The Muslim Association of Malawi (MAM) has announced that this year’s Eid ul-Fitr celebrations marking the end of fasting in the Holy Month of Ramadan will be observed either on Sunday or Monday.
The development means that Monday will be a public holiday.
According to a press statement from ministry of local government and rural development made available to Malawi24, the development is depending on the sighting of the moon.
The statement which has been signed by the ministry’s press Secretary Kiswell Dakamau indicates that the moon will be sighted either on Sunday or Monday.
Komabe mayeso a Maneb ana athuu akukalemba
Bullshit
Madolo buanji kuwawa pamenepo dzulo munatokota kwambiritu lero buanji eeee no mtaji eti mumati mungatani osamapnga against ndi zamulungu sizoti ndi holiday yoti anthu akukachedzela kumowa ai kapena kukhodzekela kuphana ngti mmene mumachitila muja ai izi ndi zapadela Dela kukamutamanda mulungu amene anatilengayo pakuzichepetsa not kukasangalala ndi zithu zomwe analetsa iye ai
Tingoyamikila Mr president thanks
Ndikumuyamikaso mwini kuthekela kwachina China chili chonse Allah subuhanahu wataghala
Eid mubarak brosz and ccters
mashah allah
Holiday while student’s proceeding with exams
Wavara chikofiya dobadoba uyo!
Kodi amalawi mukupanga ma complening zowonadi? Ozangoyamikabwanji. Ambirinu tchitoyo mukugwira kwa mwenye achisilamu omwewa ndeinuyo mulikaka kufunakugwira tchito tsiku la eid nde mabwana anuo ndeati alindichizangalalo ndemukuthandauza chani ma complen amewa ngati wapeleka ulemu president and what about you guys? Who you think you are?
Maa sha Allah
Inshaallah muchifunilo chamulungu mwezi uwoneka.winawe ufune usafune monday ukuyenera kupuma basi kkkkk eid loading
kulankhula mopusa wakutsutsa ndani kapena English inakupitilirani titanthauzile ifensotu ndi achisilamu but kumamvetsetsa
But is a Christian nation.
Nde mupanga bwanji poti holiday is granted??
To Muslims not Christians.
kkkkkkkk olo mudane nazo kma ndi holiday basi
# Felix sukuziwa chomwe ukukamba
Who declared it to be a Christian state? When was that ? And why?
musavutike holiday kulibenso, muzikamasulirana nokha nokha kumeneko
This holiday is for Muslims not malawi nation.
Bolani Ife A Maneb Takana Ma Holiday Anu Ongolotawo!
MAKHAFILI AKUDANDULA HOLIDAY IYI NGAKHALE OLENGA DZIKOLI AMANYADILA NDI HOLIDAY
Taqqiya on its best! We will regret this
Nanga mwezi ukapanda kuoneka, holiday yo ilepheleka?
So what! Does it make it diffetence
Nawo mwezi usaoneke tione ngati mumasula sipaja mumadikilira kuoneka kwa mwezi.Mwina mukamva ku Egypt kut wawoneka angakhale musanauone mumasulabe kkkkkkkkkk
Khalani ndi ulemu pa nkhani za chipembezo
Sakuziwa chomwe akulakhula ameneyo alibe nzeru #u Frazer
Maa shaa Allah
Thank you Mr president
Mashaallah
Masha allah
good
This is said Arabia
Nooo the same Malawi u knw.
Allahamudulila
Alihamdulillah
Maa shaa Allah!
F**k u Peter holiday 4 Wat mataf**k?
Mesa holiday ya maboko
Maboko akumapwala kwamako
Enjoying those comments lol?????
mulibe nzeru dats y mukunyoza chipembezo cha nzanu kod pa xrismac samaika holiday? Nde zikakanike pa Eid? # muzikula mxiiiii
ok thats good…..
Allahandulirai
^
Salaam wa laikuum….