Zongotipeza kumene: Ngozi inaso ku Blantyre

Patangotha maola ochepa anthu akukamba zangozi yomwe yachitika m’bandakucha lero, ngozi ina yachitikaso mu mzinda wa Blantyre.

Ngozi kwa Magalasi ku Blantyre.

Malipoti omwe tsamba lino lapeza akuti galimoto ya mtundu wa thilaki inaduka mabuleki ndipo inaomba galimoto zina zomwe zimadutsa.

Ngoziyi yachitika kwa Magalasi mu mzinda wa Blantyre.

Pakadali pano sizinaziwike kuti ndi anthu angati omwe akhudzidwa ndingoziyi. Nyuzipepala ino ipitiliza kukupatsilani zankhaniyi

Advertisement

291 Comments

 1. pali madriver ambiri omwe sanapite ku driving school pepani ku road trafic chepetsa ziphumphu ngati anthu akufa ndi chifukwa cha inu a road trafic

 2. When a country is ruled by the wicked, this is the results, expect more until these pipo repent all atrocities committed to innocent blood and all corruption issues crippled all over them

 3. uchimo wapadziko lapasa ndiumene ukudzetsa mkwiyo kwa mulungu ngoz zikucitikaz ndkwiyo wa mulungu cifukwa chauchimo wathuwo

 4. Ngozi zinazi ndi chifukwa chakuti anthu ena akupanga upgrade ma licence awo alibe ukatswiri ndi ukadaulo obvomerezeka ndi malamulo apa nseu.

 5. We nid special prayer for zalewa road ed let’s mek 1 bundle for those prayer to go back to the sender ed I bliv wat all my friends zomwe mwayankhura ndizoona Zake but 1 thing let’s unite ed put GOD 1st in JESUS name

 6. A malawi we call God in troubles only why? In piece we drink, dance and so many. Satan tidamuvomera malinga ndi tchito zathu sangativere Mulungu

 7. Vuto lina ndi loti ma driver ambiri akupeza ma driving licence mwachinyengo.God protect Me&my Nation . David Said’ Mau Anu Ndiyo Nyali Yakuunika Yapanjira Panga.Be My Light LORD.

 8. Amalawi kukonda zotchipa timagula magalimoto okutha kale ma brandnew second nde zizitivuta.
  Remember expensive cars are cheap the cheap ones are expensive they can break anytime and likely to cost our life ngati angatero tili mkati mwa ulendo.
  Boma liletse magalimoto opanda zokwanira pamseu apa tili pa nkhani ya Cof izipelekedwa kwa galimotodi yoti ili bho
  Magalimoto ena amaloledwa kuyenda panseu mabreak alibe amaimira engine break kapena magear . Izi sizodalilika

  Atraffic atithandize moyenera osati msuzi basi pamseu magalimoto ophotchyoka mkumaendabe pamseu.

 9. It doesnt mata kut zikuchitika chifukwa cha nsewu ka chani but zonsenzi nzokondweretsa satana yemweyo chifukwa tili naye komkuno and akudziwanso kuti masiku anchepera. And Mulungunso amalora kut tionongeke ngat sitikumumvera but tikampatsa attention will find out. What i mean is osachedwa apa ndikuyankhula zambiri coz greater is the one who gave us life, lets just put our trust in him atiwululirani zinsinsi like wat yeremiya 3 vs 33 says. Palibe zosatheka ndiYehova tikathanga ufumu wake mathews 6 vs 33 chachikulu tidzichepetse 2 mbiri 7 vs 14 God wants us kut alamulire mmitima yathu, maka tatsalafe whachidule. thank you.

 10. There-many-ways-among-them-are;
  1.Dont-drink-n-drive

  2.speed-limit-must-be-observed

  3.follow-road-sings-pliz

  4.drivers-your-machine-alwayz-b4-u-boad-in

  5.observe-carying-capacity

  etc

  1. zomwe wanena ndi zoona koma ma driver ambiri sanapite ku driving school ndipo amangogula licence ngati munthu wagula licence malamulo apamseu angawadziwe bwanji? tachepetsa ziphuphu kuti dziko liyende bwino

  2. zomwe wanena ndi zoona koma ma driver ambiri sanapite ku driving school ndipo amangogula licence ngati munthu wagula licence malamulo apamseu angawadziwe bwanji? tachepetsa ziphuphu kuti dziko liyende bwino

 11. Our government must do something about our roads……we are still using miseu yomwe inapangidwa in the 80s pamene magalimoto anali ochepa.

  1. That’s primitive thinking…. We suggesting solutions here, we can’t jst seat nd accept that its time. Something is happening here nd we need to address this issue. Our gvt is doing nothing. By the way, how good is that road u are talking about nd is it a highway? These days in Malawi we need highways (freeways), more especially busy roads like Bt- LL road

 12. We need to have very strong prayers to these things happening including our friends ma Moslems fasting yao aponyere kwakuya kuti Satan asakhare ndigao

 13. Apolice Asiye Zopusa Amachita Akakhala Pamseu Zomalandira Tima K200 Ndicholinga Chot Galimoto Yomwe Siri Mu Condition Iduse, This Is Major Agent Of Malawi Road Accidents

 14. Palibe njira zotetezera ngozi koma titha kuchepetsa ngozi ngati:kuchepetsa speed pamseu,madalaiva aziziwa kuti ali pamseu ndipo nthawi iliyonse moyo wao okhoza kutha,mahampu aikidwe miseu yonse pamitunda yosachepera 4 to 5km iliyonse.

 15. Apostles,Bishops,Priests,Deacons,sisters and Brothers tigwilaneni manja ndipo tipemphere kwambiri kut ticotse ziwanda zomwe zikuyambitsa ngozi.AMBUYE odziwa kuteteza akhale pakati pathu nthawi zonse.

 16. ngozi kusonyeza kut palibe amayembekezera out zichitika palibe njira yotetezera ngoz ndichithu chosayembekezereka ngakhale oyenda pansi ama phumtwa pakumwalira ngozi

 17. ngozi ndi ngozi zimachitika zikafuna basi anthu anayamba kalekale kufufuza njira zochepetsera ngozi koma zikuchitikabe olo atati atraffic aziyendetsa magalimotowa zizichikabe

 18. Tingogulitsa magalimoto onse ku mayiko akunja zikatero ndeyekuti ngozi zidzachepa chifukwa timiseu takwathu kuno sitoyenera magalimoto.

 19. ngozi ndi ngozi imachitika pa thawi yomwe usakuyembekezera kuti ingachitike, kondomu izibowoka iwe nkumati umaziteteza kuti usatenge matenda ngoziyokhayokha

 20. Wina wopanda nzeru akuti kuchuluka kwa magalimoto ndiko kukupangisa ngozi zoona? Ku South Africa kuli ma galimoto ambiri koma ngozi sizifika pamene zafika ku Malawi. Munthu unganene kuti kulibe mizimu yoyipa ku Malawi masiku otsiriza ngati awa?
  Ndiye ena mukumangovumbuluka wautali osapemphela chonsecho mukukakwela zokwelazi.

 21. koma mulungu zonsezi akuona ndikulilira dziko lathu lamalawi lili pamoto koma tonse titamanga umodzi mmatchalitchi mmizikiti kdziko lonse lamalawi kumanga chimodzi kusala kudya kukwera mapiri satana azolikila pansi iye ndiolephera basi akunama iye kwake ndi kuba kupha ndikuononga koma ngati mulungu anapulumutsa ana a israel mmanja mwa pharao angalephere kutipulumutsanso ife mkamwa mwa satana tiyeni aliyense payekha titengepo mbali mogonja ndimozichepetsa ambuye imvani kulira kwa ana anu

 22. POOR ROADS with alot of pot holes =NGOZI BASI ..whether u like or not
  Kumalawi zimesu zambiri nzophotchokaphotchoka zomwe zikudzetsa ngozinso…ndipo Si ma MINBUS OKHA OMWE AKUPANGA NGOZI …ALL CARS IN MALAWI INVOLVE IN ACCIDENTS NGALHALE ZI MA BUS ZIKULU ZIKULU ZOMWE ANTHU AMAZIKHULUPILIRA ZIKUCHITANSO NGOZ KWAMBIRI

  NDE GOVT YALETSANSO MA BUS AKULUAKULU KUNYAMULA KATUNDU OR ANGOPONDEREZA A MA MIN BUS OKHA??
  NGAT YAKHO NDILAKUT ALETSANSO MA BUS AKULUAKULU KUNYAMULA KATUNDU SO HOW PPLE CAN TRAVEL WITHOUT BAGS/KAPENA KUT ZIBINYIRA..KKKKK
  Gvt construct Gud Roads to reduce Accidents…komanso ma Driver apa malawi muchepetse Mowa(Drink and driver its Dengerous

 23. But to me i have got different views in those accidents,this month of Musilim i hope these pipple has all the questions to answer.Nsembe maybe nanga tiziti nchiyani? Each and everytime these Moslem do their fasting,there are so many accidents believe me, but let us Pray in ve name of Jesus our Saviour so that this will never happen again.Justice imawawa you the Moslem simungandilodze coz am a son of Jesus ndipo sizingatheke olo mutachita kutani if my suggestions really true.

  1. Am a Christian and I believe that Jesus is lord..he teaches not to judge for we will be judged and also to love one another.

   Bro your how do u look on your comments…is it good???

  2. thats why i said its my view!!Nanga zoti ku Afghanistan akhilisitu awawotcha mu Church ali mkati mopemphera vamva? Fufuza pa internet uwona.Mtundu uwu zopha achristu samawopa bwanji iweyo ukuwabakira?

 24. I feel sorry and wonder to someone who is reaptedly denying the involvement of evil demons on our roads.He insist that the government needs to build good roads and without we keep on dying, what a shame.

 25. UKALI…
  “Tikakhala ngati ndife omvana anthu tikanamanga umodzii,tikanalilanditsa dziko m’kamwa mwa ngo’na,mano aSatanaa, amene akutafuna wanthu tsiku ndi tsiku matenda,njala ndi ngozi.Tikanamenya nkhondo yachiweni~weni ndimitima yoswekaa,ofunika tigwade tipinde maondo ndikuzipempherera izo,Ngati uli ukali wochoka kwa Yehova aleze mtimaa,pajatu akakwiya tidayiwale tonse pamakhala manja pwesaa.

  Chorus…….[nakulengaa chepetsani ukali….]

  M’bukhu lachilamulo amalemba akunena opani Yehovaa,Mukakhalaa omvera ndiofunitsitsa monga mwa chilamulo,mudzadya zabwino zopezeka padziko opanda oliraa,koma mukapanda kumvera Yehova adzakupatsani nthendaa,Miliri yoopsa idzakhuthulidwa pamatupi awanthu,kudzakhala matenda Chisiki,Chinoni,Kaliwondewonde,,,kudzakhala Njala,Maliro ndi nkhondo panjira Ngozi daily, Yehova amaseka koma akakwiya pamafa ambirii,Amakana chibwana kuchita uchitsiru ngakhale zinthu za ntudzu,akanena wanena palibe angaletse poti alibe deputy [sp]
  Nakulengaaaa….

  By; Josephy Nkasa.

  1. #@Thandie,nyimbo iyi anayimba Nkasa yi sikuti anangopeka koma kuti anatenga mau a Bible,zambiri Zomwe anakamba ndi mau oti alipo chikhalire m’bukhu la moyo,ndiye nkuyankha kwanga nkoti bukhu lomwelo lidati ngati anthuwo akadziwa kulakwa kwao Mulungu yemweyo amabwerera kwa iwo nawasunga,nawateteza,nawapatsa zomwe amapempha. Now nkuona kwako mudziko ili ndi angati amene akufuna kuyenda munjira za Mulungu ?Ukamakhala,kuyenda m’madera osiyana ukuona zintchito zanji zomwe akuchita ana awanthu pansi pa nthambo ili zomwe zili zokondweretsa Mulungu ?chifukwa ndikaona zinthu zatenga malo ndi,chigololo,mwano,nsanje,kaduka,umbava ndi umbanda etc.

 26. Government must do something to cube this problem coz as we remember Bangwe bridge accident that was happened past year’s ago it was the same government were ended the problem by deploying soldiers to guard the bridge untill they were caught the person who was caused an accident by throwing chicken n it was said to here that the Boss of Siku Transport.

 27. God has promised to crash the devil under the feet of His faithfuls:Romans 16:20. True God fearing people should not be pannicking about this accidents. Because Greater is He who is in us than he (satan) who is in the world.

 28. pemperani mulungu Iona amalawi.zonsenzo zikumachitika kamba ka mphamvu ya satana amend akulamulira Malawi yonse.we are on good position ya Satanism amslawi

 29. Around 50 to 70 vehicles are imported to Malawi every day.One accident which usually involved one vehicle now amakwana atatu.In 1999 it was possible to travel BT and LL with only 4 overtakes now asume you travelling @ 120 km/h you are likely to overtake 7 or more.lets face it average cars, buses minibuses now travel at these speeds than they used to way back.The roads have almost remained the same.As cars have become quiter in cabin noise few realise the speeds until emergence…..then you blame bad spirits wake up guys…we know the reason.Mark my words we will continue having these accidents until something happens.

  1. I think Noel talks on average speed verses the influx of cars in our country whilst the roads are not wide as compared to speed limit

  2. 120km/h; reconditioned vehicle; narrow (2 lane) roads; poor driving skills and perhaps high levels of alcohol in blood! Imagine ladies n gentlemen

 30. mulungu ndinu okhulupilika ndikukwanitsa malojezo anu,chisisi changozizi mulinayo phwanvu zoziulula ndikuonetsa ukulu wanu

 31. Bwino nazotu kumipandoko!!
  Kaya mukudyesera mwazi wa anthu mlengi amatikonda nafenso siku lina tizadziwa choona cheni cheni eish! !

  1. Hahahahaha i wonder why you always say bushiri bushiri….mukanali mtulo ndithu …i have no time follow that bustard ….false prophet like that one!. You are the one with poor mind koz muli busy kupanga follow fake bushiri. Keep on shouting i recieve papa tione kuti zikutherani bwanji. Asatana inu

  2. Ziliko nkulinga utatosako mwina akuziwa chomwe akunena munthu msango msusa mwina nayeso akupanga prophesy potitu siwonse akudumpha ndi wolumala kapena ndi akhungu

  1. Khani it’s not protection but the traffic police they pretend to inforce the law. Instead if us benefiting they are getting rich.

 32. nde makape ena ali bzy ma demo kukana kupulumusa miyoyo ya amalawi pomwe khani ya chaponda amkangogona….kuma malawi timapanga zithu ngat athu onse opanda nzeru anaponyedwa ku malawi kuno..

 33. I think we need special prayers for this, complaining or blaming demons for this won’t help us, we have to engange ourselves in a spiritual war through national prayers. Its too much now brothers and sisters, this isn’t normal, something is wrong somewhere!

 34. nde makape ena ali bzy ma demo kukana kupulumusa miyoyo ya amalawi pomwe khani ya chaponda amkangogona….kuma malawi timapanga zithu ngat athu onse o

  1. Who is Bushiri? I steed of asking for a help living to a God ,your ther calling Bushiri , may God forgive you. Bushiri is not God.

  2. Who is Bushiri? I steed of asking for a help living to a God ,your ther calling Bushiri , may God forgive you. Bushiri is not God.

 35. A Malawi panopa ngozi zachuluka mwamukumbikira mulungu, Mwakolora dzinthu zankhaninkhani koma osamuyamika, ndinu mtundu otani?? Musiyeni nayenso watopa mmenenso inuyo mumatopera mukakhala pamtendere

  1. koma munthu sakunama.. kodi Mulungu azikumbukiridwa pamavuto basi? mvula ikavuta anthu amasonkhana kupemphera kut Mulungu atipatse mvula.. this year Mulungu watikondeera palibe mpingo omwe wasonkhana kuthokoza Mulungu .. tiyen tizipemphera pa

 36. It has reached to the point that almost every day people must die. If it’s someone who is creating all these accidents. I ask God to get rid of him before he proclaim that he is the most powerful than you the most high God. He has done enough to deserve a death sentence.

 37. Mulungu chonde musamusiye Malawi Ku satana mmjerekedzi yemwe akutha anthu anu kuzera pa ngozi zomwe zikuchitika modetsa nkhawa.Tumidzanu mzimu wanu woyera afungatire malawi

 38. Malipoti omwe tsamba lino lapeza akuti galimoto ya mtundu wa thilaki inaduka mabuleki ndipo inaomba galimoto zina zomwe zimadutsa.Ngoziyi yachitika kwa Magalasi mu mzinda wa Blantyre.Pakadali pano sizinaziwike kuti ndianthu angati omwe akhudzidwa ndingoziyi. Nyuzipepala ino ipitiliza kukupatsilani zankhaniyi

 39. this is a joke…. let me say it clear. .. who is sacrificing these innocent pipo? for what purpose? shuld i say bcoz of poor roads? hear me pipo…. shuld I say peter is behind all this so that he shuld win during the coming elections? we r in a demonic period. whenever u r travelling just pray n repent all ur sins… open ur bible n read it like a fool so that the devil shuld not bring anything evil into ur mind. maybe bushiri wants to increase his powers as a prophet. … I am not sure…. stop being too stupid u may end up in hell… satanic at it’s best. .. someone is being promoted indeed. enjoying all the things… God knows n he has plans for everything. ….

  1. It’s just more than too much bro…and i believe some evil people are sacrificing, but this God is too good, someone will be exposed by a powerful and righteous prayer..

  2. I don’t care… who is he not to be involved? he is a human being as well. I don’t worship him. so u werw happy coz I attacked peter? u r so evil. am not like that. Bushiri is just a mare person like me. his prophecies r just meant to make pipo happy. so shame on u. I am not here to comment something that will please ut mind or heart… may u feel sorry for urself n ur generation. if u think we follow the same christ then we t different. ur Christ tells u that following him is easy but mine tells me that if am to follow him then I shuld expect clouds n darkness. ….

  3. Surly! Us Pple We See Satan When Accidents Occurs, Bt When Friends Are Doing Evil Morals Eg Drunkedness Smorking Prostutes Envy Selfishness Corrupt Jealous Argueing & Manymore, We Support Them, Is That Not Powers Of Devil Taking Life Of Pple Everyday, All These Need Our Prayes 4 One To Be Saved From Satan Bt Time Will Come: Ecclesiastes 3:1 , Revelation 20:7 Satan Will Be Defeated, lastly, Revelation 14:13 Lord Will Bless Everyone Who Has Faith In Him When They Die , Amen

 40. All my Lord help Malawi. Tiyeni tilimbike pakupephera iyu nazikang’a atithawe chifukwa malemba amati mukanizeni ndipo azakuthawani.

 41. ngozi iliyonse anthu koma Satanic hahahaha mesa mati mapephela bwanji osathana nazo mafuna kunena kuti otsitira satana ndamene alindi mphamvu

  1. I can agree with you three, if you say these accidents are the work of the devil. But don’t blame others if you are not sure that these accidents zikumapangika ndi a satanic. Chifukwa is same bible lati usamapangire umboni unama.

  2. ndapitiliza uko kuti mafuna kunena kuti a satanic nde a mphamvu pamene inu opephelanu mulibe? chikhala kuyakna bwenzi mumayakha zamphamvu osati zachipembedzezo hahahahahahahahahahahah

  3. Lets find out first. Tsoko mtunda ndi nyanja coz oipayo watsikira komko koma poti mpanda dzinayi dzalambira Yehova like what Mathews 4 says apepesa asaone ngat watasa. Mvetsetseni mkuluyu sakudziwa chomwe akunena.

Comments are closed.