Boma la Malawi lati likudziwa kuti anthu otsatila Mayi Joyce Banda ndiwo adalemba kalata yoti a Saulos Chilima atula pansi udindo.
Malinga ndi mneneri wa boma, a Nicolas Dausi, amene analinso mkulu wa u kazitape mu dziko lino, a boma ti akudziwa anthu amene adachita mtopola onama bodza kuti a Chilima anyanyala udindo wa wachiwili kwa mtsogoleri wa dziko lino.
“Mwanaaa, anthu ake tikuwadziwa adachita upandu umenewu,” adatero a Dausi pothilila ndemanga pa nkhaniyi.
“Ndipo anthu ake sikuti angabisale ayi,” adaonjezela chotelo. “Anthu amenewa ndi amene anathawa atangoluza zisankho zija, pano ayamba kufuna kudzetsa mpungwepungwe pakati pathu.”
Ngakhale a Dausi anakana kutchula dzina la anthuwa, anthu akuganiza kuti iwo amanena anthu a chipani chotsitsa cha Peoples’ (PP).
“Pakali pano sitikutchula mayina koma anthu amenewa ndithu anjatidwa ndi a Polisi ngakhale abisale motani,” anaopseza a Dausi.
Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Mayi Joyce Banda anabanduka atangogonja pa zisankho za 2014 ndipo iwo akhala akudumphadumpha ku mayiko a kunja.
A Dausi potchula kuti anthu adalemba kalatawo ndi otsatira Mayi Banda zapangitsa anthu kuona ngati akunena anthu a PP.
Clueless gafment led by clueless leader. shupit.
Bwanji nanga osawapereka kwa a police mayinawo?

hoo ok
hoo ok
Galusi
Galusi
Wachokabeeeee!!! Mwafotaaa!! Tiyamba Chathu chipani muchiope osati MCP yophwasukaphwasukayi mukudziwa kale inu a dausi

Omaliza ku Dpp ndi peter tiyese wina
Omaliza ku Dpp ndi peter tiyese wina
mwayamba kale mwayamba kaleee! kunjenjemeraaaaaa! yoswa hoyeeee Dr chilima woyeeeee.kumamvatu, president ndi professor.vice ndi Doctor.tulursani mbundeyo tiyione.mukodza

Dr.L.C+Jesus
Dr.L.C+Jesus
Zizindikiro za kutha kwa DPP
Zizindikiro za kutha kwa DPP
mbuzi dausi
mbuzi dausi
KD MNDAN ADZABWELEPTSE CHILUNGAMO M,MALAWI MUNO? NTHAWI YA AMULUZ AMAT ADAONONGA ZINTHU NDA AKAMUZU NDPO NTHAWI YA BINGU AMAT ADAONONGA ZINTHU NDI AMULUŽ NAWONSO A PP AMAT ADAONONGA ZINTHU NDI ABINGU.KD NDAN ANGABWERE MKUNENA CHILUNGAMO NANGA NDAN ADZABWERETSE CHHLUNGAMO?

PP they must shut their mouth against the gvt

adpp musatitethese mitu milandu bas
adpp musatitethese mitu milandu bas
Madness Is Real
Madness Is Real
Wachekula nimulala wapumule daus nkhope yapanga utatavu esh daus kapume

Kicks of a dying horse
Kicks of a dying horse
Nanga sionse anali zitsilu coz once
Nanga sionse anali zitsilu coz once
Kod aDPP muzasia lit kulankhula za PP,,mufuna kutukwanidwa et..? Mesa mwat zotukwana ai,, CHLIMA nd PP zkugwrzana p@.? Zopusa…
No sense, ,,,,,,,,chalaka bakha,,,kkkkkk,nkhuku siyingatore,,,,,kkk

Mmmm madala awadi akula kkkk PP ziwakhudza bwanji anthu akuba inu nonse a dpp

Dausi ndi nzibambo mmodzi opusa ku Malawi ndipo mutu wake sumagwira nchito bwinobwino

Abale palibe angatule pandora udindo wa u vp, musanamizidwe no matter the storm can be. Analephela bwanji joyce, chilupha zikuonekelatu kuti ndi bingu pali great disagreements? Ndiye apa pali chani?

Analemba ndi a dpp
plan yao ndiyoti mpando usazapite kumpoto or pakati
muona akafuna kusankha asankha wakumwela

Analemba ndi Dausi asaname ameneyo m’malo motchula dzina akutchula chipani. Kulimbana ndi PP lero kuli bwanji pa campaign.
Nenani chilungamo a Dausi. Funso: mwapeza bwanji nsanga awawa? Nanga omwe adayatsa office ya za malimidwe, nanga opha Njauju. Aaah m’dala iwe uli shit!!
Tikifuna chilungamo M’malawi osati kulozana zala.

I’ve to say nothing …..mene mungapangile ndimomo……ine nilibe problem kkkk
Kkkkkkk paja inu si andale
kkkkk anem nkhani za #kumalawi sizimatha……

Thats malawi politics kumangoipitsirani mbili basi fuckoff

Is this a fact or fiction? If this so why then don’t you arrest the culprits

stupid Dausi
stupid Dausi
Mungolimbana ndi PP ngati ndiyomweikulamula? Dausi wakula,ndikalelija nzeruzikucepa,akawerengenso ma buku.kkkkkkk

Kkkkkk Ali ndiumboni wanji Dausiyo kuti adalemba kalata ndi A PP? nde kuti anali onse atengedwe akafunsidwe mafunso

Inu a DPP mwagwilitsa ntchito njira yanji kuti mupeze amene adalemba kalata?komanso amene wapezekayo dzina lake ndindani? Bwanji mugwilitse ntchito njira yomweyo popeza amene adapha Njaunju,chasowa,mbendera komanso amene adaba ndalama zogura chimanga komanso cash gate mu nthawi ya ulamuliro wa DPP ?osamakondera popanga zinthu

Kodi mwayamba zimenezi mukuona ngati ife ana eti?.zotchula chipanizo mukunama,tchulani maina aanthu omwe amagwira ntchito yopha anzao,chasowa,njauju,matafale,anthu odulidwa mitu kumitundu ndi ena ambiri mizimu yawo ikufuna chilungamo!!!!!Kodi mukuchitapo chani inu azachilungamo?

Daus sadayankhuleko za nzeru…ngat nduna …m’muuze pa ambwiyache

Pp did not help malawians. Those pipo wants to dress their pockets through malawi gorverment
Dpp is awaste government

Kodi chilima wasiya udindo liti?
Kodi chilima wasiya udindo liti?
Kape Daus
Kape Daus
Kaya Ndemanga Zanu Izo Ndizingowelenga Yabwino Ndizingopanga Like Bass

Ati kudanitsa anthu za Zii
Ati kudanitsa anthu za Zii
zimenezo ndiye ndale zaku malawi zolonda mapazi ngat ukuweta ng’ombe.

Musatinamize ife, munthuyu analemba yekha kalata tamufunseni akuuzeni bwino.

The problem is ,there is no new blood in politics that’s why otsutsa olamura amapanga zithu zoziwa okha even Ku football association of Malawi zimangofanana

ndale za pa malawi zimenezo kudana ndi ma vice presdent mukangowina pa elections.osangopanga kut kusamakhale vice presdent bwanji?.you are now looking for your related person kut azayimile presdent.mwa jaila heavy.mwawatola amalawi.kaya zioneka.

Dausi mutu mwake muli mamina sure
Dausi mutu mwake muli mamina sure
Nkhani zandale ndizovuta kuyambira kale nde apa osavutika ndikutaya nthawi kumatosanatosana…end zandale kulibeko phindu lililonse tingapezeko…tikhale bzy ndizomwe zingatukule moyo wathu watsiku nditsiku

Olemba kalata wapezeka kale,
Okupha njauju,chasowa,ma albinos,
Chaponda simunamupezebe kodi
Dpp govt,total disgrâce,total failure
You have failed us malawians
Olemba kalata wapezeka kale,
Okupha njauju,chasowa,ma albinos,
Chaponda simunamupezebe kodi
Dpp govt,total disgrâce,total failure
You have failed us malawians
baseless!!
baseless!!
Zayamba kuululika.
Zayamba kuululika.
Anthu Ongokhutitsa Zimimba Zawo Awa Olimbana Mzaziiiii Mmalo Molimbana Ndicaponda Ndi Pitala Mbava Atsizinamtole Shme 2 U!!!
Dot worry naweso ugoyamba kumbako. Mupindulanjji ndikumalimbana ndi chaponda? Just work hard.
enock kunganiza mopelewela kumeneko

Kkkkkkkkkk
Kkkkkkkkkk
Kape iwe
Kape iwe
Thats what I say from the beginning angofuna kuipisirana mbiri politics in Malawi esh

mwiniwa wake chilima sakulankhula bwanji? ndie kt akudziwa kanthu.

Nanga ndani anapha Njauju? Sanapezeke mpaka pano? Awa mwaapeza bwanji mnsanga chonchi? Tikufuna mnene maina aanthu osatiniza zoti PP. PP ndi munthu?

Kkkkkk zoona
Kkkkkk zoona
Nkhani zopanda pake ngati izi zithandiza chani kwa Amalawi????
Etidi? No wonder Malawi is de poorest country.

Ndale zaku Malawi zomangolimbana ndi ma vice president

A dausi kusilila azawo
A dausi kusilila azawo
ife khani tinayidziwa kale amamene analemna tikwaziwa and mapulani awo tukwaziwa sizinati zikubwela chilima chililma chilima ndaitana kangati musaxati sindinanene
kkkkkkkk auze mwina sakuziwa.

ZANDALEZ
KUZITENGERA
TITHAKUGAWIKANA
POYELAYERA.
AZIPAN AMENEWA
AMADZIWANA
ASAMATIPUSITSE
IFE SI ANAY.
ZANDALEZ
KUZITENGERA
TITHAKUGAWIKANA
POYELAYERA.
AZIPAN AMENEWA
AMADZIWANA
ASAMATIPUSITSE
IFE SI ANAY.
Mukudziwa?. Ndindani tiuzeni
Mukudziwa?. Ndindani tiuzeni
DAUS KAPE
DAUS KAPE
PP is a party (Group of people) we want a name of a person… Mwayiwala kuti paja Cassim Chilumpha munayamba chonchi?????

Adali kazitape wa kamuzu mwaiwala@ Dausi

bola kaliyati amwene osati mamulumudzanawa

Nangati kuli minister opanda nzeru nde ndi mr dausi zomwe akunena apa ndizopanda nzeru. Mwamusemera zinyawu nonkha kuti mwina mupeze chifukwa chomuchotsela Dr saulosi chilima. Bola nthawi ya Patricia kaliate Ali minister of information amayankha zogwila ntima. Osati mr dausi mumanja mwao muli magazi amcp.
Tisaiwale imfa ya njaunju, chasowa, Mbendera, ndi ena ambiri kodi inali nthawi ya Mcp?
Ma comments a chilungamo ngati awa ndi amene akuti mukutukwana pa social media, kikkkkkkk. Andale kudana ndi chilungamo
Magazi A dpp Osati Mcp

Amagidwe basi komanso mzimayi uja abwera azayakhe milandu.
mulandu wanji mukuziwa inuo. muklepera kumanga mbava zilikunozi.
A chilango khwezera,,, nanga joji chaponda mum,manga liti popeza ma umboni onse alipo??????
Why not kunjata chaponda kaye?
Amange kaye chaponda wakuba chimanga

umboni ulipo? tiuone and expose the culprits please!!

ife tamva kt kalata yalembedwa nd….
ife tamva kt kalata yalembedwa nd….
Kkkkkkk Ben Phiri NDI WA pp?
Kkkkkkk Ben Phiri NDI WA pp?
When dausi speaks such rubbish, you know he’s the mastermind behind such evil. Ok, how will that impact the nation anyway?

Ndale ku malawi
Ndale ku malawi
Beni is pp?
Kkkkkkkkk inenso kudabwatu
Beni is pp?
Kkkkkkkkk inenso kudabwatu
DPP iyi yatha basi..Ikulimbana ndi anthu a phee,kkkkkk!

sometimes i like watching fools of dausi making themselves how this affect JB and his party ?

Rubbish!!!!!