Pamene masewera a chikho cha ma timu asanu ndi atatu mu chikho cha Airtel chomwe chifumbire kuyambira lowelukali, anthu ena otsata za masewera a mpira wa miyendo ati chikhochi chikhalangati ngati kukumba madzi pa thathwe kuchipambana kuti wina akachimwelere.
Ambiri akuti kubwera kwa m’phunzitsi wa timu yayikulu ya dziko lino Ronny Van Geneugden (RVG) kupereka mpishupishu kwambiri kwa ma timu omwe amachalira kuti mwina ayenda moyera potengera mbiri zawo.
Malingama ndi yemwe adali technical director wa timu ya Nyasa Big Bullets Billy Tewesa, iye wanenetsa kuti za ulendo uno zikhala za mlingo wina chifukwa osewera aliyense afuna kuti awonedwe ndi RVG mcholinga chofuna kudzigulira malo mu timu yayikulu ya dziko.
M’mawu awo a Tewesa ati Airtel top 8 ipereka mwayi kwambiri kwa osewerawa chifukwa ukhala mpikisano wa ma timu owerengeka chabe kusiyana ndi chikho chachikulu mdziko muno cha TNM super league chomwe chimaitana ma timu 16.
“Anyamata alimbikira kwambiri nthawi imeneyi kuti m’phunzitsi ndi omuthandizira ake awawone kotero kamba ka zimenezi ukhala mpira wa dzaoneni munditsimikiza ndipo kutenga chikho chenechi sukhala mtunda wa masewera” adatero Tewesa poyankhula ndi wailesi ina mdziko muno.
Koma malingana ndi wamkulu wa timu ya Wanderers Steve Madeira, iwo atj ali ndi chitsimikizo chonse kuti chikho cha Airtel chomwe changokhazikitsidwa kumene chaka chino atenganso kumka nacho ku nsewu wa Lali Lubani monga mwa mbiri yawo. Pamene iye wanena kuti 15 million ndi ndalama zomwe iwo ali nazo nkhuli kwambiri.
Madeira wanenetsa kuti Manoma akomzeka kwambiri kuti ateteze mbiri yawo yotenga chikho chilichonse chomwe mchoyamba m’maso mwa a Malawi ku nkhani zododa chikopa.
Koma m’mawu ake sabata zapitazo RVG adati iye ngati m’phuzitsi adzisankha osewera malingana ndi umo m’mene akukankhira chikopa pa bwalo, osati mbiri ya munthu kuti wakhala akusewera kwa zaka zochuluka mu timu ya dzikoyi. Izi zatsimikizadi kuti masewera a chaka chino afumbiradi zomwe sizikhala zophwekwa kwa akatswiri omwe akhala akunyamula dzikho monga cha Standard Bank, Carlsberg, Presidential, FISD.
Chikho cha mu Airtel top 8 chiyamba ndi ma timu a Silver Strikers kuphana ndi Bullets pa Bingu national stadium, pamene MAFCO idzalandile asilikali amzawo a Moyale pa bwalo la Chitowe ku Nkhotakota.
Sizidathere pompa koma lamulungu lake Beforward Wanderers idzaphana ndi timu yomwe iwo amatapako mphamvu zawo nthawi zambiri ya Azam Tigers pa bwalo la Balaka ndipo akatswiri a chikho cha 2016 super league Kamuzu Barracks asulana msulizo ndi Blue eagles pa Civo.
Ngakhale RVG akudziwiratu kt kunyerere kuli cream
Upite kusukulu ukaphuzire kulemba topic
kkkkkkk talembani zomveka amwene
Nyasa big bullets motomoto sindingaisiye ngakhale ndiluze 1o times
Tombolimbo iwe admi
Kkkkkkkk
Kkkkkk, kma
Za mkutu!!! lyaaaaaa
Fodyatu siwabwino tikasuta tizizimisila nafeso timakoka koma sitinafikepo size imeneyi lembani zomveka
Nkhani ife palibe tikumvapo shutup
Eshhiii kodi nkhaniyi akuti chani ndithandizeni pliz sindikuvesa
Nkhani yanuyi sikugwilizana ndi mutu wakeo. Apa nyerere zalakwa chani? Kodi ma player a national team amangosankha Ku nyerere kokha? Inutu mutiuza bwino chomwe mukutanthauza chifukwa zikusonyeza kuti wonderers mumadana nayo, kapena mumaiopa kwambili. Mtola nkhani sakhala ndi mbili. Zamkutu!! Utola nkhani umeneu munauphunzila kuti makamaka???
talembani zoti timve
Inenso ndabalalika ndimaona ngati zandivuta
24 ndiyazitsiru
Mtemgo wawutali salozerana man! NYERERE NDI MBAMBANDE UNGOTI PHEEE UZIONA!
Inu ukudusisani moyera ndi chifukwa mukugeya mwano eti.
Tazingogonani apa zonse ziliko mawa.
Usangoma eti?
Mwasowa zokamba eti? mukutiyamba dala ife abullets.
Za nkhutueti!!!
Palibe chmene ndikutolapo apa iyaa
Kkkkk pepani khaniyiza yasithaso m’malo molemba zomveka akumalemba zotigawanisa
No nsence at all
Kodiii Akut Bwanjii
Gayez Pa 14 Ndikukumbukila Tsku Lmene Ndnayamb Kulowa Pa Fb Ndnso Kucheza Ndi Mafrend ,ndye Mundthandnze Pachisangalaloch,,
Eee Amanoma Zabwno Znse
Eee Amanoma Zabwno Znse
Admin of this group anakhoza ndi ma F kuthandauza kuti #FOOL
Ndimaona ngat ndiine ndekha amene sindikumva, izi ndimbwerera zenizeni
Kkkkkk koma malawi 24
????????
Nyerere nde zatani pamenepa
Zopanda mutu mkomwe
Haaaa kungokhala osalemba bwanji?? nanga timve ziti apapa kkkkk koma zinazi kufuna kutchuka kuti mumalembako nkhani? muphunzilenso kachikena kuti mawa muzalembe zolongosoka tsiku lina
Ngati mwasowa zolemba, awuzeni omwe adaita abduct hon Kamlepo Kalua akuti atsanzikiretu kwa abale awo apafupi ndi kutali chifukwa ulendo wawo ngomangamanga. Abale awowo asadzatisokonse amvekere ‘bwanji simudatitsanzike ‘?
Sono RGV Wayamba kucocha ma TIGER? Kut azitero
Zamkhutu ngati mwasowa zolemba ingokhalani palibendkuvapo apa
mmmmmm mbola yeni yeni
Ukayambilenso school.
admin apa ndiye wandichititsa manyaz munthu wamkulukulu ngat iwe kukanika kulemba zomveka
Mutu wankhani ndizimene walemba sidxikugwirizana admin
Kodi RGV amasewera Tigers? Or editor yo kumati nkhani yopanga post imeneyi? Aka nde ka Newsletter kapa Namphungo community day secondary sch. Kkkkk
Or Manyumba Primary xool….kkkkkk
Hahaha Kapena luwangwa junior primary sch , Mustafa
Kk-kkk-kkkkiest, the post is not clear… Otherwise, the impression here is that many people are afraid of Manoma.
Nkhani yosamveka ngat imeneyi!!! Amalemba ndani?
Mmmmm palibe chimene ndikuvapo apa
Ine am Bullets 4n koma apapa ndisaname palibe chomwe ndamva koma, RGV, nde ndani and yamukhuza bwanji nkhaniyi muzilemba za nzeru timataya nthawi yathu kumawerenga zinthu Zopusa ngati iziii asaaa
Ndeapa Nyerere zatchulidwiranjiii koma olemb
CHONE GUYS APA NDI PAGULU SIBWINO KUTI TANGO CHITA KUMENE FODYA WANKULU NDI KUMALE MBA ZINTHU ZOSA M VEKA NGATI IZI
CHONE GUYS APA NDI PAGULU SIBWINO KUTI TANGO CHITA KUMENE FODYA WANKULU NDI KUMALE MBA ZINTHU ZOSA M VEKA NGATI IZI
Is Theng’eneng’ene a name???? U’ve puzzled us #Zambians men
palibe chomwe ndikutola
kkkkkkk ineso sindikudziwa kut akufuna kunena chiyan mulembe ameneyu
kkkkkk wakhuta mbatata kkkkk
Kod mpila wapakamwa udakalipobe?kumakula koma pila ndmu ground iyaaaaaa inu a 6666 fc mumandkwiisa hvy
koma yaa!! ma admin a BB sasowa, kukanika kulemba zomveka chiyakhuro cha makolo anthu!! chomwechi. kapena ndi 1 points mwaza nayo ku mpoto ija idakazunguzabe m’mitu mwanu eetiii!!!.
1 points yomweyo
Angoma go back to school timati 1 point not 1 points hahaha shame
Ngoma apa ndiye waonetsa kuzindikiratu shaa shame
kkkkkk thax mr Chiwaya 4 ur points kapena point of collection which 1?.
kKkkkKkkk 1 points?koma zinazi eish paja ati masapota a team yawo amakhala ozindira apadi mwaonetsa kuzindikira kwanu.
kkkkkkk#Allan ozindira ozindikira koma yaa!! oseka mzake sakudziwika nkhani mawa kkkkkk.
Am not a journalist but I can write something better than this
Nde zikugwirizana bwanj ndi nyerere
muwerenge nkhani yose ku website yawo not za pa fb ponkha …thus why mukuona kuti zikusemphana …mukuumira airtime yomalizitsa kuwerenga kwinako thus why mukungotukwana kkkkkkkkkkkk
Nanga C 3data yawoyo?
kkkkllklkk ndawonaso
Mukulimbana ndi nyerere mukuiopa muvakuwawa itengaso
Sindikumvetsa makosana chandilambalala chinyanja
Zaziiii
Mutu wankhani ndi nkhani yomwe ukukamba zikusiyaniranatu. Kapena chichewa sumtengatu?? Koma chomwe ungadziwe noma ikaona ndalama simasewera ayse.
Kuzitero Nyelere!!!!! 15mita.
Is the picture matching with the story kodi anthuni
nkhani ndi mutu wankhani mbola ,ndimaona ngati nkhani yonse ikhala yokhunza nyerere
NDE pamenepo theng’eneng’e lili pat? Kmaso osewera aliyese akufuna kuonedwa si a wanderers okha ! Kunena zoona akuluakulu 5 games k15 million aaaa ndani xangaifune?
Maphunziro athu sakutithandiza ndithu. Mtolankhani wantundu wanji wolemba chichewa chophwasuka! Nanga izi n’chiyani? (chikhalangati ngati kukumba madzi pa thathwe kuchipambana kuti wina akachimwelere.)
Kuphunzilira mzipinda za nyumba kwa Ntopwa.
Azanthu wolembedwa ntchito chifukwa choti Uncle awo ali pa company po! Akuwoneka ndi amenewa.
Zoonadi guys simukunama
Zitayeni