Nkhani ya kuba kwa chimanga idakalibe m’bwalo ngakhale mkulu amene anali induna yoona za malimidwe a George Chaponda adachotsedwa.
Mkulu wina ogwila ntchito ku ADMARC mu boma la Nsanje, watsekeledwa ataponda matumba a chimanga okwana 107.
Matumbawa akuikidwa pa mtengo okwana K1.6 Miliyoni.
Malinga ndi a polisi a mu boma la Nsanje, iwo anjata a Matthias Muyatso a zaka 26 powaganizila kuti adachita za u Chaponda ndi matumba achimangawa.
Malinga ndi mneneri wa a Polisi mu boma la Nsanje, a Agness Zalakoma, Bambo Muyatso adapezeka ndi matumba 107 olemela 50Kg thumba lililonse pamene a Polisi adachita chipikisheni kwa ogwila ntchito pa ADMARC ya Tengani pofuna kulondola umo matumba a chimanga adayendela.
“Pa chipikisheni chathu, tinapeza kuti bamboo Muyatso anali kusunga matumba 107,” adatelo a Zalakoma.
A Muyatso agwidwa patangotha ma sabata ochepa mkulu wina ogwila pa ADMARC ya pa Nsanje atagwidwa naye ndi matumba a chimanga okuba.
Kkkkkk..amatengela bambo wao
Adamutuma nd aCHAPONDA omwewo,,
zisiru zokuba, mbava, agalu inu, nkhope zonyasazo! u r more lyke de cocloches,afinye,achule,de scorpions, mwatikwana mbuz za wan2 inu! we wil se in 2019!!!!
kkkkkkkk kkkkkk musati seketse ogwila ku adimack ndepali vuto mesa mbuzi imadya pomwe ayimangilila chaponda anaba thrack yose koma n.yeyo amakhala ali ku ofes kwake nde what about oti akumapisa thumba la chimanga alinalo pafupi ndetikava zoti mwawamanga chaponda ali nmadzi nkhani yachaponda osati kumatinamiza kuti ili nkati munaotcha ma pepala ose paja ndemukawa manga basop kunyumba kwachaponda tudziwako ivuta anthu oipa inu kazibani inde guys anthu amaba lole yose ndeinu ongotapako palibe bvuto
Kkkkkklkkkkkkkk
Kkkkkkk achita uchaponda koma malawi24 mumatha
Nthawi ya kamuzu kudalibe nyasi ngati izi
kkkkkkkkkk chaponda maize ambuye!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!1
Kkkkkkķ…koma. …
Akalowe
me wonder muma office mukumangokhala nkhalamba anthu oti anagonja kalekale more over analekeza std 5 cholinga chanu ndikuba mbava inu km chonsecho we gat well educated people to handle those offices km jxt because ndi achinyamata you ignore them ife tatopa munayambila kunene kt achinyamata ndi tsogolo LA mmawa kodi mmawalo lizafika liti nonsense chonsecho ana anu munawapezera ntchito mmakampani ambilimbili mbava za anthu inu ndipo namalenga akuoneni mbava inu
Nde mwati achita uchani? Sindinamvetse bwino pamenepo
Tazilemban nkhan zomanga Malawi inu not kupasula aaaaa-uchaponda ndiye zichan?
Ine. Lobeni.Twaliki
.ndimachokela. kumalawi. Boma. Lamangochi. Kongomwa. Tiredingi. Seta. Banja. Kwamusama. VG. Mwana. Wanga. Sifati.alibwanji
.kasi.wanga
Lafunesi. Sayidi. Ulibwanji. Ndikufuna.galimoto
.amene. alinayo.andisiwise.ndikufuna
Yogula.nambala
Yanga. Ndi. 27833426220
Ayimbe.ngati.mulipafupi.ndikumangochi.pitani.kwakasiwanga
Kwamusa. V. G.kapena.awayimbile
Foni.0881021692.ndiyine
.bambo. sifati.kapena.kuti.Lobeni
Twaliki. Ndimachokela.kukongomwa
Kito. V. G. Ndiyine.amene.ndikufuna
Galimotoyo..sikomo. amalawi. Nose
Mulungu akulangeni mbava inu mkudzunza anthu akwathu
Chapondalogy
ikanati inkhale subject ku xul ikanakhala chani
Induna ?
Dpp ndi choncho ikazangowinaso 2019 tili pa mavuto oopsa.
Achita uchani?
Sibwino. Kuba. Ngatindiyinu. Wakuba.bwelani
.kuno. kujoni. Mube. Malandi. Osati. Mulimbane. Ndi. Makwacha. Mubwele. Kuno. Kuechika. Nyumba. Yamafumu. Okuba
Kusiyana ndi kuti chizingokhala kenako mumvele hiii!! Chawonongeka chonse kapena kuwotchedwa kumene. Amalawi?
Si nanga powona kuti ambuyawo sanamangidwe. Basi aliyense azingoba. Tsopano ife mukutiuza kuti titani
Kkkkkkkk koma zinazi
Like father like son, czachilendo.
m’lomwe sangamange m’lomwe m’zake.its apart of trick
Tizingobangunga basi
Zinthu Zili Bwino Pamenepo.
Malawi wasopano siwakare ayi wasopano kumango khalira kuba basi
Ndiye tisanve kuti mwawamanga cz nkhani za chimanga mulibe bwaalo lomwe limaweluza nkhani ngati zimenezi muno mmalawi.
kkkk akulu mwaganiza bwanji
Cz ena anaononganso chimanga cha boma koma akusangalalabe kwao alibe chomwe chikuchitika
Kkkk kungot kuba chimanga smulandu kwathu kuno…..
kkkkkkk ” U CHAPONDA” asaaaah
umphawi ku malawi wanyanya