Police in Neno district have arrested 22 year-old Linly Nkomazinja for killing her husband over family disagreements.
Neno Police Public Relations Officer Raphael Kaliati confirmed the arrest of the woman who was apprehended by villagers and later handed to the police.
According to Kaliati, on 22nd February quarrel broke out between the two over family issues which resulted into a fight.
During the fight, the woman took an unspecified object and stabbed the husband on the chest before running away.
In the morning, the husband was taken to Nsambe Health Centre where he was pronounced dead upon arrival.
Postmortem by a doctor at Neno District Hospital doctor indicated that the death was due to severe blood loss secondary to aortic puncture.
Meanwhile Nkomazinja is in police custody and is expected to answer murder charge contrary to section 209 of the penal code.
Linly Nkomazinja and the deceased Leckson Mtima come from Kweneza Village Traditional Authority Dambe in Neno District.
asiyileni mabanjawo anthu okhwima nzeru!!bola ine ndili single
Mkazi ndi mfiti amawoneka ngati wabwino koma amasitha#nayenso amphedwe basi osaipondeledza nkhani imeneye
Azimayi mukuonjeza mumatenga mwamuna ngati munamugula nanji akubereketseni mwana eeer
WOW I THINK SHE IS MUCH MADNESS COZ SHE NEVER THINK BEFORE THE EFFECT THAT COMES AFTER TAKING A KNIFE azake ali ku joz olimba mtima maliro asaiyike amudyetse poti amafuna nyama muthutu chingakhale chitsilu chili ndimwini wake
Nthawi ikakwanayakwana
Sometimes its better to be single
Free her it was self defense, he was beating on her,
22 yrs old?????
Mai woipa mtima kwambiri
Akatuluka kundendeko abwere ku jon azinzake ali ku diplomat hotel kugulitsa katundu
Instead of getting support from wife, she turns out to be an opponent! It was not true relationship of wife and husband but it was unity for sex and money. Violence is baby of such families.
EISH so bad mmmm
Tiwone ngati mabugwe alowepo
Mmmm lamulo ligwile tchito basi
Zakomera mbuzi ugunda galu ukhala galu imphani
mzimayi ndi munthu wachifundo kwambiri mpaka pamenepo?
Mkazio ndi hule anamupeza akunyegetsa
Zachison kwabas
Eeeh…zosakhala bwino
Whatever inalingozi koma zikuchitakuonetsa kuti lupanga lomwe ananyamula mission inalikupha, naye aphedwe kuti azmayi antima otelewu aphunzilepo
That’s too bad
TOO BAD.OSANGOGAWANA ZIDA BWANJI.
I expect mabungwe okondela azimaiwa to act now.Tidziwe nawo meaning ya gender…..50:50der
Anapusa chanundu wanji kut mupaka nkaz amuphe. Fiti yaykulu ndi nkazidi ndasimikiza sopano
Addi Jampa Chimpeni, adha aaaaa kkkkkkk, musandiseketse pilizi
nanga kumangoti nkhaza kwa a zimayi, iz sinkhaza kwa azibambo?
Kusaupeza mtima mapeto
NDE abambowo amwalira?
Ngat watopa umangosia skut ukumangapo kapena kuphedwa
What was that that cost the life of person that was difficult to discuss you vicious woman?
Walakwitsa
Ndipo mzimai ameneyu ngopusa kwambiri.iyeyo ngati anaona kuti banja lao sakugwilizana anakangomuchokera mwamuna yo.wapanga apawu nduuchitsiru.aphedwe basi nae
amabungwe aja mumakondela kwambili lelotu ndizo mubwele poyelapa mayi kupha bambo mutu wa banja hhhaaa mpamene iye amathandiza ana ake komazo ziyiwo wokhawo aphedwawo ayi azimayi akuchita khanza mmabanjamu nangazi akhala akwachemelela mabungwe azimuna akunkhuchumulidwa kumalo obizika ndazimayi koma zimudzamfa mabwungwe akutokota kumangozimfela pa zammaboma pa MBC RADIO 2 FM koma mabungwe ali chete lelo ndi izi zatinyaza kwambili amunafe kobazi
IWE HOW CAN YOU KILL YOUR HUSBAND NOW WHO WILL FUCK YOU
tose tizafandithu komano osamate
Ndingokhala single eesh!!
Mkazi Kupha Mwamuna Ndiyekuti Chilipo Chifukwa Chachikulu,amuna Ena Amawonjeza Kumenya,amaziteteza Amenewo
kain atapha abel yehova sananene kuti kain aphedweso sonoinu azanga mphavuyi mukuyitengakuti?
Kumudziwa Kain yo Nkulinga kupita ku tChalichi kapena kukhala ndi Baibulo, ena apa za mulungu anaziyiwala
Makwatira kwatira, a chimwene Chimkazi chodziwa kupanda mpaka kuphelatu mwamuna shaaa! Zooopsya zedi.
…. When kamuzu came, NENO pple were naked, but that nakedness is still in some people’s minds until now……
Vuto lokwatila Mahule ndilomweli Mayina ngati awa ndi aku Bar
mamuna ameneyu ndikape kuphedwa ndimkazi zoona
Aaaaah Mirriam don’t provoke me ocky? Life lost anywhere is a sad day for Humanity. R I P
ooh
Zosakhala Bwino
apatu ndiye shalia ija inafunika ndithu, tichite bwanji??
women ar mo dangerous than men these days…
Devil on work
Akanakhala kuti waphedwayo ndi mzimayi mukanamva kuti anduna a za gender athamangila konko, komanso amabungwe bwenzi atayamba kale kulongolola ma wailesi.
Zachoka kuno ku Zambia zabwera kumeneko eti? Chaka chatha akazi apha kwambiri azimuna awo powabaya ndi mpeni komanso kuwaombera ndi mfuti.
Mishana ine sindikwatila ada
Palibe zoti amangidwe azikadyanso nsima yochokera misonkho yathu naye aphedwe basi azikafusana bwino za nkhani yaoyo. Mkazi oyipa eshiii
Yho!khohlakele la nkazana funeka uhambe straight ethrongoeni
we need such a persn 2b our leaders so dat all maizegate personels must b eliminated 4rm our poor country
Komatu
Azimayiso akupangakhaza pa banja bvutotimango ndilakuti azimayi amawatengangati ofoka sangapange khaza
I already lost 2 kj just trying to read what you wrote. No Panctuation Marks Eish
??????????? zochisoni????????????
Nkhnza kwa abambo? Ok
Nonse mukuti amangidwe akakhale moyo wake onse kundende ndinu opusa. Azikadya nsima yamitsonkho yathu daily mzake ali mmanda. Ameneyo aphedweso basi thats enough.
Kkkkkkkkkkk i koma zikolino ok
Kkkkkkkkkkk i koma zikolino ok
Nanga ndalama zathu zizithera pa anthu akupha
Don’t pay evil for evil.
tsoka okhetsa mwanzi
n’chiyan kod amalawi? life imprisonment needed
Amuna a masiku ano kumenya udyo akazi..mwina it was for the self defence mwatsoka wafa! Koma zooopsa
Ngat mkazi wapha mwamuna nde kuti amamenya ndindan pamenepo?
Simukudziwa comwe ndutanthauza.
Kodi adachotsa lamulo loti opha mzake aphedwe ndi ndani? Lamulo limene lija libwerere anthu sakulabada zochotsa miyoyo ya anzawo. Wina wafa wina kukamuika kundende uku mkukondera nayeso muzingeniiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii akakambirane nkhani yawoyi
Komanso chopweteka kundendeko sikuti amakhala moyowakeonse ayi amantulusa bola ndalama eshiiii
Lamulo limene lija lilipo kma ma court samapeleka.
Amangidwe basi ndipo akakhale moyo wake onse kundendeko
paja amati abambo ndiomwe amapanga chipongwe azimayi nanga apa mukuti bwaa