti ku Afghanistan akhilisitu awawotcha mu Church ali mkati mopemphera vamva? Fufuza pa internet uwona.Mtundu uwu zopha achristu samawopa bwanji iweyo ukuwabakira?
Allahuma hidhina fiman ya dhaita
iiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii koma
I feel sorry and wonder to someone who is reaptedly denying the involvement of evil demons on our roads.He insist that the government needs to build good roads and without we keep on dying, what a shame.
Mulowelelepo Ambuye
Poor roads also a contribution factor
Zaboza izi,, ngozi ya kwa magalasi ku bt inachitika pa 11 june osati lelo,, wangosowa chokamba basi
Nthawi .
Mulowelelepo ambuyeee…
UKALI…
“Tikakhala ngati ndife omvana anthu tikanamanga umodzii,tikanalilanditsa dziko m’kamwa mwa ngo’na,mano aSatanaa, amene akutafuna wanthu tsiku ndi tsiku matenda,njala ndi ngozi.Tikanamenya nkhondo yachiweni~weni ndimitima yoswekaa,ofunika tigwade tipinde maondo ndikuzipempherera izo,Ngati uli ukali wochoka kwa Yehova aleze mtimaa,pajatu akakwiya tidayiwale tonse pamakhala manja pwesaa.
Chorus…….[nakulengaa chepetsani ukali….]
M’bukhu lachilamulo amalemba akunena opani Yehovaa,Mukakhalaa omvera ndiofunitsitsa monga mwa chilamulo,mudzadya zabwino zopezeka padziko opanda oliraa,koma mukapanda kumvera Yehova adzakupatsani nthendaa,Miliri yoopsa idzakhuthulidwa pamatupi awanthu,kudzakhala matenda Chisiki,Chinoni,Kaliwondewonde,,,kudzakhala Njala,Maliro ndi nkhondo panjira Ngozi daily, Yehova amaseka koma akakwiya pamafa ambirii,Amakana chibwana kuchita uchitsiru ngakhale zinthu za ntudzu,akanena wanena palibe angaletse poti alibe deputy [sp]
Nakulengaaaa….
By; Josephy Nkasa.
akulu ndigaileniko ma verse amenewa nane ndilankhuleko anzanga
Zoonad
Koma osaiwala kuti Mulungu mdiwachifundo
Mpaka munailoweza? 😀
#@Thandie,nyimbo iyi anayimba Nkasa yi sikuti anangopeka koma kuti anatenga mau a Bible,zambiri Zomwe anakamba ndi mau oti alipo chikhalire m’bukhu la moyo,ndiye nkuyankha kwanga nkoti bukhu lomwelo lidati ngati anthuwo akadziwa kulakwa kwao Mulungu yemweyo amabwerera kwa iwo nawasunga,nawateteza,nawapatsa zomwe amapempha. Now nkuona kwako mudziko ili ndi angati amene akufuna kuyenda munjira za Mulungu ?Ukamakhala,kuyenda m’madera osiyana ukuona zintchito zanji zomwe akuchita ana awanthu pansi pa nthambo ili zomwe zili zokondweretsa Mulungu ?chifukwa ndikaona zinthu zatenga malo ndi,chigololo,mwano,nsanje,kaduka,umbava ndi umbanda etc.
Government must do something to cube this problem coz as we remember Bangwe bridge accident that was happened past year’s ago it was the same government were ended the problem by deploying soldiers to guard the bridge untill they were caught the person who was caused an accident by throwing chicken n it was said to here that the Boss of Siku Transport.
Satan watengapo gawo
Eh! Koma ngati ili satanic ndye ampatsa target ya anthu ambiritu…
God has promised to crash the devil under the feet of His faithfuls:Romans 16:20. True God fearing people should not be pannicking about this accidents. Because Greater is He who is in us than he (satan) who is in the world.
pemperani mulungu Iona amalawi.zonsenzo zikumachitika kamba ka mphamvu ya satana amend akulamulira Malawi yonse.we are on good position ya Satanism amslawi
Mapemphero akufunika as a country alowelerepo otherwise..
Ambuye loweleranipo.
Ngozi zanyanya kapena ndi careres driving? Kapena chakumwachaukali
Ndiye wina amvekele Bushiri uti pemphelere mwayamba kumutamanda etii
Mchiyani Kodi Amalawi? May Almighty God Alowererepo Ndithu, Without That Titha Ngati Nkhosa
anayamba ndi moto mmisika, pano yalowa level 2….level 3 stil to come
Around 50 to 70 vehicles are imported to Malawi every day.One accident which usually involved one vehicle now amakwana atatu.In 1999 it was possible to travel BT and LL with only 4 overtakes now asume you travelling @ 120 km/h you are likely to overtake 7 or more.lets face it average cars, buses minibuses now travel at these speeds than they used to way back.The roads have almost remained the same.As cars have become quiter in cabin noise few realise the speeds until emergence…..then you blame bad spirits wake up guys…we know the reason.Mark my words we will continue having these accidents until something happens.
true and analytical
magalimoto ambiri ali kumalawi kokha?
I do salutes you Noel A.N only the less will come across with your point.
U r big man
True
I think Noel talks on average speed verses the influx of cars in our country whilst the roads are not wide as compared to speed limit
#babache kkkkkk
120km/h; reconditioned vehicle; narrow (2 lane) roads; poor driving skills and perhaps high levels of alcohol in blood! Imagine ladies n gentlemen
Truth.
mulungu ndinu okhulupilika ndikukwanitsa malojezo anu,chisisi changozizi mulinayo phwanvu zoziulula ndikuonetsa ukulu wanu
Bwino nazotu kumipandoko!!
Kaya mukudyesera mwazi wa anthu mlengi amatikonda nafenso siku lina tizadziwa choona cheni cheni eish! !
The devil is a liar
Izi ndie zinatu
Bushiri atitha ndithu!!!!!
mmmmmmmmmmm uli ndiumboni?
Kagone nawe follower wa bushiri……satanism too much basi. Mukanali mtulo n mukanali kuohesa anthu opanda zifukwa ndi bushiri wanuyo asaaa
mulungu ndiyemwe amaweruza osati anthui
Mulungu wake uti you must say a devil koz you all belong to devil with your bushiri!
lwe you belong to God nde myb u cn tel the truth..
Kkkkkkkk. Koma kumeneko
Poor mind
Hahahahaha i wonder why you always say bushiri bushiri….mukanali mtulo ndithu …i have no time follow that bustard ….false prophet like that one!. You are the one with poor mind koz muli busy kupanga follow fake bushiri. Keep on shouting i recieve papa tione kuti zikutherani bwanji. Asatana inu
major 1.The prophet of our generation
l receive timalandra ndfe lwe zkukuvuta ndchan? he is fake to you but to me naah
Kkkkkk hahaaaaa jst go to hell with your fake n liar bushiri????. Ntchito kulalika zandalama not salvation???……flat footed rhinos
ukuziwa bwanji kt amalalika zandalama zokhazokha yet umadana naye? goodnight yob kkkkk
Usova i will never follow this bustard ……….ugone bwino ndi fake bushiri wakoyo.
kkkkkk am l telling you to follow him man?l am his follower….the daughter of major 1 The prophet of our generation. yeaaah
Zaziiii go to hell all of you….asatana inu …mwina kuti mfiti zowotha ma tyre asaaa ukhalira yomweyo ya bushiri kumangoti i recieve???…..
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Ziliko nkulinga utatosako mwina akuziwa chomwe akunena munthu msango msusa mwina nayeso akupanga prophesy potitu siwonse akudumpha ndi wolumala kapena ndi akhungu
Chrisy Kapota Ng’ona case closed apa …… miracle money basitu kuswera pakhomo waiting to to church n shout i recieve….ndadusa nawo???????
kkkkkkkkkk dusani
Ok! Ndachiziwa chifukwa chake,mukuyener kumuuza prsdnt Muthalika abwere kuno ku SA azaone misewo mwina angazuke. Fck 4 hm!
Minbus iyi.
Iwe nde wanyasidwa
Kkkkk the laws were there some are good but they inforce too much on minbus. Leaving buses and trucks
But min buses are carelessly driven and over loaded
Kutifinya kwambiri amphawi
But On other we are protected
Khani it’s not protection but the traffic police they pretend to inforce the law. Instead if us benefiting they are getting rich.
Oh OK,ndiyeno titani kapena zikale motani abwana
Malamulo Ena achoke
Tiye konkho tiauze
Eya kuchedwa kulimbana ndi minbus nyanja akutilanda ??
Za nyaja sizitheka
Tiyen tizingopemphera osalozana chala,mukamat Bushiri is behind this or that,kod iyeyo ndamene amayenda magalimotoyo???
Osamapereka ma report abozatu apa where exactly in Blantyre!??
but also we need big roads in malawi too! we have too many small main road in our country shame on us too
Lookin at the pic,this is not a minbus.so why braming only minbuses? But its now worrysome.
nde makape ena ali bzy ma demo kukana kupulumusa miyoyo ya amalawi pomwe khani ya chaponda amkangogona….kuma malawi timapanga zithu ngat athu onse opanda nzeru anaponyedwa ku malawi kuno..
I think we need special prayers for this, complaining or blaming demons for this won’t help us, we have to engange ourselves in a spiritual war through national prayers. Its too much now brothers and sisters, this isn’t normal, something is wrong somewhere!
nde makape ena ali bzy ma demo kukana kupulumusa miyoyo ya amalawi pomwe khani ya chaponda amkangogona….kuma malawi timapanga zithu ngat athu onse o
Bushiri bushiri bushiri bushiri.
Plz help us with ur players
Who is Bushiri? I steed of asking for a help living to a God ,your ther calling Bushiri , may God forgive you. Bushiri is not God.
Who is Bushiri? I steed of asking for a help living to a God ,your ther calling Bushiri , may God forgive you. Bushiri is not God.
Kķkk mulungu wako ndi bushiri???????????zz????
Your looking so beautiful . But you dont know who creates you
Kkkkk
A Malawi panopa ngozi zachuluka mwamukumbikira mulungu, Mwakolora dzinthu zankhaninkhani koma osamuyamika, ndinu mtundu otani?? Musiyeni nayenso watopa mmenenso inuyo mumatopera mukakhala pamtendere
Mwalalata kk
Koma uli dzilo lomwelino?sizikixiwika moti uzingo pemphera.basi busy kulalata.
Mmm u better think about yourself!
koma munthu sakunama.. kodi Mulungu azikumbukiridwa pamavuto basi? mvula ikavuta anthu amasonkhana kupemphera kut Mulungu atipatse mvula.. this year Mulungu watikondeera palibe mpingo omwe wasonkhana kuthokoza Mulungu .. tiyen tizipemphera pa
pamavuto komaso pa mtendere
Yes I do think of myself and I pray everyday, be it in joy or in sorrow
Mmmmh rueben ndi jaco
It has reached to the point that almost every day people must die. If it’s someone who is creating all these accidents. I ask God to get rid of him before he proclaim that he is the most powerful than you the most high God. He has done enough to deserve a death sentence.
Eshi!!!;; mwina madriver wa akumapanga dala kufuna kutchuka kuti apangitsa ngozi nanga daily?
munaendesapo galimoto inu kod? simunalankhule bwino tu apa
Palibe amene amafuna kufa, tiyeni tizilankhula bwino.
Childish behavior and remarks check ur tongue boooy?????????
Sanaonepo maliro angozi ali mnyumba mwao. Thats why akuyankhula zopeperazo. Sakuziwa momwe zimawawira
Balibenso wina ndiyemweyo wamtaliyo mesa anali ku ameleka last week.watigulitsila dzikolitu.
Ndichani kodi A Malawi, so sad lndeed,if devil controls let not leave power to him.
Mulungu chonde musamusiye Malawi Ku satana mmjerekedzi yemwe akutha anthu anu kuzera pa ngozi zomwe zikuchitika modetsa nkhawa.Tumidzanu mzimu wanu woyera afungatire malawi
Amen
SATAN wayendamo wapasi dziko muno ndipo Malawi waipa kwambiri
Chimanga munalandira chija… Abweze
Yachitika pompaja panachitikira ina ya truck paja koma po nd pa mtunda pake
Sory Malawi nzanga…
yachitika kuti?
Too much ufiti
A Zodiak Pepani Mukundpepeseleko Kwa A Satanism Tatopa Kumva Zangoz
Tanyanyaamalawi Kumangolandilazilizonse Osadabwa Ndimaprofit Awoamenewa,onlygod Knows.
Waguan ina Malawi?
all my god protect us
Next time use word God!
Ambuye atithandidze eeeee
So bad
Malipoti omwe tsamba lino lapeza akuti galimoto ya mtundu wa thilaki inaduka mabuleki ndipo inaomba galimoto zina zomwe zimadutsa.Ngoziyi yachitika kwa Magalasi mu mzinda wa Blantyre.Pakadali pano sizinaziwike kuti ndianthu angati omwe akhudzidwa ndingoziyi. Nyuzipepala ino ipitiliza kukupatsilani zankhaniyi
Chuma chapasewu aaaaaa!
Too bad
this is a joke…. let me say it clear. .. who is sacrificing these innocent pipo? for what purpose? shuld i say bcoz of poor roads? hear me pipo…. shuld I say peter is behind all this so that he shuld win during the coming elections? we r in a demonic period. whenever u r travelling just pray n repent all ur sins… open ur bible n read it like a fool so that the devil shuld not bring anything evil into ur mind. maybe bushiri wants to increase his powers as a prophet. … I am not sure…. stop being too stupid u may end up in hell… satanic at it’s best. .. someone is being promoted indeed. enjoying all the things… God knows n he has plans for everything. ….
It’s just more than too much bro…and i believe some evil people are sacrificing, but this God is too good, someone will be exposed by a powerful and righteous prayer..
Munaiyamba bwino2 nkhaniyi, koma pokha mwangonena za Bushiri mwaononga.
Aonongaditu akuluwa
walemba zambiri ndinaziwa kut atsamwidwa,comment ngat history ya Kamuzu
kkkk mpaka history ya kamudzu
mwaononga pa bushiripo kumayambiliro lnali bwino
I don’t care… who is he not to be involved? he is a human being as well. I don’t worship him. so u werw happy coz I attacked peter? u r so evil. am not like that. Bushiri is just a mare person like me. his prophecies r just meant to make pipo happy. so shame on u. I am not here to comment something that will please ut mind or heart… may u feel sorry for urself n ur generation. if u think we follow the same christ then we t different. ur Christ tells u that following him is easy but mine tells me that if am to follow him then I shuld expect clouds n darkness. ….
sizolozana chala mwina ndweyo ukupangiza ngozizi
even me I knw whm to blame bt I dnt hve power to attack such person, only God wll do something on ths issue,
but ur r not even praying. .. am just asking myself questions. I didn’t point a finger
Surly! Us Pple We See Satan When Accidents Occurs, Bt When Friends Are Doing Evil Morals Eg Drunkedness Smorking Prostutes Envy Selfishness Corrupt Jealous Argueing & Manymore, We Support Them, Is That Not Powers Of Devil Taking Life Of Pple Everyday, All These Need Our Prayes 4 One To Be Saved From Satan Bt Time Will Come: Ecclesiastes 3:1 , Revelation 20:7 Satan Will Be Defeated, lastly, Revelation 14:13 Lord Will Bless Everyone Who Has Faith In Him When They Die , Amen
All my Lord help Malawi. Tiyeni tilimbike pakupephera iyu nazikang’a atithawe chifukwa malemba amati mukanizeni ndipo azakuthawani.
” dats gud idear, its only a prayer.
Yes please prayer is a weapon to destroy Satan
kkkkkkk….kodi zikuchitikabe eti
Munalj anthu ndi matumba?
What do you mean Bertha
Ine ayi
Yachitikira pa magalasi before njanji
ngozi iliyonse anthu koma Satanic hahahaha mesa mati mapephela bwanji osathana nazo mafuna kunena kuti otsitira satana ndamene alindi mphamvu
Mulungu angapangitse ngozi et?
Banda kulakhula kosatsegula maso kumeneko open your eye and see this is the spiritual war wok up please Mulungu akuyendele.
May God forgive you coz you don’t know what you’re talking
Komanso overspeeding anthuwa
Amen ,,@Gedion
hey mind ur language @vinicent band
hey mind ur language @vinicent band
kodi iwe ndi munthu wanji? kapena ukuziwapo kanthu? uzazindikila zikazakupeza. keep ur mouth short!
I can agree with you three, if you say these accidents are the work of the devil. But don’t blame others if you are not sure that these accidents zikumapangika ndi a satanic. Chifukwa is same bible lati usamapangire umboni unama.
yah yah u speak lyk dat bcoz God is de best forgiver
Mr banda preaz change ur mindset and start reading bible or qran now
palibe wandimvetsa apa ndawona hahahhahaha
ndikuti ngati zili ngozi zoti akupangitsa ndi a satanic inu amene mati mapephera thanani nazoni tione.
ndapitiliza uko kuti mafuna kunena kuti a satanic nde a mphamvu pamene inu opephelanu mulibe? chikhala kuyakna bwenzi mumayakha zamphamvu osati zachipembedzezo hahahahahahahahahahahah
May Almighty God Forgive You Banda.
May Almighty LORD Forgive You Banda.
Lets find out first. Tsoko mtunda ndi nyanja coz oipayo watsikira komko koma poti mpanda dzinayi dzalambira Yehova like what Mathews 4 says apepesa asaone ngat watasa. Mvetsetseni mkuluyu sakudziwa chomwe akunena.
f
Devils at work.
Nanga ndi minibus iyi yamamawaso siminibasiso
Yachitikanso kuti-which part of Blantyre?
Pls GOD tetezani ana anu taonani eeeeeeeeeeeeee!
ooooooh!!!! how many people have returned to their maker?
Iiii koma asatanic tu awa akupanga zonsezi, koma tithanatu demon ukuchepa
kkkkkk ndipo kwambiri kufunika kupempjera molimba abale
Eish..koma inu
ndadutsa pomwepo mene ndimachokera ku ntchito lero madzurowu koma mmmmmmmm bad galimoto all most four plus a track
Iiii four mpaka? Koma inu talakwanji ife?
Ndinthawi basi osati satanic
Inde ndinthawidi nchifukwa chake tikuti ndi asatanic akukwanilitsa malemba koma tikuti akuchepa tithana nawo
Mukunama Kutiko Lero Maminbus Sanayende.
Kd anena kt ndi min bus?
Kkkklk