Thupi la yemwe anali mtsogoleri wa chipani cha United Independence (UIP) mayi Hellen Singh aliotcha mawa ku gome la Sikh mu mzinda wa Blantyre.
Malinga ndi m’modzi wa ku banja lofedwa a Asante Masantche, thupi la a Singh lizatengedwa ku nyumba yachisoni ya College of Medicine (CoM) kupita ku holo ya COMESA komwe anthu azakhale akukhudza thupi la a Singh ndikupitiliza ndimwambo wamapemphero asanapite ku gome la Sikh komwe akaliotche.
Pakanali pano, Boma lati ndilokhuzidwa pa imfa ya mayi Singh yemwe amalimbikisa mfundo za demokalase kudzera mu chipani chawo cha UIP.
A Singh womwe amwalila ndi zaka 64 zakubadwa atisiya loweruka kuchipatala cha Adventist atadwala nthenda ya cancer.
Malemu Singh anali katswiri pa malonda ndipo anali ndi kampani yobweleketsa magalimoto yomwe imatchedwa kuti SS Rent a Car.
Kuphatikiza apo analiso ndi Singh Trust pamene iwo amachita ndale zao mu chipani cha UIP.
Mayi Singh asiya ana awiri.
Sizoona zimenezi mpaka Kumuotcha nzanu ngati mbatata!

ndiye mwatikuwotcha heeee! izi ndizachilendo kwa ine.

kod kuotchako kumalawiko ndizachilendo kuva kut maliro amaotcha, chilichonse mkumasalira bwanji pitani mukaone nokha komweko basi dats all

respect their culture
respect their culture
Nyama yakeyo ili kwayani saotcha?
Nyama yakeyo ili kwayani saotcha?
akanawina u president bwezi atathetsa manda

Zilibwino kwa adzukulu sagwira ntchito ku manda….

Kkkkk achitabwino
Kkkkk achitabwino
ngakhale ataotchedwa koma nthawi ya chiukitso adzauka basi. chilichose chidzapelekedwa patsikulo

RIP
Burn in peace mama # B.I.P
Burn in peace mama # B.I.P
MHSRIP
MHSRIP
Palibe mvuto ndichikhulupilir chao asiyeni ok.

thank God, she ddnt win otheryz we couldhave been talking of another state funeral…. eeeiishb RIP

Clementation doesn’t matter your religious background, tribe, culture or national of your origin. It’s just another way of burrial. It helps to keep space in our already overcrowded cemeteries. It happens almost everywhere in the world.

Mpaka kuwocha mmmmm ndiye jahena wayiwonelatu basi

Ea xilibe hito, alitenthe, inu mwat aliotche” akalidwe nndan

I hope it doesn’t pollute our innocent oxygen lol, just saying.
Christians who follow JESUS CHRIST doesn’t believe that, imagine if it was the Culture of JESUS CHRIST, how could we be saved by His Blood.
Imagine if the family of Lazarus believe in that, in which body could JESUS raised?
Imagine if there were no bodies buried, after the Earthquake at JESUS CHRIST death which bodies could have been raised?
I’m not judging any culture or religious, JESUS CHRIST followers have hope for resurrection after death. He had demonstrated that before, so we believe.
Hahahahaha
Hahahaha, wasekatu kkkkk nanga Lazarus adakaotchedwa Yesu akadadzusa uti, phulusa?
Of course it could have still been possible. Spirituality has no limitations and let alone Jesus christ. Even if he was killed and fed to crocodiles, he would have still ressurected. It all happened in spirit not human understanding
Exactly thus my point, how can you live with Spirit and call it Lazarus? When we talk Spirit, we talk of invisible, you can’t see it. It’s easy for you to say it, even Peter couldn’t believe that it was JESUS until Jesus said touch me, for the Ghost has not bones and flesh, don’t you see important of your shape in Resurrection?
Anyway, we can talk about it but the fact remains none of JESUS CHRIST followers were burn when they die.I will follow JESUS CHRIST
If JESUS CHRIST body was burn, and resurrect in Spirit, where could be the Salvation? Who could talk about His resurrection # Brother Esau Mwamwaya?

Sheee
Sheee
shaaa! kuyamba kuotchera2 paziko lapasi ?nde kwa jajah kukakhara zotaa!!?

Then phulusa amatani naro please tell
Then phulusa amatani naro please tell
Mutitumizileso photo akumuotcha
Mutitumizileso photo akumuotcha
guys to burn dead body is not new.if she dead in JESUS she will be enjoying in the promised land .JESUS is always happy with this kind of death.

Rest in peace
Rest in peace
kkkkkkkKkkkk unachoka panthaka uyenera kubwerera basi kunthaka.

patsi pano ,akumane ndimoto kumwambaso?
patsi pano ,akumane ndimoto kumwambaso?
Mai Hellen Singh was a Ngoni by tribe from Ntcheu and also a Christian but am supprised today to hear all these issues that she’ll be burnt am confused!
she was oNce married to a hindu guy so ,,,may be she wanted to vo lyk her late husband.
Ok??

Akawawotcha adyedwe basi!
Akawawotcha adyedwe basi!
Chamba chija chikanali mmutu? kkkkk! Mount Zion sidzathekanso.

Ine sindikusutsana ndimwambo owotchana ayi izizilichomwechi chifukwa chamwabo wawo omwe amatsatila komanso ndibwino chifukwa akatelo ama server malo omanga nyumba ndiponso olima koma chohomwe chandikhudzaine ndifa mayiyu yemwe anayesetsa kuthandizapo pachitukuko chandale kuno kwathu mzimu wake uwuse muntendele

hiiii koma iriko.nde munamulola bwanji kuimira u president kumalawi?

Kkkkkk mpaka kum’bulusa kod ngati chikanga?kkkkkk

tilawetu nyama yake kno
eya ka
tilawetu nyama yake kno
eya ka
Which means she isn’t a Malawian?????
She was a coloured Malawian.Her father was a white man,she was born and grew up in Malawi.Only her husband was an Indian
Got u!

Yesu Anat,alekeni akufa Aikane Akufa Okhaokha Osat Okufa Aotchane

k
k
Shaaaaa nde awotchedwe koyamba pansi pano then kumwambaso akawotchedweso

kkkkk ndekutitu ndiochimwa kwambila anthu amenewa ati mpaka kumaochedwa padziko lapansi mpanpano guyz ndizilangotu zimenezo

kkkk
kkkk
Koma tikawelenga baibulo palipo pamene anati munthu akafa aotchedwe?kapena winawake wochuluka nzeru anangoyambitsa zootchana ndi malamulo amulungu?

Sizachilendo kuno Zimenezo ma Hindu ndi chontcho Sunday lililose amaotcha anthu ndikumakaika Phulusa.

Kodi malemuwa adali mu India,then adaima nawo pa chisankho?
She was a coloured,Her father was a white man.She was born and grew up in Malawi.Only her husband was an Indian
Okay, thanks for that information

I don’t believe she was christian because those they do such things are Hindu and Budapest

Mtembo ndi mtembo kuotcha or osaotcha palibe chingasinthe. Palibe mgwirizano pakati pa kutentha mtembo ndi chikhristu komaso palibe mgwirizano pakati poika mtembo kumanda kapena ayi. Kutentha mtembo ndi chikhalidwe, kuika mmandaso mchikhalidwe. Sikuti amatentha mitembo ndima Hindu okha.
Moreover she was a coloured not an Indian or asian.Her father was a white man and she was born and grew up in Malawi.

This is good way to save land for cultivation and infrastructures

Eee zodabwitsa izi
Eee zodabwitsa izi
Yooo
Yooo
Ndikubwera ndikufunako fungolo eshiiii
Ndikubwera ndikufunako fungolo eshiiii
zinazi tiyeni tizisiye mwambo wakwawo sukutikhuza

Dont Waste time 4 dat jas leave dem,dats dere cultural

Nde nanga bwanji yesu sanamuotche
Nde nanga bwanji yesu sanamuotche
sopano aziliotcha thupi kuti latani
sopano aziliotcha thupi kuti latani
expect no mercy,, akazingidwe basi mesa ndimene amapangila kwawoko… anywe, Rest In Ashes (RIA)

Kod meyesa amat fumbi ku fumbi dothi kudoth? tonse tikuyenera kubwerera komwe tidachokera kudoth! tsopano mukayika mmabotoro means wat?

Zakachasu lol milungu yakufa chifukwa chani zindidzagwada sellas

Ofunika kutenga chere ndi tsabora
Ofunika kutenga chere ndi tsabora
Ofunika kutenga chere ndi tsabora
Ofunika kutenga chere ndi tsabora
MMMMMMMM OWOTHAYO SAMUIMBA MULANDU
MMMMMMMM OWOTHAYO SAMUIMBA MULANDU
Mmmmh mwambo wa kuno malawi timaothananso?

mmmm nde akuotche.. uzavayeso ku hell… eeeee!!! kufa kuwiritu

tivaye nd mchere nd sabola?? kkk
tivaye nd mchere nd sabola?? kkk
No adzukulu needed
No adzukulu needed
Koma mwambo wake nde nkhan zinatu
Koma mwambo wake nde nkhan zinatu
heee!! go konko tikamve momwe zikaphulikire ziwalo

nde aliotchela khuni kapena mateyala?
They use firewood.
ndmaona ngt mateyala2 ndnali nawo pena pake

Mwikho
Mwikho
a DPP ndinu afiti & 2019 simuzaona vote
a DPP ndinu afiti & 2019 simuzaona vote
kaya aotcha kaya akazinga kaya akaika mmanda wafa basi y bothered about trivial tingz..inunosangoyamika kut manda athu sadzadza??

Yoo zootchana kodi?Alekeni ndi chikhalidwe chao komanso sizachilendo izi kuchitika bwanji nafenso kuno Ku Joni zathu akatisiya akatipatsa malo okumba manda timakumbunso mudzi pomwe eni ake sakumba mudzi aotchedwe basi phulusa litumizidwe ku India kwaoko abale akakhudze mmesa zimatero kwa amene musakudziwa Kathu tathauzo lake.
She wasn’t an Indian. She was a coloured, her father was a white man and she grew up in Malawi.Only her husband was an Indian.But indeed there’s no problem with cremating her body.Mwina ndizomwe anasankha iwowo mwini akanali moyo

i 3nk ambilinu sumukudziwa mungonvetsetsa basi mundipatse ma # anu a whts app ndikutumizren vidio yake mawa cz ndilikonkuno

Koma zootchanazi ,sizindimvekera bwino
Koma zootchanazi ,sizindimvekera bwino
Kod was she a christian pastor??? Or a Hindu pastor mmmmmm mpaka kuotcha nde iti iti imeneyi kkkkkkk
Eee?

Mmmmm kma zikhulupililo zinazi abale,ungasiye nazo kupemphela mbambadi mpali agundani kumtenje. Munthu kusankha kukaotchedwa ukamwalila,kma chonsecho ankati aluleya aleluya mtchalichi kutsogolo kwa anthu?. Ngati siidali nzika ya mbadwa ya dzikoli, bwanji osangonyamula malirowo nkukaotchela kwawoko?. Ana ndi zidzukulu adzachite kudziwa kuti, munthuyu adaotchedwa kamba kachipembedzo?. Zandiopsya kwambiri ndisanamepo apa, chabwino ndimomwemo mwambi wa gulu gufe poti nchakonda mwini mulekele.
Haha
#Rose_patrick dziotchedwani kumeneko, poti ndizo mudasankha mukadali moyo.
if nothing to comment on then spare your time dude
#wongani_wanda who are you?, just take your stupidity somewhere else not to me here ok?.

Thus shit
Thus shit
I like Godfrey’s comment
I like Godfrey’s comment
Mmmmmm ok?
Mmmmmm ok?
Barcelona 3-2 Real Madrid
Barcelona 3-2 Real Madrid
Akaotcha mpaka makala kapena kukazinga
Akaotcha mpaka makala kapena kukazinga
Gyz we may respect dem for it iz dere cuture. They also respect urs 2. Yap

Uku Ndiye Kufuna Kuwononga Mitengo. Mkuni Zomuwotchelazo Bwanji Kuzisunga For Better Use.

okaotchawo ndiye ndiolimba mitima eeee mmmm ayi

she wasnt hindu pliz,why are u spreading lies?? she was a christian and maliro ake akaika mmene timaikila enafe

Ngati imanukhira nkhuku chithu chaching’ono ikamawotchedwa.ndiye kulibwanji munthu koma yaa! zizakhalakotu kumeneko.vuto tilikutari bwezi titakhala nawo pa mwambowo kuti tizamvere nawo kafungo ka munthu wowotchedwayo m’mene kamamvekera.

Ife timafuma kumvesetsako zootchazo nde osalembanso bwinobwino ma details ake iyayi,

Abale ndithandzen zoochanazi ziko lathuli zilachitikapo ???
Zimachitika ndithu.There are places in Lilongwe and Blantyre where cremation of bodies is done

kunonso ku South Africa azungu amachita kuotcha.pulusa amaiika mu ka coffin kakang’ono then when the family have time amapita kukaimwaza phulusa ija ku mphili.ndimwambo ndithu enanu zisakudabwiseni

Zili Konko
Zili Konko
and ngati simukudziwa akaotcha phulusa lake amakataya kunyanja pamwambo wawo

In India this is what they do,also in china and other parts of Asian Continent in Malawi Lilongwe and Limbe where Hindu,Sikhs communities live they also practice this, it is not new iam one of the witness of these.By the way if you follow their teachings even in Catholism if one wishes to be clemented they do so but under the wishes of the person in question like what Pastor Ellen has done,after all if one dies his/her body is no longer of use thus why when you burry a dead person thus the end of it.We all shall have new bodies after resurrection day so why worry?Come to think of somebody dies and crocodiles consumes the body?what do you think of his/her tomb will be?We shall all have new bodies for our bodies that we have now are all perishable and we need unperishable bodies i mean heavenly bodies.
That’s very true. Moreover the lady was a coloured,her father was a white man.And cremation is not done by Hindus or asians only
truth Geoffrey ,the body is of no use!! l agree with u
Amen to that broh
koma amayimira bwanji u president ku malawi?
You are explaining in Christian way but was she also a christian.Do you know that some they believe that there is no life after death? So be very careful when commenting on such issues of religion matters.
Ndimene amapangira kuno ndimacheza ndi mzanga waku Nepal amatero kuti akamwalira thupi lawo amaocha

RIP Helene seen
RIP Helene seen
Burning ndi dhiru with this land scarcity!

palibe vuto awotche mesa wafa…
palibe vuto awotche mesa wafa…
Zoopsa
Zoopsa
Mhsrp
Mhsrp
kodi boma likukanidza manda,mpaka achite kuotcha kuli kuzingwa kwa a chibale?

BRAAI MEAT KKKK
BRAAI MEAT KKKK
palibe chachilendo pamenepo . akawotchedwe bas

Zimathandiza kuseva ndalama zogulira bokosi komanso potumiza Thupi ngati anali akutali

Mmmmmm paka kuotcha mtembo abale
Mmmmmm paka kuotcha mtembo abale
Rest in Peace
Rest in Peace
learn to understand and respect other people’s cultural views.this’ sympathetic to the party and any malawian for losing our productive political learders.may her sauls rest in peace!

So sad
So sad
Mayi busa mpaka kuwotchedwa.kaya ndizikhululupiliro zawo.

Malawi24
Mpaka kuti aliotcha mawa….. osangoti mwambo wa maliro uchitika mawa .

Tipite konko tikaonere mmene amaochera kenakaa?????

Ndiye akaotcha atani naye??
Phulutsalo amakataya munyanja. Hindu cultural

Zayambaso liti izi.
Zayambaso liti izi.
maro olima ndi omanga manyumba akazayamba kusowa ndipamene muzazindikire ubwino otchaa mtembo.ukafa wafa suzaukaso.
ZIUZEN MBULI MAN KUMANGOTSUTSA 4 DA SAKE OF ALGUMEMT BA2 KUPUSA WANTHU.

Mukaotcha mundipatse ine ndidye
Kkkkkkkkkk makalatu mudya bwanji?
Tizikanyotsola isanafike pamakalapo
Kkkkkkkkk
Mukaotcha mundipatse ine ndidye
Kkkkkkkkkk makalatu mudya bwanji?
Tizikanyotsola isanafike pamakalapo
Kkkkkkkkk
Rest in peace mama
Rest in peace mama
kd zimaiyu sanali wakuno?
kd zimaiyu sanali wakuno?
apart for kukhala mwenye Anthu achikuda or azungu amaotchedwanso ngati anali wachipembezo cha hindu ndipo palibe chilendo apo mwina kwa inu osayendanu ndiamene musakudxiwa zimenezo yendani muphunzile xool ina paja xool si class mokha ayi
Was she a christian pastor or else???
She was a Christian pastor.But when she was alive,she told her family members to cremate her body when she dies

Kod awauza kt kuno manda kulibe kkk nanga mpaka kunkazinga munthu

Kungofuna kuwononga nkhuni basi
Kungofuna kuwononga nkhuni basi
#INDIA
#INDIA
shaa!! abale tikanalanditsa dziko anali mwenye kani?
The lady was a coloured.Her father was a white man and she was born and grew up in Malawi.Only her husband was an Indian

Guy why are we so negative on wishes of other people. This lady was a Indian its their culture. And even you burn, you bare, you fry whatsoever they is no difference she is dead. Why so fussy wakufa samva kuwawa
I think the headline has no respect to the dead person .
Some people know that anthu amaotchedwa koma there is no need to be a headline .
But its just burning. And need to look on over population growth. And the land is get small. Most of the land will be grave. In Europe its their culture. And this lady is Indian and its their culture.
Kuotchako ndi dhiru koma ndi kusowa kwa maloku!
And it saves money than to spend money now but when he/she was alive we didn’t. Easy to transport no need to hire aa car for the body. 10years to come trust me lot of people will be just doing that
The lady was a coloured,her father was a white man.Only her husband was an Indian.And cremation is not only done by Hindus or Asians only
One thing you need to know is that if every dead person has to be burned because of land problems then this burning process will be expensive too.
Mudziko losowa nyama soya pieces amakwera mtengo.
But that was her wish. And her right must be respected. To me I don’t know why people are so fussy
It’s because tikamva kuti munthu waotchedwa ndiye kuti wavekedwa thayala ndi kumuthila petrol basi .
Zootcha maliro zimachitika behind people’s back koma sizimafika mpaka kukhala headline mu news.
When Fidel Castro passed on one news headine on BBC was “Fidel’s corpse to be cremated on Saturday”And that’s the same with Mw 24’s headline only that poti ndi Chichewa ndie zikuoneka ngati zosapatsa ulemu.
if Abraham and moses were not burned wat about us…lets follow their footsteps….
Vuto ndi lakuti kusukulu aphunzitsi anatiphunzitsa kuti Kuotcha = burn Not Cremation.
Nkuona tikuzimva udyo .

Munthu akaotcha munthuyo sanali wazikolo akufuna kunyamula mafupa wokha kupita nawo kwao

ma hindu kkklkkk
ma hindu kkklkkk
she was axrian pastor for goodness sake.y burn her remainings?

So abusa samapangidwa cremated?
achristu sitiotchana mr
Yah that’s not Christianity, we don’t practice cremation!!

kodi mesa anali abusa mayiwa?
Eya anali m’busa kuchipembedzo chawo
kodi mesa anali abusa mayiwa?
Eya anali m’busa kuchipembedzo chawo
kodi mesa anali abusa mayiwa?
So whats the connection
kodi mesa anali abusa mayiwa?
So whats the connection
Mmmm mot. Simumaziwa zot amwenye amawocha munthu akamwalira
Osati amwenye onse, koma omwe amatsatira chipembedzo chachi HINDU.
And the lady was a coloured.Her father was a white man and she was a Christian pastor. Maybe ndizomwe iwowo anasankha asanamwalire because creamation is not done by Hindus only or amwenye okha
Eyad ndkugwirizana NAzo
Its only hindu

R.I.P
R.I.P
.
.
Koma Ziliko Kumalawi Mpaka Kumuotcha
Koma Ziliko Kumalawi Mpaka Kumuotcha
Hahahaha MOTI SIMUMAZIWA ZOT AMWENYE MWAMBO WAWO NDIWOTERE KKKKK KOMA AMALAWI AAAAA

offcourse tommorrow is a brai day!
offcourse tommorrow is a brai day!
Adya
Adya
Ooooo kumwambaso akaotchedwa
Ooooo kumwambaso akaotchedwa
mmmmm tell us ndim’malawian or what? mpaka kuotcha,zoopsa izi ana kutali
Kkkkkkk tell ours et? Kkkkkk koma yaa xul ya Muluzi
kkkkkk ya mulimotsemo bola wamva, us = ours

Zachilendo kuno ku malawi kuno si kuindia

r i p
r i p
M’malawi muno zimenezo
M’malawi muno zimenezo
Paja kusiyana zipembezo eti??
Paja kusiyana zipembezo eti??
Oho zayambaso liti zootchanazo ,mpingo wanji?
Akuti Hinduism religion, zauchitsiru
kkkkkk
Kkkkkkkk
Her husband was an Indian. She was a christian pastor. But maybe ndizomwe iwowo anasankha asanamwalire because cremation is not only done by Hindus
Zautsiru koma zootchanazo zilibe ulemu
Kkkkkk ma Hindu awa zachamba bas

Ndiye akaiotcha akaidyera kuti?
Hahahahaha koma anthu ndiye mumaganizatu
Aaa nanga si ndi braai imeneyo bro
Amatenga phulusa Ku pang’ono kugawana pachibare pawo

awotche chifukwa ndi maChinese chani ehewu

Zayambikaso lit zootchanaz
Abusa akt anasankhiratu ali moyo
paja zimatengela church
Ok apo nf
Ok apo nde ndakuvan
koma analid mmalawi iyeyu?
anali wa mpingo wa chi hindu ameneyu ndye aka mwalira basi awotchedwe bas, phulusa ku phulusa.
eeee
She is Hindu that’s there culture
Komatu ankanena Halleluya halleluyah ku Comesa Hall kuja mai wa
Her husband was an Indian.She was a Christian pastor but maybe ndizomwe iwo ananena asanamwalire because cremation is not only done by Hindus.
Mbusa??? Ndeno amapanga zandale? Iiiii za ulendo uno