Thupi la Singh aliotcha mawa

437

Thupi la yemwe anali mtsogoleri wa chipani cha United Independence (UIP) mayi Hellen Singh aliotcha mawa ku gome la Sikh mu mzinda wa Blantyre.

Malinga ndi m’modzi wa ku banja lofedwa a Asante Masantche, thupi la a Singh lizatengedwa ku nyumba yachisoni ya College of Medicine (CoM) kupita ku holo ya COMESA komwe anthu azakhale akukhudza thupi la a Singh ndikupitiliza ndimwambo wamapemphero asanapite ku gome la Sikh komwe akaliotche.

Hellen Singh

Hellen Singh adatisiya dzulo.

Pakanali pano, Boma lati ndilokhuzidwa pa imfa ya mayi Singh yemwe amalimbikisa mfundo za demokalase kudzera mu chipani chawo cha UIP.

A Singh womwe amwalila ndi zaka 64 zakubadwa atisiya loweruka kuchipatala cha Adventist atadwala nthenda ya cancer.

Malemu Singh anali katswiri pa malonda ndipo anali ndi kampani yobweleketsa magalimoto yomwe imatchedwa kuti SS Rent a Car.

Kuphatikiza apo analiso ndi Singh Trust pamene iwo amachita ndale zao mu chipani cha UIP.

Mayi Singh asiya ana awiri.

Share.

437 Comments

 1. kod kuotchako kumalawiko ndizachilendo kuva kut maliro amaotcha, chilichonse mkumasalira bwanji pitani mukaone nokha komweko basi dats all

 2. kod kuotchako kumalawiko ndizachilendo kuva kut maliro amaotcha, chilichonse mkumasalira bwanji pitani mukaone nokha komweko basi dats all

 3. Clementation doesn’t matter your religious background, tribe, culture or national of your origin. It’s just another way of burrial. It helps to keep space in our already overcrowded cemeteries. It happens almost everywhere in the world.

 4. Clementation doesn’t matter your religious background, tribe, culture or national of your origin. It’s just another way of burrial. It helps to keep space in our already overcrowded cemeteries. It happens almost everywhere in the world.

 5. I hope it doesn’t pollute our innocent oxygen lol, just saying.
  Christians who follow JESUS CHRIST doesn’t believe that, imagine if it was the Culture of JESUS CHRIST, how could we be saved by His Blood.

  Imagine if the family of Lazarus believe in that, in which body could JESUS raised?

  Imagine if there were no bodies buried, after the Earthquake at JESUS CHRIST death which bodies could have been raised?

  I’m not judging any culture or religious, JESUS CHRIST followers have hope for resurrection after death. He had demonstrated that before, so we believe.

  • Of course it could have still been possible. Spirituality has no limitations and let alone Jesus christ. Even if he was killed and fed to crocodiles, he would have still ressurected. It all happened in spirit not human understanding

  • Exactly thus my point, how can you live with Spirit and call it Lazarus? When we talk Spirit, we talk of invisible, you can’t see it. It’s easy for you to say it, even Peter couldn’t believe that it was JESUS until Jesus said touch me, for the Ghost has not bones and flesh, don’t you see important of your shape in Resurrection?

   Anyway, we can talk about it but the fact remains none of JESUS CHRIST followers were burn when they die.I will follow JESUS CHRIST

   If JESUS CHRIST body was burn, and resurrect in Spirit, where could be the Salvation? Who could talk about His resurrection # Brother Esau Mwamwaya?

 6. I hope it doesn’t pollute our innocent oxygen lol, just saying.

 7. guys to burn dead body is not new.if she dead in JESUS she will be enjoying in the promised land .JESUS is always happy with this kind of death.

 8. guys to burn dead body is not new.if she dead in JESUS she will be enjoying in the promised land .JESUS is always happy with this kind of death.

 9. Mai Hellen Singh was a Ngoni by tribe from Ntcheu and also a Christian but am supprised today to hear all these issues that she’ll be burnt am confused!

 10. Mai Hellen Singh was a Ngoni by tribe from Ntcheu and also a Christian but am supprised today to hear all these issues that she’ll be burnt am confused!

 11. Ine sindikusutsana ndimwambo owotchana ayi izizilichomwechi chifukwa chamwabo wawo omwe amatsatila komanso ndibwino chifukwa akatelo ama server malo omanga nyumba ndiponso olima koma chohomwe chandikhudzaine ndifa mayiyu yemwe anayesetsa kuthandizapo pachitukuko chandale kuno kwathu mzimu wake uwuse muntendele

 12. Ine sindikusutsana ndimwambo owotchana ayi izizilichomwechi chifukwa chamwabo wawo omwe amatsatila komanso ndibwino chifukwa akatelo ama server malo omanga nyumba ndiponso olima koma chohomwe chandikhudzaine ndifa mayiyu yemwe anayesetsa kuthandizapo pachitukuko chandale kuno kwathu mzimu wake uwuse muntendele

 13. kkkkk ndekutitu ndiochimwa kwambila anthu amenewa ati mpaka kumaochedwa padziko lapansi mpanpano guyz ndizilangotu zimenezo

 14. kkkkk ndekutitu ndiochimwa kwambila anthu amenewa ati mpaka kumaochedwa padziko lapansi mpanpano guyz ndizilangotu zimenezo

 15. Koma tikawelenga baibulo palipo pamene anati munthu akafa aotchedwe?kapena winawake wochuluka nzeru anangoyambitsa zootchana ndi malamulo amulungu?

 16. Koma tikawelenga baibulo palipo pamene anati munthu akafa aotchedwe?kapena winawake wochuluka nzeru anangoyambitsa zootchana ndi malamulo amulungu?

 17. Mtembo ndi mtembo kuotcha or osaotcha palibe chingasinthe. Palibe mgwirizano pakati pa kutentha mtembo ndi chikhristu komaso palibe mgwirizano pakati poika mtembo kumanda kapena ayi. Kutentha mtembo ndi chikhalidwe, kuika mmandaso mchikhalidwe. Sikuti amatentha mitembo ndima Hindu okha.

  • Moreover she was a coloured not an Indian or asian.Her father was a white man and she was born and grew up in Malawi.

 18. Mtembo ndi mtembo kuotcha or osaotcha palibe chingasinthe. Palibe mgwirizano pakati pa kutentha mtembo ndi chikhristu komaso palibe mgwirizano pakati poika mtembo kumanda kapena ayi. Kutentha mtembo ndi chikhalidwe, kuika mmandaso mchikhalidwe. Sikuti amatentha mitembo ndima Hindu okha.

  • Moreover she was a coloured not an Indian or asian.Her father was a white man and she was born and grew up in Malawi.

 19. Yoo zootchana kodi?Alekeni ndi chikhalidwe chao komanso sizachilendo izi kuchitika bwanji nafenso kuno Ku Joni zathu akatisiya akatipatsa malo okumba manda timakumbunso mudzi pomwe eni ake sakumba mudzi aotchedwe basi phulusa litumizidwe ku India kwaoko abale akakhudze mmesa zimatero kwa amene musakudziwa Kathu tathauzo lake.

  • She wasn’t an Indian. She was a coloured, her father was a white man and she grew up in Malawi.Only her husband was an Indian.But indeed there’s no problem with cremating her body.Mwina ndizomwe anasankha iwowo mwini akanali moyo

 20. Yoo zootchana kodi?Alekeni ndi chikhalidwe chao komanso sizachilendo izi kuchitika bwanji nafenso kuno Ku Joni zathu akatisiya akatipatsa malo okumba manda timakumbunso mudzi pomwe eni ake sakumba mudzi aotchedwe basi phulusa litumizidwe ku India kwaoko abale akakhudze mmesa zimatero kwa amene musakudziwa Kathu tathauzo lake.

  • She wasn’t an Indian. She was a coloured, her father was a white man and she grew up in Malawi.Only her husband was an Indian.But indeed there’s no problem with cremating her body.Mwina ndizomwe anasankha iwowo mwini akanali moyo

 21. Mmmmm kma zikhulupililo zinazi abale,ungasiye nazo kupemphela mbambadi mpali agundani kumtenje. Munthu kusankha kukaotchedwa ukamwalila,kma chonsecho ankati aluleya aleluya mtchalichi kutsogolo kwa anthu?. Ngati siidali nzika ya mbadwa ya dzikoli, bwanji osangonyamula malirowo nkukaotchela kwawoko?. Ana ndi zidzukulu adzachite kudziwa kuti, munthuyu adaotchedwa kamba kachipembedzo?. Zandiopsya kwambiri ndisanamepo apa, chabwino ndimomwemo mwambi wa gulu gufe poti nchakonda mwini mulekele.

 22. Mmmmm kma zikhulupililo zinazi abale,ungasiye nazo kupemphela mbambadi mpali agundani kumtenje. Munthu kusankha kukaotchedwa ukamwalila,kma chonsecho ankati aluleya aleluya mtchalichi kutsogolo kwa anthu?. Ngati siidali nzika ya mbadwa ya dzikoli, bwanji osangonyamula malirowo nkukaotchela kwawoko?. Ana ndi zidzukulu adzachite kudziwa kuti, munthuyu adaotchedwa kamba kachipembedzo?. Zandiopsya kwambiri ndisanamepo apa, chabwino ndimomwemo mwambi wa gulu gufe poti nchakonda mwini mulekele.

 23. Ngati imanukhira nkhuku chithu chaching’ono ikamawotchedwa.ndiye kulibwanji munthu koma yaa! zizakhalakotu kumeneko.vuto tilikutari bwezi titakhala nawo pa mwambowo kuti tizamvere nawo kafungo ka munthu wowotchedwayo m’mene kamamvekera.

 24. Ngati imanukhira nkhuku chithu chaching’ono ikamawotchedwa.ndiye kulibwanji munthu koma yaa! zizakhalakotu kumeneko.vuto tilikutari bwezi titakhala nawo pa mwambowo kuti tizamvere nawo kafungo ka munthu wowotchedwayo m’mene kamamvekera.

 25. kunonso ku South Africa azungu amachita kuotcha.pulusa amaiika mu ka coffin kakang’ono then when the family have time amapita kukaimwaza phulusa ija ku mphili.ndimwambo ndithu enanu zisakudabwiseni

 26. kunonso ku South Africa azungu amachita kuotcha.pulusa amaiika mu ka coffin kakang’ono then when the family have time amapita kukaimwaza phulusa ija ku mphili.ndimwambo ndithu enanu zisakudabwiseni

 27. In India this is what they do,also in china and other parts of Asian Continent in Malawi Lilongwe and Limbe where Hindu,Sikhs communities live they also practice this, it is not new iam one of the witness of these.By the way if you follow their teachings even in Catholism if one wishes to be clemented they do so but under the wishes of the person in question like what Pastor Ellen has done,after all if one dies his/her body is no longer of use thus why when you burry a dead person thus the end of it.We all shall have new bodies after resurrection day so why worry?Come to think of somebody dies and crocodiles consumes the body?what do you think of his/her tomb will be?We shall all have new bodies for our bodies that we have now are all perishable and we need unperishable bodies i mean heavenly bodies.

 28. In India this is what they do,also in china and other parts of Asian Continent in Malawi Lilongwe and Limbe where Hindu,Sikhs communities live they also practice this, it is not new iam one of the witness of these.By the way if you follow their teachings even in Catholism if one wishes to be clemented they do so but under the wishes of the person in question like what Pastor Ellen has done,after all if one dies his/her body is no longer of use thus why when you burry a dead person thus the end of it.We all shall have new bodies after resurrection day so why worry?Come to think of somebody dies and crocodiles consumes the body?what do you think of his/her tomb will be?We shall all have new bodies for our bodies that we have now are all perishable and we need unperishable bodies i mean heavenly bodies.

 29. learn to understand and respect other people’s cultural views.this’ sympathetic to the party and any malawian for losing our productive political learders.may her sauls rest in peace!

 30. learn to understand and respect other people’s cultural views.this’ sympathetic to the party and any malawian for losing our productive political learders.may her sauls rest in peace!

 31. apart for kukhala mwenye Anthu achikuda or azungu amaotchedwanso ngati anali wachipembezo cha hindu ndipo palibe chilendo apo mwina kwa inu osayendanu ndiamene musakudxiwa zimenezo yendani muphunzile xool ina paja xool si class mokha ayi

 32. apart for kukhala mwenye Anthu achikuda or azungu amaotchedwanso ngati anali wachipembezo cha hindu ndipo palibe chilendo apo mwina kwa inu osayendanu ndiamene musakudxiwa zimenezo yendani muphunzile xool ina paja xool si class mokha ayi

  • The lady was a coloured.Her father was a white man and she was born and grew up in Malawi.Only her husband was an Indian

  • The lady was a coloured.Her father was a white man and she was born and grew up in Malawi.Only her husband was an Indian

 33. Guy why are we so negative on wishes of other people. This lady was a Indian its their culture. And even you burn, you bare, you fry whatsoever they is no difference she is dead. Why so fussy wakufa samva kuwawa

  • But its just burning. And need to look on over population growth. And the land is get small. Most of the land will be grave. In Europe its their culture. And this lady is Indian and its their culture.

  • And it saves money than to spend money now but when he/she was alive we didn’t. Easy to transport no need to hire aa car for the body. 10years to come trust me lot of people will be just doing that

  • The lady was a coloured,her father was a white man.Only her husband was an Indian.And cremation is not only done by Hindus or Asians only

  • One thing you need to know is that if every dead person has to be burned because of land problems then this burning process will be expensive too.

   Mudziko losowa nyama soya pieces amakwera mtengo.

  • It’s because tikamva kuti munthu waotchedwa ndiye kuti wavekedwa thayala ndi kumuthila petrol basi .

   Zootcha maliro zimachitika behind people’s back koma sizimafika mpaka kukhala headline mu news.

  • When Fidel Castro passed on one news headine on BBC was “Fidel’s corpse to be cremated on Saturday”And that’s the same with Mw 24’s headline only that poti ndi Chichewa ndie zikuoneka ngati zosapatsa ulemu.

 34. Guy why are we so negative on wishes of other people. This lady was a Indian its their culture. And even you burn, you bare, you fry whatsoever they is no difference she is dead. Why so fussy wakufa samva kuwawa

  • But its just burning. And need to look on over population growth. And the land is get small. Most of the land will be grave. In Europe its their culture. And this lady is Indian and its their culture.

  • And it saves money than to spend money now but when he/she was alive we didn’t. Easy to transport no need to hire aa car for the body. 10years to come trust me lot of people will be just doing that

  • The lady was a coloured,her father was a white man.Only her husband was an Indian.And cremation is not only done by Hindus or Asians only

  • One thing you need to know is that if every dead person has to be burned because of land problems then this burning process will be expensive too.

   Mudziko losowa nyama soya pieces amakwera mtengo.

  • It’s because tikamva kuti munthu waotchedwa ndiye kuti wavekedwa thayala ndi kumuthila petrol basi .

   Zootcha maliro zimachitika behind people’s back koma sizimafika mpaka kukhala headline mu news.

  • When Fidel Castro passed on one news headine on BBC was “Fidel’s corpse to be cremated on Saturday”And that’s the same with Mw 24’s headline only that poti ndi Chichewa ndie zikuoneka ngati zosapatsa ulemu.

%d bloggers like this: